KOMA LAYTON MANGOCHI YU MWATI AMALIMBIRA MTIMA CHANI? MPAKA KUULURA ZINSISI ZA MCP IZI PA GURU?

  Рет қаралды 11,613

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 26
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 2 күн бұрын
Iyi ndiye ngamo
@DaudBonomali
@DaudBonomali 2 күн бұрын
Nayeni chakwela nayeni ❤❤❤
@ChomboNgosi
@ChomboNgosi 2 күн бұрын
APM my vote
@allanwadi2579
@allanwadi2579 2 күн бұрын
M'busa uyu ndiwachinyengo heavy...ndipo Malawi wataika basi..we must bring back leaders who have the capacity and capability to unite Malawians not these fools who are only looking out for themselves.
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Bolani yona anabwelera kwa mulungu koma lazaro wawuma mtima wake sakufuna kukapakwa Allah subuhhanawattallah
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 күн бұрын
Auzeni agalu amcp atumbuka mbuzi za anthu anthu achabe
@yunusuPhili
@yunusuPhili 2 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤
@MphindiraChimwemwe
@MphindiraChimwemwe 2 күн бұрын
Tamva chakwera at lyton samakuopa ndy ut chan
@Eqrah-hj2nu
@Eqrah-hj2nu Күн бұрын
Kuno ku makanjira Mangochi mp wakuno chambo kwao ku karonga titha kumupha ndithu yelekedzani
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 2 күн бұрын
Angalure agalu amenewa
@dikenzthomo8284
@dikenzthomo8284 Күн бұрын
Mukhalira yomwe pa social media
@ManuelMagombo-m2u
@ManuelMagombo-m2u 2 күн бұрын
Osawasiya a Congress, ndi athu a Bodza.
@FinlyMateyu
@FinlyMateyu 2 күн бұрын
😂😂😂😂
@EMMANUELJsefasi
@EMMANUELJsefasi Күн бұрын
Ponda cha kumanjacho mangochi
@HenryManda-m9h
@HenryManda-m9h Күн бұрын
Mwawanyane wakuno ku mpoto , Karonga kuganiza kwithu nkhwakuperewera chifukwa niunenesko yayi kuti mhanya uno naumo vinthu viriri muyowoye kuti Lyton Mangochi walutenge kwake ku Mangochi m'Malawi muno pala kuli chipani chankhaza kujumpha pa nkhaza mbwenu ni mcp ,mcp mu 1986/87 chipani ichi kwizila muwena john Tembo nawachewa wanyake ndiwo wakachombizga wabali withu wose wasabizgi awo wakasambizganga ku mwera,pakati kuti walutenge kwawo ku m"mpoto and ndiwo walikuperekeska ukavu ukulu chomene kiwanthu wakuno ku m"poto imwe mose mwababikila mu vyaka vyamuma 1990'/muma 2000nkhaza za mcp mukuzimanya makola yayi and wakuno ku mpoto wakwenera yayi kuyowoya nthena wabaliwanyane chipani cha mcp ichi ntchankhaza chomene kujumpha pa nkhaza
@MariaNkhata-i9q
@MariaNkhata-i9q Күн бұрын
Penanso us Northeners mmmmm kaya mantha kaya chani
@tasmania527
@tasmania527 Күн бұрын
Despite what you said, DPP is even the worst against northerners. After all, it was the old MCP under one-party rule. DPP or UTM are not better options. Ganizani makola. Northerners started MCP and must be attached to it.
@Bbbbwesgtcjoug
@Bbbbwesgtcjoug 2 күн бұрын
Chitsilu chilli ndi mwini mulungu ali ndi anthu ake satanayo Ali ndi anthu ake kotero chakwera ali ndi anthu ake enawonso ali ndi anthu awo mulungu asankhapo yemwe akufuna osati yemwe anthu akufuna ayi koma mulungu kufuna kwake mukuwona chaka chino nyozani momwe satana akugwilitsileni nchito koma zotsatila zili ndi mwini zonse mulungu mwini zonse but to me chakwera my vote ❤️❤️❤️❤️
@CarolyneGunda
@CarolyneGunda 2 күн бұрын
Kkkkk koma akuluakulu mukuganiza kuti ife mziko muno tizivutika chifukwa chaanthu ochepa zoona zimenezo
@Bbbbwesgtcjoug
@Bbbbwesgtcjoug 2 күн бұрын
@CarolyneGunda sankhani yesu akiuzani kuti zomwe mukuzionazi ndinakuuzani kale zisanafike lero mukudabwa bwanji
@MzadziWanga
@MzadziWanga 2 күн бұрын
Umbuli kma ndiomwe wachuluka tikutha kukuvetsetsan ndithu ndine mchewa mzanu from nkhotakota sindipanga support zinthu zopusa in the name of ndiwakwathu pa central region, 😅
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Ase ndine chewa mcp silibwino ase tizivomeleza
@Bbbbwesgtcjoug
@Bbbbwesgtcjoug Күн бұрын
@MillieMalakam monga chiyani
Мясо вегана? 🧐 @Whatthefshow
01:01
История одного вокалиста
Рет қаралды 7 МЛН
Мен атып көрмегенмін ! | Qalam | 5 серия
25:41
Quilt Challenge, No Skills, Just Luck#Funnyfamily #Partygames #Funny
00:32
Family Games Media
Рет қаралды 55 МЛН
Мясо вегана? 🧐 @Whatthefshow
01:01
История одного вокалиста
Рет қаралды 7 МЛН