Bravo Sylvester Namiwa ,mawu amphanvu,God bless you
@dinchisale3 сағат бұрын
Even if you will be in there Mr. Namiwa you cannot influence the Team to stop manipulating because you will not be a Leader
@JailosIsaac3 сағат бұрын
Mr Namiwa can you please 🙏 just exclude yourself from this crew
@GRACEKUMWEMBE-rv2seСағат бұрын
Ayitu apite abweletse report ife tudikila
@thulanimpphiri6873Сағат бұрын
Amene amafunika mu inquiry. Pastor chumba .enock chihana .bon kalindo. Namiwa bakili TV tanyiwa akubanja mubusa wa ccap uja anamangidwa .mutumiki yasini gama. Mafumu ayi ose ndi adyera pamaunikaso jb abiti maness mery navisha suleman anthu amewa ndi amene amafunika mu commission of inquiry
@BrightZiongaСағат бұрын
Ndipo live
@ancientnkhata1137Сағат бұрын
Iwe khala chete
@FrankMsiska-i9j56 минут бұрын
Samasankha mbuli,,, achina ntanyiwa nde ndani ??
@thulanimpphiri687343 минут бұрын
@@FrankMsiska-i9j mbuli ndi izi zimamena kuti ndege inafika kuno ku mzuzu ndipo anayibweza mdipo inagwera kutali ndi muzi komaso inazaza kaya inazaza ndindani zimagula fertilizer kubucha zinapereka ndalama ku foundation bridge zimezi ndizo mbuli zazikulu kuno kumalawi
@FrancisNyayi29 минут бұрын
Wapatower
@AlexMofolo3 сағат бұрын
Mr namiwa mukayelekeza kukalandir ndalama kt mutseke pakamwa mizimu ya athu idxakwiya kms 🇲🇼 sadzakhulupirira no chinyengo ulendo uno tidxiwe zoona mulungu akuonat
@ShamimuBisani2 сағат бұрын
Zoona timamva pa Bakili Muluzi TV ndlam idyani kwa Mulungu kulibe chibazi guyz
@HaroldMasanga13 минут бұрын
Anyway Mr. Namiwa wishing you all the best and may God guide you.
@SajeedYunus2 сағат бұрын
I trust you namiwa God be with you in this journey
@bysongeorge32432 сағат бұрын
We are giving you benefit of the doubt, Namiwa. You are outnumbered. The rest of the team has MCP DNA.
@ManMen-kp2zeСағат бұрын
Bravo Namiwa, be strong, my home boy, fear God and He will bless you, I like ur saying " I wii expose who ever tries to bribe me,"
100%×100. Wow! Mr. Namiwa takunyadilani kwambiri. Eish! Thank you so much, keep it up.
@GiftPhiri-n8r3 минут бұрын
God bless you Mr namiwa
@DalitsoPhiri-sq5nl3 сағат бұрын
Coach is in the field of play endeed, let's support the Namiwa the great go bring the truth of Our late vice president SKC mlungu akusogoleleni
@harrymicah61402 сағат бұрын
Bora nawe namiwa ukapange zachilungamo kumeneko
@ShakiraJackson-x8w34 минут бұрын
All we need family members to be involved radios and tv have to inform us live accept MBC radio and TV we don't trust them go well mr nawiwa All the best
@JessieNgwira40 минут бұрын
Namiwa you have our trust please don't let Malawian regret
@dalitson35583 сағат бұрын
I don’t trust this Namiwa guy, but he needs to be very careful with this sensitive issue
Commission of Enquiry imeneyi ( maka maka its composition) sikundipatsa chikhulupililo olo pang'ono. Kwangodzadza ma delegate aKhongelesi basi. Don't expect any justice from these party loyalists. Namiwa, extricate yourself from this pantomime.
