Рет қаралды 13,542
Zodiak Malawi
Mupologalamu ya Mphepo Zinayi imeneyi tikukambirana ganizo la Dziko la America loletsa akulu- akulu ena akale a boma kulowa mu dzikoli kamba ka milandu ya katangale yomwe akuyankha.#zodiaktv #zodiakmalawi #mphepozinayi