GULULU NDI ZONKE :- Tayidziwa Bangwe

  Рет қаралды 35,728

Mikozi Network

Mikozi Network

Күн бұрын

Пікірлер
@bmbboymstyles5894
@bmbboymstyles5894 Ай бұрын
Amene amafila bingala for real ndiangati apa🤣🤣🤣🤣 zooonaa
@amtondogman
@amtondogman Ай бұрын
Bingala fans let's gather here😂😂😂
@KumwendahLyson-t6u
@KumwendahLyson-t6u Ай бұрын
Ndipo chi bingala sichikufuna zachisawawa
@blessingskadewere2070
@blessingskadewere2070 Ай бұрын
Bingala ndi dolo😂😂
@wahabimkumbira7197
@wahabimkumbira7197 Ай бұрын
Bingala aise For Real 😅😅
@CollingsGondwe
@CollingsGondwe Ай бұрын
Tangomgulireni 4n Bingala mx zaa gululu samaziziwa thus wi 😅😅😅😅😂😂 # Ndaseka for real
@SylvesterJambo-m8n
@SylvesterJambo-m8n Ай бұрын
Bingala 😂😂😂 eeeeeee ndiwa security 😊😊
@JohnjrnPhiri-uw2op
@JohnjrnPhiri-uw2op Ай бұрын
And i quote "Nanuso musamangoyakhulatu Zonke ndi wanthu''😂😂😂😂Bingala ase
@MALISHER-no1qt
@MALISHER-no1qt Ай бұрын
We all need a friend like him
@EuniceKanthewa
@EuniceKanthewa 3 күн бұрын
The guy is not real , no need for a friend like him he is fake if he was real he wouldn't have taken those guys to zonke
@alinunemulebe8922
@alinunemulebe8922 Ай бұрын
Kuchokera komwe kunali zonke kutenga two guys ikhale ngati ikuchokera kwina kenako nkubwerera pamene panali zonke akakhale ngat akuthawa kma kothawra kunalibe njira kkkkkk NYC ......
@chebuaarts
@chebuaarts Ай бұрын
wayiwonaeee!
@JamieKili
@JamieKili Ай бұрын
😂😂😂 zonke thawa kwabwera a gululu😂😂😂😂
@SydneyMakwiti-mp3im
@SydneyMakwiti-mp3im Ай бұрын
Bingala akufunika show yake yake mbukaman big up
@JulLah-gq8pi
@JulLah-gq8pi Ай бұрын
Kod mesa mabwelala limoz 😅😅chnavutaso ndchan kod
@EarlyCelebration
@EarlyCelebration Ай бұрын
Chaba anawa
@blessingskadewere2070
@blessingskadewere2070 Ай бұрын
Bingala aaah
@chisomomakiyi-os9bc
@chisomomakiyi-os9bc Ай бұрын
Abingala ati awabhowa ndimafikidwe 😊🤗
@StevenJalifu
@StevenJalifu Ай бұрын
Zochita kupangana izi
@PaulChaposa
@PaulChaposa Ай бұрын
😂😂😂😂😂 a bingala ndi class ina ❤ at ndi zoonatu
@Chrispine-jy5zw
@Chrispine-jy5zw Ай бұрын
Bingala simasewera eh! 😂😂😂 akanakuphulisani
@AlexSakalani
@AlexSakalani 28 күн бұрын
😂😂 Alaa kwa mvula ndi kwa ma gangster 😂😂
@PABLOMARCUS8
@PABLOMARCUS8 Ай бұрын
Koma mene anachipopera muja😂😂😂 bingala bangwe ndiyeyooo
@mikeaschimkono1920
@mikeaschimkono1920 Ай бұрын
Bingala aaa 😂 ndibangwe payokha😂
@InnocentCharlesp
@InnocentCharlesp Ай бұрын
Kape uyo akusokosayo ndi wachimidzi sure 😂
@blessingsmunthali9202
@blessingsmunthali9202 Ай бұрын
Koma ma yoh a mu bangwe kkkk 😂😂
@ChifundoThumula
@ChifundoThumula Ай бұрын
Sono ikhala bwanj Gululu akamafika bwno 😂😂😂😂 apapa Sizinakome
@DavisSaukile
@DavisSaukile Ай бұрын
Mmayenda m'bali aphwanga mwakumana nd bingala🔥🔥
@GeoffreyHardson
@GeoffreyHardson Ай бұрын
