Mukasuntha pamenepo bro... Dziko muzalimva kuwawa zed Mack my ward's
@BenaSamuel28 күн бұрын
Iweso uzatiuza bwino bwino mene ana fela witika
@RobertLuka-wy9clАй бұрын
😂😂😂😂😂 Kunkuyu ndi munthu womvesa chisoni kwambili koma muziwe mulungu alipo tsiku lina dziko muzalimva kuwawa
@hamstonelwesha808229 күн бұрын
Well clarified
@StanleyMunthali-s1dАй бұрын
Thanks for the clarification Mr Minister ! Aponzoonadi !
@mosesdc8810Ай бұрын
Mboli yako iwe
@KamwachaleАй бұрын
Kodi a Nkunkuyu mukuti kusankha mamembala a MCP kukhala atsigoleri a MEC ndizotsatira malamulo ? Mpesi was once a personal assistant of Chakwera, Mphatso Sambo is MCP IT expert and MEC chair is John Tembo's daughter, how can the election be free and fair in that situation. Take two of these to be replaced by UTM member and AFFORD Member to balance the equation otherwise this is already unfair before the election is conducted. The government should just comply to the demands otherwise election of the president can be done through demonstrations just before the actual election
@LandonChitsendaАй бұрын
Jen,namathanga nda zake aja mwaiwala kod😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂musanati
@jameschiwangaАй бұрын
Jen anser uja mwayiwala Kut Ife ntinkati ndiwa DPP inu mumakana siuja Lero akuyimila u MP as DPP candidate mwayiwala?
@jameschiwangaАй бұрын
Komaso Anabel mtalimanja simwana WA Joni Tembo osapusisa anthu
@KinziWindasoni-h4bАй бұрын
Galu Iwe amalawi ake atiwo
@LyneckMphepo-lv4djАй бұрын
😂😂 kumkuyu owe ngalu kwabasi Kodi munkalowa mboma with mademo lero ukudana ndi mademo why
@kennymwanyongo816510 күн бұрын
Iwe ukunama. Nkhani ndiyoti nchifukwa chani mwasankha SMARTIMATIC momwe inu munawina chisankho kuzela mwa Manual process of voting!!!??? Na iyiyiyiya SMARTIMATIC siyitheka.
@DYSONISSA29 күн бұрын
Amene ukufuna kupweteketsa anthu ndi iweyo kunkuyu .
Commission of equally sangaiyambitse akuopelatu sangazipeleke
@JasonMailosАй бұрын
Kuyakhula moputsa kumeneko
@MbeedaJamesАй бұрын
Nde inu mulindi mfundo anamachende inu pathako pako 😢
@AdielJumbeАй бұрын
Chizungu chavuta dyomba 😂😂😂😂enquiry
@sandramkaligida1163Ай бұрын
Game zikwanje Mcp ❤fire 🔥🔥🔥
@kelvinmphande3754Ай бұрын
Positions like Mec chair, not those who are in embassies iwe. We need independent Mec
@isaihmagani5697Ай бұрын
Kulankhura mosayang'ana mbali a Kunkuyu apa apalankhura mwa nyoo momveka bwino
@McshonWilliamАй бұрын
tell us more about comision inquiry thats all
@SiphamandlaNcaphayiАй бұрын
@@McshonWilliam ukati tell us about commission inquiry how do you mean?you mean skc will arise again it's just a matter of wasting your time tell the government what are you going to do to people when you are in government not skc each and everyday mmmmm come on you opposition ppl
@McshonWilliamАй бұрын
@@SiphamandlaNcaphayi drop your realy name idont reply fake name kuli ngat kuthamangisana ndi chinthunxithunxi chako chomwe olo ndiwe folena kumalawi
Ankukuyu inu ndi munthu ovesa chisoni. Inu simuli ku mec komaso simuli ku nrb. Nanga mukudya fulumira kuyankha inu bwanji.
@andrewsitima-qm6buАй бұрын
Kulilongwe munawomcha offers ya utm athunuso munayiwara
@anusahjenala106329 күн бұрын
Mbuzi imeneyi kodi
@NikolasNanaweАй бұрын
my vote ❤ 🙏 🗳
@YassinzaoZao23 күн бұрын
Foseki iwe
@RhodiWhiteАй бұрын
Moses black box ili kuti eeeee bakili muluzi tv is best
@kingsleyhopematchaya5184Ай бұрын
Za ziii zikugwilizana patipo ukufusazo
@JasonMailosАй бұрын
@@kingsleyhopematchaya5184black box ilikutiiiii
@InnocentKasonga-n8kАй бұрын
Umbuli sizinthu 😅😂..
