Mkangano wa Lucius Banda ndi Bingu

  Рет қаралды 100,662

Sam Malvitha

Sam Malvitha

4 ай бұрын

Пікірлер: 111
@sammalvitha
@sammalvitha 4 ай бұрын
Remember to subscribe ❤
@werlemsitima
@werlemsitima 4 ай бұрын
😊
@werlemsitima
@werlemsitima 4 ай бұрын
😊
@werlemsitima
@werlemsitima 4 ай бұрын
😊
@werlemsitima
@werlemsitima 4 ай бұрын
😊
@twenage
@twenage Күн бұрын
Q😊😊q​@@werlemsitima
@DeboraNembele-ri3bh
@DeboraNembele-ri3bh 4 ай бұрын
Freedom fighter anali Evison Matafare oyamba komanso osiriza anthu opanga za person siabwino nthawi zonse
@Jermah51kennias
@Jermah51kennias Ай бұрын
Inu ndi anthu aja okonda munthu ukufaaaa
@giddymarley112
@giddymarley112 4 ай бұрын
Bingu nd great man. Amaona patali. Malawi pano akuvutika coz Bingu sanamalize tym yake
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 4 ай бұрын
Ndie ngat siwantha bwanji relo asalakhula namapwalayu alikut
@user-rv5ow7xy3i
@user-rv5ow7xy3i 4 ай бұрын
Lucias Banda ndi wadyera komanso munthu waziphuphu kwambiri amayendera MSCE yabodza cholinga chofuna kulemera, pano siuyu aChakwala ampasa mpando wakhala pheee
@patricgama4788
@patricgama4788 4 ай бұрын
ali biz kuba ndalama dza boma ndi mcp iweso masu mutu wako sugwila ncthito iwe ungamayamikile galuyu
@ArexBright
@ArexBright Күн бұрын
Sorry wapita mwachangu coz timadikila kt ayibe nyimbo mubo lilipoli koma ay zidko limatha bas kulimbanila nkazi kaya zichani tilibe nazo ntchito koma ife tingoti abuye wayakha bas RIP BINGU MUTHALIKA
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 4 ай бұрын
That's why Lucious Banda panopa sakuyimba nyimbo zolongosoka,, mmbuyomu album yonse imakhala nyimbo zonena Bingu yekhayekha
@loidchikoti9338
@loidchikoti9338 3 ай бұрын
Abodza inu munene kuti inuyo mzanu ndi bingu osati bandayo
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 22 сағат бұрын
The woman probably was Calista as all these were parliamentarians. Not so ?
@user-kh4wy6ze9b
@user-kh4wy6ze9b 4 ай бұрын
Ndy Pano akuti chani agalu okonda ku dyesa mimba zawo😢
@user-zv9zk2wr6u
@user-zv9zk2wr6u 4 ай бұрын
Okay ndakumvani auncle Sam
@nysonzeperiana9869
@nysonzeperiana9869 4 ай бұрын
Munthu oipa uyu ndiokonda ndalama nthaw amadana bdi bingu chifukwa samaonapo cholowa...ngati ali munthu osaopa why now ogokhala or nyimbo kuimba ..sakuona anthu kuti akuzuzika
@JanetJamesMachila
@JanetJamesMachila 4 ай бұрын
Lucius banda dyera amafuna bazi koma anaona kuti bingu anali dolo sanamupatse 😂😂palibenso president angazafanane ndi bingu 😢😢alucius nanga lero muli kuti dziko lili pa moto ili
@user-lq2zj1vy5e
@user-lq2zj1vy5e 3 ай бұрын
Mumatiuza zomwe sitimaziwa bwana mupitilize
@SurprisedDrumKit-ql7rj
@SurprisedDrumKit-ql7rj 4 ай бұрын
Boss apa ndie meatinamiza zoti Lucius dagulidwazo mmm
@davidwakhokamoto1124
@davidwakhokamoto1124 4 ай бұрын
I hate Lucius Banda ndipo ndiwadyera kwambiri amkagofuna kumamudyera bingu nde ataona kut bingu simuthu oti akhoza kumupusisa ayi
@franciskameko2586
@franciskameko2586 4 ай бұрын
Si wabwino Lucius Banda
@chisalebeston
@chisalebeston 4 ай бұрын
I like you Sam a historian
@user-ux1gc7qo3i
@user-ux1gc7qo3i 16 сағат бұрын
Sir Paul banda is alive
@hendsonmaganizoofficial1758
@hendsonmaganizoofficial1758 4 ай бұрын
Taphunzilapo kanthu brother 🤝🙏🙏
@NzeruDesign-ut1go
@NzeruDesign-ut1go 4 ай бұрын
Mot uzingofotokoza apa ndye ukuopa zchan?
