“KABAMBE ACHOKE IFE SITILORA” OTSATIRA UTM KU DOWA AKUYIMBA IZI. NDE TANVANI ZOMWE VP USI WATOKOTA

  Рет қаралды 3,565

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Пікірлер: 57
@JeremiahPhiri-j8p
@JeremiahPhiri-j8p 9 сағат бұрын
The Saviour, mahatma Messiah has come Usi tybe fufiller of SKC Visions
@kennymwanyongo8165
@kennymwanyongo8165 20 сағат бұрын
Michael Usi never liked UTM. He is a traitor that is hell bent at distracting a Party that honored him with a high profile position of a vice presidency. His actions speaks volumes with regards to his relationship with the late SKC.
@MfuneWaluEckson
@MfuneWaluEckson Күн бұрын
Kuwaina athu akewo otse a kuonekeratu kuti agona ndi njala komatso mitu yawo siigwira 😂😂
@DavieAlumenda-u6y
@DavieAlumenda-u6y Күн бұрын
A Malawi Pena pake tidzidzimvera chison zilizonse zopusa kumangoyimbira mmanja zoona?
@ChimwemweMkumbadzala
@ChimwemweMkumbadzala 14 сағат бұрын
Had it been kuti chilima anadziwa mtima wa Manganya,he would not have took him to be his running mate,,This is Judas Scaliot
@SailotaSamuel
@SailotaSamuel 12 сағат бұрын
Koditu dziko sikuti lidzathela Malawi yokha bwanji zithu zanu palibe chomwe munthu ungaloze😮
@DereckSumbulero-i4z
@DereckSumbulero-i4z Күн бұрын
Eeee kma ngati kulikusaka ndalama mwafikapo anyamata inu, zikuchita kuonesa. Holy ghost fire....manganya munthu oyipa ndipo usamatchure dzina la mulungu iwe.
@JackMvura
@JackMvura Күн бұрын
Usi ndidolo agwetsa UTM komaso DPP muona naye nyenkhwe simunati zayambika chonchi kabambe achoke basi zavuta
@NolityKondowe
@NolityKondowe Күн бұрын
Kuvara makaka a utm kuti mwina a Vice angawanyemereko kangachepe.
@AyamiMustafa
@AyamiMustafa Күн бұрын
Malawi police yomvetsa chosoni kwambili
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Күн бұрын
Mcp idusa moyela chifukwa opposition yongona ngati imeneyo
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 17 сағат бұрын
Zikang'a zilitho kumvesa chison mukhalira yomweyo
@BrightonChirwa-b5c
@BrightonChirwa-b5c 19 сағат бұрын
akungovuti, chabe, usi zake zinada
@BlessingsSeleman
@BlessingsSeleman 19 сағат бұрын
Manganya alibe umuthu ndiposo manyazi zisilu ndi ife amalawi zopepela zomwe bwana bwana zamanyi bs
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 18 сағат бұрын
Avala ma Ti shirt a UTM aluchita kuonekeratu kuti ngotumidwa zigawenga aganyu
@StevenGJohn
@StevenGJohn Күн бұрын
Manganya ndi mbuzi yamunthu ukulimba ndi UTM osangoyambisa Chipani chako bwanji galu iwe
@IsaacTsinde
@IsaacTsinde Күн бұрын
Anthu agule awa ndiwofoila palibe chanzeru choti chingasinthe malawi apa za ziiiiii
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 21 сағат бұрын
KKK AWA NDI ANTHU A MIKAL USI .KUMPANGIRA DALITSO KABBE DECAMPAIGN.ZA ZII MIKAL USI .UGWA MAYOTU NSANJE YSKOYO
@CatherineMkwaila
@CatherineMkwaila 22 сағат бұрын
Kodi inu simukuona kuti ndi mamembala a map angowapatsa makaka a utm kuti avale kufuna kusokoneza otsatira utm.
