BON KALINDO LERO PA 9 JANUARY WATI UTHENGA UWU UMUFIKE CHAKWERA NDIPO IYE AKUTI SAKUOPA AYI

  Рет қаралды 30,741

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 64
@wellingtongodwillkapande
@wellingtongodwillkapande 11 сағат бұрын
We love you the DC in representing poor Malawians. Please continue exposing these mafia government. These mafias have become rich at the expense of poor Malawians that suffering
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 15 минут бұрын
Inu cikangawa aliyense akudziwa kuti walephela ndicifukwa bushiri nae walankhulapo monga iye mzika. Ana a kukhonde nawonso anena kuti cikangawa sakumufunanso, A malawi tisadandaule caka cake ncino nyau izi d zidzipita.💙💙💙💙💙💙boma la a malawi
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 7 сағат бұрын
we love you bon kalindo 🎉🎉🎉 big up umati imilila ife 🇲🇼 ku tiya khulila ambuye azikutezelani potse pomwe muku yendaaaaaa
@SecretMaganga
@SecretMaganga 7 сағат бұрын
Kumwamba juli mulungu zolankhura zidzattha
@MagretHassan-d9i
@MagretHassan-d9i 4 сағат бұрын
Bon kalindo the DC continue the good work
@JohnNdengu
@JohnNdengu 10 сағат бұрын
You are useful man continue working with Malawian ❤
@DominiqueChitimbe
@DominiqueChitimbe Сағат бұрын
your number one the best ❤️💕😍 akatundu 🔥 I love you my brother DC
@AkiduSilaju
@AkiduSilaju 10 сағат бұрын
Bon kalindo ndi #1 .chakwera no matter what sulamulilanso another 5 years.Malawi osauka salora zimenezo.
@ShipileAnafie
@ShipileAnafie 12 сағат бұрын
Mmmmm koma galu ameneyu atiphaadi zowona fetileza K114000 mmmm chakwera ndi galu basi wakupha🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊
@AkiduSilaju
@AkiduSilaju 10 сағат бұрын
Kalindo your # 1 .chakwera ayi ndithu mizimu ya anthu osauka sikulora kuti ulamulilenso zaka 5 zina.olo mutaganiza zozabera but nothing will work.muzagwabe basi.
@EdwardAlli-c6j
@EdwardAlli-c6j 45 минут бұрын
Zoona akalindo,apatseni moto osafooka osatopa ndipo sitikulola zophutsanso
@AkiduSilaju
@AkiduSilaju 10 сағат бұрын
Bon kalindo ndi #1 .chakwera no matter what sulamulilanso another 5 years.M'malawi osauka salora zimenezo.
@lilianprince661
@lilianprince661 11 сағат бұрын
Or mutayankhula motani chikangawa ndi anthu ake sazamva even mutavura zovala poyankhula zosamveka kwaiwo chifukwa zose zikuchitika akuziwa zosezo ndi plan yawo chomwe muziwe amalawi kufika nthawi yomwe tizavotere boma Lina zinthu zose zizakhala zitawonongeka kale pazakhala povuta kuzibwezelesa chofunika apa tiyeni pansewu mademo tipange agalu awa achoke tisanafike kovota
@BantonAli
@BantonAli 5 сағат бұрын
Mwanenatu zoona apa
@ChrispinHyper
@ChrispinHyper Сағат бұрын
Km chaka chake ndichibo achoka ndinthu 😂😂😂
@MariaDandazaraJSDmoio2024e
@MariaDandazaraJSDmoio2024e 9 сағат бұрын
God bless you theDC born kalindo
@MartinMaulidi
@MartinMaulidi 27 минут бұрын
matrida patrick
@WatsonMtegha-r1c
@WatsonMtegha-r1c 6 сағат бұрын
Kuzipatala Mr Bonikalindo kumeneko yesetsani chifukwa sikudzatheka,kuchokera kuyambira mu ulamuliro wa Mr muluzi mpaka pano madokotala amadyela m'makwalamo inu simuona kuti madocter ambiri ali ndi mafamacy.mankhwala akafika madocter wo amazembesanso .ndizovutatu imadya pomwe aimangirira.