@BeatriceSindizaАй бұрын
Mmmmm koma akunena zoona popanga malamulo sapanga ndi aphingu a boma okha otsutsaso amakhala Ali pomwepo ndiye cholozelana zala ndi chiani
@PatinceChifuniroАй бұрын
Majority are them the ruling ones
@henrymwale8994Ай бұрын
Inuso zikuoneka kuti palibe chimene mukuchidziwa
@IbrahimWezelyАй бұрын
Mbambande mr minister
@justinmalala-e4oАй бұрын
Even ku Kenya kunali ma demonstration bill itadutsa kale
@WonganiKatchaleАй бұрын
Kulibe kusitha boma ndilomweli ❤
@mbelengamavuto2517Ай бұрын
Inu ndi dpp bwanji simunakambilane
@WakisaNjeghenje-i2n22 күн бұрын
Tisekelere kusakwabasi kuyendesa zikomo ndi mwano wanuo msiyanise kwambil
@andrewsitima-qm6buАй бұрын
Kkkkkkkk koma apa ayaluka adpp sure mukamanama chonde otsutsa namani mosamara
@OsmanYusuf-u1vАй бұрын
Dpp my vote
@MacdavieItetaАй бұрын
Uyu munthu uyu 😢😢 ndi adzizako chauta akukhululukireni ndithu
@MarcyKamagaАй бұрын
yes ifeyo tikufuma nkhani ya chirima mumene munapanga anthu 9 koma anthu Inu muri ndi chipongwe murungu akurangeni
@ancientnkhata1137Ай бұрын
Pita ukafufuze
@mbelengamavuto2517Ай бұрын
Udziwe yesu iwe
@NtchindiChirwa-l8oАй бұрын
I love the guy MCP my hope
@eddiesilika618Ай бұрын
chisiru iwe
@MzadziWangaАй бұрын
😂😂😂😂 kma zinazi mwina ndi umbuli kma ukupangisa ,hope yanji pano 4 yrs zinthu zikusokonekera n u r saying MCP is ur hope?? Kapena sindikudziwa tanthauzo la hope
@sylvesteralfred8355Ай бұрын
You love this guy chifukwa ndichitsilu ngati iweyo
@ancientnkhata1137Ай бұрын
@@MzadziWangaZikusokonekera kwanuko
@robertzambia8697Ай бұрын
Kunokha nkamwa
@WilsonFriday-z8wАй бұрын
We need commission of inquiry mr man
@GilbertKuchipinda-w9wАй бұрын
Commission of inquiry Mr kunku
@adamashrafi5875Ай бұрын
Very big man
@FrancoKaunga-rq2kiАй бұрын
If you obey the laws of malawi government, when are you going to make commission of enquiry?
@PaulMandala-n7cАй бұрын
Iwenso kumkuyu nde nyanyiii kupha mkati
@MrMagomboАй бұрын
MEC is indipendent and it has its own Spokes person. Nanga a Kunkuyu akuyankhulira MEC bwanji?
@OsmanYusuf-u1vАй бұрын
Ngat kuli kusokonekela kwathu ndiye kut zikoli takumana osokonekela okha okha cause asabalalike athu aku opposition okha nanga ena akusitha chichewa atachoka ku dpp aja siwosokonekela? Ineyo ndisiyen ku blue konko nga nga ngaaaa
Ndiwe wabodza basi ndipo wuzabwedza ndalama dza amalawi
@henrymwale8994Ай бұрын
Pa 15june 2017 ndinu nomwe munkatsutsa nkhani ya ma ID kuti sakufunika ponena kuti adpp akufuna kudzabera ma vote kudzera mma ID, lero zayamba kukubowani
@AmosShadreckАй бұрын
😂😂 uku atolankhani kulibe aa nanga achereuka pali fuso apa monga mtola nkhani?
@JamesFred-v1vАй бұрын
Bwanji chilima simunakambirane naye kaye muss amigas taste mu chikangawa
@AchiwaNikisyaАй бұрын
Iwe bona lako lidayamba liti kupha kubweraso pano nkupitilizabe mpaka kupha eeee
@blessingssaitiАй бұрын
Anthu adya njanjizo Pano mafuta kulibe
@EvansEgraАй бұрын
Wosaphatikiza nkhani inu, nkhani siya Chirima akulankhula apa ai, nkuona Malawi ali onukha kaamba ka anthufe kusamvetsa
@PhilipGwazanyoniАй бұрын
Nanga nkhani ikukambidwa apa ndi ya ma albino? Simukuvetsa Pati mumangoona za u zokha kuti nde zolondola basi?
@JoeMulekanoАй бұрын
Munakapanga press briefing ya chipani not zomwe muyankhazo
@andrewsitima-qm6buАй бұрын
Kwayinu amene mumkapha nawo alubini sure mudzavitera dpp koma ife timava kuwawa popeza amalawi ena ndinu mbuzi tiyeni nazoni
@RichardZatopetsaMandaАй бұрын
Well spoken❤🎉
@mbelengamavuto251726 күн бұрын
Mukumvesatu chisoni man mukamayakhula muziganiza
@JosephiriillovoАй бұрын
Kali gwaaaaa ,za commission of inquiry nde zosayankhika kkkkkk kuseka ngati zabwino koma zomvesa chisoni kwabasi
@AmosShadreckАй бұрын
Ndie mwati MCP ili one part of MCP just because manganya oenda ndazimai okhaokhauja ali muboma? Battery lako iweyo kwabasi
Vuto andale athu anatiziwa Kuti chilichose atanene timangoti yomweyo galu iwe or akutinamiza Khani zamalaumo zimatipeta kwambili
@NicolasKamunga-rv9vrАй бұрын
Iwowa a U D F a chair adanyoza M C P koma mukudyera limodzi bwanji nanunso kodi mwasiya kununkha? 😂😂😂😂😂
@jamesmsonkho4830Ай бұрын
aaaa ine kuvota mayaz chochi ndale za ma grudges zaziiiiiiiiiii
@AgnessKalindoАй бұрын
Iwetu kunkuyu usazitenge ngati ndi ochenjera ndipo ndi iwe chisilu kwambili. Bwanji sumayakha za chilima .? Inutu mudzamva kuwawa ndipo mulungu ndi amene akuziwa.
@AlexanderYovatiKhumalo29 күн бұрын
Ufulu usakhale oononga ufulu wa anthu ena.
@user-cg5ml7ym4vАй бұрын
A kunkuyu musathamange kuyankha makalata azipani kusiya nkhani ya ndege