Zikufikadi mmanja mwa anthu oyenerera. God bless Dr Usi and God bless Malawi,
@PatrickcDecembers2 күн бұрын
Ngati olemera aliyese atagwilitsa ntchito k20 million kugula zipangizo za ulimi ndikuwathandiza anthu ngati mmene akuchitila a Usi njala ukhoza kutha ku Malawi. I salute his work.
@tandtrefrigeration2 күн бұрын
True
@EsnartGirivin2 күн бұрын
True zoonadi
@bridgetmajor36462 күн бұрын
Heavy
@lameckmajiga54262 күн бұрын
Athu ambili mukulakhula zipongwe koma ziwani kuti or yesu amadalisa ochepa omwe wapeza pathawiyo!! Michael usi payekha sangathe kupeleka kwa athu onse feteleza koma kwa omwe imyeee wafikila!! God bless and gives you everlasting life my Muthu Bizeck Michael usi!!
@KeithGondwe-tq4kt2 күн бұрын
Powerful point sir
@RingstoneGondweКүн бұрын
Tiyeni enafe titengeponso mbale osangounguza while we do nothing@@KeithGondwe-tq4kt
@ChirwaConstructionКүн бұрын
Papene ena akulimbirana maudindo ndipomwe ena akufikira anthu ovutika ku mudzi amalawi tikuona
@PrinceBlessings-bv5bs2 күн бұрын
Angoyenera kulira ndi chimwemwe anthuwa malingaso mkuti zinthuz zikuwapeza mu nthaw yake... Mulungu adalitse Usi chifukwa wachita mau...❤❤❤
@ChristopherMunlo2 күн бұрын
Aliyense Ali nduna ya boma akanati azipanga chonchi ,njala ikanachepa.only 4 today big up usi!
@ernesthkaunda79022 күн бұрын
Anthu phunzirani kuyamika....Bravo Micheal Usi
@freddemster6542 күн бұрын
God bless you richly Bwana Micheal Usi VP. Ena sakuonabe kuti mukupanga ntchito yabwino, ndipamene akukunyozani. Wabwino apange chiyani? Some time you tend to wonder kuti kodi anthu akufuna munthu apange chiyani kuti akhale wabwino. Mungodziwa kuti Ena ndichibadwidwe chawo samaziwa Kuthokoza. Koma ine ndikuti Mukugwila ntchito yabwino kwambiri. Zopeleka ndi zachifundo zanu zimange chikumbutso pamaso pa Yehova.
@yplackcedes45342 күн бұрын
Watching from Zambia. God bless you Mr Vice president for helping the needy. Why can't other rich people do the same?
@FrancisKatunga-u5fКүн бұрын
he's using Malawian taxes its our own money and he gonna do to how many people in this country why they can't just reduce the amount of fertilizer so that everyone should benefit
@InnocentMtafya2 күн бұрын
Umunthu Ndi umeneu nanga, munthu wabwino apange chani??? Abale. I😊 salute you Dr .Usi, our VP.May God bless you.
I'm watching from south Africa cape Town stellenbosch God bless you Mr usi
@ColetteMalungaКүн бұрын
Aliyense amene ali ndikuthekera atalhala ndi mtima othandizako atleast munthu mmodzi or awiri, dziko lathu litha kusintha. Vuto lathu anthufe chikondi tiribe, kudzikundikira mkusiira andale kupanga chirichonse. Tiyeni aliyense achitepo kanthu, ndale sitidya. Chikondi chitsogole. Viva apule Michael Usi. Dziko siliyamika koma Mulungu amaona mkudalitsa. ❤
@FionaKhoma2 күн бұрын
God bless you mr usi athu muziona zonyoza izizi ofunika kuyamikira osat kunyoza wagwira tchito mulungu akudalitsen
@MMK-p3y2 күн бұрын
This lady uyu wa mwanayu eee sakutha kumvetsa🎉
@sunflexmunthali90512 күн бұрын
Thanks Dr Michael Usi.This is commendable.If the pocket allows,do the needful and help the poor.
@masoyaonamunkhondya90742 күн бұрын
We can't change by using hoes whenever working in the garden. This takes longer hence time really is waiting
@ExtratremendouszeusКүн бұрын
What recommendable here...this is seggregative...munsewumo...azigawa village by village not this manyaka
@YusufJimmy-v1o2 күн бұрын
Usi ndioganiza bho...thats why sanapeleke 20 mita ku convention....Usi umatha kwwmbiri pitilizani ku thandiza anthu
@LinkyShabalala2 күн бұрын
Tonse titengepo mbali osamangonena ona.Tigwilane manja ndikupephelera Malawi.God bless you Mr Usi.Mupitilize zabwino zonse.
