Eeee this song is very powerful glory to the most high God, the owner of everything, king of kings and lord of lords 🙏🔥
@user-fg7qg3ce7fАй бұрын
Amen
@FloraChibambo25 күн бұрын
Q
@ArvinKankhuni16 күн бұрын
This is so powerful song wawooo ...glory to the almighty father ...I have played this song 7times ...AMEN AND AMEN
@rabeccadytone877213 күн бұрын
Ooih yes
@user-sg7wk3vn5vАй бұрын
What a powerful ministration remain blessed
@mirriamwilliam-nq9wgАй бұрын
Oh yes Hallelujah ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤I'm in love with this song
@EllahEllah-hu7hi16 күн бұрын
Mwayenela kulandila ulemu ndi matambo,,bondo lililonse layenela kugwadila inu baba,,, powerful song
@Lyn-c4m6sАй бұрын
Oh yes chifukwa chammene mulili baba I dont know why am singing this song with tears 😢 Jesus
@daughterofzionphalycemalik1296Ай бұрын
Glory up God
@user-fg7qg3ce7fАй бұрын
❤❤❤❤Amen
@VanessaChisale-k2o9 күн бұрын
Am blessed with the songs. ... Munyimbo muli mphamvu yopoosa kwambili
@NamasekoАй бұрын
Mai mumaimba, koma nyimbo iyi mmmmm 🙏🙏🙏 Ambuye apitirize kukugwiritsani ntchito!!! Tikulemekeza Yehova osati chifukwa cha zimene tiri nazo ayi koma CHIFUKWA CHA M'MENE IYE ALIRI!!!
@RK-xw1ofАй бұрын
Musadzasinthe Mama. Yehova wayeneradi Ulemu ndi matamando chifukwa Cha mmene Alili. Nyimbo yokoma kwambiri kwa ma Worshippers onse. Indiphe ndi sitepe ine kuno ,on repeat . Ooooooo Yesu landirani Ulemu Woyera wankulu wa Israel, opanga njira popanda njira, Alefa ndi Omega , Thandizo lopezekeratu, Moto Onyeketsa,Tate Osakwiya msanga. Tate wa Amasiye onse . Dzina lanu Lili pamwamba pa Maina onse. Otimenyera nkhondo, otiweruzira milandu yathu. Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah HallUpelujah Hallelujah 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🥁🎷🎵🎶🎺🎤🎻🎸🎧🎹🎧🎹🎻🎸🎷🎵🎶🎶🎶🎶🎶🎶🎤🎺🥁
@daughterofzionphalycemalik1296Ай бұрын
Amen amen amen
@rabeccadytone877213 күн бұрын
Amen Amen Amen
@vivianjackson654010 күн бұрын
Amen 🔥
@beatricenkhoma110917 күн бұрын
Yes Lord, your no 1 palibe ofanana nanu baba ulemu,matamando kukwezedwa konse ,kwayenera inu🙏🙏