MUNTHU WAMULUNGU kuling'alura boma la CHAKWERA...lalephera

  Рет қаралды 26,365

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Video from HONEST

Пікірлер: 92
@harrisonkalimbakatha5339
@harrisonkalimbakatha5339 3 ай бұрын
That's a very greatful speech we need such type of people who can't fear but they stand for the right thing keep it up pastor/bishop
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 3 ай бұрын
You have spoken wisely and positively to all the audience that's true kuti this government of Chakwera and his tonse alliance have totally failed and destroyed Malawian economy and it will be difficult for the next government to restore it
@brunobonkainga
@brunobonkainga 3 ай бұрын
I LIKE YOU FATHER AWUZIDWE ZOONA NGAKHALE ALI OSAMVA KOMA TIDZAWONANA PA 2025
@RabeccaMkandawire-i9j
@RabeccaMkandawire-i9j 3 ай бұрын
A Malawi kususuka zithu zoti sizitithandiza kukopeke nditu k500
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 ай бұрын
Boma anachita kulilira ili that's y vamunyera chakwera pls anthu apa central region musamuvoterenso uyuyu atipha
@stanleymollen7273
@stanleymollen7273 3 ай бұрын
A patriot.....kuphunzitsa economics momveka bwino...economics 101
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 2 ай бұрын
i can vote for this pastor in 2025!..if he joins politics.Chakwera has failed this country..
@MphatsoMvula-k6e
@MphatsoMvula-k6e 3 ай бұрын
Udatani umuwuza peter wakoyo mbuli ya mbusa iwelenge yohane 10 mbusa wakuba iwe
@ChimwemweMuhelliwah
@ChimwemweMuhelliwah 2 ай бұрын
Kkkkkk mwina tiyese kutenga anthu oti Ali mkanthu kalewa bwanji...anthu ngati Mpinganjira aja ndi amchina Simbi ,,,osaukawa akuwonjeza kuzilemeletsa kaye okhatu.....😂😂😂
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr 3 ай бұрын
Kodi abishop mawuwo basi antha siinu mikuyankhula ndimulungu wakutumani. Tikudikila titsegulenni maso ndi chilungamo
@OFG-th3st
@OFG-th3st 2 ай бұрын
Iyiyi atiwonelele😂😂
@martinmoyo4211
@martinmoyo4211 3 ай бұрын
Kudzudzula kulipamenepo koma inunso atsogoleri athu achikatolika mulindivuto. Timakonda kuloza chala anzathu koma ndichani timapangapo polithandiza bomalo. Tikati tiyang'anitsitse kumpingo kwathu inuyo atsogoleri a ntchito anunso simumawasala molongosoka mumalipiro. Mwachitsanzo a Gulupa samapatsidwa malipiro abwino komanso a ntchito ena. Ifenso tikonze gawo lanthu mpamene tidzizuzula enawa. You should also set good example in leadership. Zisakomere mbuzi kugunda galu.
@VictorKachulu-y3n
@VictorKachulu-y3n 3 ай бұрын
Popeza mwati ndi munthu wa Mulungu bola tamva koma sanafike kukhala mwana wa Mulungu popeza nayeso ndi wochimwa koma ndi wa bodza uyu Ngati kumpingo kwawo walephera ndiye alonze chala wina angoyesetsa nayeso kutukula dzikolino ndizofunika kugwilana manja koma mukalowetsa ndale ndi mu mpingo momwe ndiye Kuti tigwa tonse ndi nkhosa zomwe or iye sungayendetse dziko ife a DPP zinatikanika kale 😅😅😅
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 3 ай бұрын
Oro muthalika a lowe mudzavutika chimodzimodzi musaone kuti akalowa Mutalika ndiye zinthu zisintha ayi mukuzinamiza kwambiri tiyeni tiziwelenga mau aMulungu atiuza zoona awatu ndi masiku otsiliza Buku lopatulika linanana kale kuti masikuotsiliza mudzaona nkhondo kukangana mu maiko osiyanasiya and munthu afzakonda ndalama not munthu nzake ndipo zinthu zambiri zidzakhala zokwera mtengo kwambiri ine ndakambako zokomo abale mwabuye
@johnkambala692
@johnkambala692 3 ай бұрын
These are part of Malawi disaster
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d 2 ай бұрын
Mawu okhala ndichilungamo mkati mwake ndithu pitilizani kuwawunikira anthu bwana
@Doreen-vw9ws
@Doreen-vw9ws 3 ай бұрын
Palibe chomwe amaziwa chipani chosaziwa economy chipani chomvesa chisoni
@AbdulrazaaqLeyani-k2i
@AbdulrazaaqLeyani-k2i 3 ай бұрын
True and lovely words
@PETERSINKADZIWA
@PETERSINKADZIWA 3 ай бұрын
Chakwera ndi Tambala Wakuda anabwera kuzaononga Dziko lino
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 ай бұрын
Akanakhala wins chakwera akanangoimika manja chifukwa zinthu sizilibwino muno mu Malawi walephera yekha anthu chance anamupatsa
@AlexNjanje
@AlexNjanje 3 ай бұрын
Ndipo zimafunika kutii uthengawu uwafikire ndithu ukulu amenewa munthu osamva ngati ameneyi sindinamuonepo inee maulendo mbwee mbwee
@ConradccjSokoSoko
@ConradccjSokoSoko 3 ай бұрын
Church silimakhala ndi anthu a opposition okha, mliso a m boma, ukulalika mosasamala utha kuyambanitsa anthu m MPINGO. Maka nthawi ya campaign tilimoyi.
