MFUMUKAZI | 31 JULY 2024 pa Times TV

  Рет қаралды 60,495

MALAWI 265

MALAWI 265

Күн бұрын

Entertainment

Пікірлер: 195
@jumawasi9038
@jumawasi9038 2 ай бұрын
Am number 1247 to watch within one hour🤗
@kinggomani2676
@kinggomani2676 2 ай бұрын
Anthu alipachangu
@HappyAnord
@HappyAnord 2 ай бұрын
Km ching'aning'ani umakwana ndakupasa ulemu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@WilfredMapelera-tw7fs
@WilfredMapelera-tw7fs 2 ай бұрын
Koma padela iweyo anakonza, ati "tiziuzanapo zoonatu apa chilichonse chikhoza kuchitika"😂😂😂😂😂
@HappyAnord
@HappyAnord 2 ай бұрын
Chiphanya iweyo umatha ❤❤❤❤
@DaguDere
@DaguDere 2 ай бұрын
🔥🔥Uyu Danken adakoza kusogoloku afusila nkadz wabombo ake uyu 😂
@PeterBendeka
@PeterBendeka 2 ай бұрын
Padera ndiyekaya kuterlkosukulumulibe zamanyazi mmakwana mrs padera
@SquareBoma-vl2rj
@SquareBoma-vl2rj 2 ай бұрын
Kkkkkkkk komatu mumuphesa Mzunguyu Mai Padela
@RhodaMwanza-o5b
@RhodaMwanza-o5b 2 ай бұрын
Kkkkkkk apadera mutikomora tu kuseka😅😅😅😅
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx 2 ай бұрын
Achimwene tabwelani tinenekane ndekuti chani 😂😂😂
@Boleflats
@Boleflats 2 ай бұрын
Tilakhilane
@IshmaelSaizi-pt5bd
@IshmaelSaizi-pt5bd 2 ай бұрын
Ndangoononga chizungu changa kkkkkkk koma iwe aching,axy
@geofreydzinyemba6107
@geofreydzinyemba6107 2 ай бұрын
Kkkkkk Mr padela inuyo mumaganiza bwanji pa ndalamayo kkkk koma Mr padela inuyo anakonza
@alinafesawasawa3905
@alinafesawasawa3905 2 ай бұрын
I love ❤️ you guys 😂😂. Imakhala ili love ❤️ 😅🥳
@KelvinNthenda
@KelvinNthenda 2 ай бұрын
Watching from Malawi Vg misomali
@MphatsoSiwango-io4gr
@MphatsoSiwango-io4gr 2 ай бұрын
Koma chuzungu ndichofunikadi
@RoseChiphiri-ts8jx
@RoseChiphiri-ts8jx 2 ай бұрын
Ati ndangoononga chizungu changa 😂 koma chiphaliwari chizungu chake chachizungulilecho mpaka kuchidandaula 😂😂😂😂
@daniellchinjati2557
@daniellchinjati2557 2 ай бұрын
Nafuneya ndi mlamu wakeyu mumandiwaza koooopysa🎉
@daniellchinjati2557
@daniellchinjati2557 2 ай бұрын
Pali xool inayake kwa munthu oxindikila
@GiftMwalabu-l3g
@GiftMwalabu-l3g 2 ай бұрын
Watching from Nigeria
@fletchermoyo4223
@fletchermoyo4223 2 ай бұрын
padera you r the champion kkkkk
@MathewsMustaph
@MathewsMustaph 2 ай бұрын
Kkkkkk Padela wayaka Moto wampinda mzungu actor wabwino
@Iblahim-t9l
@Iblahim-t9l 2 ай бұрын
Mumaita ❤❤❤❤
@FreeMan-xs1fq
@FreeMan-xs1fq 2 ай бұрын
😂😂😂like father like son Maliro ndi Duncan 🎉 Duncan kusilira stepmom ake
@DrolieDongowa
@DrolieDongowa 2 ай бұрын
Kkkkkkkkk imakhala ili love 😂😂😂😂😂😂
@CliffJoeKacheche
@CliffJoeKacheche 2 ай бұрын
Nice next kuchema chitsime wamuiwala manager solomoni eti akamuswatu 😂😂😂😂😂😂😂
@MosesMwengo-ku1lv
@MosesMwengo-ku1lv 2 ай бұрын
