BOMA LA ACHAKWERA ALEPHERA IZI ZAKAMBIDWA PAMENE ANTHU ONYASIDWA APANGITSA PRESS BRIEFING LERO

  Рет қаралды 52,229

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 223
@DadTshepo
@DadTshepo Ай бұрын
I never knw this Guy until today BIG UP BRO We All MALAWIANS WE ARE BEHIND YOU 🙏🙏and GOD BLESS YOU MAN
@MariaNkhata-i9q
@MariaNkhata-i9q Ай бұрын
Weldone Mr Namiwa that's powerful
@victormbewe7462
@victormbewe7462 Ай бұрын
Mr Namiwa chiyambireni sindinamverepo speech yanu komano lero ndamvera💪💪 Ndiwe olimba mtima ngati Julias Malema osaopa osatopa ndipo osafoka 💪💪
@billymhoni9527
@billymhoni9527 Ай бұрын
Mr Namiwa you our truly freedom fighter we as malawi you have our support
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Ай бұрын
Opusa ndife amalawi...mbuzi za anthu We toralate nosense
@BeatriceProfessor
@BeatriceProfessor Ай бұрын
Mamawe now namiwa ukubwera ngati coming new Generation 😂😂😂kodi ku Malawi kuli anthu olimba mtima ngati chonchi aaaaa mumwa chani? Mr true leader I don’t believe this yooo am so proud of you namiwa i hope mwabwera ndi Mulungu angokusiyani kenako Mulungu apitaso kumwamba basi ✊✊✊✊✊💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤❤❤respect pati
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala Ай бұрын
Tili nanu limodzi dziko lamalawi silibwino😢
@AmosBandula-up4yb
@AmosBandula-up4yb Ай бұрын
That's true powerful message thank you my brother .
@ElliottBelon
@ElliottBelon 15 күн бұрын
Real freedom fighter...mr namiwa
@jamesjillan9687
@jamesjillan9687 Ай бұрын
Anamiwa our hope now lies on you,mwina Malawi nkupulumuka kumavuto omwe tilinawo,big up sir.
@ernestphiri5507
@ernestphiri5507 Ай бұрын
The president must step down to allow the commission of inquiry to investigate about the chikangawa accident freely
@clementgama-u5p
@clementgama-u5p Ай бұрын
Keep pressing mr namiwa God bless you
@SailotaSamuel
@SailotaSamuel Ай бұрын
Kupanda Inu omenyela ufulu bwenzi tonse titafa ndi njala osatopa anamiwa please 😢😢😢
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Ай бұрын
Viva Mr Namiwa, ur freedom fighter like Julias Malema
@KennethMugabe-f9l
@KennethMugabe-f9l Ай бұрын
Very good and powerful speach namiwa
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Ай бұрын
We need people like u who honest in poor Malawians
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
❤❤❤ we are with you bro let's fight for our country Malawi dziko lathu lawowa chiwewa under the ulamuliro wa chakwela mcp this people they must go
@emmanuelalbertbotolo
@emmanuelalbertbotolo Ай бұрын
Chakwerayu chikuvuta ndiyani kupanga resign awapatse atsogoleri ena ,iye chimene akudziwa kuba ,kuyendayenda maulendo opanda ntchito ndikupa bac ,achoke walepera zomwe adalonjeza kuti azachita
@GiftMingo
@GiftMingo 29 күн бұрын
Nsanje ikuphani. Apange resign chifukwa chainuyo? He was voted by Malawians.
@DoreenMuhota
@DoreenMuhota Ай бұрын
Mr namiwa mulandire ulemu wanu 💪💪❤
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n Ай бұрын
wow, wow, wow, speech yomveka bwino ndipo yogwira mtima ndipo Yoona . atiuze zoona agalu amenewa
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed Ай бұрын
Agalu amenewa achoke atikwana a mcp. Awonjeza, kupha, katangare, tsankho, kuononga, komanso jealous ndi dzipani dzotsutsa.
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug Ай бұрын
Mr Namiwa You for one thing the Kunkuyu said that state got blackbox and its self .. pano akuti mu denge munalibemo blackbox anthuwa akudziwa chomwe chinachitika
@memoryziyaya2593
@memoryziyaya2593 Ай бұрын
i salute this papa..#SN💥no fear!!
