MAYI BRENDA SAIDI A DPP OMWE AOMBWELWDWA DZULO AJA NDI AWA NDIPO PA NSONKHANO WINA ANAYANKHULAPO IZI

  Рет қаралды 25,448

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 55
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 19 сағат бұрын
Mbuli kupha anthu kamba kofuna maudindo, Chakwera Akufunika ataphedwaso naye, Amalawi tisamaonelele anthu azifa chonchija. Kukhala ku South Africa ndi maiko ena imfa Yachilima ija Chakwera adakathawa enanso okhudzidwa adakaphedwa
@MalawiWaLero
@MalawiWaLero 13 сағат бұрын
That's very true Our main problem is that achinyamata ambiri sali mziko lathu chifukwa cha mavuto kotelo osalafe tuchitidwa overpower ndi agalu a MCP
@yohanekanjana4925
@yohanekanjana4925 4 сағат бұрын
kupha kwake pofunika ndizikwanje, kamunthu koipa kwambiri. zonsezitu ndi umbuli, ndale zophana zinatha kale kale
@ChrispineMuzungu-l8h
@ChrispineMuzungu-l8h 3 минут бұрын
Km guys ifeyo a Malawi tili ndi vuto we only know kuyankhula km action we don't show tien tiphe nkhumba imeneyi🎉🎉
@yusuflifa2923
@yusuflifa2923 16 сағат бұрын
Imeneo ndi KK lady, simaphwekesa
@AmisiDytoni
@AmisiDytoni Сағат бұрын
A mcm kumwela kuno tizingogenda ndipo tiphana
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 19 сағат бұрын
Azimayi ochangamuka pa town, chakwela amadana ndi chilungamo...
@Lincs3765
@Lincs3765 20 сағат бұрын
Politics centered around food. Tingatukuke chonchi? We need to change systems NOT ruling parties. Its just a vicious circle
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni 17 сағат бұрын
Koma salu simunatigawire 😂😂😂
@shafiemalobvu
@shafiemalobvu 17 сағат бұрын
Mwatipwetekela wathu wathu waku nkhotakota 😢😢
@MarkElia-i7q
@MarkElia-i7q 16 сағат бұрын
Mpaka zafika poomberana eshiii Koma democracy yavuta 😢😢
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 11 сағат бұрын
Wapolice wawomberayo anachita kutumidwa nanga chinamulimbitsa mtima mpaka kuwombera ndi chani?
@LosanThawale
@LosanThawale 17 сағат бұрын
Ipakule bola wadya DPP woyeee🎉
@KestherMkandawire
@KestherMkandawire Сағат бұрын
Inuyo nenani zomwe mudzapange. Ndipo amai mfundo mulibe apo .
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 14 сағат бұрын
Iweso ndiwe garu azikarima zichani poti ukudya ndarama zausataniki
@EdwinMsukwa
@EdwinMsukwa 10 сағат бұрын
Dpp yomweyo
@Chisomo-q3e
@Chisomo-q3e 19 сағат бұрын
Tokotani sister
@IvyMkhura
@IvyMkhura 11 сағат бұрын
Dpp boma
@JemimahPaligolo-dj2uz
@JemimahPaligolo-dj2uz 16 сағат бұрын
Eish😂😂😂
@JamesMwanancho
@JamesMwanancho 9 сағат бұрын
Anamuphonya mutu wamuwombela pa mkono
@MeruMitha
@MeruMitha 17 сағат бұрын
nokha mukuti Malawi sidzabwereranso mbuyo nde kupitanso ku DPP si kubwerera mmbuyo?
@yusuflifa2923
@yusuflifa2923 16 сағат бұрын
Ukutanthauza kuti sitikufuna kubwereraso ku ulamuliro wachipani chimodzi cha MCP.
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman 14 сағат бұрын
Inu ndiofoira kupusa
@MsondaBanda
@MsondaBanda 16 сағат бұрын
Kalimeninge
@LameckNgwangwa-g3p
@LameckNgwangwa-g3p 20 сағат бұрын
Bravooo sister
@DuffJuma
@DuffJuma 11 сағат бұрын
Pa home
@ElizabethMbewe-l2c
@ElizabethMbewe-l2c 11 сағат бұрын
Komatu chakwela chakwela ohooo
@MasaukoChinthowa
@MasaukoChinthowa 13 сағат бұрын
Bho boss
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 12 сағат бұрын
Chakwera ndazizake apangidwe zangati zimene apanga ku DRC akaphwedwe amenewo life sentence akaphewe basi
@HyTy-r3m
@HyTy-r3m 19 сағат бұрын
Koma nkhotakota kutuluka azimayi olimba uyu ndiye gereuja alinaye mmadzi agereaja akathera ku mcp konko ingobwererani mukapepese kwa adadi
@lasmoboko5989
@lasmoboko5989 16 сағат бұрын
Za PETER zokhazo ndiye ayi ena avinemo
@IsaacSombani-b8v
@IsaacSombani-b8v 15 сағат бұрын
Amene washutidwa .Oswat mbiri ikumveka be specific other wise you can gv as wrong information. Don't scare some tell us reality, okay?
