We need interviews like these bravo Joab..... this was educative and very true plants are medicinal .....we thank God for this educative interview!
@mtenderekabuluzi3986Ай бұрын
Mulungu atitsimikizira zomwe anakamba kuti masamba anaiwa kuti atichize❤...God bless you Dr banda
@ChipatsoNdalamaАй бұрын
Wow we thank God for this interview.. God give him life
@makinacharity5174Ай бұрын
One of the most educative cruise 5
@chikumbutsoBonfaceАй бұрын
Have you ever watched good interview with Joab Frank Chankhaza,this is one of the best ,i really like this ,its so interesting and educating
@DanielMbingwaniАй бұрын
The best interview ever!❤❤❤
@stenfodgondwe9341Ай бұрын
Probably one of the best interviews. Iyiyi yokha yatipundulira heavy
@samuelcleophusАй бұрын
Best interview so far
@cliffordernestnjirazafa6723Ай бұрын
Joab Frank Chakhaza umachita zinthu mokonda anthufe zedi. Umabweretsa zinthu za mtengo wapatali zedi. Ndimakumbukira zinthu ziwiri zikuluzikulu zimene udandiphunzitsa za malo osafikirika: Sapitwa komanso Khuluvi. Lero wandigwiranso pa mtima ndi dolo ameneyu. Ichi chi cholowa chimene udzasiyira a Malawi chifukwa chidzakhalabe chuma chobisika ku nthawi zonse.
@LonjezoBuleyaBandaАй бұрын
I'm really impressed with your job , ndili ndi knowledge ya ma herbal komano ndufuna nditakumana nanu ndiphunzire zambiri. Amene angandithandize link me
@AubreyYokoniaАй бұрын
He is a genius I respect the man
@salomykampira-e8fАй бұрын
best cruise 5 interview ever🔥🔥
@cuthbertmanda584Ай бұрын
Am diabetic...Mr Banda is a solution
@zellinakadamika3325Ай бұрын
I will wait with you
@EllenWahiya-f6dАй бұрын
Wowb so educative and interesting interview
@PatrickPhade-uu5xvАй бұрын
Best interview ever❤
@PililaniChipendoАй бұрын
The best Cruse 5 ever
@MphatsoNjanjiАй бұрын
Nice presentation chakaza and Dr banda
@paulzgambo1115Ай бұрын
The man is great...
@Cathy-oc7vdАй бұрын
Best cruise 5 ever
@faithkapindula9032Ай бұрын
Amapezeka kwa mtsiliza, ask aliyese mukafika pa stage .
@chikalesoft-techs8109Ай бұрын
Wow🙌🙌🙌🔥🔥🔥
@EdokelzLightMalengaАй бұрын
This is incredible
@KingstoneKaliuАй бұрын
This man is fully educated
@beckkasanjah9606Ай бұрын
Genius bwana Alex Holistic Banda
@MercySKayangeАй бұрын
Wow🤗
@eliaskamvamthupi494Ай бұрын
Nambala yawo ya foni bwanji mutigaile tilumikizane nawo
@shukransmart1902Ай бұрын
long live dad
@OliHauchaАй бұрын
Uyuyu ndi dolo 🔥
@YoungMtamboАй бұрын
The only thing that is missing here Joab ,is the number pliz distribute this pangolin 's numbers pliz
@TrizaKajaduАй бұрын
Sayankha phn yao kungopita konko
@euniceMgala-o2cАй бұрын
Mtsiliza opposite area 47 sector 5
@Edward-t2zАй бұрын
Anenatu kuti kwa Mtsiliza, kupitako given sikungasowe
@HarrisonSaikonde9 күн бұрын
Zilibwino koma ndimafuna number ya Dr banda
@madalitsoyakobe2123Ай бұрын
Dr banda🔥🔥🔥🔥
@yohanemalata737Ай бұрын
Koma muzachezeko ndi abusa akambalazaza or sister liniry mbeta
@geoffreymanasseh35316 күн бұрын
Am looking for his number. Amene alinayo please share here
@kingnavitcha6243Ай бұрын
Kodi Dr Banda wa tingalumikidzanenawo bwanji?
@MarthaMkombeАй бұрын
❤
@emmanuelseuleАй бұрын
Kwamtsiliza ku Lilongwe
@magretmgawa2992Ай бұрын
Koma mpiru udyedwa osati masewera😊
@ChrissiePualАй бұрын
Ndaphunzira Zambiri
@LizzieSherifАй бұрын
Uwu ndi mutu mphangala
@PatrickMtenje-e9uАй бұрын
But number palibe how do we contact him now pliz
@acksonkamanga3367Ай бұрын
Koma Joab ati amakuonetsatu pa glass 😅
@gladyschapima8670Ай бұрын
Inu a Joab chonde tipezereni numbera ife tudwala ma ulcers..