I see pride and bostifullness in him but his presentation looks good. I don't know if he becomes citizen number will he change this pride and bostifulless.
@AiwaMedia-sh6vx4 ай бұрын
Mumba is not exposing the truth on how he came to knowing the president. You can't be introduced by a friend to his friend just be your friend too.. to my understanding Mumba came from a benefit from the government
@chitanibenito11094 ай бұрын
Mbava imeneyi!!!
@Littlefair74 ай бұрын
Ndi anthu ozindikira okha amene angaone ndi kuzindikira kuti Vitumbiko ali pa mission yayikulu, zimenezi anthu ongotsatira ndale mwa umbuli sanguine, Mumba kauyangana patali kwambiri ndipo madolo ena mu MCP akudziwa zimenezi
@kennethmakweya35614 ай бұрын
I find it hard to differentiate between times exclusive or times special
@FrynessMoyo-to2du4 ай бұрын
Amumba munaphapo munthu chifukwa mcp ose mukuwaonawo ali ndi magazi mmanja😢
@masakaunga40994 ай бұрын
Awawa sangakhale a President funso loyamba anakanika kuyankha anati ndinu ndani akuti engineering what what
@voicedumathindwa4 ай бұрын
Timafuna anthu ngati awa koma vuto chipani cha mcp chankhaza alowe chipani china
@RemitterFlik11304 ай бұрын
inu amumba mcp sikukukhalani or pa ng,ono munakapita ku Dpp kukufunika anthu ofasa ngati inu anthu amzelu ndi achaumulungu ngati inu
@yassinn56344 ай бұрын
DPP siingaithe kwadzadza ma bootlicker apeze kwina kwabwino ngati UTM azikathandizana ndi Kabambe. This Mumba is well informed person.(Odziwa zambiri)