@GeofreyMkhala
@GeofreyMkhala 12 сағат бұрын
Ndale zizakupwetekesan kufika poti ine niwonbele kuti tinyazise zipani Zina mmmmmm anthu akuma vekedya ma bomba akafe bola ana kapena family yake ikhale pamtendele ndale za malawi kuipa manye pang,ono
@danielmapulanga1321
@danielmapulanga1321 14 сағат бұрын
Amakatani ku police ,walapa
@harrypetros1216
@harrypetros1216 11 сағат бұрын
Mmmmm ali chemwali any mungave bwa
@StythewsMkwiyo
@StythewsMkwiyo 19 сағат бұрын
Kaya nkuombedwa,kaya kuphedwa,chilungamo chiyende ngati madzi. Ngakhale mutamuotsa mayina ochuluka chodziwika mwapanika
@WilliamMajiwa
@WilliamMajiwa 17 сағат бұрын
Mayi mukhala bwino, Chakwera wafa nayo. Mangolomera akuchekerani.
@Twaibuishmael-j4v
@Twaibuishmael-j4v 18 сағат бұрын
Ufulu kulibe andale atha tabwelela kuchipani chimozi
@RoseMkandawire-e2g
@RoseMkandawire-e2g 14 сағат бұрын
1:16 1:16 1:16
@MusaMusa-h3v
@MusaMusa-h3v 18 сағат бұрын
Osadandaula.mayi.mulungundiwachifundo.mukhalabwino
@DysonTembo-g6h
@DysonTembo-g6h 19 сағат бұрын
Timafuna mfundo zozesa chitukukoo osati kunyoza si kampeenii yotukula miyoyo ya aMalawi lyiiii . Wukunamaaa tiwinaaa wuonaa
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 19 сағат бұрын
Ngati timavota ndife sawina chakwera km ngati amavota ekha awina anthu tinachangamuka tatopa ndimanyaka a mcp
@ReginaMzunga
@ReginaMzunga 18 сағат бұрын
kkkkkkk paka chikagawa kuwina malodza ndithu
@LafickDickson
@LafickDickson 13 сағат бұрын
Dpp moto
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 20 сағат бұрын
Kod mukulakhula bwanji azimai 😂😂😂
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 19 сағат бұрын
More fire 🔥
@EdgarBuleya
@EdgarBuleya 16 сағат бұрын
Kkkk mayi awwwa
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 17 сағат бұрын
Agalu even nonse mufe no complain because dziko la Malawi wanawonga ndi Peter chisale, 😂😂😂😂
@LloydVenter-o7e
@LloydVenter-o7e 20 сағат бұрын
Azimayi atopa awa ndichulungamo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅
@SylvesterSululu
@SylvesterSululu 16 сағат бұрын
Chipani cha mcp ndichasatanik ndithu
@DysonTembo-g6h
@DysonTembo-g6h 19 сағат бұрын
Mahule a a zimayi awaaa awululilaa ana zakuchipindaaa
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 19 сағат бұрын
Kamwe panado uchila iweee😅😅
@JafarWiati
@JafarWiati 18 сағат бұрын
Kabwila wako uja kaje kuyipa nkhope ngati sinkazi
@ReginaMzunga
@ReginaMzunga 18 сағат бұрын
Kkkkk achila koma mochedwa
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 17 сағат бұрын
Agalu even nonse mufe no complain because dziko la Malawi wanawonga ndi Peter chisale, 😂😂😂😂
Don’t Choose The Wrong Box 😱
00:41
Topper Guild
Рет қаралды 62 МЛН
Sigma Kid Mistake #funny #sigma
00:17
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 30 МЛН
coco在求救? #小丑 #天使 #shorts
00:29
好人小丑
Рет қаралды 120 МЛН
Assista na íntegra o Interacção Matinal 13/01/2025
MIRAMAR
Рет қаралды 4,2 М.
Russian secret base uncovered / Russia abandons the region
14:15
NEXTA Live
Рет қаралды 752 М.
Em direto: 13 de Janeiro de 2025 - Jornal da Manhã
DW Português para África
Рет қаралды 1,3 М.
Mary Chilima new song lyrics
2:26
KULINJI TV 🇲🇼
Рет қаралды 44 М.
Ku ukwati wa chibwenzi chako chakale
3:50
Robert Chiwamba
Рет қаралды 166 М.
Don’t Choose The Wrong Box 😱
00:41
Topper Guild
Рет қаралды 62 МЛН