@TsArKhaii
@TsArKhaii Күн бұрын
Awa anangofunako ndlama anthu omvetsa chisoni they don't even know what they're doing
@SailotaSamuel
@SailotaSamuel 12 сағат бұрын
Alibe mbali manganya
@susantembo2076
@susantembo2076 21 сағат бұрын
Kusafziwa nkufa komwe
@DumiMhango
@DumiMhango Күн бұрын
Mbuzi ndianthuwa komaso yemweatuma sakusiyana
@Jane-qb5qf
@Jane-qb5qf Күн бұрын
😂😂😂😂😂 Zoona pali chanzeru apa ndani angagwedezeke ndi izi zaziiii awapasa ma pin uko tiyeni akakujambuleni anthu akuoneni zaziii koma amalawi mavuto sazathadi tisaname Usi akukoka anthu wa kuti apite ku mcp anthuwa sakuziwa moti amalawi ngati tikufuna kusintha zithu onse anayima kale asayimise tiyese zina inu plz
@Jane-qb5qf
@Jane-qb5qf Күн бұрын
Nyimbo ya Mlaka maliro ndayimvesesa pano akuti si uyu ngakhale amapemphera koma si uyu David tidikira mpana David abwere meaning yake ndayiziwa onse awa takhala tikuwayika pampando si achina David plz tisatope kuyesa David adzabwera
@Jane-qb5qf
@Jane-qb5qf Күн бұрын
Si uyu by Mlaka maliro amalawi mveserani mwachidwi nyimbo ija ikunena zoona si uyu ayi David tisatope kuyesa David abwera plz tisabwereze zomwe taziyesa kale fisi ndi fisi musatenge america ndidziko lachuma kale lija
@IsaacTsinde
@IsaacTsinde Күн бұрын
Akungofuna kusokoneza
@MemoryZiyaya
@MemoryZiyaya 20 сағат бұрын
Kuvesa chisoni..aza ntiiii ukooo
@SamukLungu
@SamukLungu Күн бұрын
Inose ndinu zisiru bwana chifukwa amagura masamba musikamo tikukuziwani ndi a m cp koma manganya sazaramuraso u t m
@IsaacTsinde
@IsaacTsinde Күн бұрын
Ndipo anthuwo salitu organised ndiwogulidwa awa
@MathewsMbaluko
@MathewsMbaluko Күн бұрын
Zopusa aaaaa Ife tifuna kabambe emweyo zinazo ayi
@EmmanuelkpPraise
@EmmanuelkpPraise Күн бұрын
Anthu aku Dowa mudzisiyanitsa ,Kuti Michael Usi ndi vice president wa dziko komanso ndimembala wa chipani cha UTM kutengera ndimmene anapangira convention
@Elizabethmanda-es7se
@Elizabethmanda-es7se Күн бұрын
manganya ndiwe galu
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde Күн бұрын
Koma usi ndimfuti osati masewela
@UncleShopRite
@UncleShopRite Күн бұрын
Kkkkkkk manganya wawapatsa tima 10 thousand
@MathewsMbaluko
@MathewsMbaluko Күн бұрын
Chokani aganyu inu😊😊
@EmmanuelkpPraise
@EmmanuelkpPraise Күн бұрын
Amenewo simasapota a UTM,amenewo ndi aganyu
@StevenGJohn
@StevenGJohn Күн бұрын
A Manganya zipaseni ulemu musasokoneze Chipani cha UTM inu ndimunthu wamba Ku UTM musiye kuwaveka anthu a Mcp Maka a UTM musazitukwanise chonde
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko Күн бұрын
koma awa afuna chani makamaka akuna kukangana ndazizawo
@StevenGJohn
@StevenGJohn Күн бұрын
Kwasala mezi 9 Kuti u Vice President uthe mwina sukuziwa tikukumbuse
@OliverChimsewu
@OliverChimsewu Күн бұрын
😢kodi ausi ndinudi aseventh day?
@Elizabethmanda-es7se
@Elizabethmanda-es7se Күн бұрын
ndifunsireniko
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde Күн бұрын
Ndezikutathauz chani
@TauraiTsaka
@TauraiTsaka Күн бұрын
Chifuwa akudziwa kut ndizawo wa mcp
@GrecianWyson
@GrecianWyson Күн бұрын
MCP party sakudziwa ndani
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 Күн бұрын
Zaziiii
@MebleKalitsilo
@MebleKalitsilo Күн бұрын
Kodi mangaya akufuna chani munthu opanda nzeru
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko Күн бұрын
koma ifeyo nkhope yathu yimene mkuvara ifeyo takubanja chonde manganya ukutirakwira panga zako chonde please uziva ukufuna tikafike kuti
@RuthKaledzera
@RuthKaledzera Күн бұрын
Tiziona eeee chaka chake mchino
@JaphetSakala-u5j
@JaphetSakala-u5j Күн бұрын
Anyamata azikwanje yawa
@FosterKasola
@FosterKasola Күн бұрын
Apasidwa ndalama awa
@AssanChimaimba
@AssanChimaimba Күн бұрын
Awa ndiye mabodza usi si wa UTM so mumufunilanji
@UncleShopRite
@UncleShopRite Күн бұрын
Ndi a MCP anthu awa palibe wa UTM apa
@EmmanuelkpPraise
@EmmanuelkpPraise Күн бұрын
Amenewo simasapota a UTM,amenewo ndi aganyu
How Many Balloons To Make A Store Fly?
00:22
MrBeast
Рет қаралды 190 МЛН
Sigma Kid Mistake #funny #sigma
00:17
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 26 МЛН
So Cute 🥰 who is better?
00:15
dednahype
Рет қаралды 18 МЛН
Новости дня | 12 декабря - вечерний выпуск
11:36
Euronews по-русски
Рет қаралды 15 М.
CDEDI PRESS BRIEFING - NAMIWA WAGENDA KU POLICE
36:53
AM TV MALAWI
Рет қаралды 2 М.
BUNGWE LA CDEDI ZOMWE AYANKHULA __12 December 2024
25:50
HOT 265
Рет қаралды 22 М.
CYCLONE FREDDY FUNDRAISING DRAMA #malawi
1:31:45
Kanema Online
Рет қаралды 530 М.
Каха и дочка
0:28
К-Media
Рет қаралды 1,6 МЛН
Сломал Алкотестер Своими Лёгкими 😂🌬️🚔
0:43
Реакции Гениальности
Рет қаралды 2,2 МЛН
Color Train Adventure
0:48
Mushroom
Рет қаралды 66 МЛН
Cats Reflexes 💀🗿
0:26
Midov
Рет қаралды 21 МЛН