KOMA MWATI DPP IKUDALIRA CHANI? ~ NANGA TAONANI KALATA YOMWE WALEMBA NAMALOMBA YOPITA KU MCP DZULO

  Рет қаралды 46,537

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 209
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er Күн бұрын
Ndichoncho kumene namalomba sakunama ayi😎😎😎😎
@CharlesMaganizo
@CharlesMaganizo Күн бұрын
Mcp ndichipani chakupha chankhaza never vener again mcp please my god
@PromiseNduna
@PromiseNduna Күн бұрын
Munthu amene amapanga support MCP Ndiye Kut munthuyo Moyo wake amaphanso anthu
@spargomw
@spargomw Күн бұрын
Moses Kumkuyu boma la MCP kungotuluka m'boma tilinayenaye 2025 pa nkhani yopha Witika. Asaoneke ochenjera lero. Mulandu suwola. Nkhani ya Witika oro patatha zaka zochuluka motan koma Chilingamo chidzadziwika
@InacioCement-t7n
@InacioCement-t7n Күн бұрын
Mfiti akuyesa azakhala wamuyaya
@StanleyMkandawire-d5k
@StanleyMkandawire-d5k Күн бұрын
MCP, they play games ,Koma Ife Malawi tikudziwa Kuti ndi anthu akupha
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Күн бұрын
Ndimalira kwambiri Chifukwa makolo anga anandiuza za mcp, koma Chilima anandigonthetsa nkutu.....lero ndi Chilima yemweyo kulibe ...MCP never again.
@MaxwellMilanzi-w5k
@MaxwellMilanzi-w5k Сағат бұрын
❤❤
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g Күн бұрын
MCP , MWAPHA NOKHA MUTHUYI ZONSE MUKUCHITATU ANTHU AKUONA. MUSANAMIZIRE AZANU AI
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Күн бұрын
Mulungu wathu kumwambapo chitani monga mukufunila pa dziko la Malawi ndipo chisomo ndi zifundo zanu zikhale pa dziko la Malawi chititsani manyazi asatanawa akudziweni kuti ndinu mulungu
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula Күн бұрын
Chakwera ananena kuti azakhesa mwazi asanalowe muboma pano si izi apha skc sidic mia kunamizila colona virus aphaso mavuto ife tikukuziwani a mcp
@LuciusMowa
@LuciusMowa Күн бұрын
Pafunika kunkuyu kuzamumanga kupita naye ku maula chifukwa iye anapha witika koma nkhaniyi sakuyikoka kuona ngati ochenjeralero mawa aputsa ndithu
@xxxrepair
@xxxrepair Күн бұрын
Agwireni ndipo mufufuze osaiwala anaphedwa ndi mfuti yanu uja,komanso Ku chikangawa kuja osaiwala omenyedwa pa mbowe
@InacioCement-t7n
@InacioCement-t7n Күн бұрын
True tikati tisamale tonse atipha
@bornface4786
@bornface4786 Күн бұрын
Kodi DPP ingaphe chimwanza? Tiyeni tiziganiza bwino a Malawi coz is the first time for to hear about chimwanza in political history of Malawi and for me I just see that people are following MC P bcz of money not good governing
@PabroKadams-q7y
@PabroKadams-q7y Күн бұрын
Ndi afiti wina akumetsere koma ndiiwowo
@MkwandaFaiz
@MkwandaFaiz Күн бұрын
Nonse amene mumasapota mcp machende anu
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe Күн бұрын
ineso a DPP machede osandulao limozi ndi family yano yose
@TimeAbilu
@TimeAbilu Күн бұрын
Mwana wamkaongo ndi mwana wamkaongo sangabale nkhosa apapa ifeyo Ana a pompano tadziwa kuti Mcp si chipani chabwino, koma agogo akanena koma makani
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri Күн бұрын
Viva Dpp
@SpencerKadewere-cd5ok
@SpencerKadewere-cd5ok 9 сағат бұрын
Even Ndege ija ndiomwewa a MCP adawapha ku chikangawa kuja
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl Күн бұрын
MCP ndichipani chankhaza they're always abuse
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Күн бұрын
Mwaona akufuna a Mcp awononge dzina la dpp km akunama
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Күн бұрын
Koma sizitheka kuyipisa mbiri ya DPP coz mau amati okumbira nzake dzenje amagweramo yekha.
