Selina Dumbula Mkaka ndi Abena Chizanja Khoma Bekete mumatha 🔥🇲🇼 Ku program ya GWEDE-GWEDE kuja mmmmmmmmm mumandiwaza bwanji ndi Steve Konda Banda mumazukuta bwino nkhani posatengera mbali
@sirarexsamiunah-rt8wd Жыл бұрын
Mpaka tidayamba kukuiwalanitu😮
@modiseusi4412 Жыл бұрын
Tapeza chochitano pano iyaaaaaa munali kuti kodi
@StevenSaturday-u6j Жыл бұрын
Kkkkkl zili bhoo
@meganabigail-ye7fw Жыл бұрын
Asellina nda Bena mumapangaso izi et ndakunyadilani a Dt
@ndazionakunkani3214 Жыл бұрын
Welcome back
@ChrisChumba Жыл бұрын
Welcome back is have been long time
@RobertKBanda Жыл бұрын
Welcom after wina atasowesa camera
@BabraKamanga Жыл бұрын
❤
@ChrisChumba Жыл бұрын
Koma a OC.mumadyako ku holiday kapena Fredy emweyo