Kabambe wawina basi!!! Zilibe kanthu kuti enawo amazimva unkhalakale...but DK has all the potentials to govern the UTM❤❤❤❤
@AdenaGuest-g4b7 күн бұрын
😊
@HenryManda-c4i7 күн бұрын
Kabambe and the late SKC same watsup group....the leaders we want to have in Malawi... Kabambe deserved it🎉🎉🎉
@NicolasKamunga-rv9vr6 күн бұрын
That's true my boss
@JameGona7 күн бұрын
angovomereza bas.... koma kabambe alankhurepo mwachangu pa zomwe akupanga usi kuveka anthu nsaru za chipani cha utm ku misokhano yaboma ngat otsatira ake
@KennedyNjiwa-k5r6 күн бұрын
Captain B square and their staff all the best excellent job keep it up and thanks for your Manager to arrange this program all mighty God be with you and save you all no fear for any body or further but saying the truth
@petrokagona17087 күн бұрын
Delegates are not voting for money. They are voting for a change. The contesters should learn this. Am not a UTM member but the results are felt to be true reflection of what's on the ground.
@AjidahZmachemba7 күн бұрын
Mpira ndi pa ground ma delegate amapanga zomwe afuna nthawi imeneyo. This is what we called Politics 😅
@FrankKambwani7 күн бұрын
Ndimafuna ndimvetsere dza a Usi ndiye mwakayisiyanso ku silent 😢😢
@EmanuelMuotcha7 күн бұрын
Deligeti ndiwa chabe kwambiri a chakwela a chimwendo banda opani Deligeti wa ku Malawi 2025 akuyesa mwala uyuyu
@ChristopherChembezi6 күн бұрын
Kabambe anawina mosabera even 1 vote chomwe chavuta amutumbuka zikuonesa kuti anthu ena kumbali ndiomwe akuwanamiza chabe let kabambe proceed his job. Ngati ineyo ndine waku mupoto koma according to the manifest kabambe has better manifest than others that's why we voted for kabambe
@mtawalihastings64607 күн бұрын
Nanga mukudulaso zikafika pa Usi bwanji. Nanuso a Times mukudya nawo banz
@GodfreyWhayo-hh1dm7 күн бұрын
Pologramu ibwerezedwenso iyi, kumapetoko achita hack voice anyamata a Manganya a technology .
@Martha14367 күн бұрын
Akuti N(M)PK 23, 21, 20😊
7 күн бұрын
The pigeons have gone back to roost - UTM back to perch under DPP......Kabambe is the son of DPP! The NPK syndrome is not a good thing for UTM. Soon we are going to hear three have mobbed up to establish a new UTM probably a Malawi Transformation Movement (MTM) Kkkkkkkk! A joke kkkk
@lungisanishezi10237 күн бұрын
Kabambe oyee❤❤
@BrieMajoni7 күн бұрын
Kabambe alibe matukutuku ngat enawo a, m happy kuwina kwawo🎉🎉
@FrankFrancis-ch3xv7 күн бұрын
Watching from SA Durban KZN ❤❤❤
@vincentchatsala-i5s7 күн бұрын
Chipani chilamulila dziko izi enawa atotooetsa Ife U T M Moto kuti buuuu
@Lydia-t4b7 күн бұрын
That is ngati tose tili oganiza bhoo
@ElizabethMulinde7 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥👆👆👆👆👆🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥@@Lydia-t4b
@leveltrapper43227 күн бұрын
First interview ya kabambe ndi mene inandipangtsa kumukonda kabambe
@MatthewsIsaac-sp1ft7 күн бұрын
Anthu aja sadali a UTM ija idali link ya DPP
@TiwongeWaonanji5 күн бұрын
Unexpected is continued until next year let us wait and see mlungu simunthu
@MackdeusieKambwazira5 күн бұрын
Ena zinawavuta cihifukwa chakudzikweza werengani 1 Petro 5 : 6 pali zodabwitsa apa?
@BlessingsChilongo-o8o7 күн бұрын
Program iyi yikubebatu
@MuhammadSamson-yz1kl7 күн бұрын
Koma anyamata amwano awa mpakana zafika pa NPK 😂😂😂😂
@McFranklinBanda6 күн бұрын
Come again pa nkhani ya a Usi
@AnorldKamponda7 күн бұрын
😮Wonder anthu azakuswa... Wati ma figure aja anawapatsa ndi DK yooo???
@RuthMaluwa-v6s7 күн бұрын
😂😂😂
@Fatima-d9n3y7 күн бұрын
Kwa amene mwaluza osafooka osatopa go ahead
@McFranklinBanda6 күн бұрын
I have not heard anything about what you discussed on the former president of UTM.... it's silent...... I treat the information you wanted us to know as incomplete.
