Hon Suleman Vs Mr Sambo: Interview Ndi Chimwemwe Magazi

  Рет қаралды 26,808

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

On Nyasa VoiceBox, Honourable Sameer Suleman engaged the NRB Principal Secretary in a discussion with Chimwemwe Mangazi about the issue of Malawi National IDs being stored in a warehouse in Kanengo, Lilongwe.
Pa Nyasa VoiceBox, olemekezeka a Sameer Suleman adacheza ndi mlembi wamkulu wa NRB pokambitsirana za nkhani ya zitupa za dziko la Malawi zomwe zasungidwa kumalo osungira katundu ku Kanengo mu mzinda wa Lilongwe.
#malawi

Пікірлер: 269
@MagretKamwendo-o8b
@MagretKamwendo-o8b 13 сағат бұрын
Mr Sulaiman well done we need more people like you osawopa osatopa osawfoka Mr Sulaiman
@WysonChilonga
@WysonChilonga 20 сағат бұрын
Sambo anangofunika kumpatsa makofi basi akuona ngati ndiife mbuli eti 😢
@maxwellmajawa6091
@maxwellmajawa6091 15 сағат бұрын
Always Mr NRB amayakha zosephana ndi zomwe zikufusidwa,have listened to him several interviews,zomwe akunena apa zotsiyana
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 16 сағат бұрын
Sulemani....osazaderele.....ayi Anthu akusowa ma cad........iwowo akugowasunga ....why....afuna kubera... osaopa osatopa osafooka 💪
@HessiLimani-n2o
@HessiLimani-n2o 16 сағат бұрын
Big up mr sulemani
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 23 сағат бұрын
Awa akuziluma okha kosungira katundu aikako bwanji mpaka akaika ma computer office table why anthu Inu somunati mulungu akuikanidi poyera somunati,it's my prayer kuti muchitedi manyazi.
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 11 сағат бұрын
A Sambo ndinu munthu wa bodza kwambiri mukupangazi ndiupandu mukuononga dziko lanthu mavote mukuberadi musakanee ayi... Koyamba mu history ya malawi mpaka mukapanga ku ja🙌
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 14 сағат бұрын
It doesnt make sense ngati ma khadi akucjokera kunja to the ware house how come kukupezeka a lilongwe okha Okha? Nanga ma gadgets akutaniko ku ware house instead of kwa DC? Is warehousing processing? Futseki NRB
@MichaelBefore
@MichaelBefore 18 сағат бұрын
Mr sambo mukuchita kuonekelatu kuti mbalumezanu ndi phala lenileni ndipo mwagwidwa apapa mbava zachabechabe mumangidwa chaka chikubwelachi mudzanyela tudzi aphwanga
@YusufGafa-s3j
@YusufGafa-s3j 15 сағат бұрын
Bwana nsambo ngati adakulengani ndi mulungu chilungamo chidzakutsatani ndithu tsiku likubwela
@ManfredNakhuba
@ManfredNakhuba 17 сағат бұрын
Amene akumugwirirsa ntchito Sambo akumulakwira kwambiri 😢mmmmm a Sambo mukuyankhula zosamveka sure
@KondwaniZivale
@KondwaniZivale Сағат бұрын
Thanzi likuvutanso mbali imenei kapena sindikuona bwino 😎😎😎
@ConexKamulole-be5bp
@ConexKamulole-be5bp Сағат бұрын
Bwana wamkulu mr Sambo mukufuna muthandawuze kuti ma warehouse a NRB ali busy moti simunga kwan e ma ID awanthu a😜🧐🧐kumalawi ndiye ndichifukwa chani mumayamba bungwe limeneli 😂😂😂😂😂😂😂😭😭😭😭😭😭😭🙃🙃🙃
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 18 сағат бұрын
Chiphatso ndi ukapolo kwa anthu achikuda..sisitimu yanu ndiyolakwika.musindikiza bwanji national ID mdziko la ena.
@esterechamba9343
@esterechamba9343 12 сағат бұрын
Pamenepo??????
@MosesNgombeyayera-tc3ru
@MosesNgombeyayera-tc3ru 15 сағат бұрын
All these warehouses in Lilongwe what's the point of sorting cards in nfra warehouse nanga Ku mpoto akuwerengera kuti?
