Mai Mary Chilima report la Ku Germany lija.............................

  Рет қаралды 3,828

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

29th September was our wedding anniversary.
Ndikupempha nonse okhudzidwa kuti mundithandize kumema kafukufuku wapadera, kuti timve tsatanetsatane wa zomwe zinachitika pa 10 mpakana pa 11 June. #commissionofinquiry
Mai Mary Chilima, amene anali mkazi wa malemu a Saulos Chilima, apempha Amalawi kuwathandizira kuti pakhale kafukufuku wina wapadera pa ngozi ya ndege yomwe idapha amuna awo ndi anthu ena asanu ndi atatu.
Iwo alemba izi pa tsamba lawo la Facebook pomwe lero akukumbukira tsiku lomwe adalowa m'banja ndi a Chilima.
Pempheroli ladza pomwe magulu ena kuphatikizapo CDEDI, Public Affairs Committee komanso chipani cha UTM akhala akupemphanso kuti pakhale kafukufuku wina.
Maguluwa akukhulupilira kuti lipoti la akatswiri aku Germany silingabweretse poyera mayankho ena monga chomwe chidachedwetsa kufufuza ndegeyi itasowa.
Koma m'mbuyomu, nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu idati boma laika chikhulupiliro chake pa akatswiriwa.
Mu chithunzimu, mai Chilima pa malo omwe padachitikira ndege ku nkhalango ya Chikangawa.

