KOKUDA-IDA CHIMWENDO BANDA WAYALUTSIDWANSO NDI COMRADE CLIFF CHINYAMA

  Рет қаралды 8,639

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 30
@StellaDindimanga
@StellaDindimanga 7 күн бұрын
anthu ngt awa ndamene akufunika m'dziko muno ambuye akudalitse ase 🙏🙏 umphawi sumaphadi ai
@EllenNyirenda-ne4hv
@EllenNyirenda-ne4hv 9 күн бұрын
Akunama brother akufuna munthe ngati Ben Longwe auzeni chilungamo achimwendowo
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 6 күн бұрын
Mulungu akudaliseni ndi mau anuwo🙏🙏🙏🙏🙏
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 10 күн бұрын
Man mudzipemphera molimba tikukhal dziko lomwe satana watizungulira koopsa komas simumadya pakhomo lamunthu simumapempha munthu ndye mtima pa center basi mitima yathu iyadzamire kwa Mulungu bc
@ChristianMalingamoyo
@ChristianMalingamoyo 5 күн бұрын
We still have angels in malawi
@MathewsJanuary
@MathewsJanuary 10 күн бұрын
Powerful message
@CourageBanda-d1g
@CourageBanda-d1g 10 күн бұрын
Well done 👍 bro
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 6 күн бұрын
🙏🙏
@rajtwaihassan
@rajtwaihassan 6 күн бұрын
Zoona zake❤
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 10 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂komatu zochititsa manyazi mwava achimwendo
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 10 күн бұрын
Mulungu akudalitseni brooh
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 10 күн бұрын
Aaah amafuna akuguleni bigy apapa nde cimwendo wayaluka basi ndizomwe mcp ikucita kugula anthu za zii a malawife cisankho tapanga kale 2025 APM boma! Osati inu aaah palibe ca mzeru mwapanga.comrade cliff big up 2 u mwaonesadi kuti mumatiyimilira ufe osaukafe pitilizani tili pambuyo panu bigy musatenge kobili za cikangawa za magazi.
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 7 күн бұрын
Auzeni malume a chimimba chachikulucho
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 4 күн бұрын
Chilungamo bro
@AlexanderBilliat
@AlexanderBilliat 10 күн бұрын
Auze ase
@MartinKapito
@MartinKapito 10 күн бұрын
Ambuye akudaliseni ndipo adzikutetedzerani powaimilira amalawi amene sitingathe kuyakhula zikomo brother mukanireni ndalama. Zake zasayanic
@ChristinahNkwanda
@ChristinahNkwanda 7 күн бұрын
😊
@McshonWilliam
@McshonWilliam 10 күн бұрын
Akagwere bas
@AaronByson
@AaronByson 3 күн бұрын
Mbambande bro mumakwana km inuyo chakwera achoke bas
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 10 күн бұрын
What is this world turning into pliz God hv mercy on ur pple ndlama zomwe akugawazi tasisan fertilizer tigule otchipa amphawife abale sisan chimanga akapolo ife tisamagon ndinjala sife aulesi koma pavuta mpaground akumipandonu pliz pliz tionane ku inbox mundipze
@LovemoreChiwaza
@LovemoreChiwaza 9 күн бұрын
Strong man
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j 10 күн бұрын
Ndipo bans imeneyo ikboza kukuthimba pakhosi kuwasiila zaphulikile okha
@IbruraAmadu
@IbruraAmadu 3 күн бұрын
Iweyo ndi opepera moti ulandile ndalamayo then ndikumayankhula..ubwino wake samatipeza ife ayawo
@NelsonKalongonda-s4w
@NelsonKalongonda-s4w 10 күн бұрын
Umakwana
@LimbaniSamueli
@LimbaniSamueli 6 күн бұрын
Ndiwe dolo 🫡
@lawremmakanyenda3390
@lawremmakanyenda3390 9 күн бұрын
Za ziiii
@peterbyson6269
@peterbyson6269 6 күн бұрын
Madala auzeni anthu amenewa sakufunika mmalawi aononga kwabasi
@AlabAjuli
@AlabAjuli 5 күн бұрын
Kkkk zoonad big
@StarchJonas
@StarchJonas 5 күн бұрын
Man musati umphawi wanu umakukwanirani ayi inu si mphawi koma amphawi ndi iwowo amene alinazo zambiri koma akukakamira kuti azipezabe zina.
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 10 күн бұрын
Mau Mau Mau achoke basi crocodile muthu oyipa kwambili ngati idya amin ameneyo ndi nzake manganyayo achoke snake manganya
Face To Face Harapan Episode 25 | December 13, 2024
42:15
TV5 Philippines
Рет қаралды 3,8 М.
How many people are in the changing room? #devil #lilith #funny #shorts
00:39
路飞做的坏事被拆穿了 #路飞#海贼王
00:41
路飞与唐舞桐
Рет қаралды 25 МЛН
So Cute 🥰 who is better?
00:15
dednahype
Рет қаралды 18 МЛН
TAMVANI ZOMWE NSUNDWE BARRACKS YAUZIDWA- ISAIAH MSUNGAMOYO
10:54
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 19 М.
Новости дня | 13 декабря - вечерний выпуск
11:50
Euronews по-русски
Рет қаралды 6 М.
COMRADE NTANYIWA 10/12/24 ZOKHUZA MAI YOLAMU
22:45
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 7 М.
How many people are in the changing room? #devil #lilith #funny #shorts
00:39