KODI CHI SULEMAN CHIMADALIRA CHANI? TAONANI WAPELEKA ZIFUKWA 10 ZOMWE SANAUZILE BOMA LA MCP ZIJA

  Рет қаралды 30,489

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер
@MacfensonManyamba
@MacfensonManyamba Күн бұрын
Muthu Ngati ameneyi ndimene akufunikila muno malawi osat zinazi
@geoffreykamoto-ex9wu
@geoffreykamoto-ex9wu 2 күн бұрын
Katundu omanga ndi mawaya thus great bravo
@yakinidagalasi
@yakinidagalasi 3 күн бұрын
alowa mmalo mwachilima ameneyu keep up man
@vivianmkwate8536
@vivianmkwate8536 2 күн бұрын
God protect Suleimana 🙏🏾
@HappyPhiri-s4l
@HappyPhiri-s4l 23 сағат бұрын
More fire big boss❤
@LukeMapukusa
@LukeMapukusa 2 күн бұрын
Our president keep fire burning 🔥
@MoseChikopa-qy3og
@MoseChikopa-qy3og Күн бұрын
Inu ndi big boss keep it up
@AimanTwalid-o6o
@AimanTwalid-o6o 2 күн бұрын
Wow Sameer sulyman,Maa Sha Allah, big up no fear
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Күн бұрын
God bless mr sulemana ❤❤❤❤
@TakalaniGlenda
@TakalaniGlenda 3 күн бұрын
Kodi Usi akamapita ku ma department boma Ena amauza akumeneko???? MCP zaChamba basi botanical hara kudzolowera kuyamwa magazi iwe ndi marshal ndi mamyna wako
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 күн бұрын
God ahead u my brother suleman
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 3 күн бұрын
Akatundu ❤❤❤❤❤❤❤
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Күн бұрын
Uremu wanu mr Sulemani......osaopa
@StainDandize
@StainDandize 2 күн бұрын
❤❤❤
@RuthJopilo
@RuthJopilo 2 күн бұрын
Kwa anthu oyipa mtima chilungamu chimawawa.koma apapa pitilizani big❤
@samsonhavenoyayshonga2609
@samsonhavenoyayshonga2609 2 күн бұрын
Abwana Suleyman amayenera kupita amagwira ntchito yawo thanks Mr
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w Күн бұрын
Amina.. muna
@StevenCatherineLazaro
@StevenCatherineLazaro 3 күн бұрын
❤❤❤❤ I love you Mr SM
@BernaChauluka
@BernaChauluka 3 күн бұрын
Osangotitu akatundu chabe , koma akatundu Omamga ndi mawaya ,
@GiftAndrew-d5n
@GiftAndrew-d5n 2 күн бұрын
amakwana kom sama u gays
@FelixMboma-o5v
@FelixMboma-o5v 2 күн бұрын
Give him a good position this guy plz plz bravo big
@omarajibu860
@omarajibu860 3 күн бұрын
Feteleza amene amasungira kumeneko amagula kugwiritsa ntchito ndalama zathu za misonkho, therefore any Malawian has the right to visit the place any time he wishes to.
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 күн бұрын
Good to see people recognizing excellence despite party. But you will find those in his own party jealous of him.
@ClementNkhata-w1o
@ClementNkhata-w1o 2 күн бұрын
Bwana ulemu wanu 15:16
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 күн бұрын
All ministers must be doing what Suleman is doing. He is doing his job!
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 3 күн бұрын
Eeeh mwala
@MikeChankhaza
@MikeChankhaza 2 күн бұрын
Nice bos
@EdwardMagaleta
@EdwardMagaleta 3 күн бұрын
Big man
@HolmanDazah
@HolmanDazah 2 күн бұрын
Ulemu wa Bwana suleman!!
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 3 күн бұрын
Our future president
@rodglae6657
@rodglae6657 2 күн бұрын
Mmwenyeyu?
