Tap to unmute

KALIATI ALI NDI CHIKOKA - TAMVANI ZOMWE WATOKOTA LERO, NAWO A KABAMBE ASAMBWADZA - LIRANGWE UTM LIVE

  Рет қаралды 42,811

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Пікірлер: 110
@judithStuwart
@judithStuwart 14 күн бұрын
Mama Kaliat akweni am Happy to see you ,Mai owugwira mtima opanda nsanje ozichepetsa ,Ambuye azikudalitsani mamay❤
@TonyMhone
@TonyMhone 14 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤ Thump up Akweni for still clinging to UTM
@victormaluwa6710
@victormaluwa6710 14 күн бұрын
Very much Happy to see Mai Kaliati again,,, Mai wathu, Mai wapfuko. Mulungu akudalitseni Mai wathu. UTM forever
@LingsoneChitsulo
@LingsoneChitsulo 14 күн бұрын
God bless you mama Kaliati for your humbled decision and tolerance.
@FracksonMadani
@FracksonMadani 14 күн бұрын
Zonyaditsa kwambiri kuona Kaliati akugwirana chanza ndi DK, kuli ine kuno kubva tseketseke. Salima woyeeeee😂😂😂
@ubs7030
@ubs7030 12 күн бұрын
Iweyo kuthyolo kwanu, anthu Ali ndi njala koma iwe ndi ankolo Ako a pitara simukuwathandiza, koma muli m'boma munawabela ndalama ndikudzilemeletsa nokha.
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 13 күн бұрын
Listening from cape Town pa boma that's the man l lov Dr kabambe and am happy to hear that your at my home place rirangwe that where l grow up from yoooo guy keep it up and go down kwa lundu uko plz
@kaberaericdeo118
@kaberaericdeo118 10 күн бұрын
Very happy to see Dr DK together with his advisor Dr Akweni Kaliati Patricia and UTM committee members in this rally.
@SusanZulu-k1q
@SusanZulu-k1q 12 күн бұрын
Down to earth honourable Kaliati that's great God Almighty bless you.
@merryMaele
@merryMaele 13 күн бұрын
Mai Kaliati.Good morning 🎉 pitirizani ntchito yabwino.ndinu munaonetsa dziko kuti mphunzitsi angachitenso zakupsa give support to UTM.Gods time.is.the best One day you will be our Thatcher.Good Times .Akweni
@DeborahNyirenda-ls1ip
@DeborahNyirenda-ls1ip 13 күн бұрын
Mai Kaliat,nimai wachikondi Komanso uyu ndiolemela kale Sangapange sanje ,mzimai olimba mtima uyu . Mulungu akudalitseni aMai Kaliat,ndipo nakondwa kumva mau anu mama may God bless you 🙏🙏💕💕💕
@stevennthukwa
@stevennthukwa 14 күн бұрын
Love this woman l tell you a woman who knows what is right at the right time we honor you mama God bless you
@chimwemwebanda9939
@chimwemwebanda9939 14 күн бұрын
Mama kaliat love you without you we are nothing 🎉
@MikeChimombo-n6w
@MikeChimombo-n6w 14 күн бұрын
utm chipani cha athu ozindikila 🔥🔥🔥kaya azawina kaya azaluza km i will vote for Kabambe
@FracksonMadani
@FracksonMadani 14 күн бұрын
Kuganiza kwa bwino, inenso DK my vote
@LinlyMathewe
@LinlyMathewe 14 күн бұрын
Indee iwe Dr Kabambe my vote ❤❤❤❤
@dennisgunsalu7934
@dennisgunsalu7934 14 күн бұрын
DK my way to go❤
@Faidesi-t4k
@Faidesi-t4k 13 күн бұрын
Sorry. Utm
@CeciliaArmandoArmando-r8e
@CeciliaArmandoArmando-r8e 13 күн бұрын
I support UTM koma mukadaasiya za ndege komanso imfa ya Chilima tiwasiye aunse mumtendere basi tidziwapempherera kuti Mulungu auusitse mu mtendere nzimu wawo
@honestakamata474
@honestakamata474 13 күн бұрын
I salute you Mama Kaliati,,, strong woman ❤
@HarryMsudzula
@HarryMsudzula 14 күн бұрын
Now I can see solidarity in UTM fire mabomba
@ShalonChombo
@ShalonChombo 14 күн бұрын
Mai kaliyati more fire
@kaberaericdeo118
@kaberaericdeo118 10 күн бұрын
Mature politician Dr Patricia Kaliati Akweni is indeed among the UTM pillar members who knew the party and late UTM's President Dr Saulos Kraus Chilima and his vision for Malawi.