@DouglasDazuKamwendo
@DouglasDazuKamwendo 3 ай бұрын
Kodi umafuna anene kuti zithu zilibwino zisali bwino? Taganizani kae bwinobwino amwene osathamanga poyakhula taonani kwa nthawi yoyamba anthu a Mulungu kuyankhulapo m'mene dziko likuyendera ndipo ndi ambiri zedi moti mukwanitsa kuwaletsa onsewo? Tadekhani inuyo ngati simukuona manvutowa khala phee muzingodyelera apa sakunena za campaign ayi koma kutsegula maso anthu amene akunvutika, ndipo idakakhala campaign in church bwezi pakunveka ena kumutsutsa pompo koma ngati akumuombera m'manja choncho ndekuti anthuwo akunvomerezana nazo zomwe munthu wa nzeruyu akuyankhula ku mpingo wa Mulungu. Dziwani kuti mudziko Mulungu adalenga anthu anzeru kuposa azitsogoleri anthuwa koma kuzichepetsa kokha kumapambanitsa so you better watch your mouth.
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 3 ай бұрын
Chilungamo chilibe zoti wochimwa ali momwemo ayi. Truth will remain and the wise will choose the right way to go. The foolish will blame the advice.
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 3 ай бұрын
Akulu mulungu adzikusogolelani mukuyankhula chilungamo ngati munthu wamulungu
@ShambululaModel
@ShambululaModel 2 ай бұрын
Great on Man of God
@Michaelchimwala-c6l
@Michaelchimwala-c6l 3 ай бұрын
God bless you pastor don't fear for that you know is no clear but to talk people to know
@DesireMphatsogama
@DesireMphatsogama 3 ай бұрын
Zochezatu mukauze Tatopa ndimbuz izi Mpaka anthu aMulungu kuyamba kuwayankhulisa zandale chifkwa chakuononga ndalama mopusa
@DalitsoNgalawesa
@DalitsoNgalawesa 3 ай бұрын
This pastor should not get arrested 🔥🔥🔥💯
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 3 ай бұрын
Akulu mulungu adzikusogolelani mukuyankhula chilungamo ngati munthu wamulungu
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 3 ай бұрын
That's true i do respect your massage father keep it up i like the ward's you taling as
@ChristopherJohn-z5z
@ChristopherJohn-z5z 3 ай бұрын
Ku bandura osaopa osafooka kkkk
@LETUSCHIPHUPHU
@LETUSCHIPHUPHU 3 ай бұрын
Muli nzeru umu this audio shud reach to the state 🏠
@YasinThomuVakhaniMilanzi
@YasinThomuVakhaniMilanzi 3 ай бұрын
Zikumveka bwino ndithu kuchokera pa mawu amenewa boma la abusa a Chakwera lalepheradi. Zikufunika kusankha moyenera.
