KOMA HOT CURRENT YA LERO MPAKA KUFIKA POYANKHURA CHONCHI? ANTHU AWAWA ALIBE MANTHA NDIPO SAMAOPA

  Рет қаралды 16,871

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 80
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 4 сағат бұрын
Atleast there are guys like Wonder and his team who love Our Country!
@RabbecaMbukwa-y1z
@RabbecaMbukwa-y1z Сағат бұрын
Wow gyz,without beating the bush u r direct in speaking.U r hitting the nail.Osaopa,osafooka komanso osatopa gyz.We r with u.
@victorbanda9039
@victorbanda9039 2 сағат бұрын
Chunga you are professional
@UnityBasikolo
@UnityBasikolo Сағат бұрын
I salute U gentlemen
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 2 сағат бұрын
Keep it up guys i always waiting for this program amalawi ambiri aseguka mmanso chifukwa cha nu limbikirani ndithu
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma Сағат бұрын
More fire Mr kamangira
@georgenewa3508
@georgenewa3508 3 сағат бұрын
The only important radio station in Malawi Times
@HappykamwanamwanaBwaila
@HappykamwanamwanaBwaila 2 сағат бұрын
Mbambandee azibambo odziwa kuyankhula...... Time's Radio number 1 pa Malawi
@Yungjoe786
@Yungjoe786 3 сағат бұрын
Kamangila he’s there to save us,keep it up guys let’s support this guy
@SurprisedDrumKit-ql7rj
@SurprisedDrumKit-ql7rj 3 сағат бұрын
Kuri chawez Banda mtorankhan wamanyi😊😊😊
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 сағат бұрын
We have a government which we have never had in Malawi ever. Useless government.
@GiftKhwambala
@GiftKhwambala 35 минут бұрын
Keep it up
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 сағат бұрын
Times Tv Malawi ndi no.1, akulu akulu pitilizani mumalankhula bwino kwambiri, ndipo mulibe mbali.
@DanielNkhata-wt9ov
@DanielNkhata-wt9ov 3 сағат бұрын
No 1 guys paliso Chavez banda amaryaso chibazi
@MichaelKaerama-dd4bk
@MichaelKaerama-dd4bk Сағат бұрын
Hot current imayenda pamwamba kamangila alimomwemo ist afamily member thus why wabaya pofunikira ndi aliyense wamvesa and this is true
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 3 сағат бұрын
A chunga God bless u your talking sense
@NewtonTembo-q4t
@NewtonTembo-q4t 3 сағат бұрын
Very good guys please keep it up
@esmybanda2227
@esmybanda2227 3 сағат бұрын
Isalute you guys good speaking mcp zakuvutani basi vomerezani
@GeorgeTambala-j1m
@GeorgeTambala-j1m 4 сағат бұрын
Watching from Johannesburg in south Africa we Malawians we made a very big mistake by putting these stupid people into government but I hope we have learned a lesson
@Kelvin-hj5qv
@Kelvin-hj5qv Сағат бұрын
Inali bh🎉
@NickUpoche
@NickUpoche 2 сағат бұрын
Ndipo nde kwambili za equally zokhazo asamale ndipo masiku akupita pangono pangono mpaka 2025 tizafuna umboni koma wina Ali nkati
@TimeAbilu
@TimeAbilu 2 сағат бұрын
Kamangila (lets Government please give protection from him, this guy never seen and Allah gave long life Alex
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 3 сағат бұрын
Good advise but MCP imadzimva kudachulukako omwe adakhalako atsogoleri akudambwe kunyau. Athu ake amakhala okakala moyo.
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂okakaladi moyo😊
@KondwaniGondwe-y3d
@KondwaniGondwe-y3d 2 сағат бұрын
Kamangila pakufunika sapot yayikulu
@MikeNtantha
@MikeNtantha 25 минут бұрын
Ndizoona chawez wachibwana amayakhula mopusa kwambili ndipo anapatsidwa ndalama zambili
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 2 сағат бұрын
The only best way to change the rottness of how Malawi is run is by voting into government a new political party that has never managed the affairs of the country .
