Ku SA kuli Malema amalongolola kuposera suleman koma sinamvepo liu lot impeàch.ntchito yamakhot imeneyo. Amuimika ku parliament konkha osat nga chair kpma ngat mp olankhula .mmu parliament
Kuyesa yesa kukokera pansi, koma pang'ono ndi pang'ono anthu akuzindikira kuti ena amwebweretsa zofuna zawo mnyumbai safuna kuti zinthu ziziyenda.
@GladysndilimbiraBonongwe-g6cАй бұрын
Koma speaker ndiye akuyelekedwatu
@GladysndilimbiraBonongwe-g6cАй бұрын
A position musawaope a gudwaniwo
@YoungMwachoАй бұрын
Money ndi satana, onse agulidwa ku parliament ndi Chakwela, very bad for our country. We are now in a one party state. Amalawi zimene tinkafuna ndizimenezi? Now I understand that Chakwela has very weak members in MCP. Third term and open term nthawi ya Bakili analephelesa ndi members of UDF themselves to avoid one party dictatorship rule. Be careful MCP members, look at Mkaka, he is not even a member of NGC of the party. Panopa mukuwona ngati mukulimbana ndi opposition later on Chakwela will even be killing members of MCP who will be threat to his leadership, Kamuzu Banda did the same and killed many MCP members. History repeats itself and history is the best teacher. Dziko sungamusiyile Chimwendo Banda kuti azilamulira, chibwana chachikuli chimenecho. One day you will reap the consequences.
@ChristopherJumuАй бұрын
Chimwendo banda pa ntumbo pako. Kod unabadwila chani galu iwe???
@dorothymosimbwa3638Ай бұрын
When are you going to build after you failed for 5 years???
@YonaTaulo-o8qАй бұрын
Koma judge ameneyi ndye akusimbhwa kom aaah wasala pangono
@GiftallannyirongoАй бұрын
Agaru inu
@YasenYasen-q9gАй бұрын
Richard galu zakufuna kufomeleza mcp zindu zawafuta
@StythewsMkwiyoАй бұрын
Zafika powopsezana. A good leader shouldn't tell his subordinates that he is a boss. That's cowardly luck of of knowledge
@MasterBlack-r2nАй бұрын
Kuzimva u chair kumeneko? Kunaliti anzanuso pamenepo. Matama ndizochita kuikidwatu sizabwino mawa umazachota manyazi akazakupanga fired
@Dickson-t3hАй бұрын
Don't taken amalawian like fully we gonna see Malawian is anger
@ArnoldBanda-b9qАй бұрын
Nyakhulani chichewa pls
@PaulChafikirahАй бұрын
Amalawi anzanga tiyenitonse Ku parliament konko tikangotseka nyumbayo or tikangogumulapobas fetereza kulibebasi kungovomeleza basi
@AnnieMaudzuАй бұрын
No voice bwanji zukhala bwanji
@EvansNkumba-q7tАй бұрын
Kodi speaker anaphunzira school yake yanji chizungu chake chimenecho
Nonse zitsilu kumeneko anu parliament or English yosaveka amakuvotelani ndan inu kod
@mavutokazembe-r6wАй бұрын
. My mom. No
@JonathanLimunyeАй бұрын
Speaker uyu ndi mkayidi sakuyenera kusogolera nyumba ya malamulo bola mzimayi analiko dzulo uja , uyu amapanga za against and salemekeza ufulu wa anthu, ubwino wake si za muyaya
@Dickson-t3hАй бұрын
Opposition we needed to make united stronger to moved the government of mcp amalawi tonse sitikufuna chakwera vuto ndinuyo Opposition mukufuna amalawi atani George chaponda tulo too much we need wekup make one united to standing stronger to make one decision DPP, UDF, AFORD AND OTHERS OPPOSITION COMING TOGETHER TO MOVED OUT AKUMALEMBA ANA ANGONO KALEMBERA WA VOTE CHOLINGA NDICHIYANI AMALAWI TONSE SITIKUFUNA CHAKWERA AI AKUKAKAMIRA BWANJI IFE SITIKUFUNATU
@LoleniShabani-mt7nzАй бұрын
Is useless to listen the speech from this parliament
Ku MCP ndale zakukuvutani guys mukuludza majolite chifukwa Cha zochita Zanu koma udindo wa MP Ku MCP mumauziwa olo ayi munangopezeka mwa tenga bomali tifutseko Kaye mwina mumandisekesa bwanji zochita zanu
@PatumaDaudАй бұрын
The speaker is picking sides😭😭😭😭😭😭
@BOSTONMALISAWO55Ай бұрын
A MCP PANYAPAMANO
@YasenYasen-q9gАй бұрын
Sachamba 2025 ndipafup
@ThomuChiwangaАй бұрын
Ine ndayileka MCP zochita zake si zofuna kuramula Boma koma nkhondo ndiye ine zimenezo ayi tiyeni tilamure Kuti mawa tizawinenso guys osati zachamba mukupangazi ayi
@AbbassKharid-m8tАй бұрын
Man ma audio anu voice imathawathawa you have to fix it
@ChaxyChimbalanga-c5uАй бұрын
😂😂😂
@trifoniachilunda6263Ай бұрын
Ajaji ndinu okondelà
@SueWahna-y8mАй бұрын
Maudindo amatha palibe chosatha
@SamsonKamanga-g2kАй бұрын
Abisa mau bwanji nakha
@MfuneWaluEcksonАй бұрын
Makape inu,,
@noelliwonde8661Ай бұрын
Patumbo pano nonse a MCP
@BerthaMkwinikaАй бұрын
Or mutukwane mupindula chani?? zinthu zachitika ndipo owinaawina
@AbdulsharifulKalipinde-m6uАй бұрын
Why do you mean Owina awina kale Mwaponyela kuti ma vote ake
@giftmakoyo1441Ай бұрын
Akuwona ngati azabera mavote mwakhaula
@TaunessNambelaАй бұрын
Awoneka amabwela atamwa mowa
@MjombaMoosaАй бұрын
Tangowaziilani a MCP parliament inu nonse a opposition tangotulukani kunyaza ngati kunyelo galu wachabe chabe
Hon Chimwendo or Chimutu whatever his name is. Should stop fooling people. Anyone can go to Chonde where the houses are to be constructed if there is a single house. Pls pls stop fooling people.
@JonathanLimunyeАй бұрын
You MP of Dedza east are you serious you thank president for construction of police houses, what for? Your people there can eat houses, be serious you are old enough, don't be like you have nothing in your head. Your people there are suffering and you are at parliament speaking nonsense there
@giftmakoyo1441Ай бұрын
Koma ndiye vice speaker mphamvu nzako zawonjeza mmmmm kuyankhula ngati ukuyankhula ndi ana aaaaa watch your mouth
@LameckGamahАй бұрын
I have question to ask how much did you receive the money from chikangawa? Fake speaker he doesn't know what he's doing.
@TimothyKamanga-t2zАй бұрын
You are not helping the people whom you represent
@KondwaniLimbeАй бұрын
No sound
@Dickson-t3hАй бұрын
Don't taken amalawian like fully we gonna see Malawian is anger
@Dickson-t3hАй бұрын
Don't taken amalawian like fully we gonna see Malawian is anger