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 2 күн бұрын
@rodglae6657 he is Malawian by birth
@CeciliaNchesi
@CeciliaNchesi 3 күн бұрын
Machine
@jacklinenkhata
@jacklinenkhata 2 күн бұрын
Probably the best guy Suleiman.
@ManganiStanley
@ManganiStanley 3 күн бұрын
Machine eni eni ndipo live atenge mpando wachaponda
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 күн бұрын
God bless you suleman❤
@MynessChirwa
@MynessChirwa 3 күн бұрын
🔥🔥💙
@MosesIssa-v5d
@MosesIssa-v5d Күн бұрын
Suleman ndi katakwe munthu ozisata bwino kwambiri bola bomali lisatipherenso munthu wathuyu ameen
@JosephDavid-e5g
@JosephDavid-e5g 2 күн бұрын
Live brother
@JulietMunthali-g9b
@JulietMunthali-g9b 2 күн бұрын
Our on pangoline machine bwana ❤❤❤❤❤❤
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 күн бұрын
MCP Gotani sapangapo chinthu instead of holding SSFMRA accountable kuti akonze zinthu afuna kumulangiza Suleman.
@Steven-q4u
@Steven-q4u 2 күн бұрын
Julius Malema 2 !!!!
@IvanRoux-vl8gu
@IvanRoux-vl8gu 3 күн бұрын
100% Big boss Samule Suleman go ahead saving the Nation Malawi
@MbeweMoosa
@MbeweMoosa 2 күн бұрын
Munthu azilimba mussah from south Africa
@andreabanda7838
@andreabanda7838 3 күн бұрын
Suleman minister of agriculture mu DPP 2025 oooooyyeee!!
@MacWilliamKaunda
@MacWilliamKaunda 2 күн бұрын
Kodi Mkulu wa SSFRM akudandaula chani,?Kampaniyo ndi yake? Suleiman Mumaitha Biggy
@Lhanow
@Lhanow 3 күн бұрын
Kodi maulendo amanganya aja amayendela madipatment aboma popanda notice aja ndi dipatment it yomwe inadandaula
@BlessingsTchapo
@BlessingsTchapo 2 күн бұрын
Alimbikile asara pang'ono kufika level ya Julius malema waku RSA,,,BIG UP Mr suleman
@jamessheki4293
@jamessheki4293 3 күн бұрын
Abwana
@alexsumani6823
@alexsumani6823 3 күн бұрын
akatundu
@wilsonchimtikaphiri9496
@wilsonchimtikaphiri9496 2 күн бұрын
Sure man osafooka,pulumutsani anthu osati awa kiyendetsa boma ngati chipani,akubisa chani??
@SaimonBanda-ez6km
@SaimonBanda-ez6km 3 күн бұрын
Samiya umakwana koma 🎉💙💙💙
@GiftBanda-s6c
@GiftBanda-s6c 3 күн бұрын
Sammer suleman machine
@MaxyMaida
@MaxyMaida 3 күн бұрын
Bi boss samaopa
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 2 күн бұрын
Mcp kulibe anthu anzeru ngati ndikunama chisanzo ndi chakwera oyamba mwanthu a mcp opanda nzeru
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 3 күн бұрын
Sureman ndiwe katundu osati enawa
@OvikhelhaNgomba
@OvikhelhaNgomba 3 күн бұрын
Kkkkk ati khani zopepuka koma Suleman ndikatundu
@HussenSinoya
@HussenSinoya 2 күн бұрын
Ndipo timasowa anthu olimba ntima ngati awa amaina achizungu osati achichewa,,,,chakwela,,,,chimwendo,,,zikhale,,,,kunkuyu,,,, nkaka,,,,gotani,,,si anthu omaika m'boma koma Sameer suleman ndi international sangakhale ndinzeru zokakwela njinga kunja koma zokawalilila anthu ake...
