Ur the best guys ..mulibe mbali koma good explanation of things
@riccodeeforces80974 сағат бұрын
I like the idea🎉🎉🎉😂😂
@GiftBello-v1i17 минут бұрын
Gwede gwede
@JohnWasili27 минут бұрын
Team imeneyi idabwera kuzakhala
@jozyomar5361Сағат бұрын
Pankhani yazola ndi kuyikila zakazizo ayi Mr Banda that is very bad idea mukufuna akufuna atisoko ezele mabaja zimadula kale 😂
@LouisChabwera-y2w3 сағат бұрын
Nkhani ya fetereza yalephereka osati sikuoneka bwino yakanika mwezi uno wa January mmene muli mbewu yabwino chimanga chaphatika kale
@MDALASAIDIISSA-r9p3 сағат бұрын
MCP he's one heavy power president you don't have a power MCP he's the one tell president what to do that's why all this problem come my name is MDALA SAIDI ISSA CAPE TOWN
@munachangombe2 сағат бұрын
ndipo wa polic yo mulungu a dzimudalitsa mzimu wa athuwo ndiumene unamuwuza kuti enafe tiwone kuti anadzunzika?
@IsabelLuka-i8f3 сағат бұрын
Musadzasowe anthu inu pa mibawapo,ndimakufilani hevest
@BlessingsChitekwe-k5z3 сағат бұрын
Kod program iyi imakhala masiku atiati???
@thatgirrroskrr35703 сағат бұрын
Lachiwiri ndi lachinayi
@CardoJustin-l7m4 сағат бұрын
Madokotala nawo a kuopa kusamusidwa ndi chifukwa chake akunena zonama koma chilungamo akuziwa kuti mayi said anaomberedwa ndi wapolice