@SymonPaul-s8h
@SymonPaul-s8h 3 ай бұрын
It's true that they failed
@AndrewMukhwapa-qj4vo
@AndrewMukhwapa-qj4vo 3 ай бұрын
Thanks very much God bless you. Your talking the truth
@giftnyirongo-ey3qy
@giftnyirongo-ey3qy 3 ай бұрын
What an intelligent gentleman
@marryphili5419
@marryphili5419 3 ай бұрын
That's true pastor we need to use the brain life now is expensive
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 3 ай бұрын
Samuel told Saul kuti umfumu wanu wakanidwa. Ndiye abusa azingoti zakumwamba?? Kulowa kumwamba ndi umphawi aaaaah
@BressingsMahele
@BressingsMahele 3 ай бұрын
Powerful
@clalesschisale3792
@clalesschisale3792 3 ай бұрын
Our next Bishop of blantyre archdiocese
@AndrewMukhwapa-qj4vo
@AndrewMukhwapa-qj4vo 3 ай бұрын
Your talking the truth God bless you thanks very muh
@TamandaniMaseya
@TamandaniMaseya 3 ай бұрын
🙏🙏🙏🙏🙏
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 3 ай бұрын
Uyu ndi wabodza anthu malo poti awauze anthuwa mau achipulumutso akupanga kampeni yandani inu mungafanizile dziko lamalawi la Mozambique or zambiya zambia ndi dzikolimene limagulitsa miyala ya mtengo wapatali komanso muli Ma boulder ambili amatolera ndalama zochuluka komanso kumalawi timabalana kwambiri sizigwiliza ndikuchepa kwadzikolo Mozambique kuli ma madoko awili amene ama bweletsa ndalama plus mogodi anthu amulungu ngati awa ndi amene amapangitsa kuti dziko lisamayende bwino chifukwa amaiwala mau aMulungu amayamba kulalikira ndale mudziko simungakhale m'dalitso ayi toyeni tizipemphera kuti mulungu afalitse Malawi zikomo
@BrightZionga
@BrightZionga 3 ай бұрын
Akunenatu chipulumutso kupulumutsa miyoyo ya anthu apulumuke kunjala kuumphawi kukukwera mitengo ya zinthu Kodi mau oti kupulumukawa amakamba zakumwamba kokha pepani ngati ndakulakwirani koma sitingamakambe zaulemelero ukudzawo pamene apapa anthu tikuvutika
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck 3 ай бұрын
Thank you man of God
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 2 ай бұрын
inu a busa awa akulankhula chilungamo...MCP HAS brought misery in this country.and we are tired of mbuzi zimenezi
@gabrielmulowe8481
@gabrielmulowe8481 3 ай бұрын
Anthu Ngati awa ndi amene timawacuna
@victormasambuka8366
@victormasambuka8366 3 ай бұрын
Mu church mumakhala anthu azipani zasiyasyana sibwino kukamba za ndale mufzagawanittsa church as a pastor keep your opinion to yourself
@EmanuelMuotcha
@EmanuelMuotcha 2 ай бұрын
zoona father imani pachilungamo zikoli silili bwino anthu akubvutika+++
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 3 ай бұрын
Well said......👏👏👏👏👏👏👏👏
@paulbanda9638
@paulbanda9638 3 ай бұрын
Patakhala kuvota mau anu ndavotera kale,u r a good preacher
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 3 ай бұрын
Takumvani Abusa
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 3 ай бұрын
Good speech ❤❤❤❤
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 ай бұрын
Zochezatu😂😂😂😂😂 chilungamo
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 3 ай бұрын
Good advice thanks
@beakab2378
@beakab2378 3 ай бұрын
Well said
@AchinaKellz
@AchinaKellz 3 ай бұрын
Kukhala ngati kachilungamo
@KennethMchenga-j9c
@KennethMchenga-j9c 3 ай бұрын
Very true man of God
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 3 ай бұрын
Zamphanvu 🙏
@MarcosDjussa
@MarcosDjussa 3 ай бұрын
Mumakwanila fr 😂😂
@NdalamaCharse
@NdalamaCharse 3 ай бұрын
🙏🙏🙏🙏
@EdsonKamwendo
@EdsonKamwendo 3 ай бұрын
Mbambande Father
@RonicSouza-sk5ux
@RonicSouza-sk5ux 3 ай бұрын
Mau
@HedgensChisale
@HedgensChisale 3 ай бұрын
Ine ndinauza koma sakuva
@ConradccjSokoSoko
@ConradccjSokoSoko 3 ай бұрын
Sizocheza
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 3 ай бұрын
Alomwe awa tazilarikilani za ufumu wa Mulungu
@PeterBendeka
@PeterBendeka 2 ай бұрын
Akanene kumene atikwana amenewa
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 3 ай бұрын
Uyu ndiwabodza zambia nayo ili pamavuto azachuma munthu wa mulunguyu ndiwabodza kwambiri
@LamekiSamson
@LamekiSamson 3 ай бұрын
Wabodxa ndi iweyo
@AliJack-e6r
@AliJack-e6r 3 ай бұрын
Akumanganitu
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 3 ай бұрын
Dont fear everything akulu
@Patricia_Chisankha
@Patricia_Chisankha 3 ай бұрын
Unenesko uli papa
@JosephAMoses-ne8ji
@JosephAMoses-ne8ji 3 ай бұрын
It is very true that they have failed
@ConradccjSokoSoko
@ConradccjSokoSoko 3 ай бұрын
Iweso ukulalika zopusa, economics yakuti unaphunzira iwe, you do not compare zinthu zosiyana,, Mozambique ukuchita compare ndi Malawi, kapena Tanzania .... Just chinthu chimodzi like DOOKO,LA PA NYANJA ..... what it earns cannot compare ndi Malawi.Ukawauzenso nawe omwe akutumawo.
