KOMA HOT CURRENT YOOPSA IYI ~ AWULURA ZOMWE ANABISA AKOMISHONI AJA NDIPO SANGAKANE AGWIDWA UFITI

  Рет қаралды 26,446

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 135
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 15 сағат бұрын
Komatu anthu ambiri mutenga nazo tsoka pa imfa ya anthu ameneaja, Kunjakutu kuli Mulungu, ingotulusani black box kuti anthu adziwe chilungamo basi, chomwe mukuiwala nchoti kumwambaku kuli Mulungu, anafa aja ndi anthu ngati inu nomwe, tsiku lina mwazi wawo uzafuula pansi panthaka, mpamene muzadziwe kuti chigwada sitipanga salad😢😢😢, Ambuye dzukani anthufe tione ukulu wanu Yaweh 😭😭
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 3 күн бұрын
One day is one day..... Komano mwapindulanji powatsogoza azanuwo.........😢😢😢😢😢😢
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 15 сағат бұрын
Don't misslead people, that tv is national TV you must work without taking side, why you don't talk about black box
@chickob3859
@chickob3859 Күн бұрын
Guys hot current iyi mwamangika simukumasuka tidziti apule adakukozelani ka dongosoro kapadela dela? zikuonetsa ngati muli pachingwetu. Mukuti bwanji mr ndevu zamwai ndi anzanu.
@TywellShumba
@TywellShumba 3 күн бұрын
Kodi ngt sanachite kuphedwa munawapeza anthuo ali ndi zovala mwachidule munatolako ma phone 📱 zinthu mkubisa koma mkuti mumalankhula chilungamo chabozacho😢😢
@dennisrobert4617
@dennisrobert4617 3 күн бұрын
Ngozi iyi ikanakhala yachilengedwe bwezi black box atapereka kale
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 3 күн бұрын
Ngati ine mulungu anandiuza mmaso phenya kuti sinali ngozi
@jowiemhango5058
@jowiemhango5058 5 сағат бұрын
Ndipo ineso chimodzimodzi I dreamnt zimenezija zisanachitike ndipo ndimkalita anthu aja akuphedwa ndi anthu mmmhu
@lawrencedanielmandauka
@lawrencedanielmandauka 3 күн бұрын
Kupanga renew licence kungapangitse munthu amene Ali ndi experience ya 7 years kulephera kuyendetsa ndege zabodza izi zonse mukunena
@kennymwanyongo8165
@kennymwanyongo8165 3 күн бұрын
Why going round and round when information can be obtained from the BLACK BOX?
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
Iwe Ryan uzitenge bwin timakupatsani ulemu kodi vuto chiyani kune kunena kuti ngozi ija ndiyochita kupanga
@ShalmoInvestments
@ShalmoInvestments Сағат бұрын
Ndipotu wandinyasa
@BlessingSikefa
@BlessingSikefa 3 күн бұрын
Mulungu ndiamene akuziwa chilungamo
@BillyP0lly-x6n
@BillyP0lly-x6n 5 сағат бұрын
Good job azibambo
@ConduanieDicksonie
@ConduanieDicksonie 12 сағат бұрын
Kod lincence ikapanga expire, for example ya galimoto, umakhala kuti waiwala kuika ma gear??? Koma2 guyz, kunjaku kuli mulungu
@HolmanDazah
@HolmanDazah 2 күн бұрын
Ife akubanja tikuti, we've learnt more kuti they are really maphias our hero has gone .
@AnthoniohMazengera
@AnthoniohMazengera 14 сағат бұрын
Ma guys mwalandla ndalama simukusowa your speech all of you,mukufuna amange ndani guys muzalapa day one
@Ertyvhk
@Ertyvhk 3 күн бұрын
Why around the bush nkhani ya sikusinja ndi gwenembe iyi musaiwaretu panali kukanganira udindi wina 5 years wina 5 years ndiye ulendo usanafike wina akuti ine ndiimanso zivute zitani ndiye muzizungulira mutu wankhani mukuuziwa?
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 4 сағат бұрын
Ndili ku Matandani ku mpingo wa Thindi,ndidalika uthnga woti,"Tiuzane zoona."
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 3 күн бұрын
Koma mulungu yekha akudziwa zonse pangapite nthawi bwanji koma adzayankha zonse.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
😅😅😅😅😅 akulu akulu simukufunsa black box bwanj 😅😅😅 ,God knows.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
Guys osabisa chichewa apa,chilingamo mukuchidziwa,our brothers and sisters anavhita kuphedwa inu imeneyo ndichito gwirani chilungamo mukuchidziwa guys,no matter wat,angakupheni.
