KOMA DPP NDE IKUYESESA NDIPO ILI NAZO SERIOUS ~ ZOONA ANGAMUPANGE IZI WA MCP? TIKAPUMA KUMWAMBA BASI

  Рет қаралды 38,865

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 124
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 16 күн бұрын
Mukamatitu siichoka,muzionanso mbari inayo....Aganyu nde ntchito yanu....Kuombela m'manja,zosayenela uombela...Cholinga mupeze ndalama.....Nde dziko lapansi limenelo....AMUM ndi Adad Kumpanda❤❤❤❤
@MaryNgola
@MaryNgola 16 күн бұрын
Ife ndama brues 💙💙
@MandalaChaona
@MandalaChaona 13 күн бұрын
Amene akuti MCP sichoka ali ndi Ufiti obadwa nawo nayenso ndi mphyodza Magazi ndi mikodzo Ali mgulu wothudzula Dzithuphya Kupha basi
@rashidadan2533
@rashidadan2533 16 күн бұрын
His exllence professor Peter muthalika , The president of the republic of Malawi 🌹 Congratulations 2025 election 🌹
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 16 күн бұрын
Zinthu sizilibwino ku Malawi, bola APM ndi DPP. Chakwera adzikavina nyawu kwao
@IssacMateyo
@IssacMateyo 13 күн бұрын
Kodi sizilibwino apm amagawa ndalama kapena amakupatsani chiyani zazi ayi bola kalelo udali ndichiyani apm akulamula
@MandalaChaona
@MandalaChaona 13 күн бұрын
@@IssacMateyo 🤪🤪🤪🤪Shame on you ndiye Kuti Mkhamza akupanga mnyamata wanu wothudzula dzithuphya sukuziona ?? Kupha, Kuombera paliponse ukufuna unene chani apa
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 13 күн бұрын
MCP sichoka Koma ichotsedwa ngati chipani cholamulira dziko pa 16 September chaka chino.
@ArnoldSefasi
@ArnoldSefasi 13 күн бұрын
Amene akuti sachoka ndi garu komaso amatamba ndi kupha komwe
@ChionetseroGabriel
@ChionetseroGabriel 12 күн бұрын
Ife tkunjoya
@RosinaPatel
@RosinaPatel 16 күн бұрын
APM my vote
@MasaMasina
@MasaMasina 16 күн бұрын
MCP my vote
@MandalaChaona
@MandalaChaona 13 күн бұрын
@@MasaMasina 😜😜😜😜 Enanu CHAKWERA yo ndi Ankolo anu musatipusise apa. Kapena muli mgulu logulisa Ufulu ndi 2000 Kwacha hahahaha 🤣🤣
@isaaczuze
@isaaczuze 12 күн бұрын
Chakwera achoka ilitu ndi ziko .....sitingamapitilile kuvutika chonchi ayi
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h 16 күн бұрын
APM my vote my favorite
@Dayanschirwa
@Dayanschirwa 13 күн бұрын
Waona nyekwe
@KondwaniGumba
@KondwaniGumba 2 күн бұрын
Boma sitikusintha komaso mtsogoleri. Akusangala ndi olimbikira osati only m'chewa.