@DysonGonthi
@DysonGonthi Ай бұрын
Keep the fire burning Mr namiwa🔥🔥🔥
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 Ай бұрын
Following and straight to the points ena ali pa mpando chifukwa Biyeni anthu anamukonda ndikumvera kuti tisankhe izi
@chrisboyce2
@chrisboyce2 Ай бұрын
Thank you Comrade NAMIWA we need people like you woyipa pa Chilungamo nthawi Zonse Ndipo Osaopa, osafooka and Osatopa 💪 SKC 💔
@Halima-i4x
@Halima-i4x Ай бұрын
Namiwa kulimba m.tima uku ndikomwe timakufuna your are big ma chine
@EsetaGerate
@EsetaGerate Ай бұрын
❤❤❤ anapanga chiwembu chaumburi agaru amenewa
@LuskaMoses
@LuskaMoses Ай бұрын
Ambuye akudakitseni bwana mulungu akukuteni ine tsiku tsiku kulira abiyeni anapha Muthu wofunikira kuntundu wa anthu chakwera munalakwitsa koopsa😢
@PatumaCassimu
@PatumaCassimu Ай бұрын
😅😅bambo asikono bweran muzamuyakhire mr chikangawa kuno wapanika nd mafuso 😅😅
@bennihope3272
@bennihope3272 Ай бұрын
Mr Namiwa, the God's appointed servant. osatopa, osafooka, osawoopa. Malawians are behind u 200%. Let the truth prevail
@FortyoneHarwa
@FortyoneHarwa Ай бұрын
inu a Mr namiwa pitilidzani kutiimilira ngati tsimtero tonse adzatipha anthu awa ife tilinanu limodzi
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 Ай бұрын
❤❤❤❤ thax anamiwa
@AmosJere-k9g
@AmosJere-k9g Ай бұрын
We need Men like you in our Country
@ImranYusuf-p6c
@ImranYusuf-p6c Ай бұрын
You are number one Mr 👑
@douglasturner2992
@douglasturner2992 Ай бұрын
We are PRAYING day and night.
@MarriamBakalie
@MarriamBakalie Ай бұрын
1 mistake that we dd nw we r crying for 5yrs.. oh God hv mercy
@EnochDondah
@EnochDondah Ай бұрын
Big up mr namiwa lero ndachita kumvera 10 times mpaka tinayika chimkuza mau koma simomwe kunazazila athumu kumvera inu bwana
@AllanBinali
@AllanBinali Ай бұрын
Strong man ,, do not allow fear to rule our lives
@Chikulamayembe57
@Chikulamayembe57 Ай бұрын
We are with you brother!
@cynthiataulo5211
@cynthiataulo5211 Ай бұрын
Aliyense amene ali ndi umboni awupeleke, Mafia Chikangawa Party( MCP) yatiliza. These ppl must resign and appear before court of law.
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie Ай бұрын
God should protect you Silvester Namiwa
@memoryziyaya2593
@memoryziyaya2593 Ай бұрын
Ndithudi..coz this Rulling Party no trust @all kkkk
@AllieJonassi
@AllieJonassi Ай бұрын
Ku malawi ko tikadakhala kut tili ndi anthu azelu ngat Inuyo Mr namiwa bwesi anthu asakufutika ngat m,mene zilili pakadali pano proud of you Mr namiwa
@jonathanmasebo1591
@jonathanmasebo1591 Ай бұрын
God protect you anamiwa
@Yaqub-nk4pu
@Yaqub-nk4pu Ай бұрын
You will still see mcp lovers crapping hands for such huge devaluation of kwacha, Achewa inu mumadziwa koma kuti dziko limayenda bwanji?
@FelixKachera-je4yk
@FelixKachera-je4yk Ай бұрын
Penaso aseeee ukumatibalalisa aaaaa wayambaso kukaikisa😂😂😂
@NickUpoche
@NickUpoche Ай бұрын
Keep it up br ,osafooka osachita matha
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 Ай бұрын
Chakwera wakupha Galu wachabe chabe Mfiti Mbudzi yopanda manyu kunsi chilungamo tikuchidziwa Anatipweteka Chakwera ndithu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@NEBRA-lm7ji
@NEBRA-lm7ji Ай бұрын
Words without action aaa zuttiwawa😢lets fight
@HassanJimmy-r1n
@HassanJimmy-r1n Ай бұрын
Ayankhe mafuso amenewo,afune asafune ngat sakufuna kuyankha angotula pansi maudindo awo mwaulemu chonde ,komanso Apuresidenti mutiwuze maphindu amawulendo anu amene mukuyenda tsiku ndi tsiku ndalama zimene mukuwononga ndizambiri nankha ifeyo A Malawi tikupeza ndalama zingati pamawulendo amenewa ? Komanso zikugwirizidwa tchito yanji ku Malawi kuno ? nankhano chikusintha ndichiyan? Komanso nthawi yatha pankhan yawulimi za AIP zilipati ? Please Mr President tiyankhen mwachangu🙏
@BvutoOsman
@BvutoOsman Ай бұрын
Your more than Limpopo FM and bakili miluzi TV
@CharityKantunda
@CharityKantunda Ай бұрын
As malawi we are waiting for the truth
@charleskalajira380
@charleskalajira380 Ай бұрын
Powerful
@ElizabethKalonga
@ElizabethKalonga Ай бұрын
God help Malawi.
