EXCLUSIVE - WITH MOSES KUNKUYU | 14 DECEMBER 2024

  Рет қаралды 3,583

Malawi News Update

Malawi News Update

Күн бұрын

Пікірлер: 68
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 12 сағат бұрын
Zawavuta basi 😊
@jamesmtukula3062
@jamesmtukula3062 13 сағат бұрын
Brayani banda keep it up....….... koma kunkuyu amayankhula mwathamo
@usherjamson174
@usherjamson174 11 сағат бұрын
Brain akuyenela 99% guys he is very good
@jackalview7491
@jackalview7491 12 сағат бұрын
Vomeleza iwe nkukuyu mwalephera
@EnockTheu-dp8ep
@EnockTheu-dp8ep 11 сағат бұрын
Kunkuyu you deserve to answer on behalf of mcp and government ndipo boma sitisintha sitibwereraso kumbuyo we looking forward
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 15 сағат бұрын
🎉Fotseki kumkuyu
@HiltonZaone
@HiltonZaone 12 сағат бұрын
Just promise but know action
@HassanSaid-q8q
@HassanSaid-q8q 12 сағат бұрын
Chisilu iwe kumkuyu ukukhala ngati siukuziwa chilungamo bwanji
@TonyMhone
@TonyMhone 12 сағат бұрын
Akafunse achina Mark Botoman nthawi yimeyo ankapanga bwanji? Mwina wayiwala. Mongomukumbutsa chabe.
@MemoryKamanga-jv4jh
@MemoryKamanga-jv4jh 12 сағат бұрын
Brian banda god bless you to follow Malawian
@dubemontfortmataya2619
@dubemontfortmataya2619 11 сағат бұрын
Za phunzisi zokhazo a nduna mwanama aphunzisi akuvutika kumalawi kuno. Ndipo ngati kuli civil servant amene akuvutika is a teacher. Especially primary teacher
@FlintKatunga-b1h
@FlintKatunga-b1h 12 сағат бұрын
Mkukuyu ndi mfiti uyu
@MosesTangwe
@MosesTangwe 12 сағат бұрын
Zaziii zenizeni
@RichardKumadzi
@RichardKumadzi 12 сағат бұрын
Akukuyu ndi chisiru samakha mafuso Mulungu akukuwona
@JamesSaiti-h1l
@JamesSaiti-h1l 11 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂 koma kumkuyu
@OscarKathumba
@OscarKathumba 11 сағат бұрын
Moses Mkukuyu si Munthu wamba
@StewartO.DChizaka
@StewartO.DChizaka 12 сағат бұрын
Brian Banda and Joab Frank Chakhaza there two different people. Chakhaza he is special one. He knows how to treat politicians. While that one, they can run away from his questions
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 11 сағат бұрын
There two different people kkkkkk! Vizungutu
@BenjaminMalinga-m7y
@BenjaminMalinga-m7y 12 сағат бұрын
Kunkuyu ndi kape chitsulo
@aubreygambatula2002
@aubreygambatula2002 13 сағат бұрын
Iwe aise,,, ndondomeka ya fertilizer,,, sikugwila ntchito yoenera,, sometimes mukamayakhula osanayakhulw as if izi ndikila ndinunokha
@YusufuAmini-r8r
@YusufuAmini-r8r 11 сағат бұрын
Tikufuna kafukufuku wa chikangawa
@gabrielmaluwa1038
@gabrielmaluwa1038 13 сағат бұрын
Chitsiru uyu
@SimionDmtande-z8v
@SimionDmtande-z8v 13 сағат бұрын
Ameneyo ndi Bryan banda akupanikiza ndi.afuso
@AmahleMokoena-dw5wp
@AmahleMokoena-dw5wp 12 сағат бұрын
Kondi kunkuyu ndi ameneyu eti??
