Atleast there are guys like Wonder and his team who love Our Country!
@RabbecaMbukwa-y1zСағат бұрын
Wow gyz,without beating the bush u r direct in speaking.U r hitting the nail.Osaopa,osafooka komanso osatopa gyz.We r with u.
@victorbanda90392 сағат бұрын
Chunga you are professional
@UnityBasikoloСағат бұрын
I salute U gentlemen
@ShakiraJackson-x8w2 сағат бұрын
Keep it up guys i always waiting for this program amalawi ambiri aseguka mmanso chifukwa cha nu limbikirani ndithu
@BrunoChakukumaСағат бұрын
More fire Mr kamangira
@georgenewa35083 сағат бұрын
The only important radio station in Malawi Times
@HappykamwanamwanaBwaila2 сағат бұрын
Mbambandee azibambo odziwa kuyankhula...... Time's Radio number 1 pa Malawi
@Yungjoe7862 сағат бұрын
Kamangila he’s there to save us,keep it up guys let’s support this guy
@SurprisedDrumKit-ql7rj2 сағат бұрын
Kuri chawez Banda mtorankhan wamanyi😊😊😊
@MathewKalinkhu3 сағат бұрын
We have a government which we have never had in Malawi ever. Useless government.
@GiftKhwambala23 минут бұрын
Keep it up
@MathewKalinkhu3 сағат бұрын
Times Tv Malawi ndi no.1, akulu akulu pitilizani mumalankhula bwino kwambiri, ndipo mulibe mbali.
@DanielNkhata-wt9ov3 сағат бұрын
No 1 guys paliso Chavez banda amaryaso chibazi
@MichaelKaerama-dd4bkСағат бұрын
Hot current imayenda pamwamba kamangila alimomwemo ist afamily member thus why wabaya pofunikira ndi aliyense wamvesa and this is true
@CathleenMsaya3 сағат бұрын
A chunga God bless u your talking sense
@NewtonTembo-q4t3 сағат бұрын
Very good guys please keep it up
@esmybanda22273 сағат бұрын
Isalute you guys good speaking mcp zakuvutani basi vomerezani
@GeorgeTambala-j1m4 сағат бұрын
Watching from Johannesburg in south Africa we Malawians we made a very big mistake by putting these stupid people into government but I hope we have learned a lesson
@Kelvin-hj5qvСағат бұрын
Inali bh🎉
@NickUpocheСағат бұрын
Ndipo nde kwambili za equally zokhazo asamale ndipo masiku akupita pangono pangono mpaka 2025 tizafuna umboni koma wina Ali nkati
@TimeAbiluСағат бұрын
Kamangila (lets Government please give protection from him, this guy never seen and Allah gave long life Alex
@Blessings-td4cr3 сағат бұрын
Good advise but MCP imadzimva kudachulukako omwe adakhalako atsogoleri akudambwe kunyau. Athu ake amakhala okakala moyo.
The only best way to change the rottness of how Malawi is run is by voting into government a new political party that has never managed the affairs of the country .
@HamzajOsman50 минут бұрын
Dziko lovesa chisoni😂$440=K1,000,000
@HassanChibwana3 сағат бұрын
Kamangila way more fire
@AkiduMakwinja-x1h2 сағат бұрын
Look at South Africa mafuta it's already decrease last month koma Malawi ndipamene akupanga increase...what is that ma group wa Chakwera
Oky! Iyi simutchira mayina coz s allegations, about chimwendo yolesedwa kukwera ndege ija is not allegations??
@TiongeSimkonda2 сағат бұрын
Uyu watitenga a Malawi
@Blessings-td4cr3 сағат бұрын
And dziko azitsogoleri adakamakhala ndi nzeru ngati zanuzi panopa tili patali koma alliance iyiyi manyaka,,,Evance Meleka poimba nyimbo ya nthata zanjala ija mzimu udamulakhula mwapadera.
@benjaminjobo35252 сағат бұрын
Malawi is captured by the big mafias 😢😢😢
@JonesChingaya-yf4ggСағат бұрын
Ya Chizuma imandiwawa ngat Imfa ya Chilima. Boma ili limadana ndi Chilungamo.... Always bodza,....