@HamzajOsman
@HamzajOsman Сағат бұрын
Dziko lovesa chisoni😂$440=K1,000,000
@HassanChibwana
@HassanChibwana 3 сағат бұрын
Kamangila way more fire
@AkiduMakwinja-x1h
@AkiduMakwinja-x1h 2 сағат бұрын
Look at South Africa mafuta it's already decrease last month koma Malawi ndipamene akupanga increase...what is that ma group wa Chakwera
@FatimaAdam-r5y
@FatimaAdam-r5y 3 сағат бұрын
Tithokoze kamangila potuluka poyela n,nyamata oganiza boo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@fleshar-j6i
@fleshar-j6i 2 сағат бұрын
Oky! Iyi simutchira mayina coz s allegations, about chimwendo yolesedwa kukwera ndege ija is not allegations??
@TiongeSimkonda
@TiongeSimkonda 2 сағат бұрын
Uyu watitenga a Malawi
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 3 сағат бұрын
And dziko azitsogoleri adakamakhala ndi nzeru ngati zanuzi panopa tili patali koma alliance iyiyi manyaka,,,Evance Meleka poimba nyimbo ya nthata zanjala ija mzimu udamulakhula mwapadera.
@benjaminjobo3525
@benjaminjobo3525 2 сағат бұрын
Malawi is captured by the big mafias 😢😢😢
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 сағат бұрын
Ya Chizuma imandiwawa ngat Imfa ya Chilima. Boma ili limadana ndi Chilungamo.... Always bodza,....
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 3 сағат бұрын
Ulemu wanu Inuyo mmmmh 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌❤️❤️❤️❤️❤️❤️
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 сағат бұрын
Ku Maida kuli George Kasakula, akubakila mcp komanso chakwera. Koma tiyamikile Mr. Kamangila , wakeup Malawians pls. MBC ndiyowola kwambiri.
@jonathanmbewe4246
@jonathanmbewe4246 4 сағат бұрын
Azibambo inu ayi mukuyankhulila amalawife zikomo kwambiri
@GiftMlinde
@GiftMlinde 2 сағат бұрын
Minister of Justice wake kutii kapee ameneujaaa
@MercyKishombe
@MercyKishombe 4 сағат бұрын
Ya Mai Chidzuma nde imandiwawa kwambiri. We didn't support that noble lady eeeeish! Malawi wanga😭
@dysonmasiye5736
@dysonmasiye5736 3 сағат бұрын
Ku NRB plus MEC kukufunikanso a Kamangira ena ukuku...akanika kuti amalawi apeze ma ID a unzika koma pano mukuti kalembera akuyamba m'mawa, what's that? Ndiye anthuwa adzavota bwanji?
@ShaibuSmart
@ShaibuSmart 3 сағат бұрын
Kamangila ulibooh anthu akukanika kumwa tea chifukwa chaiwe kamangira .Wagwedeza
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 44 минут бұрын
Atola khan ose aku mbc ose ndi achinyengo
@PaulBeyad
@PaulBeyad 3 сағат бұрын
Yes amazitengad ngati ndizawozawo anthu okanika awa
@RabbecaMbukwa-y1z
@RabbecaMbukwa-y1z Сағат бұрын
Osapanga ngati za khuluku uyu chawezi.Ndiwamadyera mphoto munthuyu.
@JawardBenard
@JawardBenard 2 сағат бұрын
nthawi yikakwana yimakwana basi tiyenazo musabwelere mbuyo nthawi yakwana iyi
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h 3 сағат бұрын
Kamangira azakhale nduna ya minister of justice and constitutional affairs muboma likubweralo. Kuti izi zizatheke pabwere boma Lina. MCP ndi DPP ndiamozi sangamangisane zitavuta motani. Aliyense alinawo ma jaji Ake ku judicially. Pakufunika boma Lina la new blood. Boma losaona nkhope ndipume tikufina kuti Kamangira azagwile ntchito yake bwinobwino.
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 3 сағат бұрын
Tafwa mwafwa enough is enough Malawi shocking country Martha Chizuma my comrade Mmmm xool mate 😂
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 сағат бұрын
100% ndiye kiyankhula ... Judiciary, mizila manja nonsense
@MrMagombo
@MrMagombo 4 сағат бұрын
A Jaji akulu imitsani ma Jaji akutchulidwa wa.
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h 2 сағат бұрын
Kupupuluma aboma. Mukuopa chaini? Asyeni a mademo, ndiufulu wap.