@mosesharoldngolombe
@mosesharoldngolombe 4 ай бұрын
Pano zinthu nde zikuyenda bwino? Ali kuti nanga bwanawa 😂😂😂
@lingstonenagoli7729
@lingstonenagoli7729 4 ай бұрын
Achitsiru aja
@WisdomKmsiska
@WisdomKmsiska 3 күн бұрын
Anapangitsa kuti mnyenyembe afe si uyu mkumutama apayi?
@user-vt9cw1dw1d
@user-vt9cw1dw1d 15 сағат бұрын
Sam mavita kapenso
@user-zu2cc6qs9r
@user-zu2cc6qs9r 4 ай бұрын
Amanena bingu emweyo
@user-vq7rs7zj2r
@user-vq7rs7zj2r 4 ай бұрын
Uyu ndigalu wadyela
@chiefjusticie
@chiefjusticie 4 ай бұрын
Lucia's Banda anayesesa mokwanila kutimenyela khondo ndipo oyimba ambiliwa akutchuka chifukwa cha iye he is bg boss
@BornMandala-rz1dk
@BornMandala-rz1dk 4 ай бұрын
Ndisiyileni kanga nyimbo ija imanena Bingu😊
@user-pj7rl5fq6p
@user-pj7rl5fq6p 4 ай бұрын
Amanena bingu kuti watani?
@user-kl5fo1rb5z
@user-kl5fo1rb5z 4 ай бұрын
Komanso ngat kumalawi kuli andale osadziwa chomwe akupanga one of them ndi Lucius
@raymondchautsi6282
@raymondchautsi6282 4 ай бұрын
Nde Pano sakuyankhula ndizopusa zomwe akupanga achakwelazi??🙄
@alexnyirenda123
@alexnyirenda123 22 күн бұрын
Imfa ya Munyenyembe imandiwawa
@ClementKampaka
@ClementKampaka 4 ай бұрын
Kudali Billy kaunda yemwe adalimbana ndi bakili kapena mudali muli ana
@jamessaiti
@jamessaiti 4 ай бұрын
Pano anampasa bazi ameneyo
@user-ux1gc7qo3i
@user-ux1gc7qo3i 16 сағат бұрын
Paul banda alipo
@olobodokatwaha5947
@olobodokatwaha5947 4 ай бұрын
Ok chabwino tamvani man
@user-ci5cu1eq4e
@user-ci5cu1eq4e 4 ай бұрын
Ine zambiri ai guys ngati mukuidziwa kanyimbo kameveka kumapeto koo ndiuzeni kuti anayimba ndindani chonde
@sammalvitha
@sammalvitha 4 ай бұрын
Search nyimbo ya Sam Malvitha youtube chanel... muipedza ...pa youtube pomwepa boss Anaomba ndi Yb Africa ndi Kikey Malawi
@mayesohenry
@mayesohenry 3 күн бұрын
Which freedom has he fought ?