Ameneyo akufunika Kwa chinsapo kuno mbali za Kwa bwemba azakumane ndi amnzake
@davidmakoza7059
@davidmakoza7059 Ай бұрын
Bingala wangondithera bundle yanga zausilu iyaaa
@Cee_Busy_Mw
@Cee_Busy_Mw Ай бұрын
M'buka man ndiwabho amandiwaza ndiwa humble 🎉🎉 Bingala mwamuwona?😅😅😅
@ScottKeepus-i9i
@ScottKeepus-i9i Ай бұрын
Ambuye olo chiduntu ndpaseni chizaphwela kuno ndimakofi😋🙈🙌
@AgriwhatMW
@AgriwhatMW Ай бұрын
I do not know that .......boy,i like zonke iye ndikukapanga zopusa zakezo,vibe destroyed
@jonathanmaseko6057
@jonathanmaseko6057 Ай бұрын
Bingala akufunika plot coz eeee kava ze boss😂😂😂😂😂
@goodcarbsonly7581
@goodcarbsonly7581 Ай бұрын
😂😂😂
@MercyWaiti
@MercyWaiti 28 күн бұрын
Aaa😂 Koma bingala
@OwenManda-s6p
@OwenManda-s6p Ай бұрын
Kodi nkuluyo phuma bwanj.. Ndiokubatu munthuyo.. Mukut Bangalayo
@joyceloveton6461
@joyceloveton6461 Ай бұрын
Kkkkkkkkkkk ine ndaziwa chifukwa chimene amamuwuza kuti athawe sanali pa bwino zonke
@FledFled-yx2ib
@FledFled-yx2ib Ай бұрын
😂😂 akufunika treatment 😅
@MemoryMagombo-zv2xy
@MemoryMagombo-zv2xy Ай бұрын
Amene mukuti Bingala chani chani bingala chani chani ineso ndingoti bingala chani chani yo😂
@VirginiaKhumbo
@VirginiaKhumbo Ай бұрын
Uyu wandinthera bundle ndisaname
@DrugDzodzo
@DrugDzodzo Ай бұрын
Mwanayotu akupenga mudziwa kaya
@rome-jaimuphuwa2186
@rome-jaimuphuwa2186 Ай бұрын
The true definition of loyalty🙌🏾🙌🏾 Big up Bingala
@emmceeks
@emmceeks Ай бұрын
Inu muzamenyedwa inu 🤣🤣🤣🤣🤣 Zonked ndi king
@FrankZgambo-lz5hw
@FrankZgambo-lz5hw Ай бұрын
Chamba chakwera kumutu ameneyo si iyeso ameneyo 🤣🤣🤣🤣🤣
@FutureChiyo-mt4yy
@FutureChiyo-mt4yy Ай бұрын
Mwana opusa Mesa yekha wanena kale kuti gululu ndekt akuidziwaka,
@QueenWahera
@QueenWahera Ай бұрын
Chambatu Ichi akufuna. Zonkey ovuta ndi wina
@spazictrl
@spazictrl Ай бұрын
Bingala akufunika award 🤣
@MariaSichali-q1j
@MariaSichali-q1j Ай бұрын
Kodi ngozungulila Mutu🤣🤣🤣🤣
@keithhussein5138
@keithhussein5138 Ай бұрын
Tithaa kumaona ngt comedy ili misala😂😂
@innocentseleman3146
@innocentseleman3146 Ай бұрын
Bingala😂😂😂 Ndi more
@LM-gz5pk
@LM-gz5pk Ай бұрын
Achpewayo ngwachimidz 🤣🤣 mesa wakulisa khan nd iyeyo anthu akuzwa mene anakapezera
@evancenasoro-b2m
@evancenasoro-b2m Ай бұрын
Bingala😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 akut kumaona mafikidwe
@gracejeremiah910
@gracejeremiah910 Ай бұрын
A Bingala Malo mobebetsa abowetsa
@Nyakalua
@Nyakalua Ай бұрын
Zoona
@ChisoKondowe
@ChisoKondowe 2 күн бұрын
Anabowesadi
@khalifajalih1960
@khalifajalih1960 Ай бұрын
Bingala akufunika award😂😂😂
@Abhebhetsi280
@Abhebhetsi280 Ай бұрын
Bingala kuvuta uku ali mchibwenzi koma mwati 😂
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy Ай бұрын
Mkazi ololalo nde mchitsilutu kulola kape
@tuntufye
@tuntufye Ай бұрын
Nchifukwa chake Bingala amanvana kwambiri ndi Khalizima uyu😂😂
