Inetu part ya junior ndi mulelemba ndimangothamangitsa, palibe chomwe amandiwaza.
@abdullahmalikikuwini586810 күн бұрын
Ndipo akumabhowa hvy kkkkkk
@AliceThom-v1t9 күн бұрын
ndipo kwambiri tu
@husseinosman67978 күн бұрын
ife tikufuna achiphwanya
@AnajoiceSozinho8 күн бұрын
Olo inenso
@Bobby265i4k7 күн бұрын
mr shokoshoko amandiwaza apaseni more time i will be back watching from south africa
@CosmasChikwindi10 күн бұрын
Mercy ndihuletu ngakhale ku mfumukazi wapasidwa mimba ndinsing'anga😂😂😂
@nana-aka9ka10 күн бұрын
Ku mfumukazi ndi namoyo, combination yawo mumva kuti mercy ndi namoyo ndi matwinzi,,,
@EmmanuelBenjamin-p2y8 күн бұрын
Mulelemba ndi nzake mmmh ayi 😂😂😂
@rosebotoman8208 күн бұрын
Ajunior izizi szawo kwenikweni and ma scene amulelemba muzwapanga shorten
@EvenesRuchard6 күн бұрын
Sunaulule 😂😂munyanyuwa pamenepo
@franciscoduartie576210 күн бұрын
Part ya mlelemba ndi Junior very unnecessarily
@AliceThom-v1t9 күн бұрын
Ndipo part imeneyi atabweretsapo chiphwanya ndi sasoka bola
@DiolinBj10 күн бұрын
A junior NDI mulelemba mukukhalitsa komaso simukumabebetsa , muchepetse thawi ikumakula
@phillipzuze10 күн бұрын
Mlelemba actor wabwino.. vuto mumamusiya mpaka 5 minutes pa scene imodzii... mumalakwisa.. muzimvako za anthu... pali zoti mukomze ngati muli ready kumvetsera, tel me...
@VictoriaPhiri-yt9wm10 күн бұрын
Inenso nde ayiii ayi ndithu znatu zimandowa zamlele Zina zambiri akulakwitsa ndimawu ayiii saali m act yabwino inu nde nkumamueiyanso 5 minutes Ngati akukhozapo ayy
@offanyirenda10 күн бұрын
Mercy nchifukwa chake watenga mimba Kwa sing'anga mu mfumukazi. 🤣🤣🤣🤣🤣
@RoseAbba-ik9tz10 күн бұрын
Kkkkk kuchenjeresa
@richardtembo595710 күн бұрын
A junior apezeleni china chochita
@FrankJoshua-zr9pw7 күн бұрын
Kkkkk mzanu akusamalilamo banja lake umu abale ..achoke azidya chani?
@SimbiBrian-q2r8 күн бұрын
Mmmm nice guys❤❤❤
@AishahAli-v7h8 күн бұрын
Go deeper Mrs Mdyangu
@DiolinBj10 күн бұрын
Ma Ju osayesera kubwelerana NDI mwana wa mkango , bambo a Ju amakukondani
@KelvinChingwalu-s3t11 күн бұрын
Tiffany uli ndi chibwana back kwa mwana wa mkango😮😮😮 bambo ajuu akazabwera azayakhula chizungu 😂
@JamesChilinda8 күн бұрын
Sasoka ndi chiphyanya tawasowa..tawabwereseni plz
@AnajoiceSozinho7 күн бұрын
Yunis ndiwamwano
@LamekiSamson11 күн бұрын
First to coment
@ChapwetekaChauluka11 күн бұрын
Kkkkk a Shokoshoko ndi achitsirudi ndithu
@Mjnyirenda10 күн бұрын
Ma junior usabalalike msanga mdikile kaye mwamuna wako amakukonda Sasoka mpewe kaye mwana wamkango iyeyo ndimunthu wamtundu wanji ofuna kutenga mkazi wa nzake ali kupolice
@twistsosha95479 күн бұрын
Ine nde mese amandiwaza
@CollinsLingu8 күн бұрын
Koma mercy 😂😂
@portianahkalonga10 күн бұрын
A junior achoke😂
@EnockNsinja9 күн бұрын
Koma chonde muzitipasako option ya download kuti ngati tilibe bundle tiziwonera
@MosesDicostar10 күн бұрын
Junior anafupika bwino ngat wazisuzo koma ayii ndthu
@ManuelMalunga-o6b8 күн бұрын
Junior ndidobadoba uyu
@VeronicaKanyenga11 күн бұрын
A junior acting imawavuta km
@AhmedIshu-v9w11 күн бұрын
kwambiri
@Patrick-kambala10 күн бұрын
That's what I wanted to say,he doesn't make it real 😅
@gracedizelow391610 күн бұрын
True
@gloriaazele123710 күн бұрын
Ndipo sabebetsa this is true
@ChisomoKapanda-jg2uf10 күн бұрын
Ndipo samandisangalatsa
@emmanuelmaomba51639 күн бұрын
Junior acting mbola
@MlengaFrank10 күн бұрын
Mayi dyangu ndi kadzi Gani zimatengesana 😂😂😂😂😂
@LovemoreMunlo-x2p10 күн бұрын
Mlelemba ndi makina😂
@SimediPhili10 күн бұрын
Man ju sakuitha
@franciscoduartie576210 күн бұрын
Mercy wapita kukayipempha😂😂😂
@TsholofeloGraciouskabasia10 күн бұрын
Juuuuu tulukani palimbe zomwe mukupanga umu
@moseskavalo330410 күн бұрын
Mnyanyiwa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@portianahkalonga10 күн бұрын
Akazi a dyangu🔥🔥
@gloriaazele123710 күн бұрын
Tiffany ndi mwana wa mkango ma reback kunooo 😂😂😂😂 next week kuli ntchito
@YankhoKhungwa-d1f10 күн бұрын
Junior nde chomwe amafuna kulankhula sadziwatu,amangozikolakola always
@franksamalani374910 күн бұрын
Ma ju Ni kangenge mu mdyangu onse
@josephmawaya74088 күн бұрын
Ndikuwona ngati several akufuna alithese, chifukwa apa achosamo kale anthu 4, chiphwanya, seasonal,queen and mayi sasoka, week Yamaha Michigan's ena krnako basi
@HaleemahYusufu10 күн бұрын
Mayi dyangu❤
@dominicmphepo-jk8lk10 күн бұрын
Big up shokoshoko ndi amuna ochepa omwe tingakwanise kupewa zimenezi