SILVESTER NAMIWA MPAKA LERO KUYANKHURA IZI?KODI IYEYU SAMAOPA? TAMVANI ZOKHUNZA IMFA YA CHILIMA ZIJA

  Рет қаралды 16,951

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 82
@Ada-u6g
@Ada-u6g 12 сағат бұрын
Namiwa ndiiwe munthu wakoru malamuro umaziwa chonde bungwe ya cded itimenyere nkhondo ❤
@MonijaKataika
@MonijaKataika 9 сағат бұрын
Namiwa may God protect you. U are blessing to us.
@JosephCompan
@JosephCompan 6 сағат бұрын
no one is like namiwa in this country bigg up
@HurmlysLangwan
@HurmlysLangwan 10 сағат бұрын
HRDC ndyimweyi CDED yi😅😅
@BenjaminMoyo-s6u
@BenjaminMoyo-s6u 12 сағат бұрын
❤❤
@rectormasanjala
@rectormasanjala 7 сағат бұрын
Koma skc anafa imfa yowawa Kwambiri mmmmmm Ambuye akuwona zonsesi Ndipo akunva 🙏
@isaaczuze
@isaaczuze 12 сағат бұрын
Mwama mlomwe ameneyo alibe masewela ....chakwera ndi munthu wopusa kwambili
@dalitsonambazo
@dalitsonambazo 10 сағат бұрын
Zabwino zonse Mr namiwa potimilila mulungu akutsogoleleni pachimenechi🙏💪
@JeremiahKapundu-j1p
@JeremiahKapundu-j1p 4 сағат бұрын
Namiwa God bless you
@thomasphiri7799
@thomasphiri7799 5 сағат бұрын
You are the voice of the voiceless Namiwa❤
@MchengaAssama
@MchengaAssama 12 сағат бұрын
Kkkkkk anamwaliranso kawiri
@cgdammw963
@cgdammw963 5 сағат бұрын
More fire namiwa 🔥🔥🔥
@LawrenceMalinda
@LawrenceMalinda 10 сағат бұрын
Mr Namiwa this speech is well spocken
@ISHMAELFRIDAY-ki6ry
@ISHMAELFRIDAY-ki6ry 12 сағат бұрын
Chakwela ziko lamupana ngt zip wapalisani kukweza zip pain,kusisa zip pain yokhayokha 😂😂😂
@SiboNkundi-hm1si
@SiboNkundi-hm1si 5 сағат бұрын
Kuyankhula kwa Born Kalindo
@RebeccaToyoyo
@RebeccaToyoyo 5 сағат бұрын
You are the best namiwa
@SamuelAntone-mz6nq
@SamuelAntone-mz6nq 10 сағат бұрын
Ndye kuyakhula kumeneko bwan auzeni zoon avetse tse 💪💪💪👉
@MosesYokaniah
@MosesYokaniah 13 сағат бұрын
Ipase moto
@RosinaPatel
@RosinaPatel 11 сағат бұрын
Anthu anafa aja ndi anthu ndithu..tisasiyire pamenepa atiuze choona chake.. SkC anafa imfa yowawa pamodzi ndi anthu ena aja..anthu opanda chisoni nkhaza anaoanga zonyasa
@spargomw
@spargomw 7 сағат бұрын
Kufa ngat chiweto, m'malo mofera ku chipatala mkukafera kuthengo😭😭😭😭😭
@MarriamShakira
@MarriamShakira 12 сағат бұрын
I ❤ you namiwa
@AgnesGondwe-l3b
@AgnesGondwe-l3b 8 сағат бұрын
Anamiwa osaopa komaso osatopa tili pambuyo panu
@augustinkapenuka6153
@augustinkapenuka6153 6 сағат бұрын
Namiwa more 🔥🔥🔥🔥
@EsetaGerate
@EsetaGerate 8 сағат бұрын
❤❤❤❤ Namiwa
@HenryEdwinKapindu
@HenryEdwinKapindu 4 сағат бұрын
Fire them,,,, ife zikudibowa zomwe akuchita agalu amenewa
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr 9 сағат бұрын
Kkkkkkkk mpaka apulu kupanga chipidigolilo😂😂😂😂
@MwayiKalirani
@MwayiKalirani 10 сағат бұрын
Inu ngati otiyimilira munakapilira osathawamo...
