Morning Mr DC kavera odiyo yanu ndimakhala ndathana ndi MA program Ali wonse akumalawi I love DC wishing you more years to come our God azikutetezerani Mr DC I will see you one day face to face❤❤❤
@YellowmanMalawi-qe8zh2 ай бұрын
Umatiimilira Bon,keep it up
@ElizabethKoopa2 ай бұрын
Ine from America mademo achitike tili nanu keep it up
@AlgentChilanga2 ай бұрын
The DC mwana wowopsya kwambiri Bon kalindo 🎉
@SamuelAntone-mz6nq2 ай бұрын
Auzeee agalu amenewo kkkkkkkkk bigy makwana💥💥💥💯
@gvdember57542 ай бұрын
JJ
@Moses512 ай бұрын
The Dc bon kalindo 🎉🎉🎉
@limbanikamanga75142 ай бұрын
From Njedza Village TA Mabuka Mulanje
@BrightGonthi2 ай бұрын
Most of these advisors, it's the president who advises them 😂😂😂
@HappyAntenna-sf9qx2 ай бұрын
Kod zikukhala bwanj onse amane akupanga zimez akuchokela ku southern region Limpopo chimodz modzi mulomweso 😂😂😂
@ThokoLungu-tq6pw2 ай бұрын
Iwenso utafuna utha kupanga as long as uli ndikuthekela ndi mmene Malawi alili sizikutengela kochekela baba
@TrizaGeorge-q8w2 ай бұрын
Wadya ndrama zamagazi musaza mulungu si Lazaro
@yassinn56342 ай бұрын
Ndi ma DPP operatives
@OsmanSaizi-v8y2 ай бұрын
More fire
@MasterBlack-r2n2 ай бұрын
Inuyo ndi akamuna the DC Boooooooooo kalindo
@LukaThawe2 ай бұрын
Aaaaaaa mademo zaziiiii kusowa zochita mumalo mokapita kukalima SATA gwaa
@InnocentKadoma2 ай бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@JafaliAkimu-ll1bf2 ай бұрын
sangayime pa chikangawa chifukwa chakwerayo ndi amene anapha chilima ndi chigawenga satana magazi achilima amuzunguza mutu
@paulphiri-fz9me2 ай бұрын
Chilungamo nchomwe tifuna tione basi ,tikali kulila chilima 😢
@HalimaShafie-q9k2 ай бұрын
❤❤❤❤❤
@ScottTholo2 ай бұрын
Zoona man
@MaxWell-d7o2 ай бұрын
More fire Dc
@dontreybanda2782 ай бұрын
Good massage the DC
@ShamilahSaizi2 ай бұрын
More🔥
@TroubleMuthala2 ай бұрын
❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🕯️🕯️🕯️🕯️🕯️
@GodfreyKamphiripiri2 ай бұрын
Dc
@ChristinaRoben2 ай бұрын
Ayi ziliko
@KhalideNerve-mu1eq2 ай бұрын
💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪
@chiwaulaashraf46962 ай бұрын
The dc
@tasmania5272 ай бұрын
Anzanu ali busy kunjoya ndalama za fodya chifukwa cholimbikira, inu mukutanganidwa ndi mademo opanda phindu. APM anakupundulani chifukwa munkaba za ulele.Pano mwawonekera ng'amba anthu aulesi inu. Ndipo ndinu nokha nokhatu...mwauponda makape inu.
@ChisomoSaiti2 ай бұрын
Kodi iweyo ndi ife amene zake zilipabwino ndindan pamtumbo
@JohnConar-kq4hi2 ай бұрын
The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC
@johnkambala6922 ай бұрын
Void
@chadreckchibwithala14932 ай бұрын
galu iwe anthu akusangalala ndi ndalama za fodya pano ukulota or bwanji . tiwonana pa 8 pamseu mademo amenewo mkathamanga .