@watsonmhango8794
@watsonmhango8794 6 сағат бұрын
Transparency apa palibepo akunanama Sambo ndi wakuba😅😅😅😅😅
@P.Bilali
@P.Bilali 2 сағат бұрын
Kodi asambowa zonse akuyankhulazi zikugwirizana koma😂😂😂
@YusufMtendere
@YusufMtendere 17 сағат бұрын
Kumangidwa Suleiman wina afa
@HerlbertKaalis
@HerlbertKaalis 17 сағат бұрын
Very good Suleman kuganidza bho
@miriammvanda3404
@miriammvanda3404 14 сағат бұрын
zitheka bwanji Kupezeka a lilongwe okha aaa uyu ndikatakwe zosaveka
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 12 сағат бұрын
Zaka zonsenzi zimayenda bwino Koma ulamuliro uwu chilichonse chinasintha Anthuwa alibe pabwino pot munthu utha kunena kuti bolamkoni aka?😭😭😭😭😭
@PhungulaAyanda-h4c
@PhungulaAyanda-h4c 12 сағат бұрын
Zomwe mukuyakha NRB sizikugwilizana
@IvyChithyoka
@IvyChithyoka 17 сағат бұрын
Eeeedi ife a kumwera ndife atsiru.koma musaiwale ndife a Malawi big!!!!!
@georgesmart3791
@georgesmart3791 10 сағат бұрын
Well done Suleman..❤❤
@Spaw-BTheGogoBoy
@Spaw-BTheGogoBoy 17 сағат бұрын
NRB KUYALUKA kwamtundu wanji kumeneko
@StanleyChamasowa
@StanleyChamasowa 6 сағат бұрын
Ku Lilongwe kulibe office ya DC??
@farmupmalawi
@farmupmalawi 13 сағат бұрын
Ine chiphatso changa kuti chitheke ndinali pilau 40 pin +transport
@AbdulIbrahim-b6v
@AbdulIbrahim-b6v 3 сағат бұрын
A sambo vomelezani pomwe palakwika Lilongwe is national head of tale center so anything that the do must have been noted to all the political party in advance before moved to a private place like ku malo a chimanga pomwe muli ndi good big offices at MEC
@RodneyTomato
@RodneyTomato 16 сағат бұрын
Suleman respect OSAOPA OSAFOKA OSATOPA
@AbdulMmadimwanyalisi
@AbdulMmadimwanyalisi 4 сағат бұрын
NRB,ili limodzi ndi mcp ,ndipo ili sibungwe loyima palokha ayi.ili ndi bungwe La mcp .
15 сағат бұрын
Mr Suleman you big man
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 14 сағат бұрын
NRB Mukugwila tchito mopusa kwambiri 😊😊😊😊
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx 3 сағат бұрын
Ndipo Selemani ndimachine kwambiri uyu ndimuthu
@GibsonKasabola
@GibsonKasabola 3 сағат бұрын
Chifukwa chani a chimwendo banda akumayakhila a NRB? Sambo ndiwe wa bodza akumakutuma a MCP iwe
@SydneyKhakona
@SydneyKhakona 5 сағат бұрын
Ine ndie palibe angandilese kumvera bakili muluzi tv
@AbdulIbrahim-b6v
@AbdulIbrahim-b6v 3 сағат бұрын
A sambo thulani pasi udindo apa mwatondeka chifukwa mukuyimila mbali and on matters wes this is first time NRB use Admarc places
@ThomasMaulana-u4p
@ThomasMaulana-u4p 20 сағат бұрын
Sambo pokhapo walephera kuyankha funso lomaliza la Suleman, zaonetseratu kuti you are hiding something,,, mwachidule ndiwe wa MCP, pafunika mukatuluka m'boma ukaseweze kumaula.
@MfumuNgwenya
@MfumuNgwenya 13 сағат бұрын
Katole eeeeeh😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 18 сағат бұрын
Suleman big man 100%❤
@user-mx7oj1vx3l
@user-mx7oj1vx3l 15 сағат бұрын
Koma Boma la france ndiloyipa kwambriri yomatsindikiza ma ID aku Lilongwe wokha wokha basi dziko lonse la Malawi 😮😢shem on you! ndi mabodza ako wopanda nawo manyazi😅
@EmmanuelPharaoh
@EmmanuelPharaoh 14 сағат бұрын
Ndpo inu mmmhhh😢
@TelezaNtodwa
@TelezaNtodwa 12 сағат бұрын
Anthu aline ma card Iwo akungowasunga bwanji?