@TamaraSamidu6 күн бұрын
Nde Delegate yoo 😂😂😂😂😂
@TamaraSamidu6 күн бұрын
Akuti NPK 21, 23, 20😅😅😅😅
@CuspateMw7 күн бұрын
Uzizikonza izi bhobho usanapange post kmabe ukuesesa thanx
@petrokagona17087 күн бұрын
Wanda Msiska is right.
@TamaraSamidu6 күн бұрын
DK walowa bas, timakana anthu odzitukumula 😅😅
@TamaraSamidu6 күн бұрын
Olo pano mfumu ya Malawi first man tumudziwa 😂😂😂😂😂
@DoreenPhiri-b4f7 күн бұрын
Amakwanila ma biggy wa
@YOMALO.7 күн бұрын
Muli Bo ma Member!
@innocentkhumbanyiwa47807 күн бұрын
Wakuba ndi ndani??
@ToothyWebb7 күн бұрын
😂😂😂😂😂 ndevu za mwayi ati akajiye😂😂😂😂
@Lydia-t4b7 күн бұрын
Brian Banda walakwitsa kumutchula delegate dzina
@emmanuelkamwagha93647 күн бұрын
Ndiye even pa ma elections azkhale ma delegates azatsakhe president
@LeoMatiya-mn3bq7 күн бұрын
Wonder chipongwe too much😄
@McFranklinBanda6 күн бұрын
Kodi za a Usi mkuti bwanji/chani.... mwadulako kwina uku
@DavidPhiri-o6w7 күн бұрын
Malawiian home made fertilizer MPK 😂😂😂😂 mutumbuka Patricia kambala best label Malawiian fertilizer..😂😂😂😂
Before you post this videos you have to double check first because he stopped stop and stop so before you post on KZbin please make edit first and posted we love you
madam kaliati ndikukupephani muzina la yesu kristo gwilani tnchito ndi akabambe please, manganyai a. k .a ( majoti ) musamvele ngakhale mwaluza amai gwilani nao ntchito ngakhale kabambeyo akuziwa zainu please amai kaliati osanyengedwa ndi akapasule ai
@ResterKabudura7 күн бұрын
Koma zakhara bwanji kt Mai kaliati alephere sikumvetsa
@BillyKalambo-jx3vf7 күн бұрын
Zoona Hot current owina amakhala modzi nanga amati awine onse
@emmanuelmtambo30407 күн бұрын
Why did you mute za Usi?? 😂
@PaulLongwe6 күн бұрын
Kaliati wabalalika 20mita yalowa pa zenje
@bensonliffa27977 күн бұрын
Timaziwa kuti nonse ndi a UTM inu
@memorychirambo48697 күн бұрын
Powerful
@BlessingsSeleman7 күн бұрын
Pamudzi akuluakulu akakuona utsiku kuphwambana amatha kukugwilisa ntchito kukala fisi ausi ndi fisi wa mcp
@chimzynyops20317 күн бұрын
Yakhurani mwaulemu ndimoyanjanitsa. Akaliati akhale mbuzi lero? kupanda iwowo Akabambe anakachipeza chipani chili ndi mphamvu?
@DAVIEMAILOSI7 күн бұрын
Example chabe
@EstherMuwalo7 күн бұрын
Nanga za vice president sadapikisane nao?
@fatsanichibwana94387 күн бұрын
Kkk DNA ya nsima
@RABSONSIKELO7 күн бұрын
Ubwino wake ndi a family imodz
@kingtiles-g6q7 күн бұрын
koma guys mukumuyamabatu nokhatu kkkkk okonda nsima koma mumacheza bwino
@DeborahHetekere7 күн бұрын
Ndalama idyani koma musamuvotere
@RuthMaluwa-v6s7 күн бұрын
Deligate simunthu wamba 😂😂😂😂
@SaukaniMbiliyawanda-ur7zb7 күн бұрын
Koma apapa kunena chilungamo ayendedwa pasi ndi mwana wa cadet uyu anazolowera kuba
@sakalameck7 күн бұрын
Why did you mute on the Manganya section?
@StevenKabazale7 күн бұрын
Eti eti.... aaaaaa???? Mxiiii
@DavidPhiri-o6w7 күн бұрын
MPK fertilizer of UTM
@ElsaMalunga7 күн бұрын
Mwaluza basi kd paribe china chochita kumunda eeetu basi nthawi ina ivomerezeni basi Zi vain bey bey
@AndersonChimwala-hz4so7 күн бұрын
Koma deligate mmmm
@BristonDzinkambani-tx6ci7 күн бұрын
Koma mpaka NPK 😂😂😂😂 koma anthu inu
@MisheckKamwendo-w9n7 күн бұрын
Koma Brian
@innocentmatemba90347 күн бұрын
kkkkkkkk deligate ndi bwana
@lindadzaoneni7 күн бұрын
Koma azibambo inu mwano😅 akuti adawapatsa ndi a Kabambe manambala aja