ZOMWE WAYANKHURA DAN LU ANTHU ADABWA NAZO PAMENE AMAMULANDIRA LERO KU NSONKHANO WA CHIPANI CHA MCP

  Рет қаралды 7,413

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 189
@MarryUnyolo
@MarryUnyolo 10 сағат бұрын
APM my vote izi mzochititsa manyazi kukakamiza zinthu
@MarthaBango
@MarthaBango 10 сағат бұрын
Akuchita kuoneka kut akuchita manyazi😂😂😂
@aggogokina8992
@aggogokina8992 10 сағат бұрын
Zamanyazi kwambiri
@MjombaMoosa
@MjombaMoosa 10 сағат бұрын
Lozani nzanu nyimbo ya bhooo Peter oyeeeee 2025 bomaaaaaa
@mariamwandwanga3035
@mariamwandwanga3035 10 сағат бұрын
Manyazi adan .kusowa zochita .za ziiii .adad my vote
@austenbushiri-cx1kh
@austenbushiri-cx1kh 9 сағат бұрын
Apm ❤🎉❤🎉 my vote
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 10 сағат бұрын
Once upon a time, there was Chilima and Mia, komabe zabwino zonse Dan Luu ife tidakali pambuyo pa APM.
@cynthiakamwana6809
@cynthiakamwana6809 10 сағат бұрын
Zuchita kuoneka kuti,nyimboyo yodyera pasi pamtima ukudziwa kuti zonse nzabodza munyimboyi. Lozani zunu wooyeeeee. APM my vote❤
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 9 сағат бұрын
Ambiri akhamukila ku congeresi chifukwa nkhalamba ija ikukakamila pa mpando
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 8 сағат бұрын
Dpp my vote muona 2025 inuyo
@giftmakuluni
@giftmakuluni 8 сағат бұрын
Dpp my votes❤❤🥰😍
@MlaziJames
@MlaziJames 9 сағат бұрын
No vote zisiluinu a mcp
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 10 сағат бұрын
Chakwela my vote
@CheManganda
@CheManganda 9 сағат бұрын
Mbuzi yamunthu
@BarnetMwanyula
@BarnetMwanyula 8 сағат бұрын
My vote dpp 💯/
@ShalomMtonda
@ShalomMtonda 8 сағат бұрын
Apm my vote 2025❤❤❤❤❤
@PeterMsukwa-i1n
@PeterMsukwa-i1n 8 сағат бұрын
APM my vote❤️
@kingsleydaud9094
@kingsleydaud9094 9 сағат бұрын
Mzimu wa Chilima ukukwapulani ,,mukuwonekaso mwamanyazi zisiru za anthu
@heavisonjames1203
@heavisonjames1203 8 сағат бұрын
Komabe lozani zanu ija ndi number 1. 😂😂😂😂😂 Sine WA Dpp koma Utm
@MuhammadSamson-yz1kl
@MuhammadSamson-yz1kl 9 сағат бұрын
Aaaa Danlu manyi okhaokha ine Munthu uyu kt wa chiyao ndimakaikira kuchiyao kulibe chitsiru ngati ichi
@mikesandali8425
@mikesandali8425 7 сағат бұрын
Iwe ndi mbuzi sure
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 10 сағат бұрын
Dan Lu idyani ndalama yamisokho ya malawi 🇲🇼 yo ife dpp woyeee
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 9 сағат бұрын
Koma ngati nkusaka chakwaza,anthu azungulira mitu...Shaa! Akuti n'chiyani!??? Popeza ndi ndale...Zikazavutanso,tizabweleranso.....🤔🤔🤔
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 10 сағат бұрын
APM my vote
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga 10 сағат бұрын
Mesa mumati mwasita kiyimba, munali kwa atelala kosokeke kasuli ka chikangawa ka etiiii !!!! Boni kalondo sananame Ku ti tiwona zithuuuu 😂😂😂😂😂😂😂
@johnjoachim3820
@johnjoachim3820 8 сағат бұрын
Dan Lu nyimbo zako ndikuchitsa mu 🖥 yanga ndimaona ngat ndi iwe solo koma mmmm paja pamuthu
@YasinSabili-dj9xe
@YasinSabili-dj9xe 10 сағат бұрын
Apm my vote
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 8 сағат бұрын
Ndimakumbukila chaka China ndinalandila msalu zachipani chilichomse Ndidzovalatu idzo sikuti akulandilawo kuti ndimavoti anu.mukunama atidye nawo amenewo Voti ili muntima mwawo
@ElizaSoko
@ElizaSoko 10 сағат бұрын
Akuloza iwe Dan lu 😤😤😤😤😤😤😤😤😤😤😤
@WisdomMwale-j9h
@WisdomMwale-j9h 9 сағат бұрын
Eeeh, Anthu awa ndi Amodzi Asiyeni!