@doreenkaliati31663 сағат бұрын
Ulemu wanu Inuyo mmmmh 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌❤️❤️❤️❤️❤️❤️
@MathewKalinkhu3 сағат бұрын
Ku Maida kuli George Kasakula, akubakila mcp komanso chakwera. Koma tiyamikile Mr. Kamangila , wakeup Malawians pls. MBC ndiyowola kwambiri.
Ya Mai Chidzuma nde imandiwawa kwambiri. We didn't support that noble lady eeeeish! Malawi wanga😭
@dysonmasiye57362 сағат бұрын
Ku NRB plus MEC kukufunikanso a Kamangira ena ukuku...akanika kuti amalawi apeze ma ID a unzika koma pano mukuti kalembera akuyamba m'mawa, what's that? Ndiye anthuwa adzavota bwanji?
Osapanga ngati za khuluku uyu chawezi.Ndiwamadyera mphoto munthuyu.
@JawardBenard2 сағат бұрын
nthawi yikakwana yimakwana basi tiyenazo musabwelere mbuyo nthawi yakwana iyi
@WillyNyirenda-l7h3 сағат бұрын
Kamangira azakhale nduna ya minister of justice and constitutional affairs muboma likubweralo. Kuti izi zizatheke pabwere boma Lina. MCP ndi DPP ndiamozi sangamangisane zitavuta motani. Aliyense alinawo ma jaji Ake ku judicially. Pakufunika boma Lina la new blood. Boma losaona nkhope ndipume tikufina kuti Kamangira azagwile ntchito yake bwinobwino.
@DavidKanyemba-n2s2 сағат бұрын
Tafwa mwafwa enough is enough Malawi shocking country Martha Chizuma my comrade Mmmm xool mate 😂
@DavidPhiri-o6w2 сағат бұрын
100% ndiye kiyankhula ... Judiciary, mizila manja nonsense
@MrMagombo4 сағат бұрын
A Jaji akulu imitsani ma Jaji akutchulidwa wa.
@WillyNyirenda-l7h2 сағат бұрын
Kupupuluma aboma. Mukuopa chaini? Asyeni a mademo, ndiufulu wap.
@GolosiMalapata3 сағат бұрын
Chimene chingachitike anthu ose amene akuvutika asakamvote ayi aka vote okaoka sibwino kumazuza osauka ayi aba bolani so bingu wamutalika anayika ikonome osati zitsiluzo ayi sakuchita bwino
@PreciousSteven-e5s3 сағат бұрын
Ma guy awa akuyesetsa kuliwongolera boma koma eesh anthuwa ndiwokanika ndithu ndipo anthu opanda chisoni ndithu
@DavidPhiri-o6w3 сағат бұрын
Kodi jonna please give him for first time
@HamzajOsman56 минут бұрын
boma la mamafia ili 😂😂
@MathewKalinkhu3 сағат бұрын
Pankhani ya a Kunkuyu, mmmmmmm , kunkuyu ndi boma akuyankha bwanji nkhani ya MEC ndi a kalembela?
Inu anyamata inu mumatilankhulila koma andale makani mmmmm
@GolosiMalapata3 сағат бұрын
Azaona polekela asiyeni
@PeterRabson-z3w3 сағат бұрын
Ma bigy inuyo mukunyapura boma n ma institution onse mosanyengelera ulemu wanu
@MaxwellMilanzi-w5k3 сағат бұрын
Kkkkkk kkkk....
@EnockBeston4 сағат бұрын
Muli bho
@RodgersMtonga3 сағат бұрын
Inu mmatiyimilira
@hamiltonsolomon37563 сағат бұрын
Azibambo inu...More Fire 🔥 ♥ 😍 ❤
@miovekanola27803 сағат бұрын
😂
@CathleenMsaya3 сағат бұрын
Corrupt judges in Malawi peter muntharika once complain about these judges blavo kamangira God bless u indeed tonse government won through corrupt judges