@RightwellZumbwe
@RightwellZumbwe 5 сағат бұрын
💪💪anamiwa apaneni amenewa osawataya awa mpaka anene zoona
@serakillo8668
@serakillo8668 10 сағат бұрын
Kkkk love you namiwa zoona asatitole kodi athuwo anamwalira kawiri chakwera ndi ngulu lako....dont take malawi grated pls
@PatrickMwizozo-ep3vg
@PatrickMwizozo-ep3vg 11 сағат бұрын
To train a soldier is not a joke ..wake-up Malawian
@wilsonchimtikaphiri9496
@wilsonchimtikaphiri9496 6 сағат бұрын
NamiwA ❤❤❤❤
@CharlesBanda-v8k
@CharlesBanda-v8k 5 сағат бұрын
Chilima anali mwana pandale sakanayenera kupanga nawo alliance ndi mikangoyi
@SolidrockKanyenda
@SolidrockKanyenda 10 сағат бұрын
Only rast man standing NAMIWA
@SteveZimba-e8s
@SteveZimba-e8s 7 сағат бұрын
Namiwa Mulungu azikusogolera ndikukudalitsa chifukwa umaima pa chilungamo osagulika Ngati enawa timakudalira kwambiri aliuze zoona dziko la Malawi Kuti zidakhala bwanji pangozi ya ndege tikufuna chilungamo basi.
@eliasgondwe
@eliasgondwe 6 сағат бұрын
Chizeleza Mamiwa, kapelekeni umboni kumakanaso ndalama, umadyazo zikupha!! Nanga zachisankho zikugwilizana chiani?
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 6 сағат бұрын
VIVA AAA
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns 3 сағат бұрын
Following Namiwa , yes for those who are satisfied with that nosense report then just be quite ,,,,,,we want to hear and know the truth about the death of SKC & 8 others
@KelvinBandah-o5v
@KelvinBandah-o5v 5 сағат бұрын
Rip saulos chilima tiva zambiri
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 7 сағат бұрын
Kuchikamwa ngati wadya manyi iwe Namiwa wa DPP
@SiboNkundi-hm1si
@SiboNkundi-hm1si 5 сағат бұрын
Mwapusa bwanji? Apa akukamba za DPP or akuyankhula za amalawi? Ngakhale ukuyankhula kupusa choncho chonsecho ukuvutikila limodzi ndi ukuwachemelelawo akusangalala okha
@HurmlysLangwan
@HurmlysLangwan 10 сағат бұрын
Katundu
@HappyAutumnTrees-cd9ye
@HappyAutumnTrees-cd9ye 6 сағат бұрын
Mwaphera dala nabiyen dzikoli mutsale nayo😭😭😭😭
@user-jmuller
@user-jmuller 5 сағат бұрын
Dolo ka 500🤞🤞🤞
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 7 сағат бұрын
True Malawian
@BarakiChriss
@BarakiChriss 4 сағат бұрын
Za chikape wa DPP ndiwe munthu akuyimilira amalawi Ife iwe ndiwakut ulibe umunthu
@GodfreChayamba
@GodfreChayamba 3 сағат бұрын
Bwana namiwa mukukwanila pitilizani tili PA mbuyo panu
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 5 сағат бұрын
Koma Namiwa mulungu azikudalitsani pa ntchito yabwino imene mukugwira
@BenjaminMoyo-s6u
@BenjaminMoyo-s6u 11 сағат бұрын
Akutitola kwambiri abomawa
@JordanSuliwa
@JordanSuliwa 9 сағат бұрын
Mulungu asogolele Malawi. Mr Namiwa tisatope mpaka chenicheni chidziwike.
@GraceCbwanali
@GraceCbwanali 8 сағат бұрын
Mr Namiza umati yimirila Mulungu azikudalitsa
@JohnBandawe
@JohnBandawe 7 сағат бұрын
Tien naon mademo tipange commission of enquiry yathu osat nyasi izi RIP SKC
@Pangolinimw
@Pangolinimw 12 сағат бұрын
Namiwa umakwana kobasi
@MathewsWisick
@MathewsWisick 7 сағат бұрын
🎉🎉🎉🎉
@ChikumbutsoChiphaka
@ChikumbutsoChiphaka 7 сағат бұрын
Apite kulikonse namiwa, ngozi I dachitika bax
@ChikumbutsoChiphaka
@ChikumbutsoChiphaka 7 сағат бұрын
Mmmmm, kodi namiwa amadziva kudziwa zinthu kwambiri?, chifukwa chani adatulukamo mu commission mmalo moti akapeleke ma umboni wakewo, iyeyo ngati ndi dolo apange yake inquiry, and akayambe kupanga inquiry anthu amene adamwalira kumudzi kwao
@wilsonchimtikaphiri9496
@wilsonchimtikaphiri9496 6 сағат бұрын
Akadamusowetsanso
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 6 сағат бұрын
Awa ndi achitsiru ngati sanavese linawengedwa ndi amene amapanga kafukufuku koma kuti anthu akhale ndi ma copy a report azapeleka president akaliwona ndiye timavesa akulu wa
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 6 сағат бұрын
Anamiwa ngati muli ndi mayakho tangowawuzani a Malawi munthu wina aliyese Ali ndi nthawi yofera we have to accept that all of us we are going to die which malawian did not eat food for what reason
@WelingsLongwe
@WelingsLongwe 6 сағат бұрын
Ngakhale munthu atakhala wopanda nzeru sangasakhe commission of inquiry ngozi itangochitika kumene anamiwa taziyakhulani munthu mtsogoleri
@ChikondiBannet
@ChikondiBannet 7 сағат бұрын
Macheso wqsunga ndiwe namiwa
@ThandiMatin
@ThandiMatin 6 сағат бұрын
Ati boma ili akulamulira nsima mafiya😂😂😂😂 apo nde wang'aluradi
@BandahLemos
@BandahLemos 4 сағат бұрын
Munachita bwino kutulukamo kut inu mubwerese chilungamo
@EmmanuelWhite-d2f
@EmmanuelWhite-d2f 3 сағат бұрын
Koma namiwa akuyesetsa koma amalawife tili ziii
@JamesYusufu-l6d
@JamesYusufu-l6d 8 сағат бұрын
eeeeee koma chakwela. ndigalu. weniweni. lopoti limenero akamuwuze monika. kaziwake. zopusazo. ai
@ColiamAbineli
@ColiamAbineli 6 сағат бұрын
Kodi inu mudali mmodzi mwa osankhidwa kukhala mwa ofufuza nawa ndipo tidaakudalilani kuti tidziwa zambiri kuti zidakhala bwanji kuti miyoyo ya osalakwa iluzike inu mkutuluka, tizikhulupilire bwanji zomwe mukulankhula ku mtundu wa amalawi bwana?
