Professor Herman Manyora wa ku Kenya ananena pa Podcast ya kuti Vice President wa ku Malawi [ Anaphedwa NOT anafa koma Anaphedwa ] Chilima was eliminated or assassinated there is no two way about it.
@VitumbikoChitetejere-g1w17 сағат бұрын
Atafa abingu ndikaliat yemweyu anapangisa mpungwepungwe kuti joice banda asankhale President
Osamayankhula mwamikuluwiko apa a president Ali wrong u can't wait anthu poti azikupanga force pobwelesa mademo kenako uzipanga decisions that's very wrong and it's not first time kutero