@MfumuNgwenya
@MfumuNgwenya 13 сағат бұрын
Nsambo wapanikizka ndi mafuso 🤣🤣😂 bodza likuonekeratu😂
@GibsonKasabola
@GibsonKasabola 3 сағат бұрын
A sambowo avomeleze kuti ndi a MCP asatinamize
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 18 сағат бұрын
Ngati warehouse ngati amatha kumasungirako mankhwala ..Does that means they can do packaging at warehouse
@TruthReigns6
@TruthReigns6 11 сағат бұрын
Ma ID asochera bwanji and yet ukoko akuti ama sorter ko ma iD wo?
@StevenCatherineLazaro
@StevenCatherineLazaro 15 сағат бұрын
Iweyo samba ukungwilisidwa chito molakwika pleas muziwe kuti zizukulu za ana Anu mukuziyika pa moto pleas muzilingaliya songolo ya Malawi
@ChiccoTueenarNJAYA-Artist
@ChiccoTueenarNJAYA-Artist 15 сағат бұрын
Sambo should remember this is a world
@joebrown1158
@joebrown1158 3 сағат бұрын
Mutu wankhani apa mwa guidance.
@TonyMhone
@TonyMhone Сағат бұрын
Uyu Amati Sambo uyu Koma akutenga a Malawife Ngati ciani? Mbuli kapena anthu a nzeru zawo. Iiiiiiiii zotsakhala bwino idzi. Mpaka kukhokwe yosungira chimanga kwasanduka kusungira ma ID mmmhuuu!!!
@JaphronChiwala
@JaphronChiwala 22 сағат бұрын
Warehouse ndi kosungira katundu,why kupezekako ma table,machine zimafunako chani
@happyluhanga3387
@happyluhanga3387 21 сағат бұрын
Nde waphulapo chani
@happyluhanga3387
@happyluhanga3387 21 сағат бұрын
.. Ndiwe mbuli iwe
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 18 сағат бұрын
Koma gyz umbuli ndi matenda zoona, moti mwakuliramo mwalembazi ndi zoona
@esterechamba9343
@esterechamba9343 12 сағат бұрын
Bambo sulemani go deeper for this issue akutitola asambo pamodzi ndi chipani cha MCP
@MarryMartin-z6u
@MarryMartin-z6u 18 сағат бұрын
Big up suleman
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx 3 сағат бұрын
Ndipo sambo akutengenga ngat ndife ana ake chisili chimenechi kwambiri changoda chilibe zeru
@JovitastoloBridane
@JovitastoloBridane 9 сағат бұрын
Inu ataimus pankhwani zofunika kwambili ngati izizi Muzipereka atolankhani odzipereka pomafunsa mafunso nsambo pantumbo pamako
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 14 сағат бұрын
Koma ndizowona kuti mwapezeka ku warehouse ya chimanga komanso MA computer koma mkumati ndizabodza???? Eeeeeee!!!!! Koma popeza tilibe police ndi MA khothi zoyenera cz uwu ndi mulandu and mulanduwu kudikira vote yanga 2025 cz ndi nthawi yomwe chilungamo chidzapezeke iya😢😢😢😢😢
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 8 сағат бұрын
Inu palibe ca mzeru ciliconse angatiuze mwana wa cikangawayi apapa a sulemani ndi azanu mwagwila wakuba.Mcp ndi yakuba panyoo pake nsambo ndi anabelo.
@EstherCement-bo7ul
@EstherCement-bo7ul 4 сағат бұрын
Kodi a NRB mulibe ware house yanu
@MichaelBefore
@MichaelBefore 17 сағат бұрын
Munkhokwe makatanimo???? Mbava zachabechabe
@robertnamangale3504
@robertnamangale3504 12 сағат бұрын
NRB si ya mcp ayi,bwanji sanawauze a opposition ngati ma stakeholder a election? anthu anayamba kale kudandaula za NRB bwanji a Sambo akulephera kuvomereza kuti sizikuyenda?
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 11 сағат бұрын
Sambo udzaona polekera mulungu si James
@alfordchirwa3587
@alfordchirwa3587 18 сағат бұрын
Is the building lebled?
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 11 сағат бұрын
Katole wayankulatu mondigwila ntima 😂😂😂😂😂😂😂
@joebrown1158
@joebrown1158 3 сағат бұрын
Kodi iwe amene wukumunamiza ndindani? Wukudzinamiza wekha ndi banja lako wosati Amalawi
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 10 сағат бұрын
Asambo Mulungu akuyendeleni komaso next year kundende ndialo mukakhale moyo wanu onse
@leonwisikesmwkbyowner
@leonwisikesmwkbyowner 11 сағат бұрын
Sambo iweyo ukulankhula ngat wa Mcp
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera 18 сағат бұрын
Boma limeneli ndilmanyaka, why do this Stupid NRB is working in favour of MCP without working with all political parties. We will see when governments change.