@TameeraInglis
@TameeraInglis 14 күн бұрын
Viva. Mayi. Kaliyati Mayi. Odzichepetsa , mulungu azikutsogolelani. Ndi kukutetezani
@Auscarmbeye
@Auscarmbeye 12 күн бұрын
Vote akaliyati 21 remember 😂😂😂😂
@AnnieMulumbe
@AnnieMulumbe 14 күн бұрын
Akweni i love you ❤ happy to see you with Dk
@FracksonMadani
@FracksonMadani 14 күн бұрын
Muwineeeee, musawineeeee DK my vote
@feranjifeza6802
@feranjifeza6802 14 күн бұрын
Without you kaliati utm is nothing.bravo
@noorbuildingcontractors3992
@noorbuildingcontractors3992 10 күн бұрын
Kabambe my vote
@ubs7030
@ubs7030 12 күн бұрын
Iweyo mmene unkadzilandilitsa 30 million, umawaganizila anthu? Lero poti ukufuna upulezidenti nde uzikhala ngati umakonda anthu?
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 14 күн бұрын
Ur humble mama kaliati, God bless u all the time
@MariaPhiri-s3u
@MariaPhiri-s3u 14 күн бұрын
Dr, please come to the north. When you will be in the north please try to travel from Rumphi through Nthalire to Chitipa boma. The long awaited road since the British came to rule us. We are still waiting for that road to be have bitumen. I need UTM govt..inflation to be at one digit. Bravo UTM.
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 14 күн бұрын
My Vote ❤
@LucyKamoto-li9ob
@LucyKamoto-li9ob 14 күн бұрын
Mai kaliati may the Lord be your guide
@TennysonMulimbula-q5j
@TennysonMulimbula-q5j 14 күн бұрын
Will definitely vote DK for presidency
@RishardSamison
@RishardSamison 14 күн бұрын
Dr. Kabambe tsogoleri wodzichepetsa wosavala ma glass mmaso
@Wyson-bo3sp
@Wyson-bo3sp 13 күн бұрын
Kubvala magalasi zimathanthauza kuzikweza kodi?. Tadziwa nawo.
@WillyMasangwi
@WillyMasangwi 14 күн бұрын
Akweni inu ndi one
@DoreenMuhota
@DoreenMuhota 14 күн бұрын
Viva kaliyati viva❤❤
@dankopland-dp3vx
@dankopland-dp3vx 10 күн бұрын
Uyu ndi katundu anangokhala mzimayi olo Chakwera sangamake
@MilliamJonas-p4t
@MilliamJonas-p4t 14 күн бұрын
Akweni mumatha ndipo Mau anu ndi amphavu
@PiusKanjuchi-x4s
@PiusKanjuchi-x4s 14 күн бұрын
Ine ndanva kukoma mumtima powawona mayi kariyati uremu wanu mayi
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te 14 күн бұрын
Mama God bless you
@billymhoni9527
@billymhoni9527 13 күн бұрын
Kuswa kweni ati alipo mwamuna anaitanira mzake mkazi wake.....???ati boma Saendasa munthu mmodzi.
@LovenessKapindula-t6e
@LovenessKapindula-t6e 14 күн бұрын
Mumatiimilila mam inuyo ndi one palibeso
@JohnPhiri-t2r
@JohnPhiri-t2r 14 күн бұрын
God bres mai kaliyati opanda sanje.tiyeninayo mcp igwe basi
@BERNARDSIKWESE
@BERNARDSIKWESE 14 күн бұрын
Please go north, Chitipa_ chinunkha ,ifumbo, ichinga,misuku, nthalire, ipenza, kameme, chisenga, nthalire
@noorbuildingcontractors3992
@noorbuildingcontractors3992 10 күн бұрын
My vote
@TiongeChirwa-b6j
@TiongeChirwa-b6j 14 күн бұрын
Zikomo amayi kaliyati takunyadilani mayi wozichepesa
@AlicePondani
@AlicePondani 14 күн бұрын
Doctor Patricia kaliati boma
@mikekamanga45
@mikekamanga45 12 күн бұрын
Pano ndakwera utm
@LinlyMathewe
@LinlyMathewe 14 күн бұрын
Welcome mumie we love you so much❤❤❤❤
@ubs7030
@ubs7030 12 күн бұрын
Kodi alomwe mitu yanu imagwira koma? Zimenezi muzikachita ku Mlakho kwanuko.