@jamiajafali6619
@jamiajafali6619 9 сағат бұрын
Chimwendo Allah akakulange iweyo
@MpanjeHardware
@MpanjeHardware 10 сағат бұрын
Apm may vote
@JOSEPHTAPSON
@JOSEPHTAPSON 10 сағат бұрын
Kkkkkkkkk ife ndi mcp basi chete chete
@mikesandali8425
@mikesandali8425 7 сағат бұрын
Boma ndilomweli
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 10 сағат бұрын
Anthu akuoneka kuti sakukondwa 😂😂😂😂😂
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 8 сағат бұрын
Ndipo kwambiri
@WiliWili-y2d
@WiliWili-y2d 8 сағат бұрын
anthu akuopa chikangawa 😂😂😂😂
@mariamwandwanga3035
@mariamwandwanga3035 10 сағат бұрын
Akupha ndi inuyo a mcp😅
@NosiphoMazibuko-e9z
@NosiphoMazibuko-e9z 8 сағат бұрын
Inu Dan lufani pangani kapeni nick chakwera mwana president chakwera akudya ndalama uko minister ndimwana wake nick chakwera chipani cha family ichi kd nick chakwera bwanji zamabwela kuzapanga kapeni iyeyu basi asigwira ntchito mu office inu muzivutika udindo ndimwana wake wachakwera ine chipani cha mcp ndidatuluka kuyambira pomwe adakhala mwana wake nduna yoyang'anila ku immigration ndidanziwa kuti chipa cha family komatu mwanawake zabwera kukapanga kapeni ya mcp km udindo amapatsa ife mamembera amcp ndikupanga kape yopangila nick chakwera kuti zapatse udindo kachikena amamayi kuvutika kwamalawi ozasindikira kodi tikufuna atuluke mwana wa president achakwera nick chakwera yemwe Ali nduna yoyang'anila ku immigration atandize abambo ake kapeni chifukwa chipani cha mcp ndicha family mawudindo akupanzana pachi family chipani choyipa icho mpaka mwana wa president kukhala nduna km amalawi kumangoyang'anila zotero
@SqueyaHosmane
@SqueyaHosmane 8 сағат бұрын
History is best teacher
@FungulanReuben
@FungulanReuben 9 сағат бұрын
APM my vote 😊
@bissankal774
@bissankal774 8 сағат бұрын
Wachiyao mukutamikatu ku mcp mpaka munthu wankulu 😂😂😂😅
@BlazioKamagwira
@BlazioKamagwira 9 сағат бұрын
kuseliku akuti safuna ndalama koma kufuna kudzasintha zinthu koma ndaseka kkkkkkkkk
@GeorgeChirwa-i8v
@GeorgeChirwa-i8v 8 сағат бұрын
Adyeleni ndalamazo koma nyimbo zanu zizingabebe ngat zomwe mumaimba mmbuyomo
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 7 сағат бұрын
DPP my vote 2025❤❤❤❤
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 10 сағат бұрын
Mbuzi zekhazeka zili apo chakwera ni kawawa MCP nchipani cha ng'ona
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 8 сағат бұрын
Dan lu ndi wa ku balaka mangochi kmaso wa mcp uja ndi mwana wa kuzi osati kuti mcp izimenye pa mtima ai kwa m'baluku mcp kulibeko sumungqwineso anawina iye uja chifukwa choti ndi.mwana wa bwno muzimo tiyeni muimiseso wina muone pa central mangochi ngat mungazaphulepo kanthu muzawaziwe anyamata apa boma kuti amangomudyela munthu ndi kumusiya iwe chimwendo
@FunnyKatchenga
@FunnyKatchenga 8 сағат бұрын
Zosakoma anta, angotengana okhaokha kumalandilitsa nsalu,ati cholinga anthu aziti anthu akulowa Ku ng'ona party 😅😅😅😅 shame on you.