@EmilyBanda-xx8gd
@EmilyBanda-xx8gd 13 күн бұрын
Kudalira machine smartmatic
@willystima-x6f
@willystima-x6f 16 күн бұрын
Wamagarimotoyo asaname anamudyera ndalama ndimahule akuti sizikuenda nde bwezi ari nd mitara
@AlexanderYovatiKhumalo
@AlexanderYovatiKhumalo 12 күн бұрын
Mafunso a ma bodza opanda chilungamo.ukazitapee basi
@KapitoDaire-n1h
@KapitoDaire-n1h 16 күн бұрын
Very soon mcp out brother
@EnelessBanda-x5n
@EnelessBanda-x5n 12 күн бұрын
Nsabwe zake waures i
@StoreNkhoma-ii2lo
@StoreNkhoma-ii2lo 13 күн бұрын
Anthu aDPP ndinu abodza uyuyu uyu siwa MCP koma ndiwa DPP
@Mohammed-sk1fy
@Mohammed-sk1fy 12 күн бұрын
Nkhan siyakere imeneyi
@JosephGama-v7r
@JosephGama-v7r 13 күн бұрын
Bambo ndinu opanda nzelu
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 13 күн бұрын
Popanda chilima ndi Mia mcp singawine
@EmonDiel-g2p
@EmonDiel-g2p 10 күн бұрын
Inuso popanda bakili mluzi bwezi dpp kulibe bola ife mcp ndiyachikhalire munaba anthu ku udf simudzawinaso
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 16 күн бұрын
Mcp never again
@ArnoldSefasi
@ArnoldSefasi 13 күн бұрын
Ichika ndiwe garu
@EmonDiel-g2p
@EmonDiel-g2p 10 күн бұрын
Iwe ndiwe wabodza koms iwe simchewa profesa analephera amalawi tinasintha kunatha maso molowam mchewa angakhare olowa maso ngati mwakom maskini wachabechabe
@JudithNthini
@JudithNthini 13 күн бұрын
Koma akulu ndiye munadatu kumeneko kunyasa
@DolothDiness
@DolothDiness 13 күн бұрын
Ife ndima brue bas
@DoreenLivata
@DoreenLivata 13 күн бұрын
Zoona bola dpp izi ndie ai iiiiiiiiiiii
@BonifaceBanda-s5l
@BonifaceBanda-s5l 16 күн бұрын
Kama grass yo muzen azalila wasara ekha uyo ku mcp
@AlicksonMakata
@AlicksonMakata 13 күн бұрын
Zivute zitani ife tipita kwa Chakwera chifukwa dpp ndi nkhalamba zonse mukuchita apa ndi zogawanitsa mitundu ndipo dziko lidzakhala mmavuto oipa ngati dpp.
@EmonDiel-g2p
@EmonDiel-g2p 10 күн бұрын
Kom kumalawi zitsiru sizizathadi mpake maiko azathu tayandika na nawo amatiseka inu muja wakalambira pita wina azikati afunika azikalamuliras amalawi kutyolo komweko kumpoto pakati kumwera nyasi zimenezo takana mwamuwona president alumbilitsa kumozambik 48years mchamata ngati mukufunabe nkhalamba ikaponi bakili chifukwa Malawi analamulira bwino osati mbavayi
@Maul-826
@Maul-826 13 күн бұрын
Iwe ukuti boma ndilomweli mutuwako wamva
@luckychimutu
@luckychimutu 13 күн бұрын
Boma ndi MCP
@MarthaMagwede
@MarthaMagwede 13 күн бұрын
Tulukani muchigobamo baba 😂😂😂
@StevenDastan-f5y
@StevenDastan-f5y 16 күн бұрын
Koma nde ndizoona Apm basi
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 10 күн бұрын
Mafuso aukape
@LastonChamila-s3h
@LastonChamila-s3h 13 күн бұрын
Umaiziwa ifa iwe kubwedwa kwa apolis ufuna kuzachuluke mziko muno ndiyanthu
@EdenBrigadia
@EdenBrigadia 13 күн бұрын
Amwene DDP si chipani ndi akubaso kwambiri amenewo pamene anali mu Boma siziyendaso
@GraceKANYOZA-e3v
@GraceKANYOZA-e3v 13 күн бұрын
Akutumani eti pitani mukamwe panado
@AdamMwamadi-p2j
@AdamMwamadi-p2j 13 күн бұрын
MCP paulendo
@GladysMagadi
@GladysMagadi 13 күн бұрын
Wakwiyandimfiti iwe tokotazakukhosizako mavutoako siachikangawa
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 16 күн бұрын
Ndikutitu boma ndi lomweri basi kulibe kusintha 🔥🔥🔥🔥 motooooo Uwoooooo MCP woooooyeeeee My vote Or mtapanga compane ku zilabu za mowa simngadzarowetso mboma munalephela kare kkkkkkk