@marryphili5419
@marryphili5419 3 ай бұрын
Ngati ndiwe wa MCP wuzipase wulemu amalawi tilipa moto sitimasekesekerere ndi mbamva zimenezi
@ClementinaKapanga
@ClementinaKapanga 3 ай бұрын
Ndiwe opusa kwambiri ndi MCP yakoyo
@simeonbanda4240
@simeonbanda4240 3 ай бұрын
Umva pheni wa MCP ulendo uno
@johnchrispine3949
@johnchrispine3949 3 ай бұрын
Point ndiyonena kuti, zinthu zochepa zomwe tili nazo tizigwirisa ntchito bwino.
@MarvGerald
@MarvGerald 3 ай бұрын
Bg amenewo ndiye mau amphav zinthuzi zimafunika kuganiza mozama tisanasankhe otilamulira
@HarryKandani
@HarryKandani 3 ай бұрын
Anthu oipa inu ndi inu nomwe munali pastogolo kulemba ma kalata kuuza anthu kuti avotele agule wa
@KENETHMAJASA-ud5ee
@KENETHMAJASA-ud5ee 3 ай бұрын
Strong man of God
@DalitsoDjimo
@DalitsoDjimo 3 ай бұрын
Simudayankhule bwino bispo. Munthu wamulungu sanayenera kutero
@BrightZionga
@BrightZionga 3 ай бұрын
Inuyo ndinu munthu wandani malume
@JamesMalango
@JamesMalango 3 ай бұрын
Ndiponso achepesanso mauwo
@ConradccjSokoSoko
@ConradccjSokoSoko 3 ай бұрын
Osati zocheza
@RaheemMogoya
@RaheemMogoya 3 ай бұрын
Ameen Ameen tikuvutika abale mulungu atikhululukile achakwela chonde mwachose ndithu
@ChisomoNthukwa
@ChisomoNthukwa 3 ай бұрын
Opusa ameneyi zikugwilizana bwanji ndiulaliki
@YOMALO.
@YOMALO. 3 ай бұрын
This is a proof that MCP will reign again
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 2 ай бұрын
MCP NDICHIPANI CHAMA KAPE
@YOMALO.
@YOMALO. 2 ай бұрын
@@PrinceKachimanga really?
@MosesLeckson
@MosesLeckson 3 ай бұрын
Zoona zake
IMFA YA CHILIMA ENA AKUDYERERA - COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM.
27:43
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 4,9 М.
GIANT Gummy Worm Pt.6 #shorts
00:46
Mr DegrEE
Рет қаралды 105 МЛН
NKHANI YADZIDZIDZI - COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM
19:11
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 10 М.
EVANCE MELEKA - ZONSE TAONA - KWAYAKA MOTO
6:07
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 10 М.
COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - 30/09/2024 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
31:06
Keir Starmer's first speech as prime minister in full
7:05
Guardian News
Рет қаралды 371 М.
7 Signs That Someone Dislikes You and is Hiding it | STOIC PHILOSOPHY
27:50
Lilongwe SKC Candlelight - Fredo's speech [14th June 2024]
13:49
Ditaba tsa Sesotho l 02 October 2024
21:47
SABC Ditaba
Рет қаралды 968