KUYANKHULAPO PA NKHANI YA KUMANGIDWA KWA PATRICIA KALIATI

  Рет қаралды 4,421

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 38
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche 54 минут бұрын
Mulungu akutetezeni mama
@marryphili5419
@marryphili5419 Сағат бұрын
Koma Malawi pamene yafikapa ayi mtenderemulibe sure
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw Сағат бұрын
Mcp tatopa nanu muchitidwe uyu kodi anthu apha achilima bwanji sakumangidwa bwanji
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Сағат бұрын
Nkhani si imene awamangirayo ayi mumva kuti takupezani ndi mulandu wa kulankhula mofuna kudzetsa chisokonezo dziko and kumangidwaku kukuchoka pa speech ya pa nsonkhano wa atola nkhani anapanga zipani zingapo uja nkhani ndi commission of enquiry ikuwabaya.kmso manganya za ku convention.
@SylessKamanga
@SylessKamanga Сағат бұрын
Chakwera sakufuna chipani Cha utm koma wayiwara kuti chipanda utm sakanakhala president,ukakwera pamusana wa njovu usamati kulibe mame chakwera chikangawa akunama
@BeardKamuwombaHarawa-d6v
@BeardKamuwombaHarawa-d6v Сағат бұрын
Ngati sanalakwe Ambuye akuyima naye
@alickziba6756
@alickziba6756 2 сағат бұрын
Chilima anayamba ndikumamangidwa kenako kuphedwa. Apa kaliati wamangidwa. Pakuyeneka kukhala maso pamenepo.
@Andrew-nz9sh
@Andrew-nz9sh Сағат бұрын
If I was to choose politicians the first person I'd choose mama kaliyat and where ever you are mama am surely behind you it's my prayer you will be fine and strong in Jesus name 🙏🙏
@Fanie-i7z
@Fanie-i7z 2 сағат бұрын
Please musavotere usi ndichifukwa anaphesela SKC.
@patrickmwenibanda4565
@patrickmwenibanda4565 2 сағат бұрын
Praying for you mama akweni
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 3 сағат бұрын
Praying for you madam Kaliyati,ambuye alowelele ameen Akweni President
@RabeccaMkandawire-i9j
@RabeccaMkandawire-i9j Сағат бұрын
We are praying for mama
@RhodrickChauluka
@RhodrickChauluka 2 сағат бұрын
Zonsezi ndi manganya akufuna kusokoneza kuti kaliyati a kweni kuti asakapezeke ku conversation galu wachabe chabe Michael Usi
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 3 сағат бұрын
Bwanji osamangidwa iwowo anapha Anthu 9 osalakwa
@SedoMissi-m3c
@SedoMissi-m3c 2 сағат бұрын
Aaaaaa akutinamiza anthu awa sure ndale izizi akutisewera anthuwa
@IdahKadewere
@IdahKadewere 2 сағат бұрын
Manganya ameneyo akufuna kuwasokoneza akweni ku covation
@GustoAjasi-fl9oo
@GustoAjasi-fl9oo 2 сағат бұрын
Komatu mukulakwa chiyembekezo Cha Malawi ndi kaliyati yemweyo mukupanga Dala izi zandale
@BrassBrass-j9y
@BrassBrass-j9y 2 сағат бұрын
Boma ili Koma latikwana kwambiri
@FelixNyirenda-c4y
@FelixNyirenda-c4y 8 минут бұрын
Malawi is Police state under Chakwela.
@amonechirwa
@amonechirwa 2 сағат бұрын
USI ameneyo chikangawa plain yaka aaaaa 😅
@WillianBanda-p7d
@WillianBanda-p7d Сағат бұрын
Zonsezo ndi manganya.
@ellensambo6323
@ellensambo6323 2 сағат бұрын
Ndalezi mmmmmmmm Ambuye alowererepo
@bensoweto-bm6yr
@bensoweto-bm6yr 2 сағат бұрын
Manganya ndiwopepere palibe chadzeru chomwe akuchita
@MolesBrown
@MolesBrown Сағат бұрын
Apols amamnga wapols nzawo kubwanji kaliyati kd chifukwa ndi akwen?
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 2 сағат бұрын
Tiyen komweko bass not just talked
@MussahTonde-x9q
@MussahTonde-x9q Сағат бұрын
Yooo
@ElijahTheprophet-y9m
@ElijahTheprophet-y9m Сағат бұрын
Manganya ndi pimp wankulu
@UmaliGunga
@UmaliGunga 2 сағат бұрын
A police amasure kaliati awamanga chifukwa chandale masureni masureni
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 3 сағат бұрын
Kaliati tsogolo lowala❤
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s Сағат бұрын
Bull shit politics
@AcctyhBuno
@AcctyhBuno 2 сағат бұрын
Mmmmmm tawadiyeni apa apolosi ayambapo wokha tiyamba kuwotchamo misakasa yawoyi apolisi mutisamale pazomwe mwayambazi
@JuliusMtalika
@JuliusMtalika 2 сағат бұрын
Malawi malawi ai ndithu
@MarcyKamaga
@MarcyKamaga 2 сағат бұрын
koma boma rachakwera munthu uyuyu Kodi wafika kwambiri ndiwu president uwu koma akuziwa kuti kuri murungu
@LawrencePhiri-tt9zq
@LawrencePhiri-tt9zq 2 сағат бұрын
Mwano kugwilira tchito pamodzu sikuti sungamagibwe ndiwe bulu kwambiri
@VictoriaBakuli
@VictoriaBakuli 2 сағат бұрын
Akanakhala kuti wamangidwa ndi mai ako sukanayankhula za manyi zakozo
@yobesaikonde6166
@yobesaikonde6166 2 сағат бұрын
Kkkkkkkkkk let's pray, Mai Kaliat ndi munthu. Akhoza kulakwitsa komanso kupekeredwa nkhani , zonsezi mzotheka. Choona akuchodziwa ndi omanga ndi Mai Kaliat. Koma Mulungu ndi wankulu.
COMRADE SALLO KUSWA MITU OPPOSITION - OPPOSITION YAKU MALAWI  *NDIYA CHIFUFU*
12:50
Who’s the Real Dad Doll Squid? Can You Guess in 60 Seconds? | Roblox 3D
00:34
Smart Sigma Kid #funny #sigma
00:14
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 70 МЛН
Cool Parenting Gadget Against Mosquitos! 🦟👶 #gen
00:21
TheSoul Music Family
Рет қаралды 32 МЛН
Un coup venu de l’espace 😂😂😂
00:19
Nicocapone
Рет қаралды 14 МЛН
OTSATIRA CHIPANI CHA UTM AFIKA KALE KU POLICE KOMWE AKUSUNGAKO KALIATI
1:44
How Israel Eliminated Yahya Sinwar#israel #yahyasinwar
9:37
AiTelly
Рет қаралды 3 МЛН
CRUISE 5 WITH MOSE WA PA PHIRI LA BUNDA
1:14:37
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 113 М.
How to win a argument
9:28
ajaxkmr (ajaxkmr1986)
Рет қаралды 648 М.
CRUISE 5   ELIYA NZERU WILLIAM
1:20:13
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 411 М.
Netanyahu at UN: I have a message to the world - we are winning
34:53
Israel National News - Arutz Sheva
Рет қаралды 1,4 МЛН
Who’s the Real Dad Doll Squid? Can You Guess in 60 Seconds? | Roblox 3D
00:34