@JamesMachunga
@JamesMachunga 11 сағат бұрын
Sambo iwe Malawi usaone ngati analenga ndi amai ako wamva iweyo ukubeleka MCP apa usapusise anthu apa
@MjombaMoosa
@MjombaMoosa Сағат бұрын
A sambo mundilakwisa ndikati ndikuyangeni ndilakwisa iwe chidzilu kwabasi
@chancyphiri5747
@chancyphiri5747 16 сағат бұрын
Mchifukwa chani sanatcheke ngati ma id Ali kukanengowo sanalembesedwe mu system ya MEC?
@LimbaniSamueli
@LimbaniSamueli 17 сағат бұрын
Bambo sambo athu osewa sioputsa.
@IreenMughogho-z6f
@IreenMughogho-z6f 17 сағат бұрын
Kumeneko ndikusa kwambiri iwo wa NRB ine mwana wanga since 2022 up to now sanatenge akungoti sizinatuluke vyauchindere ivo vinthu vikwenda makola yayi
@MosesChazima
@MosesChazima 18 сағат бұрын
Sambo iwe SukuyaKha chifukwa chn sunapangile kwadisi😅😅😅😅
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 20 сағат бұрын
Anthu ambiri anabwezedwa Kuma Center mpakana sazavhota. Kodi zimenezi zitithandiza?
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 15 сағат бұрын
Amene tinataya ma I'd..anatipasa ma pepar..oti tizarembesa za chisoni kutikana....akuona ngati azabera...anya kunjakuno kuli Mulungu😢😢
@SueWahna-y8m
@SueWahna-y8m 9 сағат бұрын
Komatu Sambo Sambo Sambo amalawi akuyitana kangat 😮
@HalimaMussa-j6t
@HalimaMussa-j6t 3 сағат бұрын
Kkkkkk it's sambo sambo Malawi akuitana kangati for me 🌹 azayankha mwina kuti aitanidwa kamozi kkkkkk
@esterechamba9343
@esterechamba9343 12 сағат бұрын
Mphatso Sambo mukapsa chifukwa cha bodza nenani chomwe mumakapanga Ku warehouse yachimanga musatiputsitse diso likuona zomwe mukupanga ife amalawi sitikufunani tulani pansi udindo Ena aimepo
@alfordchirwa3587
@alfordchirwa3587 17 сағат бұрын
NRB officers aku Mzuzu ndi amwano koophya. Anthu akulephera kutenga ma id atanyozedwa.
@RosinaPatel
@RosinaPatel 17 сағат бұрын
Ku Blantyre nso. Eh amalankhula mwano
@GoodsonRaston
@GoodsonRaston 11 сағат бұрын
Asambowo sakugwira ntchito yawo moyenelera,chinyengo chawakulira and amenewo Ali mbali ya mcp,akupangazo zibwelesa nkhondo mmalawi muno,Mr suleman ulemu wanu bwana,ndne goodson laston kuno ku nsanama boma la MACHINGA
@Elizabethmanda-es7se
@Elizabethmanda-es7se 11 сағат бұрын
A sambo muchite manyazi ndinu.munthu wa mukulu...... musachite chi bwibwi mwagwidwa vomerani tchimo ili ndila poyera..... ndipo lero olo mutafa ifeamalawi sitingadandaule ndiwe chisilu.
@GabieBlack
@GabieBlack 17 сағат бұрын
Fire Suleman
@MemorySabola
@MemorySabola 15 сағат бұрын
Nsamboyu ife amalawi akutinyasatu akukakamira bwanji?
@FrancisMwafulirwa
@FrancisMwafulirwa 12 сағат бұрын
Kutha kwa MCP 😂😂😂😂😂😂
@PhillspicJere
@PhillspicJere 18 сағат бұрын
Warehouse anapanga rent ndi a UNDP
@ALLANNDALEZA
@ALLANNDALEZA 3 сағат бұрын
Anthu ena analembetsa kale kale mpaka kawri card ya unzika osatuluka. Ma card achulukirenji ongosungidwa why why why
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 16 сағат бұрын
All comments from southern region? Is Malawi allocated in the Southern region? Stupid ma Cadets mulira simunati. Sambo ndi ur doing great job
@markanthony5402
@markanthony5402 11 сағат бұрын
Inu chigawo chanucho akuletsani kupereka ndemanga? Ndinu achitsilu mwamva
@InnocentNgulube-f5c
@InnocentNgulube-f5c 15 сағат бұрын
Akulepherela kuyankhatu matunso a Malawi chimene chikusonyeza kt pali kena kake pakat pa boma NRB ndi meck ndye ngt sasamala chisankho sichizakhala cha mtendere
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman 11 сағат бұрын
Sambo ndinu achitsiru chiphaso changa one year now osandipasa why?
