MCP APA YAGWA CHAGADA! COMRADE NTANYIWA LIMPOPO FM!

  Рет қаралды 38,794

Malawi Lero🇲🇼

Malawi Lero🇲🇼

Күн бұрын

Пікірлер: 145
@WilliamChi-c6p
@WilliamChi-c6p 3 күн бұрын
Eeeeeeeeeeh! Koma yaaaaaah! Koma umatha
@HerlbertKaalis
@HerlbertKaalis 3 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkkkkkkk zabwino kwabasi ndithu God have mercy on Malawians!!!!!!!!!!❤❤❤❤
@AnthonyChilenje
@AnthonyChilenje 3 күн бұрын
Big up Mulungu Ali mbali yathu
@JoyceKasongo-s8k
@JoyceKasongo-s8k 3 күн бұрын
Welcome back Mr ntanyiwa
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 3 күн бұрын
God is good always 🙏🙏
@ABDURASHEEDMATEMBA-b2b
@ABDURASHEEDMATEMBA-b2b 3 күн бұрын
Achakwera mukunvabwanji apa mr Mmene alankhulilamu eeee😂😂😂😂😂
@RitaKainga
@RitaKainga 3 күн бұрын
😂😂😂😂 more 🔥🔥🔥 tiyeni nazoooo,tilipambuyo panuuuu
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂 ntanyiwa suzatheka 😂😂😂😂😂😂iiiiii love you much ❤❤❤❤❤mmatiimilila ife amalawi
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 3 күн бұрын
Zilibwino GOD Bless MALAWI
@AaronNdawu-n6z
@AaronNdawu-n6z 2 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 Akumana ndimanjanjawidi.... iiiih iwe Tanyiwa God bless you brother man
@MarkElia-i7q
@MarkElia-i7q 3 күн бұрын
Chachita bwino 😂😂😂
@WillyPhiri-l5b
@WillyPhiri-l5b 12 сағат бұрын
😝😝😝😝chaphulika chithupya🔥🔥🔥🔥
@BlessingsAustin-h2m
@BlessingsAustin-h2m 17 сағат бұрын
Remind mi my late father that song kkkkkk koma mtanyuwa pola fire shauliyakooooooo!!
@GiftMuyungu
@GiftMuyungu 3 күн бұрын
Mulungu alemekezeke ❤
@DanielJuwawo-s5n
@DanielJuwawo-s5n 3 күн бұрын
Zili bwino kwambiri ine kumva kukoma kwambiri 😂😂😂😂😂😂😂 mulungu si James
@KamozaMlunda
@KamozaMlunda 3 күн бұрын
Kuchemaaaaassas😂😂😂😂 sindidzachokako k Malawi kobeba😅
@gracekamzati
@gracekamzati Күн бұрын
Mtanyiwa wooooyeeeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥motobuuuuuuu wins aliraaaaa
@PatriciaBanda-e3v
@PatriciaBanda-e3v Күн бұрын
😂😂😂😂😂😢koma NtanyiwA uzatiphesa
@StaffordNgoleka
@StaffordNgoleka 3 күн бұрын
Km ngt zilizoona mulungu alemekezeke🙏
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 3 күн бұрын
Uuu! Yaraaah ! Nkhaniyi comrade mwakhala mukutiuza kuti smart mati sigwila tcito, ngati zili zoonadi apapa mcp isadikile mpaka dzisankho angoyamba kupakila cifukwa manyo ndimene amatiuza kuti APM ndi amene akuwina caka cino nde mcp mukudikila can? Kadzipitani ka. Comrade ngati muli inu mwapanga izi basi chimenecho muchifinye choncho cisagwilenso tchito muli boh mcp ndi makape timanena nthawi zonse💙💙💙💙💙💙💙 bluz boma!
