KODI MWAMVA? MEC NDI NRB ANABWELA LIVE LERO KUNENA MA WISE MOSAOPA MUNTHU NDI CHIPANI ~ ANTHU AWASO

  Рет қаралды 7,937

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 41
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u Күн бұрын
Iweyo ndi Yesu ukugwilizana bwanji chitsiru ngati iwe Kodi fiti nayetso amafuna Yesu
@SylvesterLupia
@SylvesterLupia Күн бұрын
Choka hule iwe wadya ndalama za MCP uko ukubwera kumayankhula zopusa machine anuwo sagwila ntchito tizagwilisa ntchito manual 😊
@EdwardSinoya
@EdwardSinoya 20 сағат бұрын
Kodi uja anakuwinitsani uja CHIFUNDO KACHALE uja munamuchotseranji?
@MacleodKumwenda
@MacleodKumwenda Күн бұрын
Ana opanda khalidwe mukutukwa anthu osalakwa
@ChidaPhiri
@ChidaPhiri 18 сағат бұрын
Achotsedwe onse anthu okula mitima amenewo
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr Күн бұрын
Munthu yemwe nthawi ya kalembera anali atagonekedwa ku chipatala, koma chaunzika alinacho. Pano wachila, mwati sakuloledwa kuzalembetsa kuti azavote? Komanso iwe Annabel umati umagwira ku mabwalo, zomwe anagamula acourt wa tiziti iwe sumazidziwa, kapena umanyalanyaza poti poti wasamila mbali ya MCP eti? Ok
@Dickies-mk8cd
@Dickies-mk8cd 22 сағат бұрын
Nde wati machine adzasiya kulemba ? kapena sindinakumvetse iwe Annabel? kodi sukumva kut machine akowo tikuwakana? zomwe zikuchitika kwa nebaku zimayamba ndiukhutukumve ngt omwewu .
@MwatithaJohnkambwiri
@MwatithaJohnkambwiri 20 сағат бұрын
Mtali manja ndi wa mcp sangagwire bwino ntchito yake
@SPEARJAMES-r7y
@SPEARJAMES-r7y 20 сағат бұрын
Kodi mukuonjezera kapena mukuyambiranso kalemberayu ?
@EladioDeyanira
@EladioDeyanira 11 сағат бұрын
Thanks for the forecast! I have a quick question: My OKX wallet holds some USDT, and I have the seed phrase. (alarm fetch churn bridge exercise tape speak race clerk couch crater letter). How can I transfer them to Binance?
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf Күн бұрын
NRB ndi amene anapanga zosokoneza Chifukwa amangobaeza anthu.Nkutopa kuyendela.Eeeeeeeee koma Za ulendo uno taziona.
@daviechannel8603
@daviechannel8603 18 сағат бұрын
Mmmmmm koma iweyo
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 17 сағат бұрын
Anthu openga ,dyera ,kudzikonda,ufiti,otembereledwa.MACHITIDWE AATUMWI 4:24 Mau amenewa achite nanu.
@CardoJustin-l7m
@CardoJustin-l7m Күн бұрын
Kumozambique ndiye kumene kuja mukuziona mmene zikuyendera
@tasmania527
@tasmania527 Күн бұрын
Mozambique si Malawi. Muzayerekeze kupanga misala ya violence mutaluza chisankho muzaona nyenyezi mmaso
@EdwardSinoya
@EdwardSinoya 20 сағат бұрын
@@tasmania527 🤣😂😂😂😂 Cadet kuopsyeza?🤣
@tasmania527
@tasmania527 20 сағат бұрын
@@EdwardSinoya Ndikunena a DPP wo. Ine si Cadet. Cadet ndi zoba. Yanga ndi MCP kumenya kugwetsa.