@ENNOCHHILL
@ENNOCHHILL 2 күн бұрын
Responsible citizen
@Efellofredson
@Efellofredson 2 күн бұрын
Ngati kuli phungu oyimila amalawi nde ndi suleman kupariament atakhalako 10 kungakome koma kupariament aphungu aboma anangopitako popanda choputila monga kudela la aphungu olamula anthu awo akumati chani akamamva akulimbana ndi suleman kupariament kuja monga akawavotelaso kukhala phungu 2025 chifukwa otsutsa ndiolamula tikuvutikila limodzi kumidziku
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 2 күн бұрын
Bwana Suleiman katundu okonda dziko lawo
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 2 күн бұрын
Kwambiri akanarengeza anthu akanankhara ma office ngat onkhulupililika true sureman
@SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON
@SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON 2 күн бұрын
No fertilizer up to date I don't know kuti tigula liti fertilizer am afraid,nthawi yatha, Suleiman sanalakwitse kupanga check fertilizer stocks...kulibenso ndiye Boma litiyankhe kuti fertilizer tiyamba kugula liti?
@AidaMwantani
@AidaMwantani 2 күн бұрын
Nkulu ameneyu Mulungu azimudalitsa
@augustinechibbalazi8897
@augustinechibbalazi8897 2 күн бұрын
Unrest in Malawi is at it's upper reaches both in political and religious sectors engendered by our viliacos' maladminstration
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda 2 күн бұрын
Suleman ndikatundu eee mp ena ku dpp zukani musagone lets fight chikangawa yajaira kwambiri
@lastonweness9877
@lastonweness9877 2 күн бұрын
Bwanawa ndi president wa msogolo Allah azimiteteza achakwera sangamuonere kukodwa asamale akhoza kuphedwa
@alicemalika677
@alicemalika677 2 күн бұрын
Commentator usamati ukawelenga point usamati ngati ndizowona Sullenman amaimilira Ife a Malàwi
@AckimMhango-v1x
@AckimMhango-v1x 3 күн бұрын
Uyu saimila chipani koma kuimila a Malawi
@RachealPongolani
@RachealPongolani 2 күн бұрын
Machine😂 kuyankha mopanda mantha😅
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr 2 күн бұрын
ulemu wanu boss
@EmmanuelPoison-n5n
@EmmanuelPoison-n5n 2 күн бұрын
Zitiyankhulilani amphawifebwana
@jogechawa6192
@jogechawa6192 2 күн бұрын
Suleiman for president
@rodglae6657
@rodglae6657 2 күн бұрын
Malawi not ready to have a president of Asian descent...mpaka Mmwenye akhale president wa Malawi?
@ClementNkhata-w1o
@ClementNkhata-w1o 2 күн бұрын
Alibwino kwambiri
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 3 күн бұрын
Boss suleman munacita bwino ukafuna kugwila wakuba sumanena umangopita.Timakunyadilani boss inuo mukanatenga malo a chaponda cifukwa ndinu olimba mtima, caponda wafatsa kwambiri.
@MavutoFodya-p1u
@MavutoFodya-p1u 2 күн бұрын
Ulemu wanu big
@SAULOSAUFI-gu5nb
@SAULOSAUFI-gu5nb 2 күн бұрын
Timakunyadilani ndinu munthu wakulu chilungamo chofuniki pangolini boss
@JustinMackiy
@JustinMackiy 2 күн бұрын
mulungu azikusogolera surman osabwerela mbuyo ndikusachita mantha chifukwa chilungamo chimayankhula ife tiri pambuyo pako ngakhale sitikuziwana km pankhondoyomwe ukutimenyela ndilinwe ndipo ndizakhala nawe
@StephenNkhoma-k5l
@StephenNkhoma-k5l Күн бұрын
Malawi atakhala ndi anthu ngat uyu bwenzi ziko lathu lili patali kwam'bili Koma am'bili amangosamala m'thumba mwawo
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 2 күн бұрын
Pangolini
@YusuffSalimu
@YusuffSalimu 2 күн бұрын
Katundu wathu WA Dpp
@HawaHussein-o5k
@HawaHussein-o5k 3 күн бұрын
Ambuye azimudalitsa sameer sureman atiimilila
@CharlesJames-f1w
@CharlesJames-f1w Күн бұрын
Achalume
@RabsonAufi
@RabsonAufi 2 күн бұрын
Ndi munthu wakulu ameneyo ndithu
@EmmanuelSambani
@EmmanuelSambani 2 күн бұрын
Sanalakwise ndi dindo modzi wa guru loona za ulimi ku nyumba yamalamulo koma enawo agolowesa ndale.