Пікірлер: 45
@FloraBanda-w7t
@FloraBanda-w7t 7 сағат бұрын
Chakwera ngat sanaphe ndiyeyo akukanilanji kupanga kafukufuku
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 7 сағат бұрын
Ka report ka chakwera kaja ndikabodza Ndipo ndikachamba 😢😢😢😢😢😢😢😢RIP SKC
@jamessheki4293
@jamessheki4293 7 сағат бұрын
Kuona amalawi umbuli
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 7 сағат бұрын
Amayi pepani tikulila limozi ndipo sitikusiyani tikhalananu pamapemphelo buyen zimu wao uziusa mu ntendele
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 7 сағат бұрын
MCP imationa kupusa kwambiri. Iwo omwewo akuti black box alinayo omwewonso akuti palibe.
@gaddiemkandawire6436
@gaddiemkandawire6436 6 сағат бұрын
Abwana ndikhoza ngakhale inuyo mukudziwa chilungamo chake . Kungoti nangasi apa ndipa social media
@WilliamMasauko-su1wx
@WilliamMasauko-su1wx 8 сағат бұрын
Inu kafukufuku uja kunali kokayikitsa silinali lokwanira
@AubreygEliasizia
@AubreygEliasizia 7 сағат бұрын
Zoonadi pakhale kafukufuku wina
@rashidadan2533
@rashidadan2533 4 сағат бұрын
Saulos Cláuds Chilimas was killed by mcp officias , and no need another commission of enquiry right now , okhuzidwa onse ali m'boma , palibe emwe wamangidwa kapena kuchotsedwa ntchito , So akubanja ingopangani chiganizo china posadikila kuboma
@RajabShahida
@RajabShahida 5 сағат бұрын
Ifeyo angoni aku mzimba nafenso tikufuna report lija litambasulidwe bwino apo ayi eni akefe tithamange pa ground tipedze chilungamo chenicheni
@LimbikaKaliati
@LimbikaKaliati 6 сағат бұрын
Mama SKC tilinanu limodzi mwina tingapeze mayankho pamafuso ochuluka omwe anthu alinawo,
@JesseKanjanga
@JesseKanjanga 5 сағат бұрын
ZOBISIKA NDIZAYEHOVA,ZOULULIKA NDIZAANA AMULUNGU.AMBUYE OONA ZANSELI AKUMVA KULIRA KWANU,NDIPO OR INESO SINDIMVETSA ZAIMFA YAATHU AMEMEAJA
@paulkalizangoma5904
@paulkalizangoma5904 7 сағат бұрын
Report yandege inachitika biased koma yomwe tikufuna ndi report yopanga involves azipani zonse komanso achibale. Anapeza anthu awo kumbali but this time we need a comprehensive report that will involve achibale ndi zipani zotsutsa. We need the truth in this. Your report was unbalanced.
@HassanMussah-i9j
@HassanMussah-i9j 7 сағат бұрын
Report la ndege lija muli mafuso ambili kom chitsilu ndi presetnt chifukwa chilichonse akudikila kukakamizidwa ndeye anthu adziwa chiyani komaso tiganiza zotani chifukwa sizoona kut anthu adzichita kukakwmiza kuti akhazikitseso kafukufuku chimene chimafunika report linabwelamo akhazikitseso kafukufuku wina komaso anthu awafuse kuti kutacha chinachitika ndi chiyani mukhoza kuona chilungamo cheni cheni tsono munthu akakhala Kut akunyala nyaza zimangoonetselatu kuti penapake sipanaende bwino mot or ine ndikumukaikila chakwela chifukwa chazichito chito zake
@jamessheki4293
@jamessheki4293 7 сағат бұрын
Munthu okuti adziwa bwino lomwe president,akanakhala ena akanazichepesa koma akulubwa kwambiri kusonyeza akudziwapo kanthu
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 3 сағат бұрын
Rip SKC 😢
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 4 сағат бұрын
Inatuluka ija ndi report inde koma sikuyankha mafunso omwe tilinawo yangonjezerapo ochuluka.
@RiteRoderick
@RiteRoderick 4 сағат бұрын
Boss mumakwana zedi n i lime your back ground eeeeee🙏🏿🙏🏿 RIP Chilima izizi zonse zizabwera poyera nwxt year after mavoti
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 6 сағат бұрын
Mcp singatulutse lipoti lenileni koma chotimudziwe anthuinu chilima anachita kupangidwa chipongwe olo mwana amadziwa izi
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 6 сағат бұрын
Like Malawian's, mum sorry, We're with you forever mpaka chilungamo chitadziwika lija ndi report lawo not la chiwembu adachikonzachi no! Kuchitike kafukufuku wapadera oti tipeze chilungamo pa nkhaniyi sinanga sakufuna kuyankha mafunso a Malawi tonse pomwe akufuna kupeza mayankho, Ndizopweteka ndipo nzowawa kwambiri "Ochita samva kupweteka Koma ochitilidwa.... Mulungu azikudalitsani nthawi zonse.
@LimbikaKaliati
@LimbikaKaliati 6 сағат бұрын
Mama SKC tilinanu limodzi mwina tingapeze mayankho pamafuso ochuluka omwe anthu alinawo,
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 4 сағат бұрын
Aaaa MCP ili papandopa anthu nsitigadziwe chilungamo koma mistake inayamba popanga ubale ndi MCP from history ndimene imapangila kuyithandidzamo zkomo wake amakhala otelo bs mai iwe limba mtima mene ukulimbilamu matso kwa mulungu bs
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 5 сағат бұрын
Report lili nd mang'alu ochuluka, one chakwela anatiwuza poyela kuti ndege inakafika kuzuzu koma chifukwa chanyengo anayibweza koma report inatisimikizila kuti ndege sinafike kuzuzu two kukunyu anatiwuza kuti ndege inali nd zose zokwanila koma report inatisimikizila kuti ndege inalibe zipangizo zokwanila even battle linali lakutha ndye tingakhulupilile bwanji phala ngati ili
@RiteRoderick
@RiteRoderick 4 сағат бұрын
MCP inachita kudya Munthu opuma, izizi sitiinvayi kwawo kwatha agaru anenewa
@FrankDamiano-u7t
@FrankDamiano-u7t 7 сағат бұрын
Ifeyo tili pambuyo panu mama tikulira nanu limodzi tikuikizani mmapemphero mpaka Ambuye atavumbulutsa zoona zeni zeni pa ngozi imene ija
@YusufLiffah
@YusufLiffah 6 сағат бұрын
Chakwera anapereka kale report mawulende awiri ndipo mosiyana nde apa akufuna afufuzeso kuti awapatse report lina kkkkk
@ManalYahya-q6o
@ManalYahya-q6o 7 сағат бұрын
Mwaganiza mochedwa akubanja inu poyamba pompaja zikanaoneka bwino
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 5 сағат бұрын
Any hiden files will be reveal. Mulungu si jemusi
@Felixbanda-q6p
@Felixbanda-q6p 7 сағат бұрын
ngat boma silibwela kunena zona chakwela tipha bas ativa kuwawa
@JasonMailos
@JasonMailos 6 сағат бұрын
MCP ikuthawa thawa cholonda chokhala Pathupi pawo iwgidwa olo itagula a Malawi ose
@EdwardChapola
@EdwardChapola 6 сағат бұрын
Ndizoona kafukufuku achitike wina
@ChemandandacassimMilanz
@ChemandandacassimMilanz 7 сағат бұрын
Continue
@EshurChimtengo
@EshurChimtengo 6 сағат бұрын
RIP SKC
@EdwardChapola
@EdwardChapola 6 сағат бұрын
Kalipot kaja ndikachibwana
@MusaJohn-t8x
@MusaJohn-t8x 7 сағат бұрын
Kwafuta mn
@PhilasandeMgavu
@PhilasandeMgavu 7 сағат бұрын
🤲🤲👍
@YammsyZebron
@YammsyZebron 8 сағат бұрын
😢
@AchinaKellz
@AchinaKellz Сағат бұрын
Mery kayimire utm pompo pompo boma utenga ndiye tiweruze angakhare mulungu adzaweruza koma tiyambe kuwaweluziratu
@LovenessBanda-p5s
@LovenessBanda-p5s Сағат бұрын
Levoness Banda iwe udziya nkhula mowopa mulungu
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 сағат бұрын
Kodi Kani ndi koyera chonchi mmesa ankati ndi kuchikhalango kosapitika ???
@lightwellsilumbu
@lightwellsilumbu Сағат бұрын
Or Chakwera kukaika Duwa, or kukaona padafera vice wake kuchikangawa ayi ndithu.
@AchinaKellz
@AchinaKellz Сағат бұрын
Awa alira a mcp ndizitsiru wina sangona
@RhodaChimoyo
@RhodaChimoyo 2 сағат бұрын
Komatu Chakwera,🙄🙄🤔😭😭
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 Сағат бұрын
Nkhaniiyi ivuta enaamangidwa
@Jarisi-hh8bs
@Jarisi-hh8bs 27 минут бұрын
AMALAWI ANZANGA KOMA MWAIMVA IYI?
6:01
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 3,3 М.
Will A Guitar Boat Hold My Weight?
00:20
MrBeast
Рет қаралды 246 МЛН
Every parent is like this ❤️💚💚💜💙
00:10
Like Asiya
Рет қаралды 12 МЛН
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Senior Prophet Rodrick Mtupa SC
Рет қаралды 47 М.
Nigerian Scammers Extradited To The U.S To Face Justice
11:49
Adeola Fayehun
Рет қаралды 220 М.
KUSEMPHANITSA KWA ZIZIMBA, ZOMWE ZINAPHETSA SAULOS CHILIMA 🤯😭
35:46
Amalawi tidzameta maliro a Chilima 2025
7:57
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 56 М.