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 17 сағат бұрын
Muzafera zaweni ndithu nthawi yanu dyeranitu musamale ndalama mwapezazo.MUZAZINDIKIRA BWINO PATSOGOLO
@EliasMandalasi
@EliasMandalasi Күн бұрын
Anabelo ubele uzamuziwa munthu kuti akakwiya amawoneka bwanji uzaphedwa malawi wakwiya pano
@edfrenkampala7342
@edfrenkampala7342 23 сағат бұрын
Bwanji akuti kuyambira 29 Dec to 4 January
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 23 сағат бұрын
Ife Tinava kuti kupoto athu an apezeka ndi MA ayid ambili komaso kumangochi bwanji sitive Zosatil zilizose chifukwa chiyan
@MoneyTiririMgwagwa
@MoneyTiririMgwagwa 21 сағат бұрын
Ndipo kumangochi sananene bwanji
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 22 сағат бұрын
Azavotese ndipita aMalawi mwatan
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 23 сағат бұрын
Chimachitika ndichani mumava Madera Ena kuti machini akuvuta simupanga changu poka Pasa machini Ena pamene inuyo masiku samayima muzitani kwina kukavuta machini kumbaliyako ya masiku, chifukwa athu amati chimakhala chinyengo choti masiku azitha machini asakugwila chito,
@alickmaunda7365
@alickmaunda7365 16 сағат бұрын
Kma muzimayi uyu ndiwowuma mutima koma
@CardoJustin-l7m
@CardoJustin-l7m Күн бұрын
Ngati zili choncho ndiye azilemba chani? Komanso aziwadziwa bwanji kuti ndioyenerera ku walemba? Chitseko chawaphana anthu awa bas
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 18 сағат бұрын
2025 usamangidwa nosenu mbafa
@ManuelMagombo-m2u
@ManuelMagombo-m2u Күн бұрын
Zouza a MCP.
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Күн бұрын
kodi za machine mulola kuti agwile nchito inu amalawi muganize bwino sure
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi Күн бұрын
Zathekano mumafunazo munalemba Ana Kale Kale
@ThomasJohn-j8x
@ThomasJohn-j8x 23 сағат бұрын
Zikuvuta pati kuwachotsa mmaudindowo
@TakalaniGlenda
@TakalaniGlenda Күн бұрын
Mbava Okuba Vinkhungu Isgebengi zonsezi
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera Күн бұрын
The problem is that MEC chairperson is apupet of MCP $NRB as well.
@AmonSugar
@AmonSugar Күн бұрын
😢😢
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 22 сағат бұрын
Koma pa nyimba panu anthu akudya😂😂😂😂😂mayi wachisili kwambwa
@HamuzahBamusi
@HamuzahBamusi Күн бұрын
Amai awa pofunika angopasidwa mimba seriously
@EstherLongwe-k8d
@EstherLongwe-k8d 23 сағат бұрын
Kkkkk
@dennismwenifumno994
@dennismwenifumno994 18 сағат бұрын
Kod anthu azipaniwo mukuwamva za mapempho awoo kapena inuyo ndee oyenera kupempha .. Anabel and your friends from NRB you are igniting the war in this country and you know it but you are just pretending.
@mikemkisi1624
@mikemkisi1624 Күн бұрын
Mumanfuna Jane Ansah
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 108 МЛН
黑天使只对C罗有感觉#short #angel #clown
00:39
Super Beauty team
Рет қаралды 36 МЛН
Tuna 🍣 ​⁠@patrickzeinali ​⁠@ChefRush
00:48
albert_cancook
Рет қаралды 148 МЛН
The Morning Show: President Tinubu Holds Media Chat
27:19
Arise News
Рет қаралды 1,2 М.
MALAWI - LILONGWE CITY TOUR
4:52
A.I.PATRICK
Рет қаралды 7 М.
AM News@7 28 December 2024 | NTA
18:21
NTA Network
Рет қаралды 40
ACHAKWERA SINDINGAOPE KUYANKHULA KWA SULEMAN
24:40
HOT 265
Рет қаралды 1,5 М.
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 108 МЛН