MALAWI PARLIAMENT LIVE - KWACHEMA PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA KUYANKHA MAFUSO AMA MP GAME ILITHAFU

  Рет қаралды 12,662

AM TV MALAWI

AM TV MALAWI

Күн бұрын

Пікірлер: 36
@EnthusiasticMountain-xd7vn
@EnthusiasticMountain-xd7vn 2 күн бұрын
Chingelezi Cha chitsamunda ,😮
@KettieNathaya
@KettieNathaya 2 күн бұрын
Chikangawa hoyeeee tidya chizungu ife? Unya uwona
@LameckNgwangwa-g3p
@LameckNgwangwa-g3p 2 күн бұрын
Ayankheso tu za ku chikangawa zija mwayi mngomweu phiri ii
@BillyChunga-u2f
@BillyChunga-u2f 2 күн бұрын
Bingu in one year of his rule he manage to have more food in the country of malawi
@BunnahAdamh-n7s
@BunnahAdamh-n7s 2 күн бұрын
Chizungu ndi Icho km samalan kye anthu akuvutika chakudya please chakwela
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 күн бұрын
koma chizungu chikamayendera limodzi ndi kukwera kwa dziko tili patali 12:33
@mthawisakaunda
@mthawisakaunda 2 күн бұрын
Rest in peace SKC
@JumahHassa
@JumahHassa 2 күн бұрын
Mamina awawa tatopa nawo koma mistake yomwe mudapanga pa moyo wanu ndikupha amzanu lmene lja ndiye eeeeeee lnshaallah
@allahslave7177
@allahslave7177 2 күн бұрын
Kungokhala ndi English basi koma opanda nzeru ndinso masomphanya mkulu yi
@BujuWhyson
@BujuWhyson 2 күн бұрын
😇😇
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 күн бұрын
Always I feel sorry for you chakwera
@temwanivinjeromfune7889
@temwanivinjeromfune7889 2 күн бұрын
Munthu sukumva ngakgale chizungu uchonga bwanji President kuti alibe nzeru? Zina ukamva umangoziwiratu kuti awa ndi mamina.
@MarySinjirani
@MarySinjirani 2 күн бұрын
Chakwela iwe magazi, malovu ndi kodzo wa aChilima ndi anthu ena onse aja unapita nayo kuti mfiti iwe
@MandalaChaona
@MandalaChaona 2 күн бұрын
Ku Mpingoko Akhristu anapuma anangothokoza Kuti Zikomo Malawi potichosera Chiphinjo Chi Chuma sichimalongosoka 😂😂😂
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 2 күн бұрын
Koma Anthu tatopa Awafunse za ku Chikangawa😅😅😅😅😅😅😅
@MacdonaldMajohn
@MacdonaldMajohn 2 күн бұрын
Paja kuchipiku anthu amabhunzirako chizungu
@RobertChiz
@RobertChiz 2 күн бұрын
Muzaone ngakhale ku sukulu anthu amene amalankhula chizungu chofuna kut atamidwe amakhala opanda nzeru
@BujuWhyson
@BujuWhyson 2 күн бұрын
😄😄😄😄😄😄😄
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 2 күн бұрын
😅😅😅😅😅
@gracemaluwa4674
@gracemaluwa4674 2 күн бұрын
😂😂😂
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 күн бұрын
Facts 😂
@EvaBanda-u8i
@EvaBanda-u8i 2 күн бұрын
Ndipo nizoona ine navomerela kuno kuzambia 😅
@BujuWhyson
@BujuWhyson 2 күн бұрын
akuyankhula chitsamunda
@LawrenceBelson
@LawrenceBelson 2 күн бұрын
Tidya chizungu chakocho
@humphreysidie4747
@humphreysidie4747 2 күн бұрын
Kuzivuta yekha, munthu waku Dowa koma speaking like waku Chicago, nonsense
@MandalaChaona
@MandalaChaona 2 күн бұрын
Chidzungu chomwera Magazi ndi mikodzo. Kuchosa moyo wamzako Chifukwa cha Udindo eeeeeeeee mdipiti wa Magalimoto utakoma Mr SMARTMATIC. Ukhalepotu pa mpandopo mpaka 2050 . Tilipano kuonera, Ana a njoka a MCP
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 2 күн бұрын
Chimunthu choyipa mtima
@liz9425
@liz9425 2 күн бұрын
Chigawenga tinavotera macholowe amalawi
@ClementMushele
@ClementMushele 2 күн бұрын
We have tired of this man
@AmissKumakanga
@AmissKumakanga 2 күн бұрын
Chithakat
@henryphiri6100
@henryphiri6100 2 күн бұрын
Kuti mumudziwe munthu yu kuti ndi chitsiru mumuvetsere mkamwa mwakemo. Nthawi imene ankagwira ntchito ku chipiku sankayankhula chonchi chizungu wapita ku America kukachedwa ndikungophunzira kuyankhula mfuno chizungu. Munthu opusa amataya chikhalidwe chake
@AnnieZiba
@AnnieZiba 2 күн бұрын
Black box lol
@AustinChabinga
@AustinChabinga 2 күн бұрын
Umaziwa kupha koka
黑天使只对C罗有感觉#short #angel #clown
00:39
Super Beauty team
Рет қаралды 36 МЛН
She made herself an ear of corn from his marmalade candies🌽🌽🌽
00:38
Valja & Maxim Family
Рет қаралды 18 МЛН
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 108 МЛН
USAUVER S10E07 - RECEPTION
26:30
Piksy TV
Рет қаралды 60 М.
Путин: "Доводят нас до красной черты"
1:11
Euronews по-русски
Рет қаралды 130 М.
Chombo chaonongeka kumwamba ndipo anthu awiri asowa mtengo ogwira
12:30
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 4,5 М.
黑天使只对C罗有感觉#short #angel #clown
00:39
Super Beauty team
Рет қаралды 36 МЛН