KU UTM ZINTHU ZIKUYENDA MOTANI?__3 December 2024

  Рет қаралды 12,277

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 61
@EnockMvula
@EnockMvula 14 сағат бұрын
Amen zikomo mayi kariati ambuye akutsogororeni nose ndibambo kambara ambuye akudaritseni mzina ra yesu
@MadalitsoMeyah
@MadalitsoMeyah 19 сағат бұрын
ONE TEAM ONE FAMILY ONE MOVEMENT UTM my VOTE🔥
@emmanueljelemani4203
@emmanueljelemani4203 19 сағат бұрын
Newton Kambala I knew you would never let us down, may God bless you always
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 19 сағат бұрын
Zikomo kwambiri azisongoreli athu UTM chifukwa ndinu nokha muzatipulumusa pa ulamuliro wankhanza, nose azisogoreli anthu timakukondani , Mulungu akudalitseni
@MisheckAselo
@MisheckAselo 18 сағат бұрын
Team Biyeni kuti nyadu🎉🎉🎉
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 18 сағат бұрын
KUMENEKO NDIYE KUKHWIMA NZERU MR KAMBALA GOD BLESS YOU SIR
@AliceBotha-o4h
@AliceBotha-o4h 18 сағат бұрын
Dr.Kambala...congrats God bless you
@RaphaelPhiri-z3r
@RaphaelPhiri-z3r 16 сағат бұрын
Viva our party let's unite and look forward for better Malawi,i unite we stand and divide we fall.
@HumphreyKasowanjete
@HumphreyKasowanjete 17 сағат бұрын
That's the way to go, Bravo !
@FracksonMadani
@FracksonMadani 18 сағат бұрын
Wakwiya ndi nfiti, by the way DK my vote
@StevenGJohn
@StevenGJohn 18 сағат бұрын
Mr Newton Kambala may God bless you
@DoreenMuhota
@DoreenMuhota 15 сағат бұрын
Kumeneko nde kuganiza bhoo akambala❤❤❤
@HarryNdala-k2g
@HarryNdala-k2g 18 сағат бұрын
This is good and let's work together it's our own Moto ..
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 15 сағат бұрын
Good Messnge Mr Kambala
@MathaNamanja
@MathaNamanja 18 сағат бұрын
Kumeneko ndiye kukhala,muli ndi kuthekera kwakukulu pa zinthu zina,Mpando umodzi sipangakhare Anthu awiri,Ambuye akudalitseni
@FredKanyerere
@FredKanyerere 17 сағат бұрын
Dr kambala thanks to you.
@GibsonChamkoma
@GibsonChamkoma 17 сағат бұрын
Kuganiza mwanzeru
@leonardmalirana7423
@leonardmalirana7423 18 сағат бұрын
Atsogoleri enawo tikuwadikira kuyamba kutumikira mwachangu ku UTM ayambepo kuthamanga pa ground
@agnesKachikunji
@agnesKachikunji 17 сағат бұрын
Thank you God we give you groly. Let us be together.
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 14 сағат бұрын
Ndinu agalu nonse kambala, kaliati njawala nonse ndinu mbuzi mwagulutsa chipani Cha sogolo.... Ndinu fiti kulilira u president tsopano ndinu nkhunguni zopanda Mano.. nonsense leaders
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda 17 сағат бұрын
Dk my vote 🎉
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 18 сағат бұрын
Takunyadilani azisogoleri a UTM ponkhalila limozi
@eliasgondwe
@eliasgondwe 14 сағат бұрын
Akambala chipani adayamba okha lero ayambaso kupemphetsa!! Koma ndalama adakoza , kkkkk
@JosephyChithope
@JosephyChithope 16 сағат бұрын
Nanga mkung,ungu uja ukufuna usokoneze bwanj? Apopo gwiranan manja guys
@ShalomShine
@ShalomShine 18 сағат бұрын
God bless you Mr kambala
@EvansKachulu
@EvansKachulu 19 сағат бұрын
God bless all
@RhodneyBenson
@RhodneyBenson 19 сағат бұрын
Tumizani ma baretawo kuno kumangochi timachikonda chipanichi
@paulmolowa2688
@paulmolowa2688 19 сағат бұрын
That's call Malawi ❤❤
@giftnyirongo-ey3qy
@giftnyirongo-ey3qy 16 сағат бұрын
Kaliyatiyo ngwabodza
@MolesBrown
@MolesBrown 17 сағат бұрын
Awapatse ndalama kababetu akugwilitsa ncthito ndalama munthu oipa onse okonda ndalama adzingovomeneza ndalama ndiyoopwa