@MikeMsamalaphiri
@MikeMsamalaphiri 3 күн бұрын
They just described the outer description of the plane but they dont explain the technical fort of the plane. Kodi ndegeyo inagulidwa ilibe computer box? Why cant they get the information from the computer box and give us?
@HolmanDazah
@HolmanDazah 2 күн бұрын
Anthu maumboni ndiosayamba ndipo ogwirika koma MCP kuyambira kale ndiyakupha, anthutu akuopa kuphedwa. Inu mukidziwa kuti R. Kasambala anachita kuphedwa ndi kamajekete, after atamva zoti SKC ndi kasambala akambirana za withdrawn mu alliance? Did you know that? Ine am one of evident holder, I know every move they have made to kill SKC. Did you know kuti Army commander ndi pilot as well as asilikali analuza miyoyo together and SKC panali selective okhawo omwe amadana nao Verentino ndi amene anali involved pa infayi? Ife, kapena kuti ine sindingamve , ngati black box palibe thus it. Chakwera and his entire MCP government akufuna kuonwtsa ungweeu pa ise na Chiuta He must bring the black box pa open air, ndipo mitima ya a Malawi izausa!!
@dikenzthomo8284
@dikenzthomo8284 3 күн бұрын
Vuto lake inuyo pamenepo mumadziva kuti mumakamba chilungamo,mukuti simunyengelera,kudziva kwambiri basi
@JaiLamu-dk8wd
@JaiLamu-dk8wd 6 сағат бұрын
Tell dem
@jowiemhango5058
@jowiemhango5058 5 сағат бұрын
Ngat awawa akudzimva chilungamo why are they not talking about black box???? Useless pple
@andreabanda7838
@andreabanda7838 2 сағат бұрын
Why are discussing the report when you don’t have it physically?
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 17 сағат бұрын
Mr Chunga abalalika zedi pa nkhani ya composition ya Commission of Inquiry ya aircraft crash. Akuti a kubanja sanayenele kukhala mu composition ya commission. Akunama. Akubanja ndi omwe akanaonesetsa kuti panalibe za chinyengo koma the whole truth.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
System yachani we all need black box,to stop all these things
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
Wonder zanu ali mpakatiyi kitenge bwino
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 3 күн бұрын
Achakwera ndi chifukwa chani atauzidwa kuti ndege yasowa anayankha kuti azipasidwa lipoti after hours komanso chifukwa chani anauzidwa kuti ndege inafika ku mzuzu pomwe lipoti lakunja linati ngege sinafike ku mzuzu
@CCHANTHUNYA
@CCHANTHUNYA 18 сағат бұрын
It is incredible and disgusting that we have so many of us who have seen an opportunity and are intent on making political capital out of this tragic death. These individuals will never accept the findings of any inquiry.
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 17 сағат бұрын
I hope nobody wants to get a political mileage from the tragic aircraft crash. People simply want to know the whole truth & nothing but the truth emineting from the findings of the commission of inquiry. No stone shouldn't have been left unturned like detailed reports on equipment like the transponder & the black box.
@khalidmakwinja2560
@khalidmakwinja2560 18 сағат бұрын
It's not about thinking but the fact of the matter is that. MCP is a killer
@IbulaMayikolo
@IbulaMayikolo 3 күн бұрын
Ngati mukufuna kuti muupeze umboni wen iweni tuluzani black box
@ShalmoInvestments
@ShalmoInvestments Сағат бұрын
Ndani angamasuke kupereka umboni wakufa kwamunthu....kodi uja ankava ndege ikumveka ngati chigayo munamfusa?
@HolmanDazah
@HolmanDazah 2 күн бұрын
Aaaaa Chikangawa anali atawerenga kale, kumeneko kunali kuwawiza lilibwino kanene Kwa a Malawi. Komano apapa akungounikira kuti anaphedwadi, tawonano, wait all will be on open air.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
Guys kodi hot current ikuti bwanji kodi,sitikuvetsani mukuopa chiyani
@MatchadoKalinda-h5z
@MatchadoKalinda-h5z 3 күн бұрын
Ko munthu liacense ukapanga expire ndiye kuti satha kuyendesa koma ndalama ndizoopsa ili ndiye silikunveka bolanso loyamba lija waoo but don't think we're all fools times be sincere with Malawians
@RaphaelWinford-t7u
@RaphaelWinford-t7u 3 күн бұрын
Amanga ndani afiti amenewa😢😢😢😢
@noelmsiska3692
@noelmsiska3692 3 күн бұрын
Flying a plain like kekeke? Kumalawi tili pa mavuto Chilima anali ndi tsoka ndithu
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 2 күн бұрын
Chimene mungadziwe ndichakuti ufa ija ndiyokoza why? Vise president angagone ku tchire pamene asilikira alipo ndichifukwa chan amaresa kupita anthu pa nthaw yomwe ndege inangwa?