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 8 сағат бұрын
Nkhondo ya pansi pansi ine Chilima kulibe mwayaluka inu Adani sory 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@LawrenceDickens-jk3zx
@LawrenceDickens-jk3zx 8 сағат бұрын
Kamanjekete yomweyo😂😂😂 DPP my vote
@Samson-ve5rs
@Samson-ve5rs 9 сағат бұрын
Apm my vote awa alephera nduna zopanda nzeru
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 8 сағат бұрын
Mwaiwala muja tinagwetsa ndede ku chikangawa chitsekoso atseka 😢
@NosiphoMazibuko-e9z
@NosiphoMazibuko-e9z 8 сағат бұрын
Km amwene mcp yata basi inu zowoona okupangilani kapeni akhale Dan lufani km mcp nde basi yata vuto mcp palibe yemwe angakope anthu chifukwa chake akugula woyimba kusowa kwachipani inu amcp okupangilani kapeni yokopha anthu kuchipani Dan lufani
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 8 сағат бұрын
Inuyo Pagani zaddwanuzo dzuwa salozelana aliyese amalionakaye musiyeni dan lu
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 9 сағат бұрын
MCP si political party koma music industry.
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 9 сағат бұрын
Copy and paste 😂😂😂😂 learn to write your own comments
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc 10 сағат бұрын
Olo takhala osaona singachite kuvotera MCP bola ndiwalondore agogo anga kumanda
@ElizaSoko
@ElizaSoko 10 сағат бұрын
😂😂😂😂😂 APM my vote❤❤❤❤❤❤❤❤
@NolityKondowe
@NolityKondowe 8 сағат бұрын
Mcp my vote.Boma ndilomweli.
@OusieSaeed
@OusieSaeed 8 сағат бұрын
Kumenya kugwetsa kwacha kulenphera kuidzutsa koma kudziwa kugwetsa ndege
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 10 сағат бұрын
May the best man win,next year
@JohnWalekana-z2f
@JohnWalekana-z2f 9 сағат бұрын
Manyaka dpp my vote
@NiccoGama
@NiccoGama 8 сағат бұрын
Kodi Dan lu sanarowetu DPP anali oyimba amalandila ndalama
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c 9 сағат бұрын
DPP my vote
@OnenessLestas
@OnenessLestas 9 сағат бұрын
Chakwera my vote✓
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 11 сағат бұрын
Akufuna kudya nawo ndalama zaphweka Ku mcp zoo awo dyeraaaaaaaaaaaaa
@ElizaSoko
@ElizaSoko 10 сағат бұрын
Mulungu nde wasiya kuonatu kuti chikangawa awinesotu😤😤😤😤😤😤😤 azatikweze ndegetu tonse amalawi tikathele mnchikangawa ndipomwe azawine ameneyotu😤😤😤😤😤😤😤😤😤😤
@veronicagullo9373
@veronicagullo9373 9 сағат бұрын
Mcp my vote
@WiliWili-y2d
@WiliWili-y2d 8 сағат бұрын
iwe Dan lu kwao ndikumozambiqe kumangochi kulibe Dan lu
@AdamPetro-v2q
@AdamPetro-v2q 8 сағат бұрын
Mmene mumkapha Chilima muja ,chitseko chanu chidatseguka???
@yamikanuledi1238
@yamikanuledi1238 9 сағат бұрын
A Dan Lu inu nde machende anu mwana opusa takusika basi
@PhillspicJere
@PhillspicJere 9 сағат бұрын
Kodi KZbin sanaipange kukhala ya anyamata a DPP pitani pa ground plz kuti adad anuwo azawine otherwise MCP ilamulaso 2025
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 8 сағат бұрын
Akupha ndinu agalu munabwelera bwanji m'boma muonanso mwapha chilima inu agalu
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 8 сағат бұрын
Musamalowetse zamulungu aaaaa inuyo ndinuwabwino kodi
@aggogokina8992
@aggogokina8992 10 сағат бұрын
Umphawi ukakupana nkusapilira umapanga zozichotsa nyota ndikuyaluka ponseponse.