❤❤ kulankhula lankhula ,kulongolola....kulathula kkkkkkk sister wa kalanka... 🔥
@promiseMtambo
@promiseMtambo 2 ай бұрын
Ati kulethura 😂😂😂 mlongo Wa karanka
@Jacular
@Jacular 2 ай бұрын
Uyuyi ndi katundu Mwene 😅😹
@PatrickMailos-j6u
@PatrickMailos-j6u 2 ай бұрын
Giring'ande your number one
@GibhoMaunde
@GibhoMaunde 2 ай бұрын
Umburi ndimatenda ndaonela mr padera😂😂😂😂
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 2 ай бұрын
Kkkkkkk eeeeh padela guys mmmmh apa pokha wandiwaza
@Jacobkathumba
@Jacobkathumba 2 ай бұрын
Padera akuti uzimuza zona cz pavutapo pano😅😅
@benjaminphiri4423
@benjaminphiri4423 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@GraciamHarrisonthom
@GraciamHarrisonthom 2 ай бұрын
Ndipo akanaphwanya mutu😂😂😂😂
@sharrifgwape7169
@sharrifgwape7169 2 ай бұрын
Anaga mukuwaziwa kale kuti achisime ndi aphuma chomawudzira nkhani ngati imeneyo ndichani
@AlickJota
@AlickJota 2 ай бұрын
Padela wanyumwa kkkkkkkk
@WEDSONLICKSON-cc2ey
@WEDSONLICKSON-cc2ey 2 ай бұрын
Amvekere ndalama zonsez ntchito yake ya m’nyumba ? Kkkkkkk padera anamva kuwawa
@DalitsoMichongwe
@DalitsoMichongwe 2 ай бұрын
Padela chingende champeta😂😂😂😂
@fatimaamidu3967
@fatimaamidu3967 2 ай бұрын
Kalamka,s sister kkkkkk
@MaganizoBanda
@MaganizoBanda 2 ай бұрын
Kkkk padera ati ndizizuze😂😂 mumatha gyz
@TriciaMakolija
@TriciaMakolija 2 ай бұрын
Kkkkk iyo imakhala love kapena chikondi
@GarciaTheresa-t1o
@GarciaTheresa-t1o Ай бұрын
Clark Laura Walker Kimberly Davis Kenneth
@gloriaazele1237
@gloriaazele1237 Ай бұрын
Nkhani ya ndalama aliyese azidzwa😂😂😂😂
@TadalaChilichokha
@TadalaChilichokha Ай бұрын
Ndangoono 3:59 nga chizungu changa
@JonesMalingaMalinga-nr6jc
@JonesMalingaMalinga-nr6jc 2 ай бұрын
Malawian 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@SamiahNyaulanda
@SamiahNyaulanda 2 ай бұрын
padela koma ayi fenkisi 😂
@YankhoBaysome-m2b
@YankhoBaysome-m2b 2 ай бұрын
Padela wadabwa ndalama zachuluka 😂😂😂😂😂 English itamupeta
@EvelynMasamba
@EvelynMasamba 2 ай бұрын
🤣🤣🤣koma danken akuti akuoneka kuti ali nditsogolo😂😂
@DavieViniciusjr
@DavieViniciusjr 2 ай бұрын
School ndyofunika padera kuchenjera kwatha
@promiseMtambo
@promiseMtambo 2 ай бұрын
Koma Duncan iiiiii 😂😂😂😂😂😂
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 2 ай бұрын
Kkkk kod maliro wasamba pat??? Mpaka kukwatila kkkk
@nana-aka9ka
@nana-aka9ka 2 ай бұрын
Chizungu chaonongedwa ulere... ntchalichi siimangidwa😂😂😂
@JuliusKasanga-o4y
@JuliusKasanga-o4y 28 күн бұрын
Kkk chizungu padera😂😂
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 2 ай бұрын
ATI ndangoononga chizungu changa😅😅😅😅😅😅😅😅
@hamzarmarch
@hamzarmarch 2 ай бұрын
padera the greater
@watipasomzungu9911
@watipasomzungu9911 2 ай бұрын
Koma Maliro wadzitenga kuti zogula Coca-Cola? Maliro timamdziwa ife ndi woshota nthawi zonse. 😅😅