@JuniorJames-u8o
@JuniorJames-u8o 12 сағат бұрын
Inuyo a hot current tangosiyani mukukhalangati mukukamba zanzeru koma palibepo mukunena ndinu mazoba
@KondwaniChaponga
@KondwaniChaponga 3 күн бұрын
Ine ndingoti Mulungu yekha aweruze pa chimenechi
@thomasmphaluranyirenda9333
@thomasmphaluranyirenda9333 2 күн бұрын
Bwanji inu mpite mkafufuze ngati simukuzivesa ngongole yantha chakwera 2025 boooma🎉🎉🎉
@MikeMoris-zp6yg
@MikeMoris-zp6yg 2 күн бұрын
Ndizooon apited akafufuze
@ConduanieDicksonie
@ConduanieDicksonie 12 сағат бұрын
Koma anthu inu muli ndi mizimu???​@@MikeMoris-zp6yg
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 3 күн бұрын
Mizimu.9.yapita.kafukufuku.waboza.ameneyu.koma.ndalama.kumaopa.nazo.mulungu.
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 3 сағат бұрын
Mbwelera zanuzo ayi,we need black box
@MofatwilsonJohn
@MofatwilsonJohn 17 сағат бұрын
Lipoti labodza amanena kuti ndeke yagwela kokhwithima why?
@SailesGumla
@SailesGumla 23 сағат бұрын
30:43
@lastonkamanga4072
@lastonkamanga4072 Сағат бұрын
Muphetsa anthu 😂
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 3 күн бұрын
ife, tilipano, kudikila, amene, muli, ndimafus, kt, musavutike, ndikumafusa, pa, 4n, simungayankhidwe, funanaoni, kopita, akakutankheni
@austinevance3964
@austinevance3964 17 сағат бұрын
Adakhala kt chakwera akuyendetsa bwino kapena kt anthu sakumvutika sibwezi akuganizilidwa izi km chifukwa cha nkhaxa zawo anthu tili padzuwa chifukwa chake
@PatrickZinenanie
@PatrickZinenanie 3 күн бұрын
Where is a black box
@KimulaniImani-z4j
@KimulaniImani-z4j Күн бұрын
Big up guys
@SamuelBhanda
@SamuelBhanda 14 сағат бұрын
Awaso ndi amodzi mwaiwo paribe chikuvekapa
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther 4 сағат бұрын
anachita kukonza inu mwatopa akupatsani ka desemmber
@MMK-p3y
@MMK-p3y 18 сағат бұрын
"i wish the dead could speak"
@JannahThomas-iw5xu
@JannahThomas-iw5xu 2 күн бұрын
Anthu Olo ali ndi umboni kma mphawi ngt ine sangabwere poyera muboma lake ili Kod ma pilot ayamba liti awa ? Izi mkukamba za mapilot papers kambani zina , mapepala ndi experience nzosiya , sayemdetsa ndege ndimapepala km munthuyo ndi experience yake
@EvanceWame-v7v
@EvanceWame-v7v 2 күн бұрын
Kaniso hot current ndi mbali imodzi ya mcp
@ZimhungaEsther
@ZimhungaEsther 4 сағат бұрын
Phone ikagwa umaziwa ikabedwa imaziiwika sinyengo bodza mwadya timamitazoo. Mawa ndi abale anu
@AlumakioChingalu
@AlumakioChingalu Күн бұрын
wina asaname osakanena ku commission
@ConduanieDicksonie
@ConduanieDicksonie 12 сағат бұрын
Inunso mukudziwa kuti MCP ndi yomwe ija. Chilungamo mukuchidziwa koma mukuopa kusowetsedwa. Shame on u guys
@andreabanda7838
@andreabanda7838 3 сағат бұрын
Zonama zokhazokha. Apopo.
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h 3 күн бұрын
Working to please the president. Zizaululika zoona ze nizeniZeptember 2025.
