Musalimbane ndi manganya mamie tithana naye ku convention uyuyu akathera konko.
@Extratremendouszeus4 ай бұрын
@@franciscoduartie5762 Good
@JohnThom-om5ke4 ай бұрын
Koma mudyana
@LACKSONJULIUS4 ай бұрын
Nkayang'anitsitsa chithunzi cha SKC ndikumagwidwa ndi mantha at the same time mitsonzi ikumatsika mmaso mwanga .. imfa imene ija ndimavutika nayo muntima mwanga 😭😭
@GraceLuwemba4 ай бұрын
Ndipo iweyo,imfa ya sck yandipangisa kakasi ine😢😢
@YassinAmbali4 ай бұрын
Zoonadi sukunama tilipo ambili ndithu 😭😭😭😭😭😭
@richardbanda99974 ай бұрын
True same as Thambani incident in 1983.
@AishaChibwana-b8o3 ай бұрын
Ine ndikangomuona nkhope mtima wanga umangoyamba okha kuwawa ngati ndikudwala😢
@vussoh003 ай бұрын
Well said Ntsogoleli wa dziko 👏🏿👏🏿👏🏿👏🏿
@aminkums5154 ай бұрын
❤ you realy knows history
@Chrissyluwe4 ай бұрын
You really understand history mama well done ur right❤🎉
@PatrickSomanje4 ай бұрын
Ndipo mutaziwa ndimakonda muthu ameneyi manganya koma sindikaziwa kuti ndiwoyipa chochi ndipo ameneyi zaimfa Dr chilima akuziwapo kanthu
It makes me crying 😭.. why zomwe zikuchita Usi mcp sinampase mpata Chilima? Koma Chilima mcp inkangomanga all time.
@BrightonKennedy-jd6fl4 ай бұрын
Mama mukulakhurazi ndi zoonadi, amene zìmuwawe akakolope mu lake chirwa. ..
@kaberaericdeo1184 ай бұрын
Very true Madam
@GraceZumazuma4 ай бұрын
Manganya UTM sanaikonde kuchokela kale or SKC samkamukonda amkamuzonda chifukwa chaudindo amkaufuna
@priscillamangata40234 ай бұрын
Ndipo usi ndiwa mcp koma athu samaziwa
@CharityMvula-y8sАй бұрын
Kkkkkkkona mzimayi uyuyu🙌
@MulangaNekhumbe4 ай бұрын
Mwayankhula zoona zake ndizimenezo😂😂😂😂
@WillmotChiuimia-vr6ou4 ай бұрын
😂😂😂😂 ndizowona zakee yaa
@MakawaPartrick22 күн бұрын
Chilima anali osogola poganiza koma watilangitsa tikumva kuwawa😂😂😂😂😂
@doreenkaliati31664 ай бұрын
Muli nzeru mwa inu mama iiiiiyaaaa mumwa chani????❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@Sabina-hw4js4 ай бұрын
I support your statement madam.Everything you are saying is true.They think Malawian are silly.
@LextonKuntaja4 ай бұрын
Let's wait ku convention madam....tikawona tokha zochita
@phinleebauleni76814 ай бұрын
Let's be normalize guys manganya didn't want to be part of utm simply because anthu onsewo ndiolephera even chilima him self analephera kuendetsa dzikoli 2 times kukhala vice president koma anapanga chani?? Aaaah ,palibe adzasinthe dzikoli onse ndiolephera let's work hard patokha bas mxew
@aarongondwe98904 ай бұрын
Chilima was a business man anahulitsa malawi ku dpp then apaso ayigulitsa ku mcp😂😂😂😂
@DesireLuka-nf5is4 ай бұрын
💥💥💥❤❤❤💪💪💪💪
@Lizzie-h1k4 ай бұрын
Come on guys, in 2024 not even a clocking machine in government institutions.....that thing is cheap and its automatic.....😢😢😢😢
The history of this country has been distorted. If you want to know the history of the politics of this country look for a gentleman called Roderick Chikapa who was part of the people who founded the MCP. The original party in the then Nyasaland was the ANC (The African National Congress).
@JboyrashiiKatundu4 ай бұрын
Manganya ndi Garu kwabasi
@glorialemani97274 ай бұрын
Nyasaland Congress Part Chair 1942 was Levi Zeliro Mumba that was before Mr. Chirwa
A Chilima anazunzika ndi ndi anthu wotipa awa zinkachita kumvetsa chisoni Rest well SKC
@alexmkolongo30894 ай бұрын
Manganya ndiwa mcp kuyambila kale
@QochiweNkhoma4 ай бұрын
😂😂😂😂Congress pant zoona eee
@greymasha8384 ай бұрын
Uku ndiye kuyakhula
@lifayohbenson19944 ай бұрын
Ambuye tonthonzani mitama yathu ndiyosweka We missed skc 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@Margaret-t7m4 ай бұрын
😭😭😭😭😭😭😭😭
@EllinaBitto4 ай бұрын
Is MCP pant for me😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@ColetteMalunga4 ай бұрын
Za clock in zokhazo ndikupangani support, ku Malawi ma civil servants amanyanya ulesi ndikuyerekedwa
@languitoneelias99724 ай бұрын
He was appointed with dr saulos chilima anthu inu ndi ovuta bwanji osakamba zimenezi asanamwalire saulos bwanji.
@henrykapinga14333 ай бұрын
Braval
@timothydonat4 ай бұрын
Malawu congress pant
@CatherineDesire4 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 yeah it not a party it pant for sure kkkkk
@fredgabrielnyangulu4 ай бұрын
Bolanso Chinangwacho koma Mbatata zophika abale inu, amene aja zomwe zimawakhala ndi zomwe zija za drama zija coz akumapanga drama awa
@PaulChida4 ай бұрын
MwajayilA mahule 😂😂😂
@Princejord-v3k4 ай бұрын
Mumatiimirira mama amenewo ndiwo mawu .