@Alexanderdzungu-i5o
@Alexanderdzungu-i5o 2 күн бұрын
Chilungamo alibe koma kupenga ndipo sadza khalapo president
@vivianmkwate8536
@vivianmkwate8536 2 күн бұрын
Akugeira ntchito zothabdiza mdziko lathu
@PatrickTobias-r4s
@PatrickTobias-r4s Күн бұрын
Mulungu aziwateteza bwanawa
@Moyoyohane-i9h
@Moyoyohane-i9h 2 күн бұрын
Inu choonadi cipweteka palibe cholakwa apa
@GrolyGondwe-e9s
@GrolyGondwe-e9s 2 күн бұрын
Katundu wenwen asulman
@Alexanderdzungu-i5o
@Alexanderdzungu-i5o 2 күн бұрын
Ndiwo penga uyo
@MichaelMtambo-j5n
@MichaelMtambo-j5n 2 күн бұрын
Amuyisiyile utsogoleri
@BwanaGD
@BwanaGD 2 күн бұрын
A hala mumati Kodi akudziwitseni inu kunali chani chanu kuti mudziwitsidwe
@EndkenChisuse
@EndkenChisuse 2 күн бұрын
Iyiyi ma guys a MCP yawawa 😅😅
@rodrickchikosa
@rodrickchikosa 2 күн бұрын
Kod a BS Malawi sizingatheke kusintha munthu oyankhulayu? chifukwa Pena mumayankhula mopanda ukadaulo komaso muyankhula ngati zamabodza nde aaaaahhh sizimasangalatsa
@JacobBelnardo
@JacobBelnardo Күн бұрын
Komaso mumachulutsa zolakhura mmalo motipatsira program
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf 3 күн бұрын
MBambande mam
@salmankhanofficiel.5018
@salmankhanofficiel.5018 2 күн бұрын
Mutu wako iwe 11 osati 9 😂😂
@McDonaldsLinthemba
@McDonaldsLinthemba 2 күн бұрын
Uyu ndi katundu
@Christopher-x4x4j
@Christopher-x4x4j 3 күн бұрын
Suleman ndikatundu
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 3 күн бұрын
Kuyimilala malawi anachita bwino asipika mukulakwisa ukufusa mafuso
@JamesYusufu-l6d
@JamesYusufu-l6d 2 күн бұрын
ndipo. imeneyo. similandu. anayendela zinthu. zamuziko. lake. bwanji. maikolo. usi . anapita. ku. lodi thilafic. kubulantaya. anafusa. ndani. zachamba. tayankhulani. zakugwa kwandege. osati. zopusazo. anthu. okuba inu. kodi. muziona. chakachino. ziliko. ziko silikusiyani. chocho. musaza misinkho yamalawi anthu okuba. boma. lambava
@PiasonAndrew-t7v
@PiasonAndrew-t7v 3 күн бұрын
Kupanda mantha kumandisangalasa
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН
To Brawl AND BEYOND!
00:51
Brawl Stars
Рет қаралды 17 МЛН
MK Party | Supporters fill Moses Mabhida Stadium
11:44
SABC News
Рет қаралды 23 М.
Sameer Suleman - Kwake kwatha
24:34
Malawi Top Talent
Рет қаралды 1,5 М.
Uthenga Wa Chaka Chatsopano wa Pulezidenti Chakwera
12:44
State House Malawi
Рет қаралды 10 М.
It’s all not real
00:15
V.A. show / Магика
Рет қаралды 20 МЛН