@AfickDaud
@AfickDaud 2 ай бұрын
Come!!come!! Feel free Come!! Kkkk atero mayi padera😂
@FasiriSaidi
@FasiriSaidi 2 ай бұрын
Padel kkkkk ntchito ya manja mpaka ndalama zonsezi
@KinosiJokole-th6zl
@KinosiJokole-th6zl 2 ай бұрын
Kkkkk padela
@Littlefair7
@Littlefair7 2 ай бұрын
Eeee koma Padera ndi katundu guys 😂😂😂😂 Replacement ya Izeki yapezeka. Komanso Maliro ndi mwana wake Duncan eeee ndi zitsiru kwambiri😂😂😂😂
@NathanielSivalingam
@NathanielSivalingam 2 ай бұрын
Maliro Lero mpaka fanta😂
@Mamaza-tr6zi
@Mamaza-tr6zi 2 ай бұрын
At ndangoononga chizungu changa😅
@shafiekbastra1459
@shafiekbastra1459 2 ай бұрын
Unena bwinotu ndalama yake iti yomwe angakupatse ndalama yonseyi😅
@gloriaazele1237
@gloriaazele1237 Ай бұрын
Padera wakalipira nzungu😂😂😂
@gloriaazele1237
@gloriaazele1237 Ай бұрын
Ndalama yapatsidwa apaaa siingakhale ya ntchito ya manja😂😂😂😂😂😂 Padera
@HopeKeyz-pr5pw
@HopeKeyz-pr5pw 2 ай бұрын
Koma padela adakonza🤣🤣🤣👍
@alfredbatumeyo9191
@alfredbatumeyo9191 2 ай бұрын
Kkkkkkkk katundu wa bambo ako😂😂😂
@gloriaazele1237
@gloriaazele1237 Ай бұрын
Wamuyankhula Chichewa 😂😂😂😂 ati bambo mufuna chani kwenkwen?
@MuhammadWitiness-u3h
@MuhammadWitiness-u3h 2 ай бұрын
😂😂❤ dzilikotu ziliko
@AdamsonPhelan-u1g
@AdamsonPhelan-u1g 2 ай бұрын
Mumakwanila❤❤
@jeremiahmalikebu2393
@jeremiahmalikebu2393 2 ай бұрын
mpaka masiten ali ndi tsogolo labwino kkkkk, Duncan ulibe ulemu😂😂😂
@MaryPiya-ns5un
@MaryPiya-ns5un 2 ай бұрын
At Kodi inunso muli ndimasoso eti? 😂😂😂
@hawahsamm9105
@hawahsamm9105 2 ай бұрын
Padera wandikomora nkuseka😂😂
@ShaffiMustafah-fz1hy
@ShaffiMustafah-fz1hy 2 ай бұрын
Malilo number one 😂😂😂😂
@MrsMtira-f2u
@MrsMtira-f2u 2 ай бұрын
Kkkkkkkk mumatimvetsa kuloma guys
@stevezulu2108
@stevezulu2108 2 ай бұрын
Mwenye Samamanga ma up stayers ku Malawi..aaaaa😅
@MrsMtira-f2u
@MrsMtira-f2u 2 ай бұрын
Kkkkk mumatimvetsa kukoma guys
@MavutoJackson
@MavutoJackson 2 ай бұрын
Padela 😂😂
@lazaluskelias
@lazaluskelias 2 ай бұрын
KKKKK A PADELA asazunzike ndi chizungu
@Alefa-vd7ww
@Alefa-vd7ww 2 ай бұрын
😂😂😂😂Muzikutumula chizungu muzisuzi
@happychimwemwe-1805
@happychimwemwe-1805 2 ай бұрын
Ndalama yonseyi ikakhale ntchito ya manja
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 2 ай бұрын
Ndiye abwana mpaka kuchoka mtawuni kuwona mai padera 😂😂😂 ayi mai padera nenani bwino
@McDonaldLinyama
@McDonaldLinyama 2 ай бұрын
ETI eti mpaka bwana angadzaone wantchito wake (Mkadzi wa mwini) Ku nyumba kwake
@peternashyo9850
@peternashyo9850 2 ай бұрын
Padela ndi 1, mumatha man
@GraciamHarrisonthom
@GraciamHarrisonthom 2 ай бұрын
Duvu duvu kulethula nafuneya kuno kkkkkkkk
@yassinrashid7012
@yassinrashid7012 2 ай бұрын
Imatokhala love kapena chikondi😂
@LofraBywell
