Amene muli ndikuthheketa chonde perekani chitetezo kwa Mr Namiwa chifukwa galu chakwera sakupuma naye bwino afuna amuphe chifukwa kupha to Mr chakwera it has become his habit,Yehova mtetezeni mkuluyu
@henryphiri610026 күн бұрын
Anali ku state house Namiwa. Chitetezo si vuto ayiii ndiodzidalira
@ShamimuBisani26 күн бұрын
Mulungu pasogolo
@abwinoamatani492126 күн бұрын
Namiwa couldn't fight from within coz he is intelligent. He knew that the report was already drafted
@AtupereSadiki26 күн бұрын
May the almighty God protect u Mr Namiwa
@MwenekabwekayondoSilumbu-g4x25 күн бұрын
Amen
@DuncanThambala26 күн бұрын
You are giving out the real facts, your explanation tells the right evidence
Kma Namiwa ndi zii. I loved chilima , chilungamo chioneke ndithu.
@JaneSelex-i6m24 күн бұрын
Go ahead namiwa.... i love it
@isaaczuze27 күн бұрын
Koma namiwa si munthu wamasewela ayi ndipo amaziwa milandu ......munthuyi ndi mwana wa amfumu a namiwa .......munthu ameneyi zina ili la namiwa kwawo ku thyolo ndi amfumu .....ineyo ndiye namiwa amandisangalasa kwambili chifukwa Ali ndi mfundo zogwilika ......chakwara akuyenela kuchoka ....mbuzi ya munthu iyi
@eunicesaiti26 күн бұрын
More 🔥 🔥 🔥🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 Zikomo Mr Namiwa.
@0wenNkhambule26 күн бұрын
Good my brother ❤
@RASHIDMALATA3 күн бұрын
A Namiwa ❤❤❤❤❤
@CharlesChibisa26 күн бұрын
Tell us what really happened during the plane crash at chikangawa forest. You are the voice of the voiceless in Malawi.on top of that you are not afraid to climb on top of the mountain fighting for our freedom.
@laurentbutao408425 күн бұрын
Komatu wamisala anaonadi nkhondo.This is real facts
@GeorgeKholongo-ew4qc23 күн бұрын
Namiwa needs people to support and stand with him in public,osati support yobisalira yosabwera ku gulu
@DaveMakondetsa26 күн бұрын
sure Namiwa ❤❤❤❤❤
@NikolasNanawe25 күн бұрын
Kd makanilanja km awa😂😂😂😂😂😂
@EthelBernard-h1m26 күн бұрын
The truth will prevail no matter how long
@PempheroMkusangonbe26 күн бұрын
Namiwa must protect this is light person who help Malawian to now the truth about the plane crushes which take place on 10June 2024 who killed our Late Vice president Dr Souls Chilima ♥️♥️♥️
@GIFTTONY-sw5qh27 күн бұрын
Koma funso la Winston kalimira ndy ndilopeperatu😂😂😂
@GivenMvula-k5k26 күн бұрын
Eti eti 😂😂😂 ndimaona ngati ineyo ndamene ndikupepera koma atolankhani ena😂😂
@RemitterFlik113026 күн бұрын
Atola nkhani akuchikangawa awa
@henryphiri610026 күн бұрын
Namiwa brilliant, u took time to read this report and replied this nosense old people call themselves advocates and lawyers. Ndege yogwa 4.5m singaoneke chonchija. The wreakage was worse
@Martha-m6e27 күн бұрын
Kuli moto kuti buuuuu❤❤❤❤.
@abwinoamatani492126 күн бұрын
Mtolankhani mene akufunsa kuti bwanji a cidec akugwiritsa report loti apanga condemn akuoneka kuti nzeru zake zili ndi malire
@costerbwino33826 күн бұрын
Salute and Stay Safe Namiwa❤
@HakeemJossam25 күн бұрын
Hero!!!