@user-od5xn5iw8x
@user-od5xn5iw8x 10 сағат бұрын
Mesa mumati mwasiya kuyimba achisiru DPP boma
@WisdomMwale-j9h
@WisdomMwale-j9h 9 сағат бұрын
Boma,,, Ndlomweri, kulibe kusintha!😂
@ChristopherMatemba-m4g
@ChristopherMatemba-m4g 10 сағат бұрын
Kuyamikila munthu yemwe wathenga forex yonse kumapita nayo ku American
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 8 сағат бұрын
Mmmmmm chisilu masavege onse achimwendowo dan lu palibepo chimene akupangapo iyeo sangawine dan lu ndipo inu osangonena kuti tawagula bwanji mesa mukuwapasa ndalama km tionesana 2025 muonaso inu masavege mcp
@charlessulumba2521
@charlessulumba2521 10 сағат бұрын
😂😂😂😂😂 a funny party
@crytoniegrantliffa2431
@crytoniegrantliffa2431 10 сағат бұрын
Chimwendo ndiye ayi .......ndinu okakamiza zithu ife sitikufuna chakwera
@PatsonmahoweNyirongo
@PatsonmahoweNyirongo 10 сағат бұрын
Chakwera ndiye satana, kwake nkupha, kuba ndi kuwononga, sangawine or pang'ono
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 10 сағат бұрын
Koma ineyo olo oyimba onse atatha kufa kumalawi koma dan lu sindingamunene kt ndioyimba komaso iweyo Dan lu kuti uziwe zoti ndi ofoila umati achiyawo saluza iwe apa siunaluze bolaso Sena
@ChimwemweMguntha
@ChimwemweMguntha 8 сағат бұрын
BOMA ndilomweli kulibe kusintha
@ConeriasPhiri
@ConeriasPhiri 10 сағат бұрын
Mmmm chipani chamangazi uchisilu Adan.asowa pogwira
@JhadahLeafs
@JhadahLeafs 9 сағат бұрын
Kkkkkk komandiye
@GoefreyBanda
@GoefreyBanda 9 сағат бұрын
Chala mmwamba Dpp yoye palibe angamake
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 8 сағат бұрын
Chikangawa km kugwesa ndalama azuse kwacha cnanga akugwesa ndie chitukuko chake sakumukonda kumene ndipo okupha ndi chakwera ndi iweyo galu kaye kunyasa khope iwe mapwala iwe okupha chilima mesa munapha chilima munapha sadiki Mia munapha anthu 9 pa ndege ija chamba eti
@GloriaChiwanda-l6g
@GloriaChiwanda-l6g 8 сағат бұрын
Potseka chitsekopo mwaiwalapo ku ekwendeni
@MadalitsoIbrahim
@MadalitsoIbrahim 9 сағат бұрын
Nkhondo yapansi pansi yogwesa ndege?😂😂😂😂😂
@MpanjeHardware
@MpanjeHardware 10 сағат бұрын
Dpp yokha ndimene timanena kut manja mwamba
@SammieDickson-ln2hp
@SammieDickson-ln2hp 9 сағат бұрын
Apm more fire😊
@OusieSaeed
@OusieSaeed 8 сағат бұрын
Dan wapisilila madzi a udhu mwe achisilu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 10 сағат бұрын
Usiye zimenezo osamati chakwera woyee uziti kwacha
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c 8 сағат бұрын
Eheeee 😂😂nyimbo yozikakamiza olo manyazi Ulibe ?
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 8 сағат бұрын
Chakweza zonse .. Dan Lu manyaka
@RajabLahlie
@RajabLahlie 9 сағат бұрын
Mcp ma kape, zamanyazi no future,
@henryvesha4183
@henryvesha4183 9 сағат бұрын
Nanga za chilima utiuza zotani sunenako
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 8 сағат бұрын
Ku show ya Mcp kkkk
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron 8 сағат бұрын
Shame on you Dan mwana wa Lufani
@EnerstManess
@EnerstManess 9 сағат бұрын
Wayiwalatu mene amaphedwa chilima
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 9 сағат бұрын
Vote ❤
@BandachisangaDoreen
@BandachisangaDoreen 9 сағат бұрын
Dan laughed motu yomweyo boma ndi lomweri moto kuti buuuu
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 8 сағат бұрын
Zianthu zosaganiza bwino
@Mahlodi_derickMaroala
@Mahlodi_derickMaroala 8 сағат бұрын
Amufuna ku zomba uyu wathawa ndi ntcheni
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 10 сағат бұрын
😂😂😂😂😂sizikukoma
@PatsonmahoweNyirongo
@PatsonmahoweNyirongo 10 сағат бұрын
APM kumenya kugwetsa
Magic or …? 😱 reveal video on profile 🫢
00:14
Andrey Grechka
Рет қаралды 90 МЛН
Will A Guitar Boat Hold My Weight?
00:20
MrBeast
Рет қаралды 206 МЛН
Как мы играем в игры 😂
00:20
МЯТНАЯ ФАНТА
Рет қаралды 2,3 МЛН
Magic or …? 😱 reveal video on profile 🫢
00:14
Andrey Grechka
Рет қаралды 90 МЛН