@leonwisikesmwkbyowner
@leonwisikesmwkbyowner 11 сағат бұрын
People ivani sambo mene akulankhulila zikuziwikilatu kuti uyu ali under chipani
@AgnesNjikho
@AgnesNjikho 13 сағат бұрын
Koma ziliko anthu akamakuchemerera ziwa kt wachenjeresa azako wasiyana nawo patali azako akukusgoza iwe uzichita zovutisa koma azako ose alido iwowo sakupanga ndare wekha mupaliyameti wekha ku NRb azanu kulibe
@AbdulIbrahim-b6v
@AbdulIbrahim-b6v 3 сағат бұрын
A sambo before musanachite zimenezi bwanji simunawuze azipani kuti muziyendela palimozi
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 16 сағат бұрын
Sambo is doing a great job, phuma ma MPs a opposition. All comments from southern region? Kodi Malawi ndi wa anthu Aku southern region basi? Zopepela zanuzo alomwe inu musiye.
@Edward-y3v
@Edward-y3v 7 сағат бұрын
Sambo wanuyo angotura pansi udindo chifukwa he completely failed
@PhiriVictor-e9l
@PhiriVictor-e9l 11 сағат бұрын
Kodi anzanu munawawuza kuti mwatsekula office Ku kanengo?akudabwa bwanji a oppositon
@PreciousGomiwa
@PreciousGomiwa 14 сағат бұрын
Akuti ma ID ndi ochuluka mma center anthu sakutenga komanso akuti ma ID ndi ochepa mma center akutengedwa... Ndiye timve ziti kkkkk
@SamuelKanongwa-k6h
@SamuelKanongwa-k6h 10 сағат бұрын
Kunali kupanga reduce anthu ovota through ma delays tactics
@alfordchirwa3587
@alfordchirwa3587 18 сағат бұрын
Nyumbayo a Sambo akuti ikugwirisidwa ntchito ndi mabungwe angapo chifukwa chani?
@ThamisonLuka
@ThamisonLuka 15 сағат бұрын
Mfiti yamunthu mulungu akulange iwe Sambo 😢
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 18 сағат бұрын
Sambo ndiwe mfiti ndinu nokha a mcp amene mukut zikuyenda bwino ndinu opusa zedi since mudayambila kalembela how many people akudandaula?
@MustafaPemba
@MustafaPemba 9 сағат бұрын
Inenso ndimadabwa kuti kosungira galimoto kukumasungidwanso matumba achimanga kkkk
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 23 сағат бұрын
Sopano ku Lilongwe kulibe DC kuti mukagwilile ntchito Ku warehouse
@SteveNdhlovu-r2x
@SteveNdhlovu-r2x 3 сағат бұрын
A sambo mukuzinamiza nokha mukuyembekezela tsoka
@JamesChingombe-l4l
@JamesChingombe-l4l 17 сағат бұрын
A Nrb akupanga zinthu so bows akungilanji ma ID's a anthu mmwalo mowa pass aniyake
Eksklusif: Prabowo Subianto Bicara | Mata Najwa
1:49:52
Najwa Shihab
Рет қаралды 23 МЛН
LIVE STREAMING Catatan Najwa: Jokowi Dilantik
3:29:44
Najwa Shihab
Рет қаралды 3,4 МЛН
coco在求救? #小丑 #天使 #shorts
00:29
好人小丑
Рет қаралды 100 МЛН
УДИВИЛ ВСЕХ СВОИМ УХОДОМ!😳 #shorts
00:49
[LIVE] Pengumuman Menteri Prabowo-Gibran | Musyawarah
2:52:16
Najwa Shihab
Рет қаралды 1 МЛН
My life began in prison | Solly Mankga
3:34:48
King David Studio
Рет қаралды 567 М.
UNTV: C-NEWS | December 13, 2024
57:34
UNTV News and Rescue
Рет қаралды 293 М.
TIMES EXCLUSIVE| 07 DECEMBER 2024| SAMEER SULEMAN - MP
58:50
Malawi News Update
Рет қаралды 41 М.
coco在求救? #小丑 #天使 #shorts
00:29
好人小丑
Рет қаралды 100 МЛН