@MissyThobve
@MissyThobve 14 күн бұрын
Akweni takunyadirani kwambiri, mwainu muli mphanvu
@JonathanBonongwe-f3s
@JonathanBonongwe-f3s 14 күн бұрын
Ine ndili konko
@MargaretNkhata-b4n
@MargaretNkhata-b4n 14 күн бұрын
Akweni chonde Musa bwelere mumbuyo liphulani ziko pamoto ili chonde pamozi ndi a adada ka bambe Ndine Michael kalikokha zhakata msimuko
@MillieMalakam
@MillieMalakam 14 күн бұрын
ndipo kaliat ndizimayi wodzichepesa kwambili guys osati usi ndimbuzi yamuthu kwambili
@AlfredJosaya
@AlfredJosaya 13 күн бұрын
Akweni sazatheka
@AbrahamLLoyd-xb2xc
@AbrahamLLoyd-xb2xc 14 күн бұрын
Powerful
@CeciliaArmandoArmando-r8e
@CeciliaArmandoArmando-r8e 13 күн бұрын
Tapangani campaign osati zimenezo za ndege zo
@MarthaChigonero
@MarthaChigonero 14 күн бұрын
Boma iro
@StellaMicheal-q1j
@StellaMicheal-q1j 14 күн бұрын
Munagulitsa UTM 24biliyoni amayi ayipa awa kukamutenga mulendo chonsecho akambala analipo Mai woyipa iwe kwen suwina u MP watha bs
@TsArKhaii
@TsArKhaii 13 күн бұрын
Propaganda yoti simupindula nayo
@JessieSuwediMasimo
@JessieSuwediMasimo 14 күн бұрын
Vava UTM my vote
@TsArKhaii
@TsArKhaii 13 күн бұрын
Viva
@EmmanuelSimthole
@EmmanuelSimthole 14 күн бұрын
Bwana ine pano ndagula kale machine koma koti ndkatenge fertilizer sindkukuzwaiii😢 tiyeni tisiye ndale malawi apite kusogolo
@RobertNgunga-b4w
@RobertNgunga-b4w 14 күн бұрын
Ndamva kukoma lero, poona Mai kaliat
@TiongeChirwa-b6j
@TiongeChirwa-b6j 14 күн бұрын
Mayi muli ndifundo zabwino
@BlessingsKachijere
@BlessingsKachijere 14 күн бұрын
Vincent kachijere boma ndilomweri osati mbwerera zinaz, kabambe yomweyo
@Princevenasiyo-b4b
@Princevenasiyo-b4b 11 күн бұрын
Akabambe azingopanga za u MP kwawo, he don't deserve to be the president, level yawo ndi chikomeni chirwa, nde akulankhula chani apapa. Tizimva za mkazi ndi ana ako ife.
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 12 күн бұрын
RBM under APM must work with himAPM.2025.