@GolosiMalapata
@GolosiMalapata 3 сағат бұрын
Chimene chingachitike anthu ose amene akuvutika asakamvote ayi aka vote okaoka sibwino kumazuza osauka ayi aba bolani so bingu wamutalika anayika ikonome osati zitsiluzo ayi sakuchita bwino
@PreciousSteven-e5s
@PreciousSteven-e5s 4 сағат бұрын
Ma guy awa akuyesetsa kuliwongolera boma koma eesh anthuwa ndiwokanika ndithu ndipo anthu opanda chisoni ndithu
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 сағат бұрын
Kodi jonna please give him for first time
@HamzajOsman
@HamzajOsman Сағат бұрын
boma la mamafia ili 😂😂
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 сағат бұрын
Pankhani ya a Kunkuyu, mmmmmmm , kunkuyu ndi boma akuyankha bwanji nkhani ya MEC ndi a kalembela?
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 3 сағат бұрын
Kkkkk komatu ndebvu zamwayi ungakwanise carat KKK manjawo umandipeza when speaking.
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 сағат бұрын
Pankhani ya mafuta, mesa Kabwira ndi Chakwera amakalandila mafuta ambiri ku Nsanje pa njanji? Alikuti mafutawo?
@patesnkajenda4258
@patesnkajenda4258 3 сағат бұрын
Malawian people samalowelera kamba kot kumankhala komvuta kulowapo komaso samadya nawo ndalama ndeeeee wina aliyese amaganizapo zoyakhula amakhala ataona phindu lake akayakhula guy's 😮😮
@KondwaniGondwe-y3d
@KondwaniGondwe-y3d 2 сағат бұрын
Koma malawi
@fanuelbanda2985
@fanuelbanda2985 3 сағат бұрын
Kamangira way
@PatrickMalenga-h5m
@PatrickMalenga-h5m 3 сағат бұрын
Kt ndizivutika vuto ndi matipate aliyeyese akakhala boma amalemera kwambiri kmas kuvota kumawonongetsa ndalama boma
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 3 сағат бұрын
Ndipo Akangila akaphedwa ndi MCP tikudzwa zioneka bola moyo
@MalumboMzumara
@MalumboMzumara 3 сағат бұрын
Chunga boma siiiii iliiiiiii
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 3 сағат бұрын
Zoona
@fjtkusamba5948
@fjtkusamba5948 4 сағат бұрын
Tokotani anyamata this government is full of educated ignorance and Malawi is dying alive
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 3 сағат бұрын
kodi mmayesa mcp inkati yalandila mafuta ndiye inuyo atolankhani bwanji simukuwafunsa achakwera kuti mmayesa paja anati alandila mafuta nanga alikuti mafuta aja ankawachemelela aja
@MaxwellMilanzi-w5k
@MaxwellMilanzi-w5k 3 сағат бұрын
Kkkkkkkk owo...
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 3 сағат бұрын
Chikangawa wamaliza folex yonse ndi ndege
@MartinRajab-w5e
@MartinRajab-w5e 4 сағат бұрын
Inu anyamata inu mumatilankhulila koma andale makani mmmmm
@GolosiMalapata
@GolosiMalapata 3 сағат бұрын
Azaona polekela asiyeni
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 3 сағат бұрын
Ma bigy inuyo mukunyapura boma n ma institution onse mosanyengelera ulemu wanu
@MaxwellMilanzi-w5k
@MaxwellMilanzi-w5k 3 сағат бұрын
Kkkkkk kkkk....
@EnockBeston
@EnockBeston 4 сағат бұрын
Muli bho
@RodgersMtonga
@RodgersMtonga 4 сағат бұрын
Inu mmatiyimilira
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 3 сағат бұрын
Azibambo inu...More Fire 🔥 ♥ 😍 ❤
@miovekanola2780
@miovekanola2780 3 сағат бұрын
😂
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 4 сағат бұрын
Corrupt judges in Malawi peter muntharika once complain about these judges blavo kamangira God bless u indeed tonse government won through corrupt judges
"كان عليّ أكل بقايا الطعام قبل هذا اليوم 🥹"
00:40
Holly Wolly Bow Arabic
Рет қаралды 12 МЛН
Smart Sigma Kid #funny #sigma
00:14
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 35 МЛН
Não sabe esconder Comida
00:20
DUDU e CAROL
Рет қаралды 27 МЛН
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 5 МЛН
LIMPOPO FM - AKULU AKULU ENA A MCP ANAPITA KUNYUMBA KWA BAKILI MULUZI
4:48
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 1,5 М.
"كان عليّ أكل بقايا الطعام قبل هذا اليوم 🥹"
00:40
Holly Wolly Bow Arabic
Рет қаралды 12 МЛН