@triphoniasimbota116
@triphoniasimbota116 2 күн бұрын
Eh eh 😂😂😂😂🙌 koma politics is really a dirty game
@PatrictGauti
@PatrictGauti 3 күн бұрын
Comrled umakwana usazafe uzangosowa coz umatipatsa nkhani zabwino kwambir❤😅
@YohaneMabutao
@YohaneMabutao 3 күн бұрын
Kuphulitsa zithupsa a comrade😂🎉🎉
@joebonface4443
@joebonface4443 3 күн бұрын
If it's true then Malawians have all reasons to celebrate. Koma pajasotu anthu anayimba nthungululu koma munthu asanafe.😢
@AliceMzumara-ci3fu
@AliceMzumara-ci3fu 18 сағат бұрын
🤣 🤣 🤣 🤣 Koma kumalawi nkokoma
@patriciamkupasha5247
@patriciamkupasha5247 17 сағат бұрын
😂😂😂😂😅🎉🎉🎉kwavuta Ntanyuwa sakugawa masweet😂😂😂😂
@StelliaKachaminga
@StelliaKachaminga 3 күн бұрын
Love god is good all the time
@worldnewschannel973
@worldnewschannel973 3 күн бұрын
Ayimitsa chifukwa chakuti amapanga analyze data ya ma new registration a NRB kuti alipo angati chifukwa ndi okhawo omwe Akuyenela kulembetsa mu supplementary exercise.. Are working on these issues kuti okhawo omwe alembetsa mukawundula wa NRB miyezi yapitayi alembetse ku MEC..
@RosinaPatel
@RosinaPatel 3 күн бұрын
Viva comrade
@LucyKulemeka
@LucyKulemeka Күн бұрын
Mulungu wakana kuti a Malawi apitirire kuzunzika. To God be the glory 🙏
@Target-xy9wr
@Target-xy9wr 19 сағат бұрын
More fire
@Alfanmoseka
@Alfanmoseka 3 күн бұрын
🎉
@BravoGamah-n2t
@BravoGamah-n2t 3 күн бұрын
😂😂😂 kumalawi ndikokoma
@giftkapitobanda8296
@giftkapitobanda8296 3 күн бұрын
ndiseke mwaufulu 🤣😂😂😂🤣🤣😋
@PaulDaka-dc3re
@PaulDaka-dc3re 3 күн бұрын
Sure!!!!!!😮😮😮😮
@NEDGIFT-p5t
@NEDGIFT-p5t 3 күн бұрын
Chithupsha chaganduka kkkkk😊
@HajrahAllan
@HajrahAllan 3 күн бұрын
Nyimboyi nditumizileni Mr akunama eeeeeeee akunama
@favourmvula6435
@favourmvula6435 3 күн бұрын
❤❤❤❤
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 3 күн бұрын
Nyengo yoongola mafupa😅😅😅😅😅😅...koma takhalira mpeni amalawi!
@Steven-q4u
@Steven-q4u 3 күн бұрын
Comrade Ntanyiwa muziyamba mwafufuza bwino bwino musanayambe kulalikira unthenga .MCP ndiyo chenjera ifuna ikuo ikuoneni Inu antanyiwa sinaone Kuti azipani zotsutsa zalemba chikalata ku MEC ndi ku NRB ndi Plano iyo antanyiwa anzanu. Nanunso ku bwereza bwereza nkhani .nkhani iyo mwayinena dzulo !!!
@PeterMwakihana
@PeterMwakihana 3 күн бұрын
😅😅😅😅😅❤❤❤❤ Thank God kkkkkkkk. Awachita bwino kwambili anthu woyyipa awa
@frankkaipa8925
@frankkaipa8925 3 күн бұрын
Mcp ndale samatha ali ndi ndale zamakezana
@HajrahAllan
@HajrahAllan 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@mphatsomakande3344
@mphatsomakande3344 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂. Akuti "ndine galu?"