@christopherZulu-q5s2 сағат бұрын
You are saying the truth and please am Zambian but I have been following this issue since June 10 ,chilima was killed so please stand for the Malawian s so that the truth must come to an end otherwise it was a plan move for chakwera why he changed his mind to stand 2025
@usherjamson174Сағат бұрын
On that list, i trusted you mr namiwa please do this for us,as a Malawian 💪💪🙏🙏
@Kenmoney-xp7tz3 сағат бұрын
Nanga akumabanja bwanji mulibemo inu a namiwa banji simunawauze aikemo? Why is it almost only namiwa included? Why not opposition and media? Madya mabanz inu nyari sanafike ma band akubwera trust me
@noahgaleta419343 минут бұрын
I'm worried for you Mr Namiwa , we can't lose you again? What if they have a plan to kill you, please almighty God be with Mr Namiwa and protect him
@CatherineChidothe-x2k2 сағат бұрын
I like the speech of u brother Namiwa keep the fire burning
@ChristianMalingamoyo2 сағат бұрын
Mr namiwa we can't trust you anymore
@MartinMartin-d3g8 минут бұрын
Mr namiwa mulungu kusogoleleni koma osakaiwala mafutso awa 1 ndindani anati ndege inatdzaza 2 ndani anatenga black box 3 ndindani anamuudza president kuti ndege inafika ku mzuzu 4 ndindani analoledza ndege kuuluka yopanda zoyenelela chifukwa chani chimwendo anakane kukwela ndege ndindani
@FabianoJohn-t9o2 сағат бұрын
Anamiwa ife takukhulupilani koma mukhale wachibale was anthu ofeledwawo akhalemo
MR NAMIWA BOLA MUSAKAPEZEKE MUTATHERA KU CHIKANGAWA NDI BOXER YOKHA.MCP IMATHATU KUTOBWANYA MUNTHU WITH JUST CLICK OF A FINGER
@StephanoIssah2 сағат бұрын
Km fuso langa ndilokut sanakupase 100 million inuyo ifetu usilu ayi apo bee mademo amene mumafuna aja azakhara anu kut mutule udindo oro museke programs iyi ndakamba
@megasounds15 минут бұрын
Koma mungochenjera a Namiwa you might be their Target 😢😢
@ChristinaStambuli-q3e3 сағат бұрын
Chonde mr Namiwa dont let Malawians down ,dont accept envelope ijayo kumeneko Ifeyo we are counting on you..dont change your mind when you get there musakalowe nkuyesedwa..kuChikangawa kuja kunachtika zoophya in the history of Malawi potengera ndale
@WendyPhiri-h5t3 сағат бұрын
Sitikufuna tizamve kuti mwalandilako billion
@joegibsonzulu2599Сағат бұрын
Inenso maganizo anga ndi omwewa. Zayamba kukayikitsa kwambiri.
@JovitastoloBridane2 сағат бұрын
Fonsolanga kwa namiwa poti presidente wasankhakare anthu mbwungweri simukuonakuti posankha muthummodzi osutsa simukudziwa kuti afuna akupheni inuo kuti otsalao apereke lipoti losalongosoka inuo mutaphedwa chenjerani anamiwa kumbikilani mauangawa
@BeardKamuwombaHarawa-d6v13 минут бұрын
wait and see
@LumbaniPolowani2 сағат бұрын
Ine I which mukamayamba commitional of inquiries tizimvera nawo azakhale live koma nkulu winayo amuikayo mmm ka Ty??
@JudithMaida-ug4oi2 сағат бұрын
All the best mr Namiwa chomwe mungadziwe kut if u made a mistake kuzadzuka Namiwa wina inuyo muku Seva ndende ya chikumbumtima
@SamukLungu3 сағат бұрын
Iwe ngati warandira kare ndarama kabweze panga choti akubanja akharepo iwe upitangati ndani
@PaulBandason2 сағат бұрын
Mwalankhulatu mau otikomela ife a malawi koma musakapange zowakhumudwitsa
@Paul-q2pСағат бұрын
Malawi we don't trust anyone because timaziwa mmene chinyengo chakwathu
@HenryChapwetekaСағат бұрын
Bravo namiwa tikudalirani mapuya
@RaffickAllieСағат бұрын
Komabe yopanda president wathu kalindo... Ujayu atha kuziwitsa dziko before chakwera lisanapedze report kkkk Safuna zakuchifwenthe
@stevenmwamadi30352 сағат бұрын
Tingomupepha Allah kuti akusogorereni Mr namiwa kuti tizamve zoona zenzen
@rashidadan2533Сағат бұрын
Mwachidule , mr Sylvester namiwa walandila chi banzi kuchoka ku mcp , Why Comrade work together with government ??? Malawians are not foolish , this is stupid
@richardkachulu866942 минут бұрын
Afrika will rise again
@ChidaPhiriСағат бұрын
Komatu Chakwera ndi clever ife tikudziwa kale kuti iyiyi ndi fake salora chilungamo ai chonde chonde pezani enanso aopositon nawo akhalepo ndithu
@MAPANGAORIGINAL-w4y2 сағат бұрын
But please 🙏 mr namiwa osachedwetsa zinthuz lija ndkare