@isaaczuze
@isaaczuze 12 сағат бұрын
Boma loyendesedwa ndi zigawenga komanso mbava ....chakwera uzaziona nthawi ikazakwana
@festonselemani4491
@festonselemani4491 7 сағат бұрын
Ku Malawi kuli anthu ena ena wolimba mtima
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 11 сағат бұрын
Chakwela analakwitsa kupha Chilima, ana achilima amafunaso adakamaona bambo awo
@HaroonKampepule
@HaroonKampepule 12 сағат бұрын
Music kumbuyoko imandichosapo apa
@VincentMapira-h1f
@VincentMapira-h1f 9 сағат бұрын
I want to be a member of cded. Ndipange bwanji
@MatiusChinawa
@MatiusChinawa 11 сағат бұрын
Kkkkk guys skc analakwa chan.
@MaulanaIriyasa
@MaulanaIriyasa 12 сағат бұрын
Kukwela ndege mpaka kuwuma magazi koma zilikoliko
@SiboNkundi-hm1si
@SiboNkundi-hm1si 5 сағат бұрын
Yeah indeed someone must pay the price, dzikoli asalitenge mopepela choncho ngati la abale awo
@JohnLyton
@JohnLyton 11 сағат бұрын
Iweyo ngopusa iwe unkathawilanji
@DoriceMagawa
@DoriceMagawa 7 сағат бұрын
Akafuna apeze nthaw yabwino yodzaona zolakwikazo and anali nd zochita zina zofunikilaso nthaw yomweyo. Apa nde tikufuna kudziwano from mcp commission
@ChristopherChakometsa
@ChristopherChakometsa 5 сағат бұрын
Go go namiwa tuliuzeni zoona
@ChoopsyaLloyd
@ChoopsyaLloyd 10 сағат бұрын
I think namiwa akufunika ku mental
@chilembwekanjirawaya4296
@chilembwekanjirawaya4296 8 сағат бұрын
Inu paja mwachila week yatha ndiye yayambilanso
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 11 сағат бұрын
Kkkk apo nde mwalasadi bigy aliense amene ali boma atimva di kuyabwa coz akuzolowela.Ma actionz a kuenela atengedwe mosacedwa cifukwa zimene anamiwa akulankhulazi ndizomwe a malawife tikulankhula ndizoona kuti lipotili angotitayisadi nthawi ndi kobili zathu zisilu zimenezi Anamiwa tili pambuyo panu osadanda.
@williempinda505
@williempinda505 10 сағат бұрын
The 😂
@PatrickKatentha-x7s
@PatrickKatentha-x7s 11 сағат бұрын
In
@DoriceMagawa
@DoriceMagawa 7 сағат бұрын
❤❤❤❤
Don’t Choose The Wrong Box 😱
00:41
Topper Guild
Рет қаралды 60 МЛН
The Best Band 😅 #toshleh #viralshort
00:11
Toshleh
Рет қаралды 21 МЛН
MOSLIMS KOMEN TOT BLOEI WANNEER DE ISLAM ONDER DRUK STAAT | KASIM TEKIN
52:44
Full Video | Episode 139 | Col. Douglas Macgregor (ret.)
1:27:00
Blenheim Partners
Рет қаралды 1 МЛН
Dr. Robert Lustig: How Sugar & Processed Foods Impact Your Health
3:29:21
Andrew Huberman
Рет қаралды 4,2 МЛН
EXCLUSIVE - WITH MOSES KUNKUYU | 14  DECEMBER 2024
1:11:12
Malawi News Update
Рет қаралды 40 М.