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z Ай бұрын
AFFORD, UDF, DPP ndi UTM ndi wotimenyera za ufulu chonde chitanipo kanthu osamangoyang'ana anthu awa ali ndi cholinga atimaliza tonse amalawi psiti apange resign chakwera yooo 2025 kwatalika
@PoriinaForias
@PoriinaForias Ай бұрын
understandable
@williammandhlopa
@williammandhlopa Ай бұрын
God have mercy on us
@DoricaGoweka
@DoricaGoweka Ай бұрын
Ulemu wanu Mr.Namiwa ndi gulu lanu.Ndipo Lazaro watitora kwambiri ife amalawi.Akudya misokho yathu mosaganixira ife. Tiyeni tichitepo kanthu achoke kanyimbi ameneyu.Nawo asilikali athu angoti pheee osamukankha chifukwa chiyani pomwe tonse tikuvitikira limodzi. Kanyimbi ameneyu watikwana kwambiri ndipo tisadikire 2025 tatopa
@benjaminchimwere9483
@benjaminchimwere9483 Ай бұрын
Exactly, how come vp osakhala ndi chitetedzo choyenera?? 😢😢
@MalonzoMazombwe
@MalonzoMazombwe Ай бұрын
Hon namiwa, chiyambireni kumenyera ufulu mulibe mbiri yoipa ngati activist enawa omangokhalira udzakwaye kwachakwera, inu mulibe dyera muli ndi ma bizness anu okuthandizani komanso simusankha munthu mukafuna kudzudzula.. pitilizani bwana, send number yanu.
@Happiness-p9z
@Happiness-p9z Ай бұрын
Munthu wamkulu kulankhula mosapsatira big up
@SamuelMukhura
@SamuelMukhura Ай бұрын
should step down as president,and also the rest should be resign
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 Ай бұрын
Boma latha ili palibe chazeru
@JanaJovian
@JanaJovian Ай бұрын
Mr namwiwa mukuyesesa koma a mcp atinzuzakwambili
@DouglasDimingu
@DouglasDimingu Ай бұрын
Wina azit chakwera boma🙄
@hopembendela
@hopembendela Ай бұрын
Today you talk like seriously big up
@wendaemily3179
@wendaemily3179 Ай бұрын
Chifiti chi president ichi
@LewisFrancisco-o3b
@LewisFrancisco-o3b Ай бұрын
Namiwa fire
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 Ай бұрын
Let's put everything in God's hands he is the one who knows what has happened and one day the trueth will come out bisani matenda koma maliro akachitika tizamva
@mailos.laisoni7001
@mailos.laisoni7001 Ай бұрын
Good work
@PatrickJames-m3w
@PatrickJames-m3w Ай бұрын
Ma men you went school keep it up.
@KumbukaniKafatia-cd2hq
@KumbukaniKafatia-cd2hq Ай бұрын
MUMAKHALA NDI NKHANI ZABWINO KOMA BACKGROUND MUSIC YANUYO IMANDINYASA KWAMBIRI. TIZASIYA KUKUPANANI FOLLOW
@LeonardDavid-tc5iv
@LeonardDavid-tc5iv Ай бұрын
Big up
@CharlesPhiri-ds1rk
@CharlesPhiri-ds1rk Ай бұрын
Ndipo ndizoona Namiwa sizikuyenda kumalawi kuno
@Dan44-x5b
@Dan44-x5b Ай бұрын
Zamanyazi bwanjiii komaaaaaa
@jaafarstenala1166
@jaafarstenala1166 Ай бұрын
😂😂😂 zithu zinasithad et dziko linapita palibe kupanga zinthu mobisa pano anthu anadukusula
@VictorUsen-f7d
@VictorUsen-f7d Ай бұрын
Km mess tinkauzidwa kt tidzaona nyekhwe?musiyeni amalize zaka zake
@raymondchilimba7010
@raymondchilimba7010 Ай бұрын
Kwawonse omwa adanamiza president Zaboza, atule pasi udindo ndikumangidwa from general wa asilikali....
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie Ай бұрын
Wosati mbuzi zija za human rights zinabwera zana zija
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo Ай бұрын
Eeee ndipo kuli mafumbo 😮😮
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 Ай бұрын
Chimene amandisangalasira namimwa ndichoti amalankhula zomveka.