@alexsumani6823
@alexsumani6823 11 сағат бұрын
miseu ndi China Aid tikonze pamenepo
@ChrispinNasiyaya
@ChrispinNasiyaya 13 сағат бұрын
Kunkuyu simunthu wamba, muyakheni akanene zeni zeni kumene amutumako!
@Ertyvhk
@Ertyvhk 15 сағат бұрын
Kodi kubomako kulibe munthu wina woyankhura awatu sakuyankha zomveka coz tikunena pano admarc chimanga mulibe anaseka kale kale
@ChikondiBannet
@ChikondiBannet 11 сағат бұрын
Boma lamisala
@Mirriumkamwendo
@Mirriumkamwendo 12 сағат бұрын
Kumkuyu savomereza
@MwenekabwekayondoSilumbu-g4x
@MwenekabwekayondoSilumbu-g4x 11 сағат бұрын
Zawakanika awa kuchulutsa maboza baai
@IdaMalango
@IdaMalango 11 сағат бұрын
Mwalephela a mcp
@MustapherMulumbe
@MustapherMulumbe 12 сағат бұрын
Alibe nzelu anthu awa inu fertilizer ndiye kunthana ndi Malawi
@IslajiBiliati
@IslajiBiliati 11 сағат бұрын
Iwe ndigalu kobasi chitsilu cha munthu
@thulambale2836
@thulambale2836 13 сағат бұрын
Brian mafutso anatha ndipo anili kale Koma lero ndi wa zitsiru Za oppositions agalu
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 11 сағат бұрын
Kapilo odya zodikulitsa ku chipani iwe.
@alexsumani6823
@alexsumani6823 12 сағат бұрын
Tayankhani kwanuku chimavuta chani 🤣🤣
@CharlesChilinde-zm9xo
@CharlesChilinde-zm9xo 12 сағат бұрын
Akunkuyu muli bwino kwambili Boma ndi lomweli
@ProsperBanda-ju2mq
@ProsperBanda-ju2mq 12 сағат бұрын
Amapezerela akape brain ndamuoona akudekhetsa kwambiliii
@AlexThembakako
@AlexThembakako 12 сағат бұрын
Brian, these people will waste your time, they can't answer your points? They are good backing themselves.
@RuthMlenga
@RuthMlenga 11 сағат бұрын
Kukweza AIP sikukonza zinthu kma funso ndiloti chomwe chalongosoka ndi chan
@RodgersMwanakhu
@RodgersMwanakhu 11 сағат бұрын
Munthu oipa uyu
@courageouslondo1986
@courageouslondo1986 12 сағат бұрын
Ine uyu anandipatsa mtima
@MorrisTsoka
@MorrisTsoka 11 сағат бұрын
Anthu akudziwa bwino awa chilungamo chake kuti zinthu sizili bwino
@DanielChipasula
@DanielChipasula 13 сағат бұрын
SCIENTIFIC REPORT YA AFROBAMERE NDIDAYITUTSA INEYO MU 2020 MU JANUARY.. ADATI MCP IDZAWINA 51 % KUTI APM _ DPP ... ma 40 % ... AMBUYE WANGA ADANDIPATSA A PROPHATIC DREAM YA 58_ 60 % WINNING KUTI ASAGUNDANE NDI APM KUKANA KUKANGANANSO MPAKANA MA RERUN ENA. MOTI A CHAKWERA ADAWINADI. MY 🤳 P DREAM CAME TRUE.. MOMANSO DZIKO MDALIDZIWITSA KUTI ' MULUNGU WANDIDZIWITSA NDI KUNDIWONETSERA LOTOLO ' Panopa mkudziwitsani m' mene Masankho akhalire.Tiyeni Tipephere Kwambiri.!! NDINEYO DAMC PP& EO 🎓✍️🇲🇼!
@YohaneStevenMhone
@YohaneStevenMhone 11 сағат бұрын
Kkkkkkkkk a koma kunkuyu ndiwochenjera apapa nde akumana ochengera okhaokha.A Brian avekere😅😅 mwakamba nkhani nayenso nayankha kt Inu mwatola nkhani kkkkkkkkk mzibwerabwera a Brian
@KelvinDickson-c1x
@KelvinDickson-c1x 14 сағат бұрын
Chiseko champana kumkuyu