@Alinafe-o1u2 күн бұрын
Ndiposo mwachita bwino kugawa nokha bwana,,,God bless you
@MatthewsNkuna-r7o2 күн бұрын
Good example of leadership keep it upGod bless u
@LovelyDumplings-yf7pd2 күн бұрын
Kwambili achilima anali ndi maso phenya oopswa kwambili amamuziwa usi kut ndisongoleri wamasophenya ambuye akudalitsen mzimu wachilima uuse muntendere amen
@FranceZitha-h6qКүн бұрын
Ena zikuwapweteka Apa. Pakamwa sipagula ndenge/ action speaks louder than words. Salute to VP ulem wanu
@PiliraniMosesNdekha2 күн бұрын
Dziko lanthuli mutakhalako anthu ngati awa 20 zinthu zintha kusintha God bless you vp
@MuhammadJohn-s5l2 күн бұрын
Pomwepa Allah bless you more usi
@GraceyohaneGomami2 күн бұрын
Wamisala adaona nkhondo God bless u usi
@MzondiNkosi-f4w2 күн бұрын
Takumbukani abale nthawi ya farao aliyense oyang'ana panjoka yankuwo ndiamene amachila nanga enawo samafuma machiliso koma uyu amandikondwelesa kwambili next time zizagwela winawe khala tchelu viva avice president ndinthawi yanu 😂😂🎉🎉❤❤
@kenzobulukutu7512 күн бұрын
Ndikufuna zimenezo a vice-president athu well done keep it up
@Staphelsavimbindhlovu2 күн бұрын
Michelle usi waulemu ndamuona 🫡🫡 km my vote Apm
@LuciusKhudzeКүн бұрын
GOD bless you DR M. USI Moti ambiri amene alindikuthekera kochita izi chonde auzeni kuti atero. Mulungu amadalitsa Opelekayo. So GOD bless you so much.
@MoffatBinali-pp8hi2 күн бұрын
If one is taking photos with poor people after giving them unexpected gifts that is very commendable and surely this is how we are supposing to do as Malawians. Mr VP all the best and keep it up
@debolahfretcher49052 күн бұрын
Biggup Mr president,'chiiyimba chili m'mimba,salute!
@CyprianoSandalamu2 күн бұрын
Good example Dr utsi, continue to do good work to the poor and elderly.We have alot of famous people who are rich,but they can't take good example of vice president to share for what they have,but kudzikundikia chuma ngatimudzapta nazo kumanda,chitani manyazi olemelera nonse ndinu andale taonani zomwe wachita manganya
@KistyMaureenMugala2 күн бұрын
This is great job Mr Hon. VP, God bless u Amen Amen Amen Amen
@SteveZimba-e8s2 күн бұрын
Thanks mr Vc president Michael usi Mulungu azikudalitsani osasiyila pomwepa kuli ambiri akuvutika ena amene mulindi chuma pitilizani kuthandiza anthu ovutika kuti apeze thandizo❤
@PatrickKapendo2 күн бұрын
Usi mukubwela bhoo this is the malawi we need osamati ndiizapanga ndikazakhala ine papando ai usi akupucha president chakwera
@ShinglaiAli-be3yn2 күн бұрын
This is wonderful...zinazo pambuyo koma mr usi you have done a wonderful job may God bless you 🙏
@HarlodLPatheretuКүн бұрын
God bless you Mr Vp, Malawi tikusowa anthu ngat inuo. Longlife Mr Vp.
@BLUR-p6c2 күн бұрын
Ndipo wakipanga bwino kobasi Michael usi congratulations
@LawrencePhiri-h3j2 күн бұрын
This is great . zandale kaye uko ndakufira Usi
@annievitumbikonkhoswe7706 сағат бұрын
President ophunzira odziwanso umphawi Thumb up Dr Manganya
@AngellinaMphamba2 күн бұрын
Wawooo what a great job, Mr vp may the Lord bless you abundantly, this what our Lord Jesus Christ command us to do.
@SerahPhiri-l4i2 күн бұрын
Thanks boss osayamikaosayamika mwapamga mphavu
@kaphika2 күн бұрын
May God bless you our VP Malawi is blessed with your work.
@BlessingsTchapo2 күн бұрын
Kulasa mtengo mchamuna chomwe,,,a big up to VP enanu musangotumiza anyamata azikwanje ayi,,,tumizani mbeu ndi fertilizer kuja akudya chitedze kuja
@ChimwemweZuze19 сағат бұрын
Wowooooo I'm very happy very very happy ,mayi awa eish athokoza ndi mtima wawo onse wowoooooo
@kamowafelamo26522 күн бұрын
Bwana usi. Mulungu. Akudalitseni ka million. Akupatseni. Thamzi labwino.