@MaxwellKapalamula
@MaxwellKapalamula Күн бұрын
MCP ,manyi party, chizalira chikachoka 2025
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i Күн бұрын
That is true this government is killer 😳 🤣 😂 government and we don't need this government again Apm is coming soon to be president of this country 🙄 👏
@LerinaKatuli
@LerinaKatuli 6 сағат бұрын
No secret underground
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley Күн бұрын
Mwayamba kumphanakotu ku MCP ko kkkkkk Old politics
@RashidPiano
@RashidPiano Күн бұрын
Apa Ndili ND Chida Chophela Chakwela Vote Nonse Khalani Chete Akuphana Okha Okha Amenewo.
@MacdonaldJackson-l8w
@MacdonaldJackson-l8w Күн бұрын
Ndizoona mcp ndiyokupha,apha okha pa zifukwa zawo
@Belinda-c6e
@Belinda-c6e Күн бұрын
Ndifuse nawo Ku mcp kodi yinakakhala kuti adpp ndiamene tinkapha ma alubino sibwez zitaululika kodi Ku mcp kwalowa athu angati omwe anachosedwa Ku dpp sibwez ataulura kt ma lubin amaphedwa ndi dpp
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley Күн бұрын
MCP imampha ma alubino cholinga chofuna kugwesa DPP sure nankha mpaka kumanpha anthu awo
@HerbertTchautchau
@HerbertTchautchau 23 сағат бұрын
Mutu sukugwira
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 15 сағат бұрын
Amene aja aphana okaokha a mcp
@AkimChangaya
@AkimChangaya 16 сағат бұрын
amuwaro achlima ajuman amiya , eshiii mhuuu
@PetroMatias
@PetroMatias Күн бұрын
Eeeee aphana sanati
@MichaelMaseko-d9g
@MichaelMaseko-d9g 17 сағат бұрын
Ndizoona mtundu wa Malawi tikulira awa achoke
@ClementinaViola
@ClementinaViola 9 сағат бұрын
Mmmmhuuu ine chetee kulingalira mmene amalankhulinga uyo amene amatiponyera pa page imenei
@PabroKadams-q7y
@PabroKadams-q7y Күн бұрын
Ndiwo zikabedya panyumba mayi amayang'ana amene amaba chimodzimodzi,chilima,witika,shanil,gadama,etc anthuwa ndasatana akamba amathamangira kukazonda
@RabeccaLoyd
@RabeccaLoyd Күн бұрын
Rip chimwanza, I feel sorry for that
@peterkakhome6976
@peterkakhome6976 Күн бұрын
MCP imapha, kuyambira kalekale umboni ndi umenewu
@JamesYusufu-m4r
@JamesYusufu-m4r Күн бұрын
mcp. ikunjemela wakuba amazidabwa ekha amcp amaliza anthu anthu ziko muno koma 2025 mcp sikuwinaso.mulimazi chipani chamagazi
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali Күн бұрын
DPP master mind of this brutal killing
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika Күн бұрын
Achina chikangwa
@Joe-h9v
@Joe-h9v Күн бұрын
Mulungu wakwiya ndi mcp munaphelanji chilima anyani aa mcp
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu Күн бұрын
Mr. Namalomba wanena zoona zokha zokha, a MCP ali ndi chipongwe. Mwamvatu kuti apha okha mu nyamata ku B.T.apha anthu ambiri a MCP.
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 22 сағат бұрын
Inuyo a mcp mwawona amene amapha muthuyo kuti ndi a dpp mwafufuza liti? Bwanji Ena aja simunafikile Kuziwa omwe amapha? Ndi inuyo kafukufu kapena?