@mathewsnachuma8086
@mathewsnachuma8086 Ай бұрын
Ma phoneo alipo? I have the possibility to recover deleted files
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Ай бұрын
Mvuto la channel yi ma video ake kuyima yima each video please try to fix timakunyadilani pantchito yabwino
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Apo mukamba chamuna big alephela awa,,zoona dziko paka ma passport kumavuta olo Zimbabwe 🇿🇼 inavuta koma ma passport sanavute , koma achakwela mmmm sikukudani koma chikondi mulibe ndidziko, kodi ngati mafika saizi yomupha chilima anakulowetsani boma, kodi ife amalawi wamba mutisunga??
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 Ай бұрын
Komano osangokambirana zoti atule mpasi udindo bwanji, ma brief akambidwa but no solution. Mukakamiziine atule mpasi upesideti basi, president wannji omangoyenda even kuchiletsa osatheka aaaaa woke up guys
@Yohane-bg8bn
@Yohane-bg8bn Ай бұрын
Ziko siliyedesedwa ndi ma little boy ikufunuka ma big boys peter ananana kale
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie Ай бұрын
Commission of inquiry Namiwa azakhalepo basi
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Wel come
@giftkayome3568
@giftkayome3568 Ай бұрын
Mizimu yakwiya the truth is coming out now
@DamianoYohane
@DamianoYohane Ай бұрын
Chakwera sakuyenela abwerereso ku Malawi kuno. 😢
@AndrewMdala
@AndrewMdala Ай бұрын
Awa azipita basi tatopa nawo Anthu akupha panyapawo munya muona onse adzafela kundende Ndipo namiwa ulemu wako awozeni panya pawo
@RiddleQuizGame
@RiddleQuizGame Ай бұрын
Atolankhani amabungwe amipingo ndi azipani kodi mukudziwa kuti nditapita ku NRB ndapeza National ID yanga akuti was issued pomwe ini sindinapatsidwe? Kodi ziphasozi zikumapita kuti? Motero pakanali pano sindine wokhutitsidwa kuti chaunzika chidzagwiritsidwe ntchito povota. Lamuloli likufunika likasinthidwe mwachangu ku Parliament.
@ThomKuyenda
@ThomKuyenda Ай бұрын
Chilipo akubusa akubomaku. Pajatu kunali gwilizano wa 5 years wina abweleso kudzalamuliraso 5 years. Zimene zija ndi zimene zinamuphetsa munthu uja kuphatikizaso mulandu anauthetsa uja. Chifukwa umakhudzaso munthu wankulu
@AffickChaona
@AffickChaona Ай бұрын
Namiwa katundu ❤
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 Ай бұрын
Tili nanu limodzi 💪💪💪💪💪
@nt625
@nt625 Ай бұрын
A Namiwa ndinu munthu wa Mulungu. Pitilizani mpaka a Malawian adziwe chilungamo.
@lastonekaponya7675
@lastonekaponya7675 Ай бұрын
True soil of man
@YohaneChitapini
@YohaneChitapini Ай бұрын
Zoona ndipo ndagwilizanana Nanu ndipo mafuso abwino
@Sammy-vb1ed
@Sammy-vb1ed Ай бұрын
Atsogoleri akamapita kwakugwa amapanga zoononga komanso kusanvera anthu akamawadzudzula. I hate chakwera the he run this government. Mcp is going to fall and shall never pass elections.
@billymhoni9527
@billymhoni9527 Ай бұрын
Nkhani ndipo isalekeleledwe otherwise tose sitili Safe mmalawi mono achakwera ali ndi mafunso oti ayankhe
@Aishajames-od5uy
@Aishajames-od5uy Ай бұрын
REAL 3D brush can draw grass Life Hack #shorts #lifehacks
00:42
MrMaximus
Рет қаралды 12 МЛН
Kluster Duo #настольныеигры #boardgames #игры #games #настолки #настольные_игры
00:47
Всё пошло не по плану 😮
00:36
Miracle
Рет қаралды 3,4 МЛН
Когда отец одевает ребёнка @JaySharon
00:16
История одного вокалиста
Рет қаралды 15 МЛН
Assista na íntegra o Fala Moçambique 23/10/2024
Portal FM | Fala Moçambique
Рет қаралды 2,5 М.
Bobi Wine yekengedde Kapere
7:01
Roots Media
Рет қаралды 177 М.
REAL 3D brush can draw grass Life Hack #shorts #lifehacks
00:42
MrMaximus
Рет қаралды 12 МЛН