@EsetaGerate
@EsetaGerate 9 сағат бұрын
❤❤❤❤ DC 🎉🎉
@DynaWilson-d1b
@DynaWilson-d1b 12 сағат бұрын
Lord have mercy on us pa chakudya pokhapa mmmm sizikuyenda
@AdamRobert-u9v
@AdamRobert-u9v 11 сағат бұрын
Mr DC mumatiimilila mumayankhula chilungamo at all time only these era lidaseka mmakutu nde poti ukamasiya kupuma mmayamba ndi mmakutu kuleka kumva
@MdalaBonomali
@MdalaBonomali 11 сағат бұрын
The DC number one true fighter❤❤❤
@Samson-ve5rs
@Samson-ve5rs 6 сағат бұрын
Nkhumba yatsekula mimba si ine wayambitsa ndi wa Bakili Muluzi tv
@UladiAbudullah
@UladiAbudullah 9 сағат бұрын
The DC number one ❤❤❤
@KondwaniPhiri-l2z
@KondwaniPhiri-l2z 12 сағат бұрын
Koma chakwera ayi sizowona...watinyasamo
@LeeanneMaddens-uw1yd
@LeeanneMaddens-uw1yd 8 сағат бұрын
Loving you Bon kalindo❤😅😅
@WilliamMajiwa
@WilliamMajiwa 5 сағат бұрын
I love people like Kalindo
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 12 сағат бұрын
Kodi adausi anangoti ziiii bwanji 😂😂😂😂
@MakwinjaOliver
@MakwinjaOliver 12 сағат бұрын
Kodi chakwera anali ndani nthawi imeyo akutuwa
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 11 сағат бұрын
Alibe or ndi khoswe yemwe
@CharityGondwe-bw9gs
@CharityGondwe-bw9gs 12 сағат бұрын
Mumakwana bg chakwera watikwana thumba la chimanga 80000 eeee😢😢😢😢 uyuyu atipha
@GraceKANYOZA-e3v
@GraceKANYOZA-e3v 12 сағат бұрын
Atiphadi munthu wathundu wanji wopanda chikondi wopanda chifundo Akuona ngati ndiwamuyaya tsiku likubwera zonse mukuziunjikirazo muzazisiya tatopa nanu ife achakwera
@McsaulosMaimba
@McsaulosMaimba 10 сағат бұрын
D.C ulemu wanu🎉🎉🎉🎉🎉
@PeterChombo-d3h
@PeterChombo-d3h 12 сағат бұрын
The DC ndi mwanadi ooopya kwambiri
@FreddieKanyerere-u2z
@FreddieKanyerere-u2z 9 сағат бұрын
That's 💯 DC.
