Mayi Wina Watopa ndikugonana ndi Ndondocha

  Рет қаралды 4,376

Mvangeli Online

Mvangeli Online

Жыл бұрын

Mverani program ya Zilipati yokhudza nkhani ya mayi wina ku Blantyre yemwe akuulura kuti watopa ndikusamalira ndondocha zomwe mamuna wake anakatenga kwa sing'anga wina ku Mozambique kuti alemere.
Mwa zina mayi-yu wauza Zilipati kuti amauzidwa kuti azigonana ndi ndondocha yaimuna ndipo mamuna wake azigonana ndi ndondocha yaikazi
Iye wauzaso Zilipati kuti anauzidwa kuti aphe mwana wawo mmodzi komanso adzipha wachibale chaka chilichonse.
Programuyi inagulitsidwa pa #MIJ FM pa program ya #zilipati, ife a Mvangeli Online tiilibe umwini pa video imeyi.

Пікірлер: 8
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o 2 күн бұрын
Dziko likufunika yesu Ili yoooo😢😢😢😢
@user-zl5gc9hx1i
@user-zl5gc9hx1i 6 ай бұрын
Timakhala limodzi kuchigumula time inayake
@DavieChingagwere-lw1kq
@DavieChingagwere-lw1kq 7 ай бұрын
Zoopsatu
@CatherineChidzaro-zw1fe
@CatherineChidzaro-zw1fe Ай бұрын
😢 koma dzikoli kumachita zinthu
@iPrinceoflove
@iPrinceoflove Ай бұрын
Zilikotu
@user-qu5gf7cd5i
@user-qu5gf7cd5i 4 ай бұрын
Kodi too yake inatuluka ndikuyesa kufufuza osaipeza
@user-zl5gc9hx1i
@user-zl5gc9hx1i 6 ай бұрын
Anali aneba awa
@iPrinceoflove
@iPrinceoflove 5 ай бұрын
Ooh?😮
Amayi Tokotani - Mamuna wa nzako akakufunsira mvomere
58:37
Mibawa Studios
Рет қаралды 31 М.
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza zambiri za nsapato ya gogoda
24:15
Living for Christ - Malawi
Рет қаралды 6 М.
How Many Balloons Does It Take To Fly?
00:18
MrBeast
Рет қаралды 191 МЛН
MISS CIRCLE STUDENTS BULLY ME!
00:12
Andreas Eskander
Рет қаралды 18 МЛН
Как бесплатно замутить iphone 15 pro max
00:59
ЖЕЛЕЗНЫЙ КОРОЛЬ
Рет қаралды 8 МЛН
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Zodiak Malawi
Рет қаралды 48 М.
CRUISE 5   ELIYA NZERU WILLIAM
1:20:13
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 384 М.
Morning Prayer with Pastor Maria Murphy | Tuesday, July 30, 2024
31:53
Impact Family Church Dighton, MA
Рет қаралды 41
Zilipati: Kulira Kwa Atsikana omwe ali m'dziko La Oman
31:09
Mvangeli Online
Рет қаралды 2,8 М.
ZILIPATI PA MIJ FM-KUCHEZA NDI OMWE ANAVULAZIDWA NDI NACHIPANTI
19:22
Ticheze Amalawi
Рет қаралды 21 М.
Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza zambiri za gule wa Vimbuza
43:42
Living for Christ - Malawi
Рет қаралды 2,1 М.
TIPANGE  DAWA  SAID ZAMBIA
58:39
AWUZENI KUTI MEDIA PRODUCTION CREW
Рет қаралды 139 М.