NKHANI ZA LERO PA TIMES ANGOING'ALURA SANABISE KANTHU PA ZOMWE ZACHITIKA LERO KU PARLIAMENT

  Рет қаралды 21,197

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@mariawachesterweluzan
@mariawachesterweluzan 2 күн бұрын
Tiyen tikamatche chakwela asiye pansi udindo wa president pompano pompano 🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃
@LusNicolus
@LusNicolus 2 күн бұрын
Mavuto ku malawi 😢😢😢😢😢😢😢apa uyu achoke basi u president wamukanika 9:29
@mussahmustafa5992
@mussahmustafa5992 Күн бұрын
😂
@blessjare
@blessjare Күн бұрын
Ndine mmodzi amene ndili dziko la Zambia koma dziko langa Malawi ndikulifuna koma ndikulephera kubwrra chifukwa Cha ulamuliro oipa wachakwera
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Күн бұрын
Uyu bushiri sangamakapangile Dziko lina zasatanic zakezo
@IbrahimIsmael-h2w
@IbrahimIsmael-h2w 2 күн бұрын
Iye amakatani kupalamentiko?Anthu akwiya m'zikomuno😂😂
@McfallenKayuni
@McfallenKayuni Күн бұрын
Ndi Chakwera yekha amene amakwanitsa kufika kunyumba yamalamulo ndi kuyankha mafunso
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Күн бұрын
Apule tu ananena kuti sadziwa chilichonse amagwila ku chipiku lero ndi zimenezi
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l Күн бұрын
Chimwendo Banda akupusisa chakwera ndibwino wose atulepasi udindo chifukwa sakuganizira anthu awo
@BlessingsAyamie-n2m
@BlessingsAyamie-n2m 2 күн бұрын
😅😅kumuphaphalitsa mafuso munthu wankhulu mpaka kuthawa sanati ameneyo athawa zen zen
@BamusiKazembe-y8b
@BamusiKazembe-y8b Күн бұрын
Chilichonse Cha kwera
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Күн бұрын
Zamukanika kutsongolela dziko
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 2 күн бұрын
Wayiona sataniki chakwera ni bushiri mwapha anthu ambiri inu
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 күн бұрын
Namachende chakwela ndi chimwendo munya 2025 mbuzi za anthu kunthawa mafunso 😂😂😂😂😂 mumati chani dzulo lija kuja mumalalata kuja machende anu
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Күн бұрын
Ichi chamunthu wawukulu chikuyesa ngati chili kunyumba kwake kuti chitha kupanga any how chimwendo
@CassimJafali-g4l
@CassimJafali-g4l 2 күн бұрын
Malawi tiyeni tigwilane manja povota mwaunyinji ndikuchotsa nyasi zaboma la chakwela watikwana
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 2 күн бұрын
Wanya nayo ma questions chikangawa
@JosephNambazo
@JosephNambazo 2 күн бұрын
Azikalima amako nyamakoso ndi Chakwera wakoyo galu iwe
@henryphiri6100
@henryphiri6100 2 күн бұрын
Chimwendo Banda kuiwala kuti president yo ali payroll yamisonkho yathu.pano akutiuza kuti nthawi yatha. Yathera ndani. Chakwera achikhala wanzeru anakamuuza chimwendo kuti ima kaye ndiyankhe funso lokhalo for the benefit of malawians
@PeterTembo-zj5jk
@PeterTembo-zj5jk 2 күн бұрын
Wakhawula 😂
@GonaMkuphe
@GonaMkuphe 2 күн бұрын
Zamanyi njala yochita kukonzayo zitsiru inu
@GodsFavourite1
@GodsFavourite1 2 күн бұрын
@@GonaMkuphe okhee...
@MphatsoChilangiza
@MphatsoChilangiza 2 күн бұрын
Koma kumeneko
@Khadija-q9r
@Khadija-q9r 2 күн бұрын
Zina umangoona waziyamba
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂
@MadalitsoMsakambewa-q1k
@MadalitsoMsakambewa-q1k 2 күн бұрын
Zipagizo zadula
@paulkayange-jr5kv
@paulkayange-jr5kv 2 күн бұрын
😂😂😂😂
@EdenBrigadia
@EdenBrigadia 2 күн бұрын
Muzilima agalu inu Boma simalima chimanga chimanga katengeni mthalika
@BrendaJailosi
@BrendaJailosi 2 күн бұрын
Mmmmmm ok? Nthawi ya Muthalika tu fertilizer otsika mtengo analiko nanga lero chikangawayu akuti bwanji? Anthu inu zisamani olankhula ngati anthu osagwira mutu tiyeni tiziganiza tikamafuna kukamba nkhani zinazo kmnso manyazi ndi umunthu muzikhala nawo mwina awa nda bale anu nde mavuvu mukupangawa eti inu ndamene mukudya aponso mwina mukugona nayo njala km makani chabe ukuchemelera zosatheka 👂👂
@GodsFavourite1
@GodsFavourite1 2 күн бұрын
Kachitsiru kopanda nzeru iwe, anthu akuvutika, mawa ndi iwe ili ndidziko...udzakumbukila mawu angawa ..pompano I swear!
@PempheroMoleni
@PempheroMoleni 2 күн бұрын
​@@GodsFavourite1ndi zoba kape ameney
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 күн бұрын
Amalawi,omwe abale awo akuba ndalama mu bomamu amatelo ngati,nyau imeneyi khope yache ngati chotsema kufana ndi mtima oipa wa chakwela,okumwa magazi,anthu osalakwa, mulungu wa amoyo,akulangeni
@MartinKapanga
@MartinKapanga 2 күн бұрын
anthu akulima Koma boma silikukonda anthu zinthu adulisa president sakukonda amakawi
My scorpion was taken away from me 😢
00:55
TyphoonFast 5
Рет қаралды 2,7 МЛН
Мен атып көрмегенмін ! | Qalam | 5 серия
25:41
Mom Hack for Cooking Solo with a Little One! 🍳👶
00:15
5-Minute Crafts HOUSE
Рет қаралды 23 МЛН
Kell Kay & Great Angels Choir -Hallelujah-(Inuyo) Official music video 2024
5:04