VITUMBIKO MUMBA WAULURA LERO PA KULINJI KUTI ANTHU ENA A KUCHIPANI CHA MCP AYAMBA KUMUCHITIRA NSANJE

  Рет қаралды 7,699

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 30
@SolomonMumba-i5n
@SolomonMumba-i5n 9 сағат бұрын
I have to recommend what Mr Mumba is doing honestly, he must just carry on the good work, and that we can all see as well as witness. He mustn't expect much from their corrupt counterparts, they are rotten to the core, you are a real Malawian and would like to change our country for the better. Big up your honorable!! We salute your effort
@RodneyTomato
@RodneyTomato 11 сағат бұрын
Imagine if we have lots of people like Mumba how our country will be congratulations minister
@rightlombe380
@rightlombe380 Сағат бұрын
Let's give Eng. Mumba his flowers 🎉while he is still alive. Munthuyo ndi Malawi 🇲🇼 weni weni ndipo akutivetsa kukoma 🎉
@HestingsMtampha
@HestingsMtampha 3 сағат бұрын
Big up Mumba, mukupanga zokomela anthu osati andale
@JoelCHIHANA-y6p
@JoelCHIHANA-y6p 2 сағат бұрын
Good initiative to work with partners Taveta .
@JoelCHIHANA-y6p
@JoelCHIHANA-y6p 2 сағат бұрын
Well done Honaurable Mumba wawachangamutsa ma company. And MBS mwayichangamutsa ndiponyayamba kugwira ntchito
@MikeChimombo-n6w
@MikeChimombo-n6w 3 сағат бұрын
President tikusintha koma nduna sitikusintha
@kondananingwira1312
@kondananingwira1312 9 сағат бұрын
Akukwiyao si amalawi Koma a app Big up mr mumba
@vitumbikophirikanyinji5055
@vitumbikophirikanyinji5055 11 сағат бұрын
Ma minister onse amene ntchito zawo sizikuwoneka ngati mining and transport
@vitumbikophirikanyinji5055
@vitumbikophirikanyinji5055 12 сағат бұрын
Times keep it up following this Mr Mumba and help him
@Andy20247
@Andy20247 5 сағат бұрын
Ndipo live mumba mpando wako ndi omwewu olo boma lisinthe tisintha boma koma minister sitikusintha
@andrewtchuwa5368
@andrewtchuwa5368 8 сағат бұрын
Keep it Mr Mumba, mwayamba bwino
@MosesBanda-h4x
@MosesBanda-h4x 9 сағат бұрын
Nduna zonse zikanakhala ngati Vitumbiko Mumba, mavuto omwe a Malawi tili, anakatha kapena kuchepa koma nduna zambiri sizigwira ntchito. Nduna nonse khalani ngat Vitumbiko komanso pewani kutsogoza nsanje ndikumalandira ndalama zaulere.,.....
@Mussa-g5m
@Mussa-g5m 11 сағат бұрын
Amumba ndinduna yothandiza isazachoke ngakhale a dpp azamutengeso yemwei amatha ntchito
@VincentBanda-g4y
@VincentBanda-g4y 13 сағат бұрын
Mumba akugwila ntchito yotamandika hvy anthu akuzuzika
@Andy20247
@Andy20247 5 сағат бұрын
Mukamakatsegura company ya CP atolankhani akajambure zomwe akhozazo
@denndavie6041
@denndavie6041 12 сағат бұрын
Mumba keep your legacy beside mention yuor giant kille Chakwera. What a fuck? Anyway keep good job.
@vitumbikophirikanyinji5055
@vitumbikophirikanyinji5055 11 сағат бұрын
Ma company ena ngati amapeleka 3 month contract kodi ndizololedwa mu malamulo aboma?
@vitumbikophirikanyinji5055
@vitumbikophirikanyinji5055 12 сағат бұрын
Keep it up Mr Mumba Pitani ku Chinese construction company Nako muoneko. Komaso ma MP Ali ndi ma company ali mgulu lophwanya ma ufulu a anthu
@Yujiang-m4g
@Yujiang-m4g 10 сағат бұрын
Keep it up mr mumba
@vitumbikophirikanyinji5055
@vitumbikophirikanyinji5055 11 сағат бұрын
Anthu amene akuti a Mumba alakwisawo si a Malawi
@CharlesEston-qv4kr
@CharlesEston-qv4kr 12 сағат бұрын
Amumba pitaninso kuThyolo ,mulanje makampani a tea estate ,akudzuza anthu kwambiri katsekeni kumeneko
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 11 сағат бұрын
Maganizo omanena kuti adziseka makampani ndi o mpusa cifukwa mudziwe kuti dzikoli silibwino, kobili kulibe palibe ciliconse cikuenda, kodi mukatseka anthu akugwila ntchito makampaniwo adzidya kuti? Mupeze njira zina osati izi ntcotoyi ili boh koma apange njira ina osati kutseka kampami aise dzikoli anthu akuvutika adzidya cani?
@DesmondChavula
@DesmondChavula 6 сағат бұрын
Morefire mumba
@willardnkhoma
@willardnkhoma 11 сағат бұрын
Amumba abwereso ku mt meru mellus Ku Lumbadzi~ Dowa turnoff nakoso sikulibwino
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 12 сағат бұрын
Anduna adzikhala Ngati Mr mumba, not ena timangomva Kuti anduna koma ntchito yawo sikuoneka.
@GeoffreyMadeya
@GeoffreyMadeya 11 сағат бұрын
ine ndimaganiza kuti zikanayambila mbomamu chifukwa nakonso kubomaku kuli anthu ogwila ntchito ochuluka omwenso akudandaula mwachisanzo kupolice ena akuzigulila okha jombo
@DelubyMarko
@DelubyMarko 11 сағат бұрын
Bravo Mumba
@KondwaniGulonyonyo
@KondwaniGulonyonyo 10 сағат бұрын
Ine ndikanakondwa anakapitanso ku african parck majete akafufuze kut kod anthu akugwila bwanji ntchito nanga ndomeko zawo zakalembedwe kantchito kawo ndindomeko zit zomwe amasata kili mavuto kwambili
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 11 сағат бұрын
Mumbai is just grandstanding. No amount of doing that will make Malawians forget about the murder of Saulos Klaus Chilima. We will never forget
Who is More Stupid? #tiktok #sigmagirl #funny
0:27
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 10 МЛН
Air Sigma Girl #sigma
0:32
Jin and Hattie
Рет қаралды 45 МЛН
GWEDE GWEDE | 21 January 2025
29:42
Malawi News Update
Рет қаралды 17 М.
Who is More Stupid? #tiktok #sigmagirl #funny
0:27
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 10 МЛН