Powerful member of Parliament of my constituency... Yes we voted for you to represent us in Parliament..... Bravo Suleiman
@babranzima81203 сағат бұрын
Ukuziwa kuti Mr Suleman ndiakatundu ndi chimwendo naopha big up Mr Suleman
@Yungjoe7863 минут бұрын
❤❤❤❤ we salute you Samier,our country needs peoples like you.Keep it up
@Sofi-p1v18 минут бұрын
Bravo Suleman Osamasekerera zopusa
@InnocentDalikiya-tz8go3 сағат бұрын
Ur one and only who stands by justice to ur fellow Malawians
@CheBarhassanVmad41 минут бұрын
This is fearless Our Own CiC Nalema
@ChicoBanda-kq7py5 минут бұрын
Number one mr sulemani
@InnocentDalikiya-tz8go3 сағат бұрын
Dnt worry we're out here to support u mr Suleiman. U got right also
@Nyson197955 минут бұрын
Big up Mr Suleman
@eliffagondewe8214Сағат бұрын
Koma nde mwatasa amcp a chimwendo kuyankhula motumbwa akuti tamanchangamukani inu aopostion mmmm mwafika.. Koma tsiku likwana..
@PatiHasan-u1lСағат бұрын
More fire suleman😅😅😅
@YoungMwacho2 сағат бұрын
Thank you Sulemani, mbuzi yikupita kukaona ma assets ake ku Arab Emirates kkkkkk osati kukagula mafuta ayi. Ntchito ya president siyogula mafuta ayi, umbuli ndi kuba basi, Chakwela koma wayalukatu. Kazombo azitenga personal parliament.
@BlessingsChimangeni-o8g3 сағат бұрын
Number one malawi we need people like that
@MiddayDelezaСағат бұрын
Long live Mr Suleman ❤❤❤❤❤ we love our
@MonijaKataika2 сағат бұрын
Man of the year Suleman.. .kukondera kukumaoneka a speaker mphavu zanu zili apo but give the right to any member as required.was watching live not even sorry was said.
@sylvesteralfred83553 сағат бұрын
Ukanyamura mbendera ya chilungamo amakuda anthu same like what happened to this truthful man big up Sameer 👊
@MathewsMynus-v9uСағат бұрын
God protect you brother Suleman
@jacklinenkhata37 минут бұрын
Big up uncle
@LaddinShaibu13 минут бұрын
Bravo mp
@JamilaJafaliСағат бұрын
Ndipo brother Samuel Allah azikuteteza
@mgarachimsybwoy38 минут бұрын
One day it's one day anthu akuoneka opusa, amantha koma time will come ndithu kuchema🤣🤣🤣🙌🏼
@UmaliMmussa2 сағат бұрын
Amakuopan big up inuyo simarora mbwerera
@YasmeenYalabi-b2cСағат бұрын
Man of the year mr Sameer suleiman
@JacobMsukwa-q6v2 сағат бұрын
❤❤ iweo umatha aseh,,,call a Spade spade.we should not fear you that's cuz yu are protected by police officers nah,,, everyone gat that right to speak what he feels❤❤
@YasenYasen-q9g2 сағат бұрын
❤❤❤❤ machine
@PaulManyamba2 сағат бұрын
Suleman osafoka amalawi ali kumbali yako brother
@JACKSONHULUWA-j2n3 сағат бұрын
Well done Suleman, ngati anakupanga point it was ur time no need to say time is up, first deputy speaker sakuziwa ntchito yake chifukwa ngati amaziwa kuti nthawi palibe samayenera atchule dzina la Suleman ai. Iwenso chimwendo ngati unali ndi say umayenera umuuze Suleman osati kumaloza chala side ya dpp ai
@ThomuChiwanga2 сағат бұрын
Mr kazombo MCP anthu sakuyifuna zifukwa zina ndi zimene mukumapangazi chonde chonde kodi ndye ndukuramura kwanji uku guys mukuzimva kwambiri Malawi maso ali kwayinu onse eeeesh
@MateusJacob-h6t2 сағат бұрын
Mmmmm mani ulemu ndizofunika pagulu mpake anthu adakuthamangitsani mu 2019
@Amina-gg5gr2 сағат бұрын
We support you suleiman
@samsonmtumbati485510 минут бұрын
The power is given by Malawian so every member of parliament has rights to speak standing by malawian don't use the power the wrong way and this is unfair
@mcsellahntv6896Сағат бұрын
True Son of the Soil.
@austinmussa69572 сағат бұрын
Long live the son of the soil Malawi
@GiftChalunda-ss9quСағат бұрын
This is Malawian parliament its not for chipani chang'ona
Inu ku parliament ko mukhakitse lamulo loti president ndi minister akapezaka ndimilandu yakuba ndalama za misonkho ya amalawi azimangadwa , chifukwa anthu andalenu anthufe timati ndinu amodzi kamba kazomwe mumachita potetezana,nde tikufuna kusintha ife .
Suleiman muli tsogolo mwa inu simulingati ma mp ena atulo ongomvomela zili.zonse timakunyadilani
@WandaMinjale2 сағат бұрын
Uku ndiye kukhomererana Mcp I kubweretsa ulamuliro wa chipani chimodzi and chair of the house was not suppose to take decisions from the leader of the house
Kodi azipembezo mukuziwona zikuchitikazi mwangoti ziiiii koma mumatumikila anthu bwanji osalemba makalata ozuzula bomali ndi kupanga sipichimenti anthuwa sazasiya nkhaza
@TamUs-u2h2 сағат бұрын
5 days out go go go to Page house and rest in peace
@JosephFulayi3 сағат бұрын
Live Sameer suleman
@AdamJames-x7x3 минут бұрын
iwe kazombo ndiwe chitsiru , nde umati akanapitiliza ukanamupasa 30 ? iwe ndi ndani Kuti ukamupase Suleman 30 , nawenso chimwendo mutu Ngati water meron galu
@BenitoCazota-q6uСағат бұрын
Kodi amalawi mumakakamila chizungu bwanji chonsecho muli ndi chilankhulo chanu?Tawonani SA,ZA,Tz, ngakhalenso Zimbabwe akulankhula mu chilankhulo chawo akakhala ku parliament koma inu kakaka kukamila chilankhulo cha eniake😂😂😂😂
@IsraelMajamanda2 сағат бұрын
Ndiwe chitsilu kwa basi parliament siya mcp panyapanu agalu inu
@thulanimpphiri68733 сағат бұрын
Chair yo ali ndi mphamvu zopusa sakuvera za anthu
@TamUs-u2h2 сағат бұрын
Rest in peace Suleiman
@LuciusScott-h7b44 минут бұрын
Katundu uyu alibe zibwana
@DominiqueChitimbe3 сағат бұрын
amenewo ndi akamunamuna
@WysonChilonga3 сағат бұрын
taona ma speaker ife, osati izi ai😢
@EdsonKamwendoСағат бұрын
Anthuwa ndi afiti ndichifukwa amadana ndi Chilima chakwera ndi woipa
@AlickMDayi54 минут бұрын
Chakwera apite ku ISRAEL akatengeko PATROL Sinanga amavotera nkhondo ku UN President osadziwa kalikonse uyu