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 4 ай бұрын
Munthu wadyera uyu galu
@user-rx3il9uk6i
@user-rx3il9uk6i 4 ай бұрын
I like some navter go ahead
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 4 ай бұрын
N hate Lucius munthu woipa kwambiri
@user-yj5xv4cy8x
@user-yj5xv4cy8x 3 ай бұрын
Well spoken
@JessicaChabwera
@JessicaChabwera 3 ай бұрын
Ndipo ameneyu anamunyoza bingu kwabasi pano akukanika kuyankhula mmene anthu akuvutikila
@YamikaniEdward
@YamikaniEdward 3 ай бұрын
Zokoma😂😂🎉
@HenryChunga
@HenryChunga 3 ай бұрын
Soja wa mphawi , speaking on behalf of the poor masses
@madalitsochabwera5903
@madalitsochabwera5903 4 ай бұрын
Ndisiyireni ena amati amanena Mulli kaya kkkk
@mosesharoldngolombe
@mosesharoldngolombe 4 ай бұрын
Ineso namva chomcho
@maggiekamphinda5699
@maggiekamphinda5699 4 ай бұрын
Muli ankayenda ndi ndani Mlaka ndi bernadetter?
@patricgama4788
@patricgama4788 4 ай бұрын
bingu anapotsa kamuzu muzochitika pa 7eyes yake ndiye mungama fanidze ndi galu yo lus
@user-lz8do1or9l
@user-lz8do1or9l 4 ай бұрын
Good ,could you please do more
@websterkausiwa8919
@websterkausiwa8919 4 ай бұрын
Nawesotu nyimbo zachamwiniyoo usamangochaputaa ndiza Tygrin zoo
@robertmakupe2863
@robertmakupe2863 4 ай бұрын
Ase iwe ukumutama galu uyu alikuti luciac freedom fighter wakunyumba kwako tu
@VeronicaSekobi-is6dk
@VeronicaSekobi-is6dk 4 ай бұрын
🔥
@mariamhassan4089
@mariamhassan4089 4 ай бұрын
Tadziwa nao
@EvalistoMilanzi
@EvalistoMilanzi 3 ай бұрын
Like it
@user-dg8qx5eq5y
@user-dg8qx5eq5y 3 ай бұрын
Am interesting
@ConfusedAtv-bs4gc
@ConfusedAtv-bs4gc 4 ай бұрын
Mmmmmm lusius wakupha uyu anapha oyimba azake ambiri ATI asachuke kuposela iye
@chiefjusticie
@chiefjusticie 4 ай бұрын
No mukulakwisa mukatelo kod mayiko enawa anthu samafa nakha anthu ena osayimba ndipo sanatchuke komwe anthu akumuzi samafa ndi infa za m'zizizi munganene kuti ndi bwana Lucia's Banda. No come on guys let's us learn to respect our favorite artist from our country because if we could no palibe Munthu yemwe angawalemekeze
@zionekanjoka7575
@zionekanjoka7575 4 ай бұрын
Mmmmmm
@user-cd8ke5pm4v
@user-cd8ke5pm4v 4 ай бұрын
Amati yimilira wulemu wawo
@franciskameko2586
@franciskameko2586 4 ай бұрын
Lucius Banda munthu woipa kwambri but he's a pretender ngat ndwa bhobho
@user-kh4wy6ze9b
@user-kh4wy6ze9b 4 ай бұрын
Zowona zake waononga anthu ambiri galu ameneyi🤔😢
@user-ok9bb3de5m
@user-ok9bb3de5m 3 ай бұрын
Mumatha amwene
@patricgama4788
@patricgama4788 4 ай бұрын
amadana ndi chilungamo wautsilu ananga pano akuti chani ku mcp chifukwa ampasa mpando kumalawi balibe amene angaipitse bungu
@Mickeykasambula265
@Mickeykasambula265 4 ай бұрын
Ndepano lucius banda wanuyo sanagudwe ndi ndalama?
@JasperKaleni-dx6nn
@JasperKaleni-dx6nn 4 ай бұрын
😂sam iwe umandiwaza 😊
@user-yj5xv4cy8x
@user-yj5xv4cy8x 3 ай бұрын
Tay green aise
@isaacdemba2401
@isaacdemba2401 4 ай бұрын
Umangoyamba nkhani ukudziwa kuti suyimaliza nanga chomabisira mayina ndichani?