@ChoopsyaLloyd
@ChoopsyaLloyd 13 күн бұрын
Akanakhala ndichikoka akanawina ku conventions
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 14 күн бұрын
Mary Chilima should be a running mate of kabambe
@IsabelLuka-i8f
@IsabelLuka-i8f 13 күн бұрын
I doubt, Mary Chilima sangapange zandale pano, mwina kutsogoloko
@ValerieSteward-m8i
@ValerieSteward-m8i 13 күн бұрын
Tangopitani ku Dpp panokha simungawine
@JohnChiyazu
@JohnChiyazu 14 күн бұрын
DK MY VOTE
@RobertSoko-p1l
@RobertSoko-p1l 14 күн бұрын
A mcp khamu lija ndilit osamangoti khamu anthu awili🤣
@Eneth-w6l
@Eneth-w6l 14 күн бұрын
Mai uyu ndipangolin pachipani kukula uku takunyadilani
@ThomasMaxwell-ks7yi
@ThomasMaxwell-ks7yi 14 күн бұрын
Mayi❤❤
@DeborahMmango
@DeborahMmango 14 күн бұрын
Akatundu mai kaliyati❤
@DaudManyamula
@DaudManyamula 14 күн бұрын
Koma kaliati mmmmm uyu anapanga kkkkkkkk
@AngelaMhango-c2i
@AngelaMhango-c2i 14 күн бұрын
Ndale Za kwanthu kumalawi kunyozana si zonse chakwela abale Zina muziwauzako chilungamo anthuwa Kuti ndalama simabwela kungokhala all kulima kuli mteza chinangwa sizimalilila fertilizer munthu ukhoza kulima kugulitsa nteza uja ndugula chimanga chinangwa ndi simaso inuyo pamene mwayimapo mupanga company sichina mwayimapo mufuna ndalama zotchulukilapo auzeni anthuwa kulibe ndalama Za milacle azikalimbikila uko katundu kulikose wakwela all mupite kuziko lina osati chifukwa cha president auzeni ayike Pasi ng'omazo akalime mteza kukamwa kokuwila pamenepo alinako Koma kulima nde ayi
@ubs7030
@ubs7030 12 күн бұрын
Mutu sukugwila
@TasiMunthali
@TasiMunthali 14 күн бұрын
DK machine
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 12 күн бұрын
@AlicePondani
@AlicePondani 14 күн бұрын
My vote UTm skc Dk
@solobertkamunga2826
@solobertkamunga2826 13 күн бұрын
28million
@TsArKhaii
@TsArKhaii 13 күн бұрын
18 million
@esthermkwapatira1693
@esthermkwapatira1693 14 күн бұрын
Apule a u t m akuoneka odzikonda akungokamba zakulirangwe pa ma president onse wabwno anar bakiri basi
@MemoryMbepula
@MemoryMbepula 13 күн бұрын
MCP tried to kill the UTM and every leader. Akweni musatope
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 14 күн бұрын
Nokha simungawine aiiiiiiiii
@muyabasamson
@muyabasamson 14 күн бұрын
Zabwino kwambili
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss 14 күн бұрын
zaziiiiii
@DoreenBanda-hg7oe
@DoreenBanda-hg7oe 14 күн бұрын
Muziona
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 14 күн бұрын
Kodi kulilangwe ndimbali yiti kumalawi abale 😮😮
@amtvmw
@amtvmw 14 күн бұрын
Blantyre Nseu wa Zalewa
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh 14 күн бұрын
@amtvmw ok🙏🙏
@MariaJaya-s9b
@MariaJaya-s9b 14 күн бұрын
@@MaryNyirenda-nq3mh my village 🏡
@RoseThindwa
@RoseThindwa 14 күн бұрын
Utm akanasewera game iyi mwa smart posakulilana mitima ndi Judas guys akanatenga position n revenge zakuchikangawa
@FrancisChafudzika
@FrancisChafudzika 14 күн бұрын
Blantyre north
@MartinMajola
@MartinMajola 12 күн бұрын
Kabambe alinizelu not chikangawa
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba 14 күн бұрын
Masanje awa
@Felie-p7l
@Felie-p7l 14 күн бұрын
Ineso ndimamukonda zimai uyu chifukwa amanena chilungamo thawi zambili
@YoungMwacho
@YoungMwacho 14 күн бұрын
Mumati mutani, chipongwe chakupwetekani. You will need DPP for you to survive.
@JoyMwenemuzi
@JoyMwenemuzi 14 күн бұрын
Camera man tajambula bwino.
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 14 күн бұрын
Achakwera bodza ngati mkazi English for nothing
@TsArKhaii
@TsArKhaii 13 күн бұрын
😂😂😂
@BERNARDSIKWESE
@BERNARDSIKWESE 14 күн бұрын
Please go north, Chitipa_ chinunkha ,ifumbo, ichinga,misuku, nthalire, ipenza, kameme, chisenga, nthalire
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 13 күн бұрын
zaziiiii
The Best Band 😅 #toshleh #viralshort
00:11
Toshleh
Рет қаралды 22 МЛН
“Don’t stop the chances.”
00:44
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 62 МЛН
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34
The Best Band 😅 #toshleh #viralshort
00:11
Toshleh
Рет қаралды 22 МЛН