@PatrickZinenanie
@PatrickZinenanie 3 күн бұрын
Inshort munapha chilima munthu wanzeru yemwe amayembekezera kuzaphula ziko la malawi lino 2025
@FridayKabade-t7x
@FridayKabade-t7x 15 сағат бұрын
Apa tiime pa chilungamo basi ngat a president sakuziwa kathu pa khani ya ifa coz iye ndi wa kulu wa asilikali police abwerese black box ndizomwe tikufuna kuti tiziwe choonadi cha ngozi kuti zinakhala bwanji ngati sipezeka black box akulu akulu ose amangidwe posatengela kut ali ndi udindo wanji
@AlexanderMbale
@AlexanderMbale 3 күн бұрын
We are proud of you mr musiska
@HarrisonMatiki
@HarrisonMatiki Күн бұрын
Lero mwadekhatu mafunso onse mumafunsa aja mwamwera burns
@MarthaMalopa-kw9xw
@MarthaMalopa-kw9xw 16 сағат бұрын
To be frank, program yokhayi munayamba mwakumana ndi akuluakulu omwe akuthowetsani zikhatho
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g 2 күн бұрын
Ngongole yatha bwa::iwe ukudziwapo kanthu::poti. Wakwanu panalibe
@StevenFombe
@StevenFombe 3 күн бұрын
Abusa anyerenda ziphaliwali corrupt pastor better kuyama
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 3 күн бұрын
Ngakhare nanuso kachilungamo mutumo kalimo kut ija singoz mukuopa kumangidwa anthu aja anachita kuphedwa nanga akut analibe magazi ndie mulungu analenga munthu opanda magazi mikozo mmmmm nanuso inuyo kharan chete inuyo simulungu simuzakharaso mulungu ndie Zina mumalankhura zaboza like nkhan iyi
@siyanimbuto
@siyanimbuto 2 күн бұрын
Awa palibe chimene akunena apa
@GeraldBanda-d2b
@GeraldBanda-d2b 2 күн бұрын
So black box anayipeza pamene ndegi inagwa zose mkamba zaboza anachita kupha
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 2 сағат бұрын
nkhani NDI black box guys:: kod Inu mcp simaidziwa aphe ndani kuti anene umboni woona
@MatchadoKalinda-h5z
@MatchadoKalinda-h5z 3 күн бұрын
Ine ndi nzimai wakumudzi koma mmene zikuonekela a times mwadya banzi bas are serious inuyo nkutelo
@bs-malawi
@bs-malawi 3 күн бұрын
Eeeeh zovuta mama
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 3 күн бұрын
Komatu Pali mafuso ena mpaka lero sanayankhidwe chifukwa chani achimendo anauzidwa kuti asakwere ndege yazaza pomwe isanazaze
@PatrickZinenanie
@PatrickZinenanie 3 күн бұрын
Funso limeneli ndilokwata pa commission of inquiry koma agalu amenewa akukanika kuyankha
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 2 күн бұрын
Panja chakwera amati ndege inafika ku dzuzu pamene sinafike ayankhapo?
@SoldieNdovie
@SoldieNdovie 16 сағат бұрын
Anachita kukodza kuti ndege yigwe
@AndrewMachemba-j2u
@AndrewMachemba-j2u 2 күн бұрын
Nanga zovala skc zinayenda bwanji
@ContentineMisati
@ContentineMisati 16 сағат бұрын
Mwayamba kudya ndlama za magazi
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 3 күн бұрын
Koma.awa..amcp.akamalankula.boza.lawo.one.day.muzayankha.
@jaynembewe7854
@jaynembewe7854 3 күн бұрын
Komatu ai zikomo
@HashimWebale
@HashimWebale 2 күн бұрын
Nonono sichoncho kapena kugwilisa ntchito chichewa chakuti amikanjo bwana simunayakhule bwino kulemekezana kwabwino ok
@ChimwemweGphiri
@ChimwemweGphiri 3 күн бұрын
Angakhale inuyo ma presenter you know the truth chinavuta ndi fighting for u President pa 2025.kodi anthu samvetsa pati? this is why Malawi will remain unsuccessful country.Always run away from reality munthu anachita kuphedwa uyu.