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 16 күн бұрын
Kamwe panado uchila wamzeru angafune mcp mufuna chani kwaife a mcp ndipo kaya ndiyamanja timenyana pa 16 September pano olo mwana wa chaka chimodzi sakufuna chakwera chifukwa akusangalala ekha ndi Ana ake ndinduna zake ovotafe tikuvutika, ngati timavota ndife chakwera akuchoka ngati amavota ekha awina
@CharityMkandawire-t8u
@CharityMkandawire-t8u 16 күн бұрын
Even kulemba campaign ukanika mulanda munya the Blue's for boma💙💙💙💙💙💙💙💙💙
@MandalaChaona
@MandalaChaona 13 күн бұрын
@@WanangwaMfune M'bututu wa MCP omwe amawugwiritsa Ntchito kutayiramo madzi Onunkha Dzuwa likalowa ndiye ndi iweyo, Munthu opanda tsogolo. AMPHYODZA MAGADZI NDI MIKODZO anthu odziwa kuthudzula Zithupsya
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 16 күн бұрын
Kkkkkkk adapha Chilima akuti 😂😂😂
@KanyoriSiwandaBanda
@KanyoriSiwandaBanda 16 күн бұрын
Bola adad
@GladysMagadi
@GladysMagadi 13 күн бұрын
Chikangawa thawisilikumbaliyake
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 13 күн бұрын
Akuwuzani kuti pezani mnyamata wosati khalamba koma inu mungotchula anthu awiri bwnaji ma president
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 16 күн бұрын
Namagalasiwe ukanandiyandikila ndikanakuthira madzi otetha
@kelvinabigkelvinchimanthula
@kelvinabigkelvinchimanthula 16 күн бұрын
Nthawi sili mbali yathu ngakhale atalowa wina palibe moyo kusintha chifukwa tikuyenda ndi nthawi nde kampeni yanuyo mudziwe zimenezi
@AllanChabwela
@AllanChabwela 13 күн бұрын
zabodza zimenezi,
@TecnoPop3-k2c
@TecnoPop3-k2c 13 күн бұрын
Munthu ozindikira osatimbzizinazo zimangoombera mmanjazirizonse
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 15 күн бұрын
Spota wa dpp gt wamwa mowa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@HerlbertKaalis
@HerlbertKaalis 13 күн бұрын
Waganyu kwake ndi kuganyula basi kuti akhale ndi ntchito yokhazikika ayi kukomedwa ndi madzi amukwawa osati a Nyanja ayi uchisilu
@LeonardNapwanga
@LeonardNapwanga 13 күн бұрын
Thupi lakutha kalero
@Ayanali-cr4vy
@Ayanali-cr4vy 16 күн бұрын
Koma DPP sangawine payokha chocho pakufunikira apange alayasi
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 14 күн бұрын
inuyo,tadziwa,mulufuna,maudindo,mcp,woyeeeeeee
@OwenMunde-d8i
@OwenMunde-d8i 16 күн бұрын
Ochitachibwana ndi dpp azigwidwa nkuwaonetsa nyekhwe
@LimbikaniTambala-z1y
@LimbikaniTambala-z1y 13 күн бұрын
Kunena kuti achewa ndiwo akujoya m'dziko muno ndi mau chabe a pandale ngati kuli boma lopanda tsakho ndi limeneli la MCP ngakhale ma MP a dpp anzeru akuyamikira Dr Lazarus Chakwera. Vuto ndilakuti amene muli kuja kwa boma simukhakhulupilira zoti Dr Lazarus Chakwera mkuwina chisankho chija komanso mumafuna kuti ma president azingochokera ku Southern Region zomwe nzosatheka. Taonani ma udindo akuluaakulu a chipani cha dpp onse ndi a kumwera chipani chimatero. Ndiye mudzaliranso pa 16 September DR Lazarus Chakwera atawina chisankho.
@NozizweJambo
@NozizweJambo 12 күн бұрын
Koma pa 16 pa olo chakwela akudziwa kuti achoka pampando wauprezident
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 14 күн бұрын
walowaliti,ameneyo,mcp,
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 14 күн бұрын
mukamati,mcp,siwina,mudziyamba,mwatifusa,ifeyo,chifukwa,ifeyo,ndamene,tikavotela,mcp,
@Efellofredson
@Efellofredson 14 күн бұрын
Kulibe zimenezo kulilongweko mukugula feteleza akugula k20000?
