When a business man is caught selling pork meat among the majority muslims who regards it as unclean. The fall out catch through a camera. 2013 production
Пікірлер: 77
@rhinowilliam85784 жыл бұрын
Kodi anthu awa amadzikonda bwanji
@veronicanyanda70667 жыл бұрын
kudzikonda koma kusetera manja aliyese Ali ndi ufulu wake ngat zimenezo mupeze dziko lanu
Umbuli kodi asilamu mumalanda akazi a enaache kwa mulungu sinchimo kumapha anthu sinchimo dziko lapasi nkhondo zimachitika ndi asilamu kukangana ndi a christu mbuli zeni zeni Muhammad si mulungu kodi analenga nkhumba ndi mulungu not Muhammad
Ngakhale kuno Ku south Africa mashop ndiyambili ofuna amagula ngati sumadya umasiya koma zopusa zanuzo aaaaa chamba kwambiri
@Slyvia-uu3wc5 ай бұрын
Zisilu za anthu khumbayo mumadya kuno ku joni,, mbuli, chimidzi kwambili tayendani muwone agalu
@Emmanuelsalifu-lc1rm3 ай бұрын
Iweso manyi ako
@lewisbonongwe8518 Жыл бұрын
Nkhumba ndi ntchimo koma chigololo ayi mmmm koma chipembezo ichi ndiye kaya Muhammad mwini wakeyo ankadya nkhumba
@Emmanuelsalifu-lc1rm3 ай бұрын
Ase manyi ako
@fostetfostet900 Жыл бұрын
Ine ndimakhala ku Newlands (JURBERG)pamalopo pali chisilamu wokha wokha koma za uchisuru zokhazokha achehe kumasintha azimayi anzizawo ankandifusa why you r eating pork? naneso ndimafusa bwanji iwe kumasintha azimayi komaso umanyenga akhazi a ena ache ? Abale zose akziwa mulungu no judgement pa dziko lapasi mu christu or musilamu tose ndife ana amulungu
@VeronicaGoliath-yg8vy6 ай бұрын
Sizoona kuletsana kupanga business Malawi ndi dziko la aliyense not asilamu okha be serious guys
@tingoalex6370 Жыл бұрын
Ine singasiye mkhumba kudya ku mangochi kutitso
@twahayusuf23847 жыл бұрын
mashaallah
@enockbwanali94727 жыл бұрын
lets keep on watching these videos.
@lewisbonongwe8518 Жыл бұрын
Dziko ndi la aliyense ili palibe ulamuliro wa ntundu umozi
@patrickmchemo68045 жыл бұрын
Inu ndi zitsilu za anthu Kodi mukumalitenga dziko la Malawi ngati ndi lanu.komatu zomwe mukupanga inu asilamu tsiku lina anthu Malawi tizanthamanga
@edisonnyasulu95685 жыл бұрын
Asilamu ndi zigewenga malingana ndi zikhulupilo chawo maiko ambiri anthu akuphedwa ndi asilamu mukawone boko halam shababu.
@macleanmachamo2 ай бұрын
I blame government
@erickunkeani47265 жыл бұрын
Mbuli inu
@alexanderkaunda95543 жыл бұрын
Pachichewa-kukwedza-mau-pachizungu-kuliziiiiiiii
@esmielaja25367 жыл бұрын
kkkkk odiii ukooooooo!!!
@alexanderkaunda95543 жыл бұрын
Kkkkkk msilamu-samavachizungu
@mcmillanalexlmanda50517 жыл бұрын
wawa
@ThumbikoChipofya-gq7sd10 ай бұрын
Ndiye akut walakwa kugulitsa nkhumba? Wolakwitsa ndi otayawo chifukwa ogulitsayo sadawakakamize ,kodi kumaboma ena asilimu kulibe nanga nkhumba imadibwa bwanji?_Nanga amene amadya sakuwaphera ufulu? Vuto ndi umbuli by the way Malawi is a secular state kod Mangochi ndi state payokha
@daudlester12867 жыл бұрын
sukulu ndi chipembezo ndi zithu zoxiyana mbuli ndi iwe chifukwa ukutukwana bcz unapita m crass koma ulibe mtnchito usauka ngati ine
@hamiltondaved15227 жыл бұрын
ayawo kusukulu ndikofunika !!.
@enockbwanali94727 жыл бұрын
eish but thanks for watching man
@user-gj8td8pc4d6 ай бұрын
Part of ignorance. Amaona ND anthu akeso
@aishakachewale81124 жыл бұрын
Umbuli ndi matenda asilamu ofunika kumangowakhulukila chifukwa apa palibe chifukwa chomuletsa munthu kugulitsa malonda ake munthu apo anaphera ufulu wake
@clivengwira99925 жыл бұрын
if you don't it pork don't buy it!
@edisonnyasulu95685 жыл бұрын
Asilamu ndi mbuli vuto ndi limero sukulu ndi mbali yina Ku chisilamu
Where is the right in Malawi? Does it mean Mangochi is a state on it's own. Oh God help the people of Malawi.
@christophershuga58717 жыл бұрын
nonsense.give them the place to sell pork.remember we are staying in the area of co-group of people,with different believes and religious.dont break others rights
@enockbwanali94727 жыл бұрын
keep on watching guys
@veronicanyanda70667 жыл бұрын
mvuto lochuruka mbuli mu zikiti KO'd did u know wat human rights its all a bout kusukulu kwabwno achawa inu Ali ndi ufulu kukhara malo komanso kupanga business anywhere in Malawi