@LucyKulemeka26 күн бұрын
Pafera mwazi ana Mulungu mosamvetsetseka mizimuyi imavuta kwambiri, 😮
@KossimasiMaluwa26 күн бұрын
Namiwa anakupanga ayise supanga ma ziyen kuchipinda 😂😂😂😂
@ChikondiBandah-q5c23 күн бұрын
🎉🎉🎉
@MariaGatoma26 күн бұрын
Mr namiwa mulungu akudaliseni,,,ifa ya chilima imandiwawa paka pano
@HarrisonMatick8026 күн бұрын
We need people like you namiwa in malawi
@DennisKankhuni-b8l27 күн бұрын
Koma namiwa 😂😂😂🎉🎉🎉respect
@LeyvanSamuel-pe5tc26 күн бұрын
Eeeeee namiwa anapasa pakamwa😅 umakwana iweyo
@asahelmachila302626 күн бұрын
We are listening and regurgitating
@MagretChitsime26 күн бұрын
Oo yes❤ Namimwa yemweyi
@GraceShaibu-i9d26 күн бұрын
Big up namiwa💪💪💪
@CassimDawood-x3l25 күн бұрын
U president uja ukufunika munthu wake ameneyu Mr Namiwa osati zinazi kungoziwa kupha anzawo basi mxieww!!!
@HibrahamMtobo-p4n13 күн бұрын
maulemu anu anamiwa ALLH azikudalisani
@alexsumani682326 күн бұрын
long live Mr Namiwa
@ChrispineTemuwa27 күн бұрын
kumbali yandale Malawi ndiziko limene Lilibe Luntha pandale Anthu ake Ndi Amzeru Za sukulu koma Alibe kulimba mtima Mbuli ngakhale itakhala yosaphumzira koma ili yolimba mtima imaposa Gulu Lama Degree omwe angozimva sukulu ndi ndalama koma ali ogonaa😢
@RobertChiz27 күн бұрын
Straight
@SinsaKachale26 күн бұрын
Fireeeeeee❤❤❤❤❤❤
@VITALISCHIKWENI25 күн бұрын
Atolankhani mpaka kugoja kufunsa mafunso?😂😂😂
@d.chemixjiya540626 күн бұрын
Chilichonse Mulungu amapanga ndi cholinga. Ntambo uja anamusiira mpando munthu oyenera, wanzeru ndi othandiza kuposa m'mene akanayendetsera zinthu Ntambo. Namiwa uja ndi boma payekha😂
We are behind you Mr namiwa osawasiya achikangawa awa
@isaaczuze27 күн бұрын
Ndiye pali sisilu zina zikuyankhila zsusilu apa ...akudana ndi namiwa popangisa press briefing .....mbuzi za anthu zomwe zimalandila ndalama zokuba kwa chakwera
@JudieBanda27 күн бұрын
Afiti okhaokha
@CelestinoVincent5 күн бұрын
Koma ine funso ndilakuti boma likakhala kuti silinachoke angatani nanga boma limene lingaza lowelo ndie liti?
@SolomonMumba-i5n27 күн бұрын
Indeed these two deaths have a lot of questions than answers
@chipilirolikatho357227 күн бұрын
Being a Catholic Namiwa it doesn't mean being holy, catholic is just a Church as others in a Christianity religion
@ThokoMsonkho-hy4uc26 күн бұрын
Ife tikuti Namiwa akunena zoona pakuyenera ena amangidwe monga Collin Mzamba,Valitino Phiri,Chimwendo,Londa wa pa Tawa kuti akanene bwino,amene adayimisa kafukufuku ku Chikangawa,ogwira ntchito ku Mzuzu airport ndi a Kunkuyu kuti chilungamo chiziwike osati kuti basi tikhare chete zatha ayi.
@InnocentNyika-t2j26 күн бұрын
Nooo Mr Namiwa you are a failure, don't cheat people, don't think that your ideas will change anything, let God be the best judge
Za imfa ya raph kasambala ndinanenaponso kuti anamuphela dala kuti ikhale nyambo yomphela chilima, if amalawi simuganiza chonchi then the whole country is dead accept namiwa
@TenganiObety27 күн бұрын
Namiwa ndiwe mwamuna phwa!
@EnthusiasticMountain-xd7vn27 күн бұрын
Bravo namiwa❤❤❤
@sparkdymon342926 күн бұрын
Mr namiwa tiyeni nawo MCP tikufuna zenizeni
@DavidMalewa26 күн бұрын
Akuluwa ali ndinzeru koma nzeru zawo akuzigwiritsa ntchito pachabe why, coz if anthu adakana the investigation not to be public akadadekha kukhala momo bwezi atadziwa zambiri kuposa pano and mwinanso ngodya zofunikirazi bwezi mafunso ambiri ataysnkhidwa .koma apapa aaaaaaaa ndikuona ngati mission yachilungamoyi ivuta plus kumathawa anthu azikwanje atatu okha basi aaaaaaa mbola iyi.