@dreetosh8502
@dreetosh8502 3 күн бұрын
We need to have better Malawi, hopefully we're going to join Africa Bricks for people's development ❤🎉
@NEDGIFT-p5t
@NEDGIFT-p5t 3 күн бұрын
❤❤❤❤😂
@KelvenNakhalare
@KelvenNakhalare Күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 Koma ase iwe ndi galu kkkkkkkkkk
@eunicesaiti
@eunicesaiti 3 күн бұрын
Welcome back Mr Ntanyiwa. 😂😂😂😂😂
@LameckNgwangwa-g3p
@LameckNgwangwa-g3p 2 күн бұрын
Pangolin wathu uyuu more fire fada
@chikondikandulu7052
@chikondikandulu7052 2 күн бұрын
Simene kulili☀☀☀
@BrianKzn-t3d
@BrianKzn-t3d 3 күн бұрын
😂😂❤❤❤koma iweyo 🎉
@JerrySaliwa
@JerrySaliwa 3 күн бұрын
😅😅😅😅
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 3 күн бұрын
Zavuta kuno 😂😂😂
@thomsonnanthupi5668
@thomsonnanthupi5668 Күн бұрын
Pena ntanyiwa sindimamukhulupilira ...mwina times ikanalengeza
@AcctyhBuno
@AcctyhBuno 3 күн бұрын
Musasekekele iyi ndipulani muona zosatila zake akufuna apepekese osusa anthuwatu asunga zonese alibazo musapepele
@PatrickMaster-m3i
@PatrickMaster-m3i 3 күн бұрын
IZI ZILIBE UMBONI, CHONCHO AZIPANI ZOTSUTSA MUSAMVELE NKHANI IKHALE YOMWEIJA YOTI SMATIMATIC ICHOKE BASI WHETHER DATA ILIPO OR MULIBE
@IdrissahKampango
@IdrissahKampango 2 күн бұрын
Fire dada mtanyiwa
@daviechannel8603
@daviechannel8603 3 күн бұрын
Ndipo inu akufuna kuba inu nanu simuziwa zinazii aaa
@LinlyMsumba
@LinlyMsumba 3 күн бұрын
Kkkkk kkkkk koma
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba 3 күн бұрын
Zinamizanani, you think it's easy, yasowa kkkkkkkkkk
@IbrahimWilliam-s8i
@IbrahimWilliam-s8i 3 күн бұрын
zawamvutadi koma awona nyekwe
@ChikuCharlie-r9u
@ChikuCharlie-r9u 3 күн бұрын
Koma ngati zili choncho kumwamba kudyele nyama
@SidreckRashid
@SidreckRashid 3 күн бұрын
Game plan..imeneyo iwee osazikhulupilira bvimbalangondo ibvi
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 3 күн бұрын
Izi aMalawi tisazikhulupile kwambiri chifukwa tilibe umboni weni weni woti machine amenewa asiyadi kugwila ntchito 😢😢😢😢 ndife a Tomas didimu tikhulupilila tikawona akuwelemga pamanja
@MoosaBanda-su3zp
@MoosaBanda-su3zp 3 күн бұрын
Apa kupanga zoti mavoti azawelengedwe manyo basi , apa a mcp ndinyambo imeneyi
@EstherLuka-m4r
@EstherLuka-m4r Күн бұрын
There is a living God in heaven. Lisamuke boma la nkhaza ili eishhhh. Kuendesa dziko amaterooo? Eeeishhhh
@ElubyBanda
@ElubyBanda 3 күн бұрын
Thus wow
@DippedJob
@DippedJob 2 күн бұрын
Koma ndaseka kkkkkkk
@JoelTchuma-g3s
@JoelTchuma-g3s 3 күн бұрын
Zoona palibe?
