Mwaononga/mwaonongeredwa ndalama zingati pa press briefing ya zii ngati imeneyi? Ngati ndalama mulibe nazo chochita, onani kopititsa ndalamazo kwa a khristu anu ovutika. Ndani sadziwa kuti the so called pastors or whatever, are easily captured by politicians. Badyani ndalama zopasitsidwazo ndi andale. Zimene mwayankhula apazi, inunso mukweluza anzanu ngati inu ndi oyera mitma kale
@CharlesLiwonde-y2y11 сағат бұрын
God is watching everything happening in malawi. One day will be one day. I rest my case.
@EmmJay9318 сағат бұрын
The truth is that the bishop has turned into a politician... Well done men of God for condemning his sentiments apo ayi akapereke umboni omwe Ali nawowo and I support your point ndithu...
@TrinityLipipa11 сағат бұрын
Azitumiki osauka ndi mizimu yomwe inu
@MarthaMtengera10 сағат бұрын
God is watching, a Bishop, akupatseni chilimbikitso poyima pa chilungamo.
Munthu ukalephere kutchula mpingo wako why? Mukanakhala amzeru mukanakuitana archbishop kumbari after that mkumapanga izi
@MUSSAHCASIM13 сағат бұрын
Koma ndalama zimatsekadi chilungamo anthu inu mwatani ambuye akuyendeleni nonse azibusa mukudya ndalama za chakwera
@saidimwanyali896912 сағат бұрын
Sisilamu uyu chifukwa Ife asilamu timakonda chilungamo ndi chowona Koma maboza amene alipo mulipoti aja allah akaweruza ma sheikh opani kunena maboza awawa
@PatrickKapendo12 сағат бұрын
Amalawi saliso amalawi ai pano amalawi ambiri ali ndi mtima ofuna kuti dzikoli lisazafike nthawi yachimalizilo tisanalawe nkhondo ndipo chikhumbo khumbo chawo akuona ngati kukhala ophunzira sikubwelesa mau achisokonezo ai kodi aliyese ali ndi njila yopitila kuyifa ngati tili ndi mtima oti adindo sakuyenela kufa pepani chifukwa ifa mwiniwake Mulungu kodi chilima sali ngati munthu woti nayeso Mulungu anampangila machokedwe ake ngati mitimayi yikufunisisa nkhondo tiyeni timupembe Mulunguyo ayankha
@AubreyMwenda-u1s12 сағат бұрын
Kodi zafika poti anthu ayamba kuyankha za mu ulaliki?
@GeraldGomati13 сағат бұрын
Afiti inu mwadya ndalama
@enockkanyerere78413 сағат бұрын
Td Jake's
@AlbertKumwenda-x2l10 сағат бұрын
Inutso amipingo mukutsowa dzochita notse ndinu andale metsa ku unga munapitila lumodzi
@AmosScott-z9x13 сағат бұрын
Nonse mungomveka mwa ugalu galu eeeh
@RoyTrading-b4x12 сағат бұрын
Ndinu zitsiru inu
@tingamasi10613 сағат бұрын
Achewa drama group. Pangani zama church anu asiyeni archbishop nawo Ali ndi ufulu oyankhula zakukhosi. Ndinu agalu mukuyankha ngati ndani?
@WarriorKB-l3i13 сағат бұрын
Za ziii ena amene akudya kobili za mcp kuti amuyikile kumbuyo cikangawa ndi awa.Anthu a satanic awa mbuzi za anthu inu mufune; musafune ife lipoti lanulo tikulikana cifukwa mulibe ca mzeru ciliconse mupanga bwanji imkwayale yopanda black box? Inu dzisilu kwambiri inuo mwadya kobili za cikangawa palibe ca mzeru mukunena inu zisilu kwambiri
@FrancisJumbe-zj4ue13 сағат бұрын
Agalu awawa
@TonykalicheloKalichelo12 сағат бұрын
Km mulungu akuonen zoona inu imfa imene ija mwalola kupeleka umbon wabodza ai zikomo