@VelonikaMazengela
@VelonikaMazengela Күн бұрын
❤ cool
@RobertGovati-f8o
@RobertGovati-f8o 9 сағат бұрын
MDF imadziva kuti they above everything and that they were born to be soldiers not applied for the jobs
@AndrewMachemba-j2u
@AndrewMachemba-j2u 2 күн бұрын
Amalawi chilungamo simungachipeze coz tiyeni tiime papempelo basi itayeni basi
@EvansNaphazi
@EvansNaphazi 6 сағат бұрын
Mwadya money
@patrickMakhumba-yc7rb
@patrickMakhumba-yc7rb 3 күн бұрын
Only god knows
@JannahThomas-iw5xu
@JannahThomas-iw5xu 2 күн бұрын
Kom kod manganene Kut anthu osewa mafoni awo amayenda bwnji?? Kod tiziti onsewo nalibe foni
@NoordeenBwanali-iw7me
@NoordeenBwanali-iw7me 3 күн бұрын
Ndikuonangati zimene zinachitika kuchikangawakuja mwaiwala mufunamuthandizile oipayu kumuelesa ndege inagwa mamawa malo owonekela kuseu koma mumapepha chithandizoku maikoakutali kutiakuthandizeni kusaka ndege chosecho ukamadusamuseu imaoneka pamene yagwela chinavuta ndichani polephela kuuzatunduwa amalawi mofulumila ndikuthandizaso mwasang
@ChidaPhiri
@ChidaPhiri 2 күн бұрын
Anthu amene aja anachita kuphedwa ndithu. Achakwera ndi gulu lawo anawapha anthu aja kuthetsa nkhani apolisi agwila Chakwera ndi Chimwendo anthu awa akaulura anzawo. Ndithu ndithu ma report onse onama oziteteza. Chonde gwirani Chakwera akaulura zonse
@JoshuaAamon
@JoshuaAamon Күн бұрын
Who was translating chichewa into English?
@MikeMsamalaphiri
@MikeMsamalaphiri 3 күн бұрын
Malume if these guys managed to kill the people who helped them to be in power, what more kadyagaga ongopelekela umboni?? Who can risk up his life to go and testify against these criminals? Only God knows them and He alone will sort them out. The true commission of enquiry will be seen on the judgement day
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 3 күн бұрын
Kod ndekut brain banda anasiya pg yimeneyi cox inuyo ndemandinyasa nsaname mabodza kwambili mukatero akupatsan ndalama zamagazi
@PatrickZinenanie
@PatrickZinenanie 3 күн бұрын
Mu black box ndimomwe mumapezeka information osati zamanyi zaozo
@RobertGovati-f8o
@RobertGovati-f8o 9 сағат бұрын
what does your conscious say about this when sit around with your family is your integrity ok
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa 3 күн бұрын
Kd Khan ya black box simukunena, kd mulichani m'box simo tatiuzan zoona.anthuwat sitingawakhulupilire chifkwa mbiri zao ndizakumpha basi,kutuluka Kwa enao ndiumbon kt chilungamo palibe,licesece simayendetsa galimoto
@paulmillion1652
@paulmillion1652 3 күн бұрын
T y nyerenda anthawamo.chani. atiuze poyera ndinu m,busa tiuzeni
@TadalaBirsonkanjanga
@TadalaBirsonkanjanga 3 күн бұрын
Anari azibale awo
@sinoiajamu9484
@sinoiajamu9484 3 күн бұрын
More questions than answers again it was better not to have this committee of inquiry did we ask if chakwera was aware of SKC been in the county or not ,hw came he as president did know where is deputy was,who are you trying to differed here MCP God is in heaven on day political power will end the truth will be know
@SailesGumla
@SailesGumla 23 сағат бұрын
Chimene chimakaikisa ndiichi anayamufunafuna mochedwa
@Mirriumkamwendo
@Mirriumkamwendo 3 күн бұрын
Chimwendo Banda ayankhe amene anamuuza kuti asakwere ndege yazaza
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 3 күн бұрын
Mukafuna kusogola musamakokele pambuyo munthu amene Ali pasogolo panu
Quando eu quero Sushi (sem desperdiçar) 🍣
00:26
Los Wagners
Рет қаралды 15 МЛН
Мен атып көрмегенмін ! | Qalam | 5 серия
25:41
We Attempted The Impossible 😱
00:54
Topper Guild
Рет қаралды 56 МЛН
UMBONI WA PASTOR TY NYIRENDA
25:58
Charles Shonga
Рет қаралды 10 М.
Kusanthula Bible ndi Quran - Nkhani ya Muhamad ndi Yesu (part 2)
30:29
Malawi News Update
Рет қаралды 8 М.
CRUISE 5 WITH ULADI MUSSA
1:27:41
Zodiak Malawi
Рет қаралды 16 М.
HOT CURRENT_FULL VIDEO //15 December 2024
51:51
HOT 265
Рет қаралды 22 М.
Quando eu quero Sushi (sem desperdiçar) 🍣
00:26
Los Wagners
Рет қаралды 15 МЛН