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Күн бұрын
Vuto zilizomse zikungoululika kuli Mulungu kunjaku
@SpencerKadewere-cd5ok
@SpencerKadewere-cd5ok 9 сағат бұрын
MCP ndizoonad imapha basi Sidik Mia,,idamupha poopa kumubwezera ndrama zake
@byson5291
@byson5291 12 сағат бұрын
Nkhaniyi ndi ya police isiyeni mmanja mwa a police
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke Күн бұрын
Zilikotu ziliko esh
@Yona-w1y
@Yona-w1y Күн бұрын
Asakane amcp ndiakupha tikuwanamizila?
@allanimindozo9937
@allanimindozo9937 Күн бұрын
Aphana okhaokha agalu amenewo DPP singapange zimenezo ayi even chimwazayo DPP sikumudziwaso ay
@jamesbanda8602
@jamesbanda8602 Күн бұрын
Panyo pako namalomba DPP mudapha anthu angati banja lija mudapha ku Lilongwe komaso anthu akumpoto mudachita uwombera ndi mfuti ndi MCP adapha? Mapolo Ako komaso nyiniyako wanva?
@GeoffreyEllias-m9l
@GeoffreyEllias-m9l Күн бұрын
Mboliyako wamva
@giftsululu4274
@giftsululu4274 Күн бұрын
Dpp mwapha miyandamiyanda ya anthu nde Lero mudziyeretse
@MkwandaFaiz
@MkwandaFaiz Күн бұрын
Galu iwe tizakumangira limodzi
@ChibweAfilison
@ChibweAfilison 15 сағат бұрын
Ndale zapamalawi zafika poyipa adpp akt ndi mcp. Mcp akt ndidpp ndy amalawi tive ziti
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n Күн бұрын
Kumkuyu umandinyasa kwambiri, skc and Witika rest well
@MabasoMafa
@MabasoMafa Күн бұрын
Namalomba,ndiwabodza
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Күн бұрын
galu
@TauacalabduremaneAbdurem-cq3pf
@TauacalabduremaneAbdurem-cq3pf Күн бұрын
MCP mwapha nokha munthu musanamizile DPP mukumbukile ku chikangawa kuja
@DoncliffFrankKambwani-k4k
@DoncliffFrankKambwani-k4k Күн бұрын
kuyambila kale mcp imapha ma mp aku mmwera a mcp.
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 9 сағат бұрын
Kunena zona mcp ndiyokupha zinangoona kuvuta kuika boma itivulazo
@Vincent-x6m5n
@Vincent-x6m5n Күн бұрын
Burea lure anaphedwa dpp Anthu 20 kuimbeledwa kumzuzu kuphelatu Dpp Albino kuzingidwa ngat nkhuku Wapolice anavulidwa Dpp Nanga banja linaphedwa Ku area 24 Lilongwe Nanga billy Mayaya kukunthidwa ndima cardet Adpp Dpp yapanga zonyasa kwambili no no Dpp isabweleso mu government bola ras chikomeni
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
ACHITSIRU INU ZEDI, TALEMBANINSO OMWE INU A MCP MWAPHA KOMANSO MADZUZO OMWE AMALAWIFE MUKUTICHITA
@Vincent-x6m5n
@Vincent-x6m5n Күн бұрын
@@RiteRoderick phwaga ine sindingalembe zosangalatsa Dpp or iweo kapena chipani chilichose ngat kut iweo umandipatsa salary kapena ndimadya kwanu or ndilembe zosangalatsa iweo ndipindula Chan kwa iweo
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
@@Vincent-x6m5n That's how stupid you're, coz zonse walemba apo zaonesa kuputsa kwako ndikupepera kwako coz suukudziwa kanthu kalikonse. Mabodza basi ndiufiti Agaru inu ndiomwe umakuchulukirani Koma mukhaula mudziwanso
@ThomasChiwaya-qx9mf
@ThomasChiwaya-qx9mf Күн бұрын
Ndithudi mcp (itheratu mu 2025 ) bas
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
MCP ikanayenera ithesedwe koma vuto ma lawyer athu ndizitsiru zosasata malamulo
@OwenMajoni-qv3eg
@OwenMajoni-qv3eg Күн бұрын
Kodi Mesa covid inayamba ndi dpp?