@RichmanMpaso
@RichmanMpaso 16 күн бұрын
Wagala ma gilasiyo makutu ake atichimwisa
@amosmwale-o3b
@amosmwale-o3b 16 күн бұрын
Ichi ndiye chimbuzi chamunthu kwambiri
@Shaicdesigner
@Shaicdesigner 14 күн бұрын
Akuyankhulayo ndi mzungu
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 13 күн бұрын
Inuso mukufuna kupangila munthu zochita ngati 2020 katundu timagula 5000 ndi zaka five katundu ameneyo timayembekezaso kuti tigule 5000 yomweyo ndiye dziko silikuyenda anthu kale amyenda pansi kupita ku rsa koma pano munthu sangayende pansi kuganiza mozondoka kumeneko dpp anawotcha dziko ili chifukwa chakuba kukhala mchewa sizikitathauza kuti ndi wa mcp ndalama anakatenga kwa yaya ndiye paja zimapanga expire akapange renew
@AchinaKellz
@AchinaKellz 16 күн бұрын
osakutha bwanji
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 16 күн бұрын
Aaaah iwe Boma umalidziwa iwe pamtumbopo ungapanene kuti Boma. Mabvuzi ako wamva
@kelvinabigkelvinchimanthula
@kelvinabigkelvinchimanthula 16 күн бұрын
Zovetsa chisoni yooo mpaka kutukwana chonchi
@Efellofredson
@Efellofredson 14 күн бұрын
Gulu limenrlo nkuti atangolowa kumene m boma osati pano anthu akulila
@AwidsMaseko
@AwidsMaseko 16 күн бұрын
Koma muli pachintchito.Koma mumapanga zina kapena mukudyera ganyu ameneyu
@victorauwana7258
@victorauwana7258 13 күн бұрын
Zakale izi
@williamsalexmbonga
@williamsalexmbonga 13 күн бұрын
Mukuchita kumkakamizstu
@BlessingsmChiipira
@BlessingsmChiipira 16 күн бұрын
Mahule adakudyela ndalama iweeeeee,,, tawona khope yakoyo, udatha iweeeeee
@IssacMateyo
@IssacMateyo 13 күн бұрын
Kumangoti ayi zithu zikuvuta muthu ukugona kukacha pa bawo zikuyendela bwanji azanu akulima inu kulima ayi mupeza bwanji ndalama
@OwenMunde-d8i
@OwenMunde-d8i 16 күн бұрын
Apm timusakha ndiifeyo osati iweyo
@IssacMateyo
@IssacMateyo 13 күн бұрын
Amwene athu mumamba adasiya athu kukupatsani katundu kuti mugulitse
@AwidsMaseko
@AwidsMaseko 16 күн бұрын
Zaziii
@BlessingsmChiipira
@BlessingsmChiipira 16 күн бұрын
Siwakongolesi uyu , angokupenta kape iwe
@OwenMunde-d8i
@OwenMunde-d8i 16 күн бұрын
Dpp yayaka moto ikudutsa bs 2025
@AlickDodoma
@AlickDodoma 16 күн бұрын
Kkkkk Dpp zosatheka kubwelela...
@alliewailesi6692
@alliewailesi6692 13 күн бұрын
Mavuto omwe tukumana nawo sangathe ndi Pita ilo ndiye bodza mitu yanu sikugwira!! Ine phee Ku ma stand
@AllanChabwela
@AllanChabwela 13 күн бұрын
inuyonso mulo ndi bodza,ngati mukunba kukoma ndiinu nokha
@alliewailesi6692
@alliewailesi6692 13 күн бұрын
@AllanChabwela Not kumva kukoma but to be honest Peter sangatithandize and he was just lucky kut zinthu zimkayenda bwino like mvula imagwa bwino etc koma tikanakumana ndi milili ngati yafika mu nthawi ya Chakwera tikanaziona kuposa izizi believe me Imagine issue ya magetsi mu nthawi ya Peter ngati inali bwanji
@MandalaChaona
@MandalaChaona 13 күн бұрын
@@alliewailesi6692 Za Mavuto zili apo koma mkhalidwe wa Kupha, Mkhamza ndi Tsankho sitikuzifuna. Kodi ambiri mudakagonabe hahaha 🤣🤣
@alliewailesi6692
@alliewailesi6692 13 күн бұрын