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc
@PaulkapesiPhirijunir-kh7vc 4 ай бұрын
Alucias inu ndinu achitsilu inu mulibe nzeru
@ChiwalePhade
@ChiwalePhade 11 күн бұрын
Tsoja wampaw
@user-wg9od3ur8h
@user-wg9od3ur8h 4 ай бұрын
Mumakwana
@user-ns7mp3fn2r
@user-ns7mp3fn2r 4 ай бұрын
Good job weldone
@MORESSRAJABOCINGANO-rz1lt
@MORESSRAJABOCINGANO-rz1lt 19 сағат бұрын
I'm sorry forget you
@Mphamdala
@Mphamdala 4 ай бұрын
Kachunyau kunena nyau king?
@sammalvitha
@sammalvitha 4 ай бұрын
Kkkkkkkk
@DamianoEdward
@DamianoEdward 4 ай бұрын
Soja ndi soja basi
@NicholasKwajama
@NicholasKwajama 4 ай бұрын
Mukutiwuza zinthu zoti tikudzidziwa kuposa inunso
@user-is9ek3ix8z
@user-is9ek3ix8z 4 ай бұрын
❤❤
@MoosaMusarh
@MoosaMusarh 4 ай бұрын
😂😂😮
@Daneck-rm1gg
@Daneck-rm1gg 16 сағат бұрын
Rest in peace
@HenlyTiyesi
@HenlyTiyesi Ай бұрын
Muli
@PeterSuwack-ox6rj
@PeterSuwack-ox6rj 4 ай бұрын
Unakana
@al-sudigang3299
@al-sudigang3299 Күн бұрын
Rip
@user-bv3px8ie5n
@user-bv3px8ie5n 4 ай бұрын
Don’t talk lies now
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 4 ай бұрын
Liciusa Banda ndi hero anamuuzaso Bingu akuopsa kuti ndinamenyana ndi Mkango kunena Kamuzu nde sindingaope IWE Kambuku, Osafanizora zomwe amapanga Bingu ndi Kamuzu Bingu zitukuko zake zinachiitikira mu mseu umodzi opita ku state house 1 chiliza Cha Kamuzu 2 parliament 3 Bicc 4 Presidential villa basi, And dziwani kuti zitukuko za term yoyamba za president timakhala za emwe wamusiyila emwe Ali Dr Bakili muluzi mu 2 years yakeyake Bingu palibe Chomww anapanga kuposaposa Kwa nthawi yoyamba mu mbiri ya dziko lathu mafuta a GALIMOTO sugar soap bread zinkasowa komaso magetsi ndi ndalama za kunja mdziko muno munalibe ndi motsogozedwa ndi Mwakadungula timapanga ma demo komaso ampingo anampatsa 90 days kuti asiye pansi udindo because malawi was worse Bingu mzimu wake usamause mumtendere anaphetsa abale Anthu muzipatala kaba kokana kutsitsa mphavu ya ndalama yathu yomwe idali itathelatu Emwe sangayamikire za soldier Lucius' Banda ndi mfiti anayamba kulimbana ndi Kamuzu, Bakili muluzi kenakoso Chitsiru Bing
@ChimwemwePhiri.1
@ChimwemwePhiri.1 4 ай бұрын
I don't agree with you... Bingu did alot...you hated him i can see.