@HarryKandani
@HarryKandani Күн бұрын
Kunkuyu mutu wako ...RIP Witika
@PartsonMdeza
@PartsonMdeza 23 сағат бұрын
eeeh mwapha anthu kwakwana inu a MCP
@EmmanuelDanitsa
@EmmanuelDanitsa Күн бұрын
Vote wise vote for UTM 🔥🔥🔥🏆 🏆🏆
@FernasonMasiya
@FernasonMasiya Күн бұрын
Chikangwawa ndichomwecho
@09914960051
@09914960051 Күн бұрын
Komatu a Namalomba nzeru umunthu mulibe
@IssahBannet
@IssahBannet Күн бұрын
Ulimbali itikodi iweyo?
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 Күн бұрын
aMCP alindiulamulilo wankanza. Zinazo akudziwa ndiMulungu!!!
@MichaelHastingsGodfreyMvula
@MichaelHastingsGodfreyMvula Күн бұрын
It's possible that opposition might have eliminated SKC chifukwa amamuopa. Misonkhano ya DPP yonse amanena kuti athana naye akamusiya ku Nsipe.
@GoldenNamanguya-q9u
@GoldenNamanguya-q9u Күн бұрын
Mboloyako namachende opusa iwe galu
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 22 сағат бұрын
Chomwe unganene ndio manyi awawa bas? Ukakhla kut ulibe chonena ndibwino kukhala chete cox munthu wanzeri sangamanenr ixi ai zoti a mcp anamupha skc cfkwa cha mpando iwe sukuonai? Kupusa bas
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 21 сағат бұрын
Mfundo mulibe inu
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Күн бұрын
Yapha mnyamata waku ndilande, Chifukwa choti amnthu amamufusa mavuto kuti ndalama za nifi zikuchedwa bwanji, Ndiye iye poona kuti akunamiza anthu iye anasankha kutuluka mcp Basitu amupha
@MagieJames
@MagieJames Күн бұрын
Amoses kumkuyu asaoneke udulo nkhope yakeyo inazaza nd magazi athu munthu kumaoneka ngt nkhalamba chifukwa cha magazi anthu
@BlessingsmChiipira
@BlessingsmChiipira Күн бұрын
Akungochedwa awa
@Venacio-d3v
@Venacio-d3v Күн бұрын
MCP ndi yachabe osabisa
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q Күн бұрын
Ine josephy ndizoona anthuonsewa ng'onazi zikuphazokha
@promixphotography8056
@promixphotography8056 15 сағат бұрын
choona chake wangono aliyetse wachiona,tiwaonetse khwiyoo chilungamo
@SOLDIERLOVE-e1q
@SOLDIERLOVE-e1q Күн бұрын
MCP ndiyakupha aliyese amadziwa
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Күн бұрын
ndiwe garu kwabasi
@GiftIsaacelias
@GiftIsaacelias Күн бұрын
mcp ndiyakupha kumene asanyengere dpp
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c Күн бұрын
Aphana okha okha
@patriciajangaza675
@patriciajangaza675 Күн бұрын
Kodi iwowo akati DPP yawapha munthu amupha pazifukwa zingati ? Ndipo Wawa lakwira chani poti ndiwawo aaaaa zosamveka
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Күн бұрын
inu anthu amene mukupanga coment kuyikila kumbuyo mcp koma Malawi alili mukumuona tinayika president wamisala pampando
@AdamYas-ec9oc
@AdamYas-ec9oc Күн бұрын
Inde namalomba mukunena zoona m c p kwake kupha kumangana ndi kuba mizongo ya malawi
@RefrigeratorRepair-c5v
@RefrigeratorRepair-c5v 13 сағат бұрын
Nzowonadi inzi awonekela poyela
@SifatiMoses
@SifatiMoses Күн бұрын
Nkunkuyu azitenge bwino ngati akufuna nkhondo angonena, tiyambe kutotholana sitimamuopatu. Mwaphana nokha mukuwapaka anthu ena chisiru cha munthu.