@mcdonardmegha60544 ай бұрын
Koma ndiona mama
@wisemanjere65724 ай бұрын
People be civilised. What Manganya is doing is reforms what Chilima was advocating. Manganya is Saling UTM. This is not the time to be quarrelling. What's wrong with we black people.
@williammandhlopa4 ай бұрын
True
@InnocentCakeSlice-zx9bq4 ай бұрын
Za ziiiii😂
@AustinSaka-e8z4 ай бұрын
Kod MCP yasandukano nachipati 😅😅😅
@patriciacraiton-sf5vu4 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@jeffchikwapata69334 ай бұрын
Ndagwirizana nanu mai pa mfundo imodzi yoti mukufuna mtsogoleri wa dziko osati wa chipani that is true
Lero tawona kuti UTM yinayi ikusangalala kufa kwa a Saulos. Nkhalani pansi ngati anafedwa kuti tsogolo lowala titanic nalo.
@GeorgeChiwanda17 күн бұрын
Awa ndie akambuku ku utm. Chilima amaweta akambuku eee amudya manganya ndithu asiyile odya zake salimbana ndi munthu msiyeni
@hassantwanje7774 ай бұрын
Mumie mwatiyimilila kom ndnu 1
@SileniPitros4 ай бұрын
Mmm mumatani kuyankhula kalero zimenezo kkkk
@HarryMtukula4 ай бұрын
Kodi mmene chilima amamusankha maiko usi kukhara vice wake munatani kumuretsa ndi mzeru zanuzo kuti asankhe inuyo ngati muli ozindikira? Ndachiona ine ndi msanje ndikusankhidwa kwa usi, ambuye akuyendereni😮😮
@Sammy-vb1ed3 ай бұрын
Manganya ndiopa ofunika kukamugwetsa ku convention.
@isaacchagwa29174 ай бұрын
I think it is high time we stopped politics that do not touch Malawians.Usi is doing more on development. Politics will never feed Malawians
@aarongondwe98904 ай бұрын
😂😂😂😂
@talandilabenedicto4 ай бұрын
Pa malawi congelesi panti po tandibwelezerani mwene sim'damvetsetse
@FelistusTaulo3 ай бұрын
Manganya zoona
@Mathews-w9f4 ай бұрын
Waitha 5:05
@Malani414 ай бұрын
Leave the tiny boy alone. He is small and short.
@halhimahkalhim3154 ай бұрын
Malawi congress pant 🩲🩲🩲yemweyoooo 😂😂😂😂
@InnocentLenard4 ай бұрын
Mukunama usi ndi wa utm uwe unali kuti nthawi yonseyi
@JamesNyson4 ай бұрын
Mumath mamie tichosa ndimanja uyu kusogoledwa ndi wa drama
@ROBERTMUKHAYA4 ай бұрын
Biguo mamma
@MsondaBanda3 ай бұрын
Vya mbula ntchito gwiraninge ntchito zinu kuti muvwirikenge pa mwekha
@fridahlutendo4 ай бұрын
Kaya Kabambe wanuyo Kaya Manganya Koma Chakwera Akudzakulamuluraso ,MCP simungamake
@lenardmakuya4 ай бұрын
Kuyakhula kwabwno mai
@KabambeFrancis3 ай бұрын
Kuti khaaaa , keep it up madam
@JonathanMsiska4 ай бұрын
100 percent.
@MuyaoComedies4 ай бұрын
Nambo pelepo , Salam alaikum
@UseniMailosi4 ай бұрын
Walykum ssalam wakahmatul llah wabaraktu
@MuyaoComedies4 ай бұрын
@@UseniMailosi allahamdulilaah ngawa Umi wambone bas
@BaxterKachelenga-mb7wx4 ай бұрын
UTM tiyeni tizuke,dont waste time ndi mapokoso tiluza osatira anu.Tamangani chipani.
@janemshanga53494 ай бұрын
Azikhala ngati zipatala zakuno ku southafrica ikamati 6 chipatala chimakhala chatsegulidwa kale
@miovekanola27804 ай бұрын
Akut MCP pant😅😅
@isabelmartin75674 ай бұрын
Udasi means Usi
@actuarialscience22834 ай бұрын
Michael Usi ndi ufulu wako kusapota MCP. Koma kunamizira kuti ndiwe wa UTM ndi uchitsiru. Ndinali wa MCP ndipo mmagulu a whatsapp ambiri a MCP Usi amapezeka.
@TheresaNtodwa4 ай бұрын
Chikangawa pant yomweuooooo
@SarahShawa-wh9iy4 ай бұрын
The problem with anthu a UTM you just know how to talk, but you don't vote.
@LextonKuntaja4 ай бұрын
Kusowa umunthu zoti ndi wopemphera enawa mmmmm mpaka ndi nkayima or nthumadzi mzako ali pompo agreement ili mma file
@Princejord-v3k4 ай бұрын
Guys ndikaganiza kuti a day before Chilima died he was just coming from Korea with his wife Mary ndikumangolira , imagine how Mary is feeling right now ine wapadera ndikungorira how about her, Malawians tiyeni tipangeko kanthu ngati wapha Chilima apange regret. Achoke basi
@StevenGJohn3 ай бұрын
Manganya mbuzi yamunthu osakamvotera ku Convention Michael Usi ndi mbuzi yamunthu galu
@IreenChilingulo4 ай бұрын
Mayiwatu koma akunena zoona zothandiza atavela zzathawizo zitha kusintha zithu
@HandyChipets4 ай бұрын
Amai Vitumbiko si Civil Servant he is free to use an MCP tag .