@RuthMkangala
@RuthMkangala 19 сағат бұрын
Good move
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 14 сағат бұрын
UKUKU NDIYE KUKHALA KOMASO KUKHWIMA NZERU AMBUYE AKUTSOGOLERENI NONSE MPAKA POKATENGA BOMA M'MANJA MWA NG'ONAZI CHAKA CHAMAWA
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 17 сағат бұрын
Zikomo kwambiri munthu wa mkulu bambo kambala kumeneko ndiye kukhala bambo ambuye akudalitseni
@KarimTapyMshanga-kd1vz
@KarimTapyMshanga-kd1vz 19 сағат бұрын
There is Future in UTM
@crispinekapenda
@crispinekapenda 17 сағат бұрын
Waiting for kaliati and Mtumbuka
@MercyKaunda-k5k
@MercyKaunda-k5k 17 сағат бұрын
Ndagwilizana nazo
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 14 сағат бұрын
OLO MUKUPANGITSA TRAINING A POLICE NTCHITO YANU PANO SIKUONEKA INUYO A POLICE MUKUTHA KUDYA MISONKHO YA MALAWI KOMA NTCHITO ZANU SIZIKUDZIWIKA MBUZI NONSE A POLICE CHIFUKWA NGATI UCHIFWAMBA UKUKULA MDZIKO LATHU GWERO LAKE NDINUYO AGALU
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 17 сағат бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@AustinRashid-s4h
@AustinRashid-s4h 17 сағат бұрын
Big up utm ife sitiopa
@ChrissieNyasulu
@ChrissieNyasulu 19 сағат бұрын
That's the way to go
@EllenNyirenda-ne4hv
@EllenNyirenda-ne4hv 19 сағат бұрын
❤❤❤❤❤
@VitumbikoKaunga
@VitumbikoKaunga 14 сағат бұрын
Bora anene zoona osati umuthira kuwiri ngat kaliati
@AlumakioChingalu
@AlumakioChingalu 18 сағат бұрын
UTM aaaaaaa
@YohaneNthala-n9p
@YohaneNthala-n9p 18 сағат бұрын
Kariyatiyo muzimuonesesa adzikodzera kkkkkk
@OmexMainala
@OmexMainala 18 сағат бұрын
Ndazikonda move on
@JonaSato-j8e
@JonaSato-j8e 19 сағат бұрын
Good team ❤❤❤❤
@kelvinwilliam960
@kelvinwilliam960 18 сағат бұрын
Zatilimbikitsa
@stubish0p-fl2zf
@stubish0p-fl2zf 16 сағат бұрын
Amati atani akaliat ndi akambala, kabambe ndi munthu wa ndalama, ngati anakwanisa kugula chipani cha utm ndiye inu ndi ndani kuti asakugureni, ziphuphu kuyambira kuyambira ku convation, ndi kumati mukazatenga boma muzathesa ziphuphu, tamangodyani ndalamzo, koma zoti mungasinthe zinthu ndiye palibe.
@FrankAbraham-e9o
@FrankAbraham-e9o 17 сағат бұрын
Ndiye akaliati ali kuti?
@BERNARDSIKWESE
@BERNARDSIKWESE 15 сағат бұрын
Kuganiza kwa boo
@kekeaufi9834
@kekeaufi9834 19 сағат бұрын
❤❤❤❤🎉🎉🎉
@blackcobra-b2y
@blackcobra-b2y 19 сағат бұрын
Zazii!!
@TheolianBanda
@TheolianBanda 18 сағат бұрын
Unya
@MaggieManda-ve6kg
@MaggieManda-ve6kg 18 сағат бұрын
Zaziiiii iweyo
@LinlyMathewe
@LinlyMathewe 18 сағат бұрын
Zaziii zili ku Chikangawa unya UTM my vote ❤❤❤❤❤
@BeatriceSaulosi
@BeatriceSaulosi 18 сағат бұрын
Yakubayani 😂😂
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 18 сағат бұрын
Or manyazi ulibe iwe chakwera
@StevenGJohn
@StevenGJohn 18 сағат бұрын
Mr Newton Kambala may God bless you
@Tracey-s3q
@Tracey-s3q 19 сағат бұрын
❤❤❤❤
TIKUDZIWENI WITH ANTHONY MAKONDETSA - 5 August 2019
30:45
Times 360 Malawi
Рет қаралды 56 М.
Beat Ronaldo, Win $1,000,000
22:45
MrBeast
Рет қаралды 96 МЛН
If people acted like cats 🙀😹 LeoNata family #shorts
00:22
LeoNata Family
Рет қаралды 35 МЛН
'I will take back ANC to honour my ancestors': Zuma
48:29
TimesLIVE Video
Рет қаралды 8 М.
LIVE: VP Sara Duterte press conference (Nov. 27, 2024) | GMA Integrated - Replay
42:52
Новости дня | 3 декабря - дневной выпуск
11:50
Euronews по-русски
Рет қаралды 13 М.
Anne Matumbi ft Nepman-NDAGOMA (official music video)
5:48
anne matumbi
Рет қаралды 81 М.
3rd December, 2024: 50th Session - 6th Meeting  - MALAWI PARLIAMENT
1:30:43