@ChiccoChunga
@ChiccoChunga 25 күн бұрын
Ichi ndi chitsiru bwanji aaaaaa
@CharlesChimeta
@CharlesChimeta Ай бұрын
Vuto LA khunyu ndilimenelo Bingala muvaye naye kuchikuda
@OWENKAPONDA-w9v
@OWENKAPONDA-w9v Ай бұрын
Bingala Eeeee🙌
@Chinsinsi_Gwaza
@Chinsinsi_Gwaza Ай бұрын
Naye Zonke amathawa cha 😂😂😂😂
@ChimwemweChirwa
@ChimwemweChirwa Ай бұрын
Bingala bingala 💔😂 thawa kwabwela agululu
@brightonmakumba9228
@brightonmakumba9228 Ай бұрын
Chinachi ndichamba aaaaa
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy Ай бұрын
Chamba ndi jada sono apengatu kubwwlaku ndikape
@KelvinGrevazio
@KelvinGrevazio Ай бұрын
Binga ndi mthera kuwiri aaaa 😂😂😂😂
@BlessingsNyambi
@BlessingsNyambi Ай бұрын
Eh yachina Bingala 😅😅😅 kufuna kuonesa unzika 😂😂😂😂
@VestnaMangani-rn9sh
@VestnaMangani-rn9sh Ай бұрын
Awa anachenjeraso mopusa aaah
@ronnexmakuluni8038
@ronnexmakuluni8038 Ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Umayenda mmbali aise kkkkkkkkkkkk Security
@DinessCholomali
@DinessCholomali Ай бұрын
Nayeso uyo za ziiii,
@desiremalichi8225
@desiremalichi8225 Ай бұрын
a Bingala akudanatu ndi mafikidwe anu ma Guy...🤣🤣
@nzeruzatate81
@nzeruzatate81 Ай бұрын
🤣🤣 Amene zikukubowan imwan panado Ife tinakonda bingala wa mapundiyu bas kkkk
@KRIANFORCE-ls4kb
@KRIANFORCE-ls4kb Ай бұрын
Bingal😁🤣🤣 pali nkhan apa
@PielCeeGenna
@PielCeeGenna 2 күн бұрын
Koma ankolo awa🙌💔🤣
@SecretChizaka
@SecretChizaka Ай бұрын
Bingala ndiwa short temper
@SuperBuild-k9s
@SuperBuild-k9s Ай бұрын
Koma zonke bale amakukonda uyu
@DesmondTsotselahMw
@DesmondTsotselahMw Ай бұрын
#😂😂Zagwa ku Switzerland #thejakishow #Nkhani #macheza #Malawi
@PeterMaxwell-fs8jd
@PeterMaxwell-fs8jd Ай бұрын
Bingala waukiraso nthawi zanji
@chifunirolungu3567
@chifunirolungu3567 Ай бұрын
Nkhani yavuta ndi mafikidwe 😂
@AlinafeKamwala
@AlinafeKamwala Ай бұрын
Ada awowo ndobhowaa
@itzstevieh4011
@itzstevieh4011 Ай бұрын
Bingala mmmm ai ndikhani Zina guys 😂😂😂
@YamiZingani-ij5kj
@YamiZingani-ij5kj Ай бұрын
Apa sizinayende The power of Alcohol
@MartinMasumba
@MartinMasumba Ай бұрын
Iyi yokha nde mwapanganatu😅
@MichaelGuninc
@MichaelGuninc Ай бұрын
Mwachitabwink taziwlamo kut zonke amacheza ndi makape
@Cee_Busy_Mw
@Cee_Busy_Mw Ай бұрын
Mafikidwe avuta😂😂😅
@hopecollinschatha3692
@hopecollinschatha3692 Ай бұрын
Mtima wanga dekha umbuli siwabwino ndapanga manyazi ngt ndine
@Jermiahwop
@Jermiahwop Ай бұрын
😂ahhh zathapo mwasanga
@YankhoChidetsa-y3t
@YankhoChidetsa-y3t Ай бұрын
😂😂😂😂😂🤣kma bingala ai zkm amatha security
@HymieZomba
@HymieZomba Ай бұрын
😂😂💔 koma ndaseka
@WebsterKaundaJunior-hl9bl
@WebsterKaundaJunior-hl9bl Ай бұрын
Anthu ayendela limodzi konse uko aaaa🤣🤣 kufikans kwanj kkk
@FrankLeeLiwonde-jd3vx
@FrankLeeLiwonde-jd3vx Ай бұрын