@MandalaChaona Ndale ndi dirty game!! Ndindani wandale ali clean?? Tsankho mwayamba kuliona lero? Ma cadet ntchito yao inali chan??? Simungandiuze zochita inu ine pano ndinazituluka koma to be honest onse andale ndi chimodzi modzi asakupusitseni
@DannyKalumbaWaBanda-q7o
@DannyKalumbaWaBanda-q7o 16 күн бұрын
Atokotatu Amayi;akut adapha chilima 🤣🤣🤣🤣
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 16 күн бұрын
Bolani Apm
@DolothDiness
@DolothDiness 13 күн бұрын
Moto kuti buuuuuu
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 16 күн бұрын
Kodi pa ground pake pati.akulu tidzaonana komweko kovotako mudzadye 70wanuyo Bambo
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 14 күн бұрын
siti,kusintha,noma,tivotela,chakwela,
@NrKasiha
@NrKasiha 16 күн бұрын
Ngt chakwela wakoyo sanalumidwe njuchi aona chaka chino kutenga kuchuluka kwa nsonkhano wa ena kumati chakwela wanyanao bas 2025
@kelvinabigkelvinchimanthula
@kelvinabigkelvinchimanthula 16 күн бұрын
Musamukakamize munthu chifukwa palibe adzakonza zinthu
@SylvesterSululu
@SylvesterSululu 16 күн бұрын
Kadye iwe zimilomo kuda ngati mcp
@AyasiWhite-l6s
@AyasiWhite-l6s 16 күн бұрын
Amayi ngoledxela km alindinzelu
@KelvinBanda-s1s
@KelvinBanda-s1s 16 күн бұрын
Kod inu kapolo otheratu ngt uyu mukut amapanga chiyan
@jamesbanda8602
@jamesbanda8602 15 күн бұрын
Komanso atolankhani zoona umalimbana ndi munthu oledzela sure?😂😂😂😂😂
@ChriOffice
@ChriOffice 15 күн бұрын
Nayenso ndi mzika
@ChembekezoSinjani
@ChembekezoSinjani 14 күн бұрын
zopusa
@OwenDubbyflitz
@OwenDubbyflitz 16 күн бұрын
Tikumudziwa uyu amakonda ma huge capital anadya yekha asanamizire chipani
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 13 күн бұрын
I have telling you stupid savege people amene amakonda kulubwa ludwa kuti MCP ndipovuta kutuluka m"Boma. Inu a DPP Kaya mbava za UTM mwachepa, mumaona ngati ndikunama, MCP sili pa social media apa AI. Ili pa ground
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 16 күн бұрын
Chavala magalasi cho chiri kukamwa nyindu ngati chadya manyi
@cynthiakamwana6809
@cynthiakamwana6809 16 күн бұрын
Nanga khani zakalekale bwanji?
@AchinaKellz
@AchinaKellz 16 күн бұрын
Sichoka chiphuno ngati nsana wa nkhono 😂
@DaudBonomali
@DaudBonomali 16 күн бұрын
amanane munthalika uja ndi ameneyu 😂😂
@ZioneMakumba
@ZioneMakumba 16 күн бұрын
Vuto Lina amaseweretsa ndalama popititsa ndalama ku chipani
@GeraldMukhuna
@GeraldMukhuna 16 күн бұрын
Koma abale osauka ndiolemela angawine ndani? Osauka amathamangila kodulachovotela like me olembela akuthanangila ndalama kumakajoya like my boss is not registered musamasewele ndianthu omweo amazisakila chakudya Chasikundisiku be careful
@LennieNyirenda-w6p
@LennieNyirenda-w6p 16 күн бұрын
Namagalasi wamwa Ambuye mtengeni😂😂😂😂
@AlexMagaleta-g7b
@AlexMagaleta-g7b 16 күн бұрын
😂😂
Zomwe Wayankhula Atupele Kumangochi, Ndipo Anthu Ndiodabwa...
5:41
Sam Malvitha
Рет қаралды 32 М.
Jaidarman TOP / Жоғары лига-2023 / Жекпе-жек 1-ТУР / 1-топ
1:30:54
Kaliati kuyankhulapo Zabodza La Michael Usi
6:51
Sam Malvitha
Рет қаралды 59 М.
MCP ndi Chakwera akuopa DPP; Report ya Afrobarometer ikuwachititsa mantha
13:30
Jaidarman TOP / Жоғары лига-2023 / Жекпе-жек 1-ТУР / 1-топ
1:30:54