@JuliaBonongwe
@JuliaBonongwe 3 күн бұрын
Mmmmm samalani machine ndi amodzi okha? Wina apusati apa owoh
@InessSalimu
@InessSalimu 12 сағат бұрын
Amalawi tidzipephela kwambili MULUNGU ndiwankulu
@KelvenNakhalare
@KelvenNakhalare Күн бұрын
Tikumva bwino KWAMBIRI mthupimu pomva Kut smatmatik yapoila
@EnetChiomba
@EnetChiomba Күн бұрын
😂😂😂😂 ehee abale zomwe zikuchitika mdziko la malawi za ma drama sure
@JamiraJamirashaime
@JamiraJamirashaime 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS 3 күн бұрын
Koma ntanyiwa wandiseketsa or dzithupya andiphulitsazi zikuwawa kkkk ntayiwa umatha
@WilsonChisoti-dz6vs
@WilsonChisoti-dz6vs 3 күн бұрын
The truth shall prevail
@StevenLihaka-l6j
@StevenLihaka-l6j 3 күн бұрын
chitupsa kkkkk
@JohnMaibeckMeaningnice
@JohnMaibeckMeaningnice Күн бұрын
Ine john maibeck kuno ku mocambiki ndikut mbambande comred
@EvaChinkhata
@EvaChinkhata 2 күн бұрын
Kkkkk zilibo chakwera azingolongeza basi shawuli yako yomweyo
@GeraldBonongwe
@GeraldBonongwe 3 күн бұрын
Kkkkkk😂😂
@SiprianoAndrea
@SiprianoAndrea 4 сағат бұрын
Mwayitha azibambo, mwayigwila ntchito
@MustaphaCassim-t7g
@MustaphaCassim-t7g 3 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@enockkumbande5165
@enockkumbande5165 3 күн бұрын
Ndizoona pano akufuna kugwilitsa ntchito mphavu kuzela kwa asilikali
@DAGAMAaaaa
@DAGAMAaaaa 3 күн бұрын
Mtanyiwa osamukhulupilila palibe umboni, mcp ikumenya pusi pusi tizalila a malawi mcp ikulowaso boma
@ThomasJohn-j8x
@ThomasJohn-j8x 3 күн бұрын
Koma chimwendo amati olo titaphatikizana zipani 15 sitingawine bwanji pamenepo
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 3 күн бұрын
Mulungu si James bwana amapanga njira popanda njira, Chilima mzimu wanu udziusa mumtendere, pitirizani kutimenyera nkhondo kumandako Biyeni
@PaulRice-n1f
@PaulRice-n1f 3 күн бұрын
Ukhala ntchocho MCP yatha bs
@GeorgeSibale-k3f
@GeorgeSibale-k3f 2 күн бұрын
I see
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 күн бұрын
Pls azipani za udf dpp Aford utm lef musakhulupilile muonesese bwino chonde
@thandomaseko4345
@thandomaseko4345 3 күн бұрын
Kkkkk
@kazembewailesi
@kazembewailesi 3 күн бұрын
Zili bwino kwambiri!!! Ndipo ndakondwa zedi.
@GregoryMchinyira
@GregoryMchinyira 3 күн бұрын
i dont think so
@GiftSichali-z7l
@GiftSichali-z7l 11 сағат бұрын
Tikumva booo ife comrafe mtanyiwa
@GiftMuyungu
@GiftMuyungu 3 күн бұрын
Palibeso plan zinangodzazanamo mbuli zokhazokha mu mcp
@MrsnKholowa
@MrsnKholowa 3 күн бұрын
Izi km zufunika, osazikhulupilila kwambiri.... Akhoza kt a MCP wo akungofuna kutimata mbula mmaso, while iwowo akudziwq chochita
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 3 күн бұрын
Koma Zowona mene anapangila zokufa zija iziso ndichocho pofunika kufufuza bwino chonde
@StephanoEbele
@StephanoEbele 3 күн бұрын
Ngati zachitikadi,,dzina la Yehova lilemekezedwe lero ndi kunthawi zonse.bola asakhale akutipusitsa
@wadyazakealibemulandu
@wadyazakealibemulandu 3 күн бұрын
Zaboza is winayo bwanji sakuveka
@royaltysales-p7z
@royaltysales-p7z 3 күн бұрын
Antanyiwa mumakwana ndipo ndimava Nanu kukoma
@WatsonMsukwa-k6d
@WatsonMsukwa-k6d 3 күн бұрын
Ok
@ismailabbah531
@ismailabbah531 2 күн бұрын
Zawavuta osati masewera
Ntanyiwa Ndi Wabodza - Lebium Mvula
12:07
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 10 М.
REAL or FAKE? #beatbox #tiktok
01:03
BeatboxJCOP
Рет қаралды 18 МЛН
Don’t Choose The Wrong Box 😱
00:41
Topper Guild
Рет қаралды 62 МЛН
Asilikali anaukira Boma la Kenneth Kaunda; Chinavuta ndi chani
5:18
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 11 М.
COMRADE MTANYIWA PA LIMPOPO FM NKHANGA ZAWONA ( KUSWAKUSWA)
16:20
Dreams Media MW
Рет қаралды 18 М.
Jaarafsluiting saam met Piet Smit
1:14:17
Woord Sonder Grense Mannebediening
Рет қаралды 7 М.