Osamapopa zilizonse bingala apo wapanga zautsiru
@KelvinMikundi
@KelvinMikundi Ай бұрын
😂😂nkhani ndyamafikidwe apa😂😂
@shyreenmitochi2982
@shyreenmitochi2982 Ай бұрын
Mayoooo bundle yanga😂😭
@MereenChair
@MereenChair Ай бұрын
Koma kunachema😂😂
@FatsaniMchenga
@FatsaniMchenga 18 күн бұрын
Bingala ase 😂😂
@JohnexNachipo
@JohnexNachipo Ай бұрын
Kodi bingalayu amapangilanji chonchi ine amandiBowa bwanji
@PrinceChakhota-t8d
@PrinceChakhota-t8d Ай бұрын
Gululu wakanika basi kkkkkkkkk
@HendrixChaputa
@HendrixChaputa 21 сағат бұрын
Osandigwila 😅😂😂
@victorcontestkamba4299
@victorcontestkamba4299 Ай бұрын
Koma yhaaa Man Dem Bingala😂
@LM-gz5pk
@LM-gz5pk Ай бұрын
Kupasa matama imeneyo nd khan
@bezakml
@bezakml Ай бұрын
Wagwan binga
@BlessingsSungani
@BlessingsSungani Ай бұрын
😂😂😂Mafikidwe 😂😂
@AbdullahWillyAbdullah-xn6jl
@AbdullahWillyAbdullah-xn6jl Ай бұрын
Eee km Bingala😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂
@MussahAnnafie
@MussahAnnafie Ай бұрын
A zonke ndekut anaishosha penapake et olakwa athawa yekha nanga liwilo limenelo ngat kwabwera mbola bwanj
@J_swagger
@J_swagger Ай бұрын
bingala galu kwabasi 😂😅😂
@thokomandanda9539
@thokomandanda9539 Ай бұрын
😂😂😂😂iiiiiii bingala ndichan 😂😂😂😂😂😂😂
@blessingsmunthali9202
@blessingsmunthali9202 Ай бұрын
Achita kuwalondolera okhatu kut ali uku kkk
@GwambyzoMhamd
@GwambyzoMhamd 25 күн бұрын
😂😂😂😂😂 Km ndaseka
@BlessingsNyambi
@BlessingsNyambi Ай бұрын
Koma honestly speaking.mafikidwe Anu guys siabho although program mumatcha GULULU
@frankchazema2059
@frankchazema2059 Ай бұрын
Scripted amwene
@ryannyondo
@ryannyondo Ай бұрын
It's just for fun. Nothing serious. Take it easy.
@ryanphilip3392
@ryanphilip3392 Ай бұрын
Bingala unakapanga naeso gululu ndichibagela
@Mgabehganesh
@Mgabehganesh Ай бұрын
😂😂😂 Nkului naye
@mphatsondalama1111
@mphatsondalama1111 Ай бұрын
Kodi adhawa ndimisaladi kapena?🤣🤣
@ALEKI1998
@ALEKI1998 Ай бұрын
Dude 😂😂😂😂 aaaaa you're not serious
GULULU NDI TUNO :- Koma Chang'alula eish
3:22
Mikozi Network
Рет қаралды 36 М.
The evil clown plays a prank on the angel
00:39
超人夫妇
Рет қаралды 53 МЛН
She made herself an ear of corn from his marmalade candies🌽🌽🌽
00:38
Valja & Maxim Family
Рет қаралды 18 МЛН
Kambodya | Season 1| Episode 1 (Ntchito)
5:00
Adzukulu
Рет қаралды 30 М.
Malawi described in one video
2:35
Phoenix Mabedi
Рет қаралды 13 М.
GULULU NDI ANITA WA SKINI KEYA
4:04
Mikozi Network
Рет қаралды 18 М.
MNYAMATA WA ZAKA 29 KOMA WA NZERU ZODABWITSA  -  DENIS MAHATA
30:19
Factory265 Media
Рет қаралды 30 М.
Última hora: Venâncio Mondlane já se encontra em Moçambique
8:41
Direito Moçambicano
Рет қаралды 20 М.
SECRET BOOTH Episode 2:- Adachitidwa chipongwe ndi Transporter
8:21
Mikozi Network
Рет қаралды 13 М.
The evil clown plays a prank on the angel
00:39
超人夫妇
Рет қаралды 53 МЛН