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 7 сағат бұрын
CHAKWERAYU akudziwa kuti nthawi yamuthera ndi chifukwa akupanga zomwe akufuna
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 11 сағат бұрын
Panop ena atop kukhal moyenda akuganiz ndkapit kuMalawi moto wake ulikumenrko makolo safa ndi njala tamamvani chison Chakwera akuti munal busa umagwirad baibul iweyo Mulungu akuone
@AtupereSadiki
@AtupereSadiki 10 сағат бұрын
Tionesa Sept ngat utazaone vote yaine uzandifunse chikagawa
@OwenNyambose
@OwenNyambose 10 сағат бұрын
The DC ❤❤❤❤
@GoodsonAnusah
@GoodsonAnusah 11 сағат бұрын
Chikangawa fm😅😅😅😅
@BistonMacheso
@BistonMacheso 7 сағат бұрын
Koma chakwera ambuye amuthandize kwambiri Boma APM boma basi
@Raffik-u2k
@Raffik-u2k 5 сағат бұрын
Malo movomeleza kut zinthu zamuvuta pano akuti timuvoteleso kut ayimeso kachikena 😢😢😢😢 chakwera ndi galu kobasi chakwer ndi mwana wa satana
@EstherNdalama-o1n
@EstherNdalama-o1n 3 сағат бұрын
True story
@EmmanuelSimthole
@EmmanuelSimthole 5 сағат бұрын
Mbiri yake itinso mu2 oti wapanga kale mbiri yonyatsa kale
@wesleykantande
@wesleykantande 8 сағат бұрын
Chilungamo chokhachokha. Wosachotsera komanso wosawonjera
@MasterstonardStonard
@MasterstonardStonard 11 сағат бұрын
Kwanthu ndi kwanjeza village t,a mabuka
@EDGARMPIKAMEZO
@EDGARMPIKAMEZO 9 сағат бұрын
Utsogoleli wa MCP ndi wa ufiti komanso anthu ake alibe umunthu. Anthuwa ndi amizimu ya ziwanda ndipo palibe chomwe chimawakhuza pa miyoyo ya mzika. Anyani amenewa. Zoona mmene amalawi akufinyikira kukwera kwa zinthu komanso misonkho yowawa koma mpaka Mtsogoleri ndi nduna zake kumagwilizana kugula ma Galimoto odula choncho? Afisi inu dziko ili mudzalinva kuwawa sindinu amuyaya. Ndipo ndikuona mmodzi otchuka mu ulamuliro uwu akufa mochititsa manyazi tisanafike ku zitsankho. I can see that
@LeonardKambavi
@LeonardKambavi 8 сағат бұрын
❤❤❤
@LimbikaniTambala-z1y
@LimbikaniTambala-z1y 11 сағат бұрын
Koma ine ndikuona kuti uyuyu adzamuitana akafotokoze yekha.
@FrankMwadzaonga
@FrankMwadzaonga 5 сағат бұрын
People are tired of this leadership by this person
@LeonardKambavi
@LeonardKambavi 8 сағат бұрын
Auzeni bwana DC tilipa mbuyo panu
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 11 сағат бұрын
Odana ndi Bon kalindo ndi mfiti, amalangiza a Chakwera koma wina mkumati Kalindo ndi wa MA drug's, R u serious???
@AggieKwekwesa
@AggieKwekwesa 5 сағат бұрын
Nepotism too much😢
@HenneryChimtengo
@HenneryChimtengo 11 сағат бұрын
Anyamata aboma ndilomweli pano adayamba kuyenda beya
@Frankkabotolo
@Frankkabotolo 12 сағат бұрын
😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@PhillipChisanu-k3r
@PhillipChisanu-k3r 12 сағат бұрын
💪💪👊👊👌👌
@AlinafeZondani
@AlinafeZondani 8 сағат бұрын
Worse government mcp
@Khoofficial1
@Khoofficial1 8 сағат бұрын
Chochi this
@JorMan-x8e
@JorMan-x8e 8 сағат бұрын
The DC
@PempheroMoleni
@PempheroMoleni Сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂
@IndopieeeMusic
@IndopieeeMusic 11 сағат бұрын
😂😂😂😂
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman 8 сағат бұрын
Inu mpakana ma sherifu
@TadalaManyamba
@TadalaManyamba 12 сағат бұрын
The DC ndi mwanadi ooopya kwambiri
It works #beatbox #tiktok
00:34
BeatboxJCOP
Рет қаралды 41 МЛН
She made herself an ear of corn from his marmalade candies🌽🌽🌽
00:38
Valja & Maxim Family
Рет қаралды 18 МЛН
Visetuonuo & Kapu Wedding Candid Moments With Royal Rider Friends
37:17
MOVIE 'YONG' PRODUCED BY ABC YOUTH MINISTRY TO BE RELEASED TODAY
31:32
Chakwera akufunika ku mental hospital akamuyeze ubongo
14:21
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 51 М.