@SteynMaduka
@SteynMaduka 12 сағат бұрын
ZAKUVUTANI akulu chiseko chakupanani, nanga fertilizer wadulayi?
@FlintKatunga-b1h
@FlintKatunga-b1h 12 сағат бұрын
Mulibe usogoleri mwa anthu away foseki
@HassanSaid-q8q
@HassanSaid-q8q 11 сағат бұрын
Opusa iwe akavotela omwewo apolice o
@TiyamikePhiri-z2j
@TiyamikePhiri-z2j 15 сағат бұрын
Nde mwayankha kuti chani?kkkkkk
@Charlesmilanzilihera
@Charlesmilanzilihera 14 сағат бұрын
😅😅😅
@MphatsogiftJerejr
@MphatsogiftJerejr 11 сағат бұрын
Brian uja musazamuphwekese ai 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 ndiye kuti mwayankha kuti chani kkkkkk
@kumbukanisapuwa239
@kumbukanisapuwa239 14 сағат бұрын
A brayani ndi mtolankhani wa bho ever
@ThaboyEst
@ThaboyEst 13 сағат бұрын
Kunkyu ulibe nzeru iwe ndipo nde uzayaluka la 40 lizakwana sure
@ChimwemweGphiri
@ChimwemweGphiri 14 сағат бұрын
Funso lililonse kumango zembazemba akuopa chani
@aubreygambatula2002
@aubreygambatula2002 12 сағат бұрын
Just answer straight sunapindule ulendowo
@EndkenChisuse
@EndkenChisuse 14 сағат бұрын
COVID 19 anabwela ndi chithumba inu
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 11 сағат бұрын
Anthu mu Chombo muja, anakumana ndi mavuto, chifukwa Mulungu anakwiya ndi munthu m'modzi YONA. pamenepo olephera anali ndani?
@YusufuAmini-r8r
@YusufuAmini-r8r 12 сағат бұрын
Kumkuyu you are talking nonsense here , just answer the Question . Malawi imadalila uli how can malawi survive without fertilizer
@Rasheedissa-f3q
@Rasheedissa-f3q 14 сағат бұрын
Akukuyu fuso simukuyanga fuseck kuyambila 2020 nkuphemba antill now why??
@brendakamwendo5544
@brendakamwendo5544 14 сағат бұрын
Koma mhhh
@MisiSaid
@MisiSaid 15 сағат бұрын
😂😂😂😂Koma
@GolaMwanza-oi3oj
@GolaMwanza-oi3oj 16 сағат бұрын
C zikumveka
@edsonkamba3170
@edsonkamba3170 13 сағат бұрын
You are just irritating the audience with your silly responses Mr honourable minister of information
@GanizanLibuda
@GanizanLibuda 12 сағат бұрын
Brian zikomo kwambiri,kunkuyu amafunika munthu wanzeru ngati iweyo ase umazwa kukhaulisa Eeeeee Ambuye azikudalisa nthaw zonse
@rodgersvaleta-j3z
@rodgersvaleta-j3z 13 сағат бұрын
BOMA lopanda nzeru.
Интересно, какой он был в молодости
01:00
БЕЗУМНЫЙ СПОРТ
Рет қаралды 3,9 МЛН
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 25 МЛН
Леон киллер и Оля Полякова 😹
00:42
Канал Смеха
Рет қаралды 4,5 МЛН
KULINJI KU MALAWI? | 11 DECEMBER 2024
51:02
Malawi News Update
Рет қаралды 8 М.
Times Exclusive featuring Wester Kossam - 30 November 2024
1:03:52
Times 360 Malawi
Рет қаралды 12 М.
SPECIAL PROGRAM - COMMISSION OF ENQUIRY FINDINGS
4:27:31
Malawi News Update
Рет қаралды 7
Xeer Ciise: Maxaa Ka Dhigay Mid Caalami ah?
1:06:12
Xogmaal Media
Рет қаралды 17 М.
Интересно, какой он был в молодости
01:00
БЕЗУМНЫЙ СПОРТ
Рет қаралды 3,9 МЛН