@LofraBywell 2 ай бұрын
Kkkkkkkk this people mmm ❤❤❤
@stevezulu2108
@stevezulu2108 2 ай бұрын
Mwenye ndi munthu wakuda chabe musati mzungu😅😅😅
@EphiehkariPhiri
@EphiehkariPhiri 2 ай бұрын
Mwana wa nyakwawa wa mfumu Duncan
@mazyjohn-hd7dh
@mazyjohn-hd7dh 2 ай бұрын
😂😂😂 padera waziona
@gloriaazele1237
@gloriaazele1237 Ай бұрын
Padera kunooo😂😂😂😂
@CasimJagaja
@CasimJagaja 2 ай бұрын
Kkkkk koma chiphwaya ndizaake sasoka sadzatheka
@felistarmgemezulu5823
@felistarmgemezulu5823 2 ай бұрын
Mwana wa malilo nyc
@Imranasedi-zw7cg
@Imranasedi-zw7cg 2 ай бұрын
Padera 😂😂😂😂😂
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 2 ай бұрын
Kkkkkk km Danken anakhoza
@gloriaazele1237
@gloriaazele1237 Ай бұрын
Padera safuna kudzizuza😂😂😂
@leonardkaumphawi2858
@leonardkaumphawi2858 2 ай бұрын
Koma mulamu wanafuneya umandiwaza
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 ай бұрын
Darken 😂😂😂😂watichani?
@MacksonTchovaNkwinika
@MacksonTchovaNkwinika 2 ай бұрын
Kkkkkk ching'axy ndikatundu eich kma ya
@ChifundoJeffrey
@ChifundoJeffrey 2 ай бұрын
Imakhala ili love kapena chikondi 😂😂😂😂
@LovenessAdrian
@LovenessAdrian 2 ай бұрын
Imakhala love kapena chikondi
@alinafesawasawa3905
@alinafesawasawa3905 2 ай бұрын
Tiyeni Tiyeni Tiyeni 😂🥳🥳
@PrinceSefasi
@PrinceSefasi 2 ай бұрын
Dunken waionamo mwa mayi ake 😂😂
@chiletsobisweck5007
@chiletsobisweck5007 2 ай бұрын
Mpaka zafika pa mzungu
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 2 ай бұрын
Kkkkk km padera
@FrankHaruni
@FrankHaruni 2 ай бұрын
Padela sakulakwisa kumalawi ndikwachichewa chidzungu kusukulu iye ayakhule chichewa sikufuna kukhala kumalawi
@JohnTMagaletaMagaleta
@JohnTMagaletaMagaleta 2 ай бұрын
Mpaka agwilanapo ufiti 😂😂😂😂😂
@GeorgeMtonga-c9k
@GeorgeMtonga-c9k 2 ай бұрын
Chisime 😂😂 always he gate a knife 🔪
@InnocentNyondo-bc7xx
@InnocentNyondo-bc7xx 2 ай бұрын
Chisime the DC AkA Dangerous Child kkkkkkk
Tikuferanji 21 April 2018
28:33
Edson Gunsalu
Рет қаралды 344 М.
Mfumukazi - 2 October 2024
29:00
Times 360 Malawi
Рет қаралды 50 М.
How I Turned a Lolipop Into A New One 🤯🍭
00:19
Wian
Рет қаралды 11 МЛН
Não sabe esconder Comida
00:20
DUDU e CAROL
Рет қаралды 36 МЛН
龟兔赛跑:好可爱的小乌龟#short #angel #clown
01:00
Super Beauty team
Рет қаралды 67 МЛН
mfumukazi
27:18
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 11 М.
MFUMUKAZI - 24  JULY  2024 pa TIMES TV
27:54
MALAWI 265
Рет қаралды 1 М.
MITEKETE 21 OCTOBER 2024 PA TIMES TV
22:42
MALAWI 265
Рет қаралды 1,9 М.
CYCLONE FREDDY FUNDRAISING DRAMA #malawi
1:31:45
Kanema Online
Рет қаралды 506 М.
Ana Amasiye
26:33
Oleku Phirie
Рет қаралды 17 М.
Muzionetsetsa, Kado: Episode 3
33:19
Jabroma Shots
Рет қаралды 100 М.
How I Turned a Lolipop Into A New One 🤯🍭
00:19
Wian
Рет қаралды 11 МЛН