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens Күн бұрын
Anthu opanda nzeru mxiew
@JohnGreen-v8f
@JohnGreen-v8f Күн бұрын
Kukuyu pakholo pamako
@OwenJambo
@OwenJambo Күн бұрын
😂😂😂
@JudithKatungwe
@JudithKatungwe Күн бұрын
Koma ndiye kung'aluratu😂
@ChimwemweZgambo
@ChimwemweZgambo Күн бұрын
Dpp never again
@BrightZionga
@BrightZionga Күн бұрын
You will be ashamed soon
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza Күн бұрын
inu mcp inayambapo ayavomera nkhani yoti apha anthu anapha anthu ngati ochuluka kom anavomerapo, nthaai amakana chocho komatu kupusa kwake, amayiwala kuti iwonso azafa, ndithu, chimagopweka kuti awapha anthuwo nthawi yawo isanakwane yomwe mulungu wathu, anawalengera koma chipani ichi cha mcp ndichoyipa kwambiri koma tsiku likubwera, inu zonse zomwe mumachiti selizi popha anthu osalakwa wa, Mulungu wathu , azakusiyani poyela ndithu, muziziwa zimenezi ndithu,
@JamesJenala-c3n
@JamesJenala-c3n Күн бұрын
Eeee. MCP
@JosephGabriel-y7w
@JosephGabriel-y7w Күн бұрын
Ndipo ine chipani chokupha cha mcp chandikwana osangowachosa mawa bwanji anayambila kuphamuja
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Күн бұрын
Mulungu ndi wa bwinotu sitimafuna kusinda zindu ndizimenezi komaso malemu aja anatitengela kuzenje uku
@SadickSikweya-f5b
@SadickSikweya-f5b Күн бұрын
Anja alandila madat Anja ndi amenewa kuti azi komenta zolibeleka bomali koma athu zisiludi
@giftsululu4274
@giftsululu4274 Күн бұрын
Mbava zaberana
@FranciscoBanda-v5w
@FranciscoBanda-v5w Күн бұрын
Mcp nkhani yakupha ndi machacha amenewa ndipo sikuyamba ananchidwe amenewa
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Күн бұрын
MCP sangatipusise AI ndipo machimo awo palibe angamupake Athu akupha
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo Күн бұрын
Nde kuti muja mcp inkati they needs sacrifice for chakwera to stay forever nde kuti ndiiwodi adapha chilima?
@IslamMapepa
@IslamMapepa Күн бұрын
Mwalo mwakukupha iweyo kumkuyo nde akamuphe okuti oloko kuchipaniko samamuzi simesa mwamuziwa atamwalila
@ManuelKamba
@ManuelKamba Күн бұрын
Namalomba amakwana zedi alibe mantha akafuna kulankhula
@CliffChisale
@CliffChisale Күн бұрын
Jah pip
@ElasmoZimbiri-w9y
@ElasmoZimbiri-w9y Күн бұрын
Amcp amafuna kusokoneza anthu pomanamizira KuDPP okupha aliiwowo
@BrightZionga
@BrightZionga Күн бұрын
MCP ndi mimbulu
@oswardzenizeni1458
@oswardzenizeni1458 Күн бұрын
Mwaphana nokhanokha mukupaka dpp bwanji
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 22 сағат бұрын
Kwambili mcp samafuna kuweruzidwa ,nyamata yemwe amupha ku ndirande amafuna kt achisiye chipan coz amakumbusa ngongore zachinyamata,mwapeto ake apanga ndare ndikuzamupha mmm guys simungatipusise and so tatopan nanu,mwayambila kupha athu pajaaaa mm inuyo ayi ndithu
@Majorleman
@Majorleman Күн бұрын
Uyu kunkuyu ndi oduka mutu zoyankhula zake zimangokhala mbwelela zokhazokha ,apapa asavitike apeleke umboni ombeka
Сюрприз для Златы на день рождения
00:10
Victoria Portfolio
Рет қаралды 2,5 МЛН
НИКИТА ПОДСТАВИЛ ДЖОНИ 😡
01:00
HOOOTDOGS
Рет қаралды 2,8 МЛН
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 269 #shorts
00:26
Patricia Kaliati wamangidwa pa mlandu wa treason
9:15
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 7 М.
Сюрприз для Златы на день рождения
00:10
Victoria Portfolio
Рет қаралды 2,5 МЛН