@WisdomMphepo2 күн бұрын
This is what we want, good development Michael Usi
@AndrewBanda-f9h2 күн бұрын
Good example ena athandizekoso nkhamba zitatu madela ena
@Giftsungani2 күн бұрын
God bless u,Dr Michael usi, this is unforgettable story.
@SolomonMatola2 күн бұрын
God bles u mr usi pokhapa ndakunyadilani mr
@Evance-t6d2 күн бұрын
Am worching from S A good job mr vp god bless u if the presdent wos doing like this malawians will happy for him
@MaxwellMangamba2 күн бұрын
Good job Dr Michael Usi. Osati awa akuti akaba ndalama kumangopakula azikazi a eni ndi tiana mma area mu. May God bless you Michael.
@FahadAssani2 күн бұрын
This is very good initiative VP. Give assistance directly to the needy. God bless you Right Honourable Dr Michael Usi.
@EmilyChiphuphu10 сағат бұрын
God bless you vp umunthu ndiumenewo kuonesa chikondi
@EliphaKamanga-jv5sh2 күн бұрын
God bless you ndiye kumupoto ku luwele mupitako lit osakondela malo ogawa fertilizer tonsefe tikufuna kulima koma fertilizer tilibe
@CHIFUNIROEMMANUEL-d3pКүн бұрын
May Almighty God continue to use you Mr vip usi as weopions to Malawians that's great and powerful 💪
@francisvisage27052 күн бұрын
Wachitapo Va zeru usi... thanks
@tamalangoma27652 күн бұрын
God bless you my VP ,ambuye akudze malire anu.
@jeanMsakambewaКүн бұрын
DR. Michael Usi our VP. You won't be poor. God is with you. To those with political eyes, let them talk. I learn a lot from your leadership style.
@wellsmchenga74482 күн бұрын
Olemekezeka a Doctor Micael Usi achita zinthu zazikulu powapatsa zipangizo zaulimi anthu akumudzi. Mabwanaenawa atengerepo chitsanzo.
@RobertKawenje-r8u2 күн бұрын
Ambuye awadalitse akupanga chinthu chamtengo wapatali keep it up
@StevenLikukuta2 күн бұрын
Ndiribe mau apa otukwana Usi landilani matemberero akutukwana kwanu. Vice president kumbali yake ngati munthu pa yekha akuthandiza. God Jehovah dalisani a Usi ndi banja lawo 🙏
@EmanyauZuma2 күн бұрын
Zabwino zonse muthu ali ndipena pokomela ❤
@captainmdima11022 күн бұрын
Well done Mr vp president god bless u abandantry
@InnocentMakungwa2 күн бұрын
God.bless u mr vice president,kunonso mufike kkkkk tikuvutika
@planbkhamisolo2734Күн бұрын
Akanakhalapo 10 otelewa bwenzi zinthu zikusintha❤❤ osangoti kuchikamwa yasa koma osathandiza anthu ena 😂😂
@GoodWill-m1m2 күн бұрын
Wowww , l salute u bwana vp keep it up , ndili pa mbuyo pako
Very impressed, achita bwino akapeleka wokha a V P. Mafumu anthuwa akanangogawana pa mtundu pawo
@WanangwaGobede14 сағат бұрын
Servant leader.osati kumangolubwa
@TamandaMagwiraКүн бұрын
Zabwino kwambiri.....God bless you
@SurprisedDriftwood-vs9diКүн бұрын
Politics aside, this is a good gesture, our spiritual aspirants would emulate after being enriched through tithings and offering. Not only the ruling politicians but all to be would take a mile beyond
@BlessingsMaloya2 күн бұрын
He is just a nice guy Michael usi to be honest, and I hope he is doing this good job frm his heart not political😍😍🐅🙏🙏
@tonnybanda836619 сағат бұрын
I'm happy to see the ordinary citizens getting farm inputs free of charge. I thank Almighty God for using leaders to help his people.
@EstherManda-ex3bc2 күн бұрын
Nice job mupitekoso mbali ya kwathu Ku nkhatabay mwina mwayi umenewu nkukati gwelako
@TinaKazembe-l7d2 күн бұрын
Aliyese amene adzinyoza avice president Michael usi , mulungu amukanthe ,
@PromiseIssa2 күн бұрын
This is great !so powerful kip it up your honour 🎉
Thank you Mr vp for that initiative,l never knew that you are going to fulfill your promise,l now know the reasons why you refused to pay the sum of mk20 000 000 at the party's convention,you are using it in the right direction by helping the neady, And an old man was asked a very simple and straight forward guestion,'do you know the person who give you these 2bags of fertilizer and seeds, Amvekere ,manganyayo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂,kkkkk.