NAMIWA KWAVUTILATU UKU

  Рет қаралды 9,179

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 29
@henryphiri6100
@henryphiri6100 2 ай бұрын
Osadandaula mzimu wa Saulos ndi anthu ena onse aja avutika nao ndipo akusowa nao mtendere.
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi Ай бұрын
Ziwembu zonsezi akunza ndi iyeyo mr chikangawa chakwera, Ndiye asanamizidwe? Palibe zonamizidwa ma style onsewo anthu ndi amodzi amakochana amangidwe achakwera chifukwa ndi zitsiru zonse
@Medsonmzumara-r9x
@Medsonmzumara-r9x 2 ай бұрын
ayankhepo pamenepa
@FelixChikaondagama
@FelixChikaondagama Ай бұрын
Ine ndizikhala chete kuvera koma chondechonde Mr chikangawa ayankhepo mzimu wa Chilima ukhale ndi anamiwa
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 ай бұрын
That stupid army general must resign for such incopetence
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 2 ай бұрын
Comrade Chakwera Manganya Kunkuyu Namajekete Varentino phili Wayezeka amenewo ndi amene anapha athu onse 9 aja ndiye Comrade chakwera ndi muthu oyipa kwambili chimene angapange apa chakwera ndi team yake angopha tonse amalawi kuti chipani chake chakuphacho asare nasho kuti asamapezeke muthu omususa
@EmmanuelWhite-h7e
@EmmanuelWhite-h7e Ай бұрын
Mpaka tower inathimitsidwaso?
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi Ай бұрын
Kaya anamiwa asauka chifukwa choti anachoka kunyumba yaboma koma khani ili ampa monga Malawi wokhuzudwa ndizoona akulakhula iwo maumboni ose amapelekedwa anali aboza tiyeni tizisata khani abale adzanga
@KondaniPhiri
@KondaniPhiri Ай бұрын
Chonde abugwe inu. Tinthandizeni. Kuliphula dzikoli pa moto pls pls
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali Ай бұрын
Anamiwa aboma atatitabwereran kut muzayambilenso ntchito ku state house mungavomere? Ndikuona ngat maluzi akupweteken
@mayamikondalama4796
@mayamikondalama4796 2 ай бұрын
ndipo enafe ndi ndani? ngati wokhala ndi bodygadi anapita
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi Ай бұрын
Ananthimisa tawa cholinga chake chinali chotani anamutuma anali ndani kwaine otuma ndi chikangawa asatiophyeze
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
😢😢 chakwela machende ako chakwela maphwala akenso nonse a mcp panyini pamanu
@LucyKay-i1h
@LucyKay-i1h 2 ай бұрын
Strong man namiwa
@christophergibson72
@christophergibson72 Ай бұрын
Olo mutani anthuwo Kodi adzuka?
@ManMen-kp2ze
@ManMen-kp2ze 2 ай бұрын
Mr. Namiwa u r so brave, we r with u, truth must prevail , not all over 20 million Malawians can be fools, if president Chakwera is not involved on this incident, a number of civil servants should have been fired, and another question , what was the president doing in Germany before the report released
@JumbeNalinali
@JumbeNalinali 2 ай бұрын
Pangani lanu lipoti
@aubreygambatula2002
@aubreygambatula2002 2 ай бұрын
Ndili nanu ,,, ndipo tili limodzi
@JosephChikabadwa
@JosephChikabadwa 2 ай бұрын
The first person to be interviewed on the scene said he called someone from OPC, Chikangawa Police Station and Other relevant authorities informing them of the plane crush. Should we say all these people he called never made an effort to reach the responsible government which could react with urgency ? Why did they decide to ignore this crucial and life saving information ? this leaves us no choice but to speculate that Indeed MCP had a hand in SKC's death and the other Eight individuals .it is up to MCP and it's leadership to prove us wrong (Malawians)
@TisungeChirwa-b1w
@TisungeChirwa-b1w 2 ай бұрын
Ndizoona zimene mukufotokoza
@EmmanuelWhite-h7e
@EmmanuelWhite-h7e Ай бұрын
Eee koma yaaa
@BrightNgulube-h4w
@BrightNgulube-h4w 2 ай бұрын
Tonse tilindi mafunso ochuluka osowa mayankho
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 ай бұрын
Alonda apatower anayimba phone to their bosses same time
@SandraMoses-y4l
@SandraMoses-y4l 2 ай бұрын
Tili limodzi ndithu Koma MCP iiii
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 2 ай бұрын
Postmoterm basi ..
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 2 ай бұрын
Amalawi 🤬
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi Ай бұрын
Imedi wa police Achiwaya Sadiq miyah Achilima Amayi shanil Ndi ena 7 Ndi ziwembu zokonza Tambala wakuda biiiiiii Achi kangawa. Angopha mmodzi mmodzi Mpaka titha psithi
@PeterChilombo-ou2cd
@PeterChilombo-ou2cd Ай бұрын
tikthadi psiti achoke chakwela ndiwakupha
@PeterChilombo-ou2cd
@PeterChilombo-ou2cd Ай бұрын
acoke chakwela anapha chilima
BON KALINDO THE DC 04/11/2024.
12:46
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 15 М.
THE KARONGA BOYS - MEC IKUONETSERATU KUTI ILI MBALI YA MCP
14:22
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 1,3 М.
Yay, My Dad Is a Vending Machine! 🛍️😆 #funny #prank #comedy
00:17
I tricked MrBeast into giving me his channel
00:58
Jesser
Рет қаралды 27 МЛН
Wait… Maxim, did you just eat 8 BURGERS?!🍔😳| Free Fire Official
00:13
Garena Free Fire Global
Рет қаралды 7 МЛН
兔子姐姐最终逃走了吗?#小丑#兔子警官#家庭
00:58
小蚂蚁和小宇宙
Рет қаралды 16 МЛН
LIMPOPO FM - MA PRISON WARDENS AKUYUZIDWA NDIMA POLITICIANS
22:55
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 9 М.
MWAZIMVA NKHANI IZI?  TINGOLIMBA MTIMA AMALAWI
36:21
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 5 М.
COMRADE NTANYIWA - BREAKING NEWS MADZURO ANO
11:09
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 11 М.
SILVESTER NAMIWA AJOINA NAWO PAMA DEMOSTRATIONS AMA LAWYER
52:02
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 9 М.
Nog veel overlast door regen in Spanje: 'Overal modder'
2:39
NOS Jeugdjournaal
Рет қаралды 57 М.
Yay, My Dad Is a Vending Machine! 🛍️😆 #funny #prank #comedy
00:17