@user-kl5fo1rb5z
@user-kl5fo1rb5z 4 ай бұрын
Nkulu uyu akunyoza Binguyu kaya ngwakuti kaya koma nzeru mmutu umu zilimo zochepa kwambiri ine nthaw yakamudzu kunalibe koma na Bingu palibenso president ndaona ineyo oposa iyeyu
@chiefjusticie
@chiefjusticie 4 ай бұрын
Respect brother pitilizani
@yamikanifischer
@yamikanifischer 4 ай бұрын
If he is strong why now
@christopherphiri8476
@christopherphiri8476 4 ай бұрын
I like your job go ahead some navitar
@chinyongakaole-qz5mh
@chinyongakaole-qz5mh 4 ай бұрын
0
@EvelynWilliams-ec5fx
@EvelynWilliams-ec5fx Ай бұрын
😅😅😅😅😅 osamasakaniza zopusa ndi za nzeru bingu ndi ophunzira komaso anali wazeru sopano winayu mmmmm mumchimwisa ngat ali apongoz ako sorry
@dreamsneverdie-242
@dreamsneverdie-242 11 күн бұрын
Chisiru ichi panopa akukanika kupanga za nzeru panopa
@chauncychauncy1683
@chauncychauncy1683 4 ай бұрын
Uztchula Maina iwe ase aah ukuopa chan
@user-md5uv2cg6i
@user-md5uv2cg6i 4 ай бұрын
Pano bwanji wangoumba mlomo akuziwa kuti chakwera amudula machende
@user-bq8gb7tb1l
@user-bq8gb7tb1l 4 ай бұрын
Sam mavitha umakhwana
@user-dk4he8zr7m
@user-dk4he8zr7m 4 ай бұрын
Pano zikumuvuta pati kuzuzura Boma la mcp
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 4 ай бұрын
Liciusa Banda ndi hero anamuuzaso Bingu akuopsa kuti ndinamenyana ndi Mkango kunena Kamuzu nde sindingaope IWE Kambuku, Osafanizora zomwe amapanga Bingu ndi Kamuzu Bingu zitukuko zake zinachiitikira mu mseu umodzi opita ku state house 1 chiliza Cha Kamuzu 2 parliament 3 Bicc 4 Presidential villa basi, And dziwani kuti zitukuko za term yoyamba za president timakhala za emwe wamusiyila emwe Ali Dr Bakili muluzi mu 2 years yakeyake Bingu palibe Chomww anapanga kuposaposa Kwa nthawi yoyamba mu mbiri ya dziko lathu mafuta a GALIMOTO sugar soap bread zinkasowa komaso magetsi ndi ndalama za kunja mdziko muno munalibe ndi motsogozedwa ndi Mwakadungula timapanga ma demo komaso ampingo anampatsa 90 days kuti asiye pansi udindo because malawi was worse Bingu mzimu wake usamause mumtendere anaphetsa abale Anthu muzipatala kaba kokana kutsitsa mphavu ya ndalama yathu yomwe idali itathelatu Emwe sangayamikire za soldier Lucius' Banda ndi mfiti anayamba kulimbana ndi Kamuzu, Bakili muluzi kenakoso Chitsiru Bingu
@FerecidadedeshilaShila
@FerecidadedeshilaShila Күн бұрын
Basi ose akumana komweko apezana azikamenyana komweko
JAI BANDA AND LUCIUS BANDA (RARE MOMENTS)
6:12
TEAM ENTERTAINERS MW#
Рет қаралды 20 М.
Must-have gadget for every toilet! 🤩 #gadget
00:27
GiGaZoom
Рет қаралды 11 МЛН
Homemade Professional Spy Trick To Unlock A Phone 🔍
00:55
Crafty Champions
Рет қаралды 62 МЛН
NERF WAR HEAVY: Drone Battle!
00:30
MacDannyGun
Рет қаралды 33 МЛН
Nancy vs Che Nkope - Zikhale Ngoma Kapena Drums?
10:46
CHE NKOPE
Рет қаралды 15 М.
LUCIUS BANDA EXCLUSIVEINTERVIEW - 20 MAY 2021
56:54
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 85 М.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Morton Baghaya
Рет қаралды 103 М.
Nthenda Yomwe Anadwala Lucius Banda
6:25
Sam Malvitha
Рет қаралды 74 М.
LUCIUS BANDA - BISA (@LuciusBandaTV )
4:42
LuciusBandaTV
Рет қаралды 970 М.
JOHN KAPITO WATOPA NAYE CHAKWERA. Ityoke ityoke Osabisa mau // PART 1
33:23
ARRIVAL OF LUCIUS BANDA'S REMAINS😢
1:22:27
VILLAGE CHAMPION
Рет қаралды 19 М.
НАДЕЮСЬ ОН ВЕРНЕТСЯ С АВТОСЕРВИСА 😂😂😂
0:40
СЕМЬЯ СТАРОВОЙТОВЫХ 💖 Starovoitov.family
Рет қаралды 1,9 МЛН
Идеальный день ребёнка😂
0:11
МишАня
Рет қаралды 4,1 